When the days were good, Namadingo sang a praise song for South African based flamboyant Prophet Shepherd Bushiri. Now he has decided to throw subliminal jabs at the man of God whose ministry is under fire in South Africa.
In his new release Dziko liri pamoto set to be featured in his to-be launched album, Namadingo has laughed off modern Prophets accusing them of fooling people.
In the first verse of the song, Namadingo is generalising his accusations. However in the second verse he throws pointers at Bushiri.
“Mtsogoleri Yesu samalimbana ndi anthu, sali ngati chipani cha ndale, safuna ma vote Yesu,” sings Namadingo.
His message might in a way be referred to Bushiri whom the ruling Democratic Progressive Party has accused of working with politicians and operating as a politician.
When Namadingo was contacted to comment on the song, he refused.
Kodi simulemba kuti show inabeba?
Eti adha, fans yoipa iyi.
Can you leave this little child alone…Who is bushiri?
kulira kwamphawi.who is namadingo? siofana ndiwosetsa wa bushiri.ingopemphani dolazo omadingo6
Thank major 1 I see comments on ur page
Nkhani ndi kwacha yatengamalo ichinchiyambi chabe yatsala ndi kolasi lets wait for.
How much is chips only when you brought your chicken,?
All i know is my Major will remain a great divine encyclopedia. He is a wonderful man of God….God is always happy with his Ministry…May God Almighty continue to bless Major 1…Give him long life so that multitudes would b saved in Jesus name….Satana Malawi 24 wandilira
Eni ake aliphe mkuvutika ndinu
Wow
inuyo a news ndi amene muli ndi vuto munthu sanatchule munthu munyimboyi komanso olo atakhala zoti bushiriyo watchulidwamo iyeyo ndindani kuti asanenedwe malingana ndimbiri takhala tikuzimva kuchokera ku south Africa zoti akumalipiritsa anthu ndalama kutingoti amuone ndi prophet wantundu wanji olipirisa anthu ndalama?olo atamamunena ife tilibe nazo ntchito za bushiri zatikwana omukhulupilira azimukhulupirira ndizisankho zawo mxiiie….bushiri this bushiri that who is he after all nosense
Takhala tikumudziwa Namabingo kwanthawi yaitali kuti ndi munthu yemwe ali woyimba wabwino ndipo amatumikiraso ku ECG bwinolomwe. Chomwe angasankhe iyeyo chikhale chomwecho kaya kupitiriza kutumikira olo ayi, sakakamiza. Ena asapezerepo mwayi apa woti adzikamba zonyoza, kutukwana ayi chifukwa ameneyo ndi satana otukwanawe. Bwanji osatakwana azibusa akwanu komwe mumapemphera ngatidi mumapemphera? Mumapereka dzimaulemu kwa a zibusa anu, ma shehe anu ndipo palibe yemwe amaatukwana koma maso kwa Bushiri adakulakwirani chiyani? Angapange zabwino kuthandiza anthu ovutika ndi chuma chambiri koma inu kopanda manyazi kutaya nthawi nkumanyoza, sizikutengerani mtunda. M’malo moti mudikire maungu aphike anthu mudye ndi kuyamika nazo Mulungu inu koma kuvutika ndi kutukwana pano.Mtundu wanji opanda manyazi. Adakulembani ntchito ndi ndani kapena? Bwino nazo mungadzavulale nazo izi. Aneneri a Mulungu ndi owoopsya.
Malawi 24 nda news paper yolemba and samalani nawo ngoyambanitsa and iwowa akanachita manyazi coz prophert bushiri ali pheee zake zikuyenda and ndimadabwa kuti phhindu lanu ndichiyani kuti mugulitse kwambiri.choti muziwe nditumiki wamulungu and woyimbayo sizinkukhuza ayi,asatana inu.
What l said to all Malawian people ,believe ur self,cos mulungu ndiwina aliyese better ngati umakhulupilira
Go deeper # Namadingo
Kkkkkkkk ndikungomva kukoma ndikamawerenga ma comments anuwa guys, tiye nawoni
Olo atakhala wanena Bushiri ndiye???? Munthu aliyense amanenedwa nkumene!!!! Ife anthu anatinena nkutopa iyeyo ndi Golide???? Bwanji Chaponda tikumunena! Isiiii
Kkkk
Please achibale msiyeni #Patience ndimunthu odekha pazandale zanu zomwe mukupangazo, musamputile mkhondo ndiluso lake lomwe adampasa Mulungu… if you are trying to insult Bushili do it by your self and not somebody’s behind
Foolish malawi 24 journalists….i thought he mentioned bushiri….yet u say u suggest he mentioned him….we want facts not your opinions
Uku ndiye kuputa imfa,waziputa limbanazo.
ndine mbuli pa nkhaniyi
Mwangofuna Bushiri ndikumuipitsa namadingo asiyeni pangan zandale zamulungu zisiyeni , zakayesala zipite kwa keyesala ,zimulungu zipite kwa mulungu
zisiyeni zikulire limodzi God himself he will separate tiligu ndi nasongole……
kkkkkkkk
leaave papa alone please!
Kkkkk kkkkkk nkhani yake kufuna kutola chikwama? koma anthu muli ndimavuto ndithu, mwayamba kutama nkhono wanyama kusiya MULUNGU? Ndakutsika aise ndigwilizane ndaliyense amene akunena kuti awa ndimathero ako amaimbidwe. ndingoyamika MULUNGU kuti akumationetsela maso mphenya iwe anzako akumaitsika iwe wati ukwere? kkkkkkkk
Ok.lets wait and see the contents of the song.after akatulusa abum.
Inuyo a news ndinumukunama monthly sanachule Bushiri kungoti simugona naye Tulo bushiri ndipo mukuchedwa si Size yanu pangani zanu ndi Dpp mungoba chimanga shame.
Zayambanatu….
Do not touch my annointed one
Nonsense leave bushiri alone major 1 iyeeeee
Ndekuti zomwe waimbazo ndizomwe Bushiri amachita?? How did u know that he talking about profit bushiri…oyipa athawa ekhadi hetiniii
He is stupid man why not to be with music poor man
whether Bushiri wants to join politics or not its within his rights and freedom. why panic. long ago church leaders were running governments as well, maybe for the better. look at ur messy bullshit u r having now
Who is Namadingo?
Nde wapindula chaaa? Za ziii
Malawi 24, plz improve on ur writing skills. The title of the story sikugwirizana ndi zomwe mwalemba m’kati. The song is very general. Ma article okhuza analyis ya nyimbo perekani kwa yemwe anaphunzirako literature plz.
Namadingo amatha …ndipo show you ndili konko…imbani zanu mutchule chaponda
Misleading headline. What a waste.
nyimbo imakhala ndmatanthauzo awili lachindunji nd lopanda chindunji nde amene mukukana inu nanunso muimvere bwinobwino then ikupasan matanthauzo osiyana
Malawi 24 takambani za Chaponda mwina mukadakhala opatsidwa ulemu.koma iyi ya anamadingo ayi ngati mwayamba kusatsa malonda yavuta zomwe timaziwa ndizakuti muli ndimavuto andalama.koma kumbari ya Bushiri ena awomboledwa – kuchilitsidwa- kutsitsimuka ku ifa- pa anthu100 amalawi 4% ambiwo amakhala azathu amaiko akunja inuyo mumapempha ndalama kusiya olumala,ndi odwala mukawona chopeleka chija eeeee mukadakhala inu tidakava kuti ku ofesi kwanu kwayaka moyo.ife ma DvD anamadingo timawaziwa musakokere agule ndi anthu ochepa 10,000 osakwana
Zamacheeeeeeeeeeeza!
Mamvedwe a nyimbo kusiyana kkk
Last days now are apon us am not wondering
This is bullshit shit leave bushir alone
q
U Malawi 24 guys zabodza timakana mwamva, lembani zina pls.Muzakhala okondwa akadana eti? Mvetselani nyimboyo kachikena. “Might in a way be referred”, kungoganizila basi!!!
let spread the gospel namadingo tel them pofuna kulakhula tilakhure iwe ukunena za BUSHIRI usova
Mmmm…..the world will neva like the truth. Namadingo walakwa pati,,,mukudana ndi choona and let me remind you that even jesus christ suffered coz of the general truth you hate. Namadingo nawe, unangofulumiza kutulutsa nyimboyi timafuna nafe amve motto buuu…. no man is above man and wait for the word of the almighty and not this village boy…. za chuma zipite uko…..
He never mentioned bushiri in the song and even if he did i would an am siding up with him .. Paja ndalama zikayankhula chilungamo chimakhala chete,,,,many hav been blinded by money but judgement day awaits us all. Be carefull
Ineso ndiiveleko bro 0735681080
I Like Every Man Who Preach The Word Of Life And Promote God’s Kingdom. I Like Bushiri.
kodi Bushiri mmamuika pampando wanji? akangoimba nyimbo munthu yokamba zomwe zikubwera mmutu mwake nthawi yomweyo mwayamba kufanizira zochita za Bushiri ndi nyimboyo why??? Bushiri mmamutenga Mulungu wanu?? kapena Profeti wanu?? kapena Satana oyambirira yemwe akuchita ufumu wake ndi zinthu zamDzikoli???
:0%
Bwanji Gwaladi Sakucomenta?
ine ndayinvera….
Walemba izi..its anyc s0ng..sanatchule munthu..or kuyakhura chining’a AYI!!!!….akungofuna kutisokomeza..komans0 kupeleka bad pic..kwa patience
Th0se u ddnt listern the s0ng yet..Can Comment…..
A Namadingo pa Bushiri sangamake wachepa, kupemphera kwake kuti? Hahahahahaha! Zomvetsa chisoni kwambiri.
Asiya kupangana inspire litinso kodi? Chilipo China chachikulu asemphana amenewo. Better to blast the devil than fellow man.
hey boy if your tired with singing you could have just stop singing rather offendind men of GOD this might lead to your downfollw caught this
Musiye akuchedwa
Philippe Fabiano koma ndie akuchedwatu
Bushiri is NO man of God. Just because someone claims to be a preacher or a man of God, doesn’t mean they are. “Ye shall know them by their fruits” he is a fraud, he preaches a false gospel and will lead people to HELL while extorting their money. Salvation is by faith alone 100% in Jesus Christ, not by following a preacher or paying money.
Amene zikumunyansa zimene Namadingo waimba akakolope lake malawi chifukwa iye sadaimbe kapena kutchula munthu koma waimba za ulosi wa masiku otsiriza zimene aneneri adalosera kale-kale
Can someone has a song, send me on 0995548266
This Namadingo is a busterd…th’s is why is called Namadingo.flee to hell with your jelousy
Panyo panu nonse mbuzi mumtengo
Nyimbo ndyabwinobwino iyi sanatchulemo munthu muli chilungamo chokhachokha
taona kwa iye otama munthu ine wanga ndi yesu basi sanandikhumudwisepo
That is the problem of being a Malawian. We are good at judging others. Why most of the Malawian musicians, amakonda nyimbo zamaboza?
Mchitibwe umenewu tizingosaukirabe. Zaka 60 tiri pa ufulu wozilamulira tokha koma kumalimabe ndi Khasu. A Malawi azanga masiku olimbana ndi anthu anapita kale. Zintchito zathu ziziwonetsa kuti ndifedi a Khristu kapena Msilam owopa MULUNGU.
Chiwerengero cha anthu opalamula omwe akudikilira kukumana ndi ifa ya kachete chete chafika pa 2, Joseph Mkasa ndi Namadingo koma Amalawi tili mmaso kuti oyimba apalamulawa akhalebe ndi moyo, asafe mwa nkhaza ngati muja anapotokoredwa khonsi ngati Matafale muja,
he is trying his luck to get fame by bushiri,tht is one of the reasons he relocated to RSA atleast be proud of your country man
Mmmmm amalawi kukonda mabodza inu iiii
Bushiri, can u pliz set his deathday
ilikutiko nyimboyo??
A guys zinatikonda izi ndimayesa zinthuk eeees better yachaponda ikubeba pa ZBS bushiri man of God
pleaz share me that song on WhatsApp 0995777843
Namadingo zangomvuta ngati akufuna ndalama angopempha,
Nyimbo za uzimu sizankuluwiko.
Neither name nor signtune of any Man of God is featured in the track…..! People where are you getting this? Malawi you said to be ndiwe Mtima wa Africa.
Namadingo zangomvuta ngati akufuna ndalama angopempha,
Nyimbo za uzimu sizankuluwiko.
Zausilu
Team Bushiri woyeee
Mwina ndiimvetsere yonse nyimbo imeneyi koma maline omwe mwaikapa sakugwirizana nzomwe mkukuwa apa ‘yi. Poti watchula chipani basi??
Leave men of God alone. You are only provoking the wrath of God.
Our Lord is in the better position to judge,so leave it to him.
Namadingo zangomvuta ngati akufuna ndalama angopempha,
Nyimbo za uzimu sizankuluwiko.
Judge not according to the appearance, but judge righteous judgment. John 7:24
Read the Bible, God TELLS us TO judge. Matthew 7:1-5 speaks against self-righteous (hypocritical) judgment but in v5 it still tells us to judge, and in 7:16-20 2x it tells us to judge, in Matthew 23:23 Jesus was furious with the Pharisees because they did not judge.
Thus typical Malawian culture.Umphawi wathu wayamba kugenda.Afuna apusitse anthu.Umenewo nde uchapondawo
Namadingo zangomvuta ngati akufuna ndalama angopempha,
Nyimbo za uzimu sizankuluwiko.
mmmmm musanamizepo anthu pano he is not attacking anyone
Namadingo zangomvuta ngati akufuna ndalama angopempha,
Nyimbo za uzimu sizankuluwiko.
Every tree is known by its fruits,this is an old saying found even in the Bible but we refuse its wonderful implication in todays world kkkkk “anthu anga akufa chifukwa chosadziwa!” I rest my case,the name of Jesus bless you all!
this is a rubbish prophet lia full of stupidity ine ndimaona zonse za boza za bushiri munthu wabwino sangakhulupile uyu ayi ndi munthu waboza ngati mumakhulupira uyu mumataya nthawi zedi tumizani whatsapp ndikuoneseni zina. za boza zomwe akupanga
+265882723240 tumizani
+27734153035 tiwone
Ndizoona zomwe ukunenazo munthu odwala kupita kwaiye akuti ipeleke R7000 uchile koma zachisoni munthu sakumachilaso posachedwapa takaika nzimayi amadwala khansa aBushill matama kkkkkkkkk pls +27742109147
+27742112286
You sound bitter & I can sense some jealousy from you people
+265884001534 tizi3re
0992217779
+27731236678 ine ndikufuna kuona zonamazo
0999 358 643
Ndione nawo
0999231396 tionetsetse thou am not either for or against
0884449786 tione basi
0882583724
0993616181
Please.
0888704304 panga zimenezo tione nao
0884601992 mama pangani zomwezo
0881337899 tione nawo
0027631978509
Inuyo a news wakuuzan kut akumuimba Bushiri???
You are insulting enmity
Namadingo zangomvuta ngati akufuna ndalama angopempha,
Nyimbo za uzimu sizankuluwiko.
Akupanga zake munthu n@ za #Bushiri leave #Namadingo alone….and mind ur own #business
keep it up patience!!! dont listen to fools who are blaming you of insulting bushirg for GOD’S sake u didnt mention anybody’s name this means its them insulting him in their interpretation,,,, umatha iweyo dont let rumours drag u down
He is a local boxer akulimbana ndi Major an int anatinal champion…. wachepa kwambili si size yake,
Sindimu3ra Bushiri wanuyo.
.
Sizikungwilizana olo atadana ndiyanthu palibe vuto, koma ngati aku opamulungu mulungu NDE njila
The problem we malawians hve z ngati unazolowela miseche ukangowona amzako akucheza pafupi ndiwe umangoganiza kuti akukunena ,2 ukazolowela kuba aliyese amene ungamulembe ganyu umamuganizilas zoti amakubela, so dnt judge, wajudge woludikila wozajudger wokha zisiyeni zikulile limodzi.
Kupusa
grace chinga blasted bushiri…..namadingo blasted bushiri…..
Umakwana
Naye waponya yake mivi yamoto mu nkhalango yowilila?
Kwagwanji ??mauka uka mkamfumbe nayo grace chinga….
Winaso ndi ameneyi kaya amaziona ngati ndani kaya after all samathaso kuimba galu ameneyi
okutha kuyimbanu imbani kuti tizasiyanise btwn u en patience osamatha mawu ngat kulibe mmawa pliz malawians
Mmmmmm apo nde mukunamatu amatha kuimba munthuyu
Atolankhani a mnyunba amenewa fools
ok
Zisandikhudze
Malawi is the land full of non precious rocks and its inhabitants most of them don’t know what they are saying but act as if they know,their freedom fighter fought off the white people just the same week they came to Malawi even before they had developed their country.most of them don’t work hard and if you do and get blessed to them you are a sinner or a witch or you are satanic.my people are so dumb that they comment on everything that they see on internet .their leaders are busy stealing while they suffer .yes they have freedom but its only for self suffering.musicians seek fame even if they were supposed to bring unity,they read only part of the bible and sing as if they know it all, the bible says its not for us to judge if you see that lam going astray Gods way pray for me not sing about me in one of your songs. You know what if we had gold ,diamond or even copper this country would have been at war too many dumb people acting like mr know it all
Namadingo zangomvuta ngati akufuna ndalama angopempha,
Nyimbo za uzimu sizankuluwiko.
KOMA YAAA
Mukapanda kulemba bodza zimumva bwino watchulamo bushiri mu nyimboyi,muli ndi moyo oti anthu azidana , nde muzipeza cholemba
Ndipo inu mmmmm can’t hear dzina la bushili umu mmmmm amalawi
Promise send me a song, ndiimvere 0995548266
I was diagnosed HIV positive in the year 2010 and Dr Abuu cured me with a herbal medicine I’m a living testimony today, if you are having any problem kindly email him on [email protected] or you can whatsapp his mobile number +2348066454364
Liar… witchcraft is evil!
The songs are not meant to insult other people but to heal the broken hearted, to heal or to entertain. Otherwise look for another profession.
Namadingo zangomvuta ngati akufuna ndalama angopempha,
Nyimbo za uzimu sizankuluwiko.
Hahahahahahaha! Masudi wayankha bwino kwambiri m’bale. Iyeyo akudzitenga wolungama kwambiri? A Malawi kumvetsa chisoni. Akuti iwowo ndiye anthu opemphera kwambiri omudziwa Mulungu kupotsa ena onse pa dziko lapansi. Mzawo akachita bwino zonena komanso nsanje thoo! shame…
PENAPAKE ANTHU KUMAVETSETSA NAMADINGO SANAIMBE NYIMBO YONYOZA MUNTHU WANU WA MULUNGUYU AKUTI ATAFUSA NAMADINGO WAKANA KUTI IYE SANAIMBE MUNTHU. MALAWI 24 ANGOGANIZILA KUTI NYIMBOYI WAMUIMBA BUSHIRI KWAINE MALAWI 24 YALAKWITSA PONAMIZA NTUNDU WA AMALAWI ZA NKHANI YABODZAI. INU AMALAWI 24 AKUUZANI NDANI KUTI NYIMBOI WAIMBA BUSHIRI PAMENE MWINI WAKE WAKANA? AMENE MUKUNYOZA MUNTHU WA MULUNGU WA NTHAWI YA PANSI PANO NDINU OSATI OIMBAYU MUSAMUIKE MAU MKAMWA
#Namadingo close us our eyes then praise in ur heart u ar gospel lie why u can mention someone in ur gospel song that’s not gospel song just praise devil bro no one is blind nowadays mr!!!
Namadingo zangomvuta ngati akufuna ndalama angopempha,
Nyimbo za uzimu sizankuluwiko.
ine nde Namadingo wanuyo sangandinamize, akudziwana ka amenewo…remember kt iyeyo sioyamba, angofuna kutipusitsa, tell him mimba yake, wachepa
Why?
Namadingo zangomvuta ngati akufuna ndalama angopempha,
Nyimbo za uzimu sizankuluwiko.
Touch not the annointed.
Namadingo zangomvuta ngati akufuna ndalama angopempha,
Nyimbo za uzimu sizankuluwiko.
Did he mention Bushiri in his song? Uku ndiye kuyikana mau mkamwa komanso kudanisa wanthu. Ma prophet ndi ambiri, ndipo ngakhale atakhala kuti akumunena Bushiri koma chifukwa choti sanamutchule dzina iwe ndiye ndani kuti ukaonjezele dzina la munthu mu nyimbo yakeyo?
Atola nkhani a pa Malawi eish!
i knw bushiri very well he z son of devil.
Namadingo zangomvuta ngati akufuna ndalama angopempha,
Nyimbo za uzimu sizankuluwiko.
Nyimbo yili bhobho heavy ndipo ndaifila komanso sanatchule dzina lamunthu
he has sent by DPp fools,to perform the song,just to decampain Bushiri”who doesn’t know?
Namadingo zangomvuta ngati akufuna ndalama angopempha,
Nyimbo za uzimu sizankuluwiko.
Kusowa zoimba basi musiyeni bushiri Watani Kodi
Kodi zomayimba anthu ena anthu amaganiza kuti ndiye nyimbo agulisa
There is a difference between attacking a person and speaking the truth. Unfortunately money is carrying more weight than the truth. Only few people nowadays speak the truth and refuse to be silenced with money.
Namadingo zangomvuta ngati akufuna ndalama angopempha,
Nyimbo za uzimu sizankuluwiko.
Yes o
Achedwa nazo zimenezo angopitiliza ntchito yotumikila poimba yomwe timamulemekeza nayo not judging others tonse ndife olephela pamaso pa mulungu
Mungofuna kuadanitsa anthu ngati patience watchula dzina
Big Up Namadingu
DO NOT JUDGE!! What someone is doing in this earth!! No one knows who is perfect’ ONLY GOD KNOWS!!
Count yourself first!! Then don’t point a finger at someone else!!
Namadingo zangomvuta ngati akufuna ndalama angopempha,
Nyimbo za uzimu sizankuluwiko.
One can not beat a dozen, Bushiri simunthu olimbana naye ungotaya nthawi yako mungoyitana manyazi pa nkhope yanu
Achitsiru a Namadingo,mwadya idya ndalama za Bushiri pano mukuti chani,za ziii.why can’t you just concentrate on your singing career other than kulimbana ndi munthu.inu mumazitenga a ngwiro kapena kuti oyela mtima.kumbukilani kuweluza sikwanu koma kwa Namalenga.
Zonse ndi zabwino.ambiri tikulephera kugwiritsa ntchito zinthuzi ndipo zimaoneka ngati zoipa.
#Namadingo mulomuwuuuuu! mulomowuuuuuu! mulomowuuuuu….mulomo uzakuphesa!
Kkkkkkkkk mulhelhe animamvuhelhelha vatlhi vanyanja oyo
kumeneko timati kuitcheranitsa nkhondo#malawi24#
kkkkkkkkkk aphareke ekhanando
When you r on top you become a topic and when you r a head you become a headline,why kumalimbana ndiazitumike for what kkkkkkkk every pastor in this country whether you u r of my church or not l love u so much and may good Lord increase his anointing upon you up to the maxmum in jesus name
Namadingo zangomvuta ngati akufuna ndalama angopempha,
Nyimbo za uzimu sizankuluwiko.
mmm
The truth has set u free. Jesus Christ is mighty
Namadingo zangomvuta ngati akufuna ndalama angopempha,
Nyimbo za uzimu sizankuluwiko.
I wonder if namadingo has mentioned Bushirs name here anyway ,what God has blessed no man can curse and when God calls one to be His Servant no any approval is needed from any man,man never wishes good things to his fellow man,mmmmmm man !!
Namadingo zangomvuta ngati akufuna ndalama angopempha,
Nyimbo za uzimu sizankuluwiko.
These Are Wat They Call Ironic Songs.No Need To Metion Some One’s Name But Similarise With His Or Ha Characters.
Bushiri is not of God, he is of Satan. If there is one thing I would have the brothers and sisters of Africa learn, it is this… just because someone SAYS they are a Christian, or SAYS they are a preacher of God, DOES NOT mean they really are. “Ye shall know them by their fruits” – first thing ever, check if they preach the right Gospel – salvation by faith ALONE in Jesus Christ just like in Romans 10:8-13. Not “repent of your sins to be saved” or “baptise to be saved” or “there must be a change in your life afterwards”. Faith alone, not of works. Ephesians 2:8-9 Romans 4:5. Then make sure they use a real Bible, in English that is the KJV (old one, not NKJV) and there’s a long study about that but you can see the free movie New World Order Bible Versions on Youtube to explain that.
Fake miracles/healng – fake preacher. Preaching only positive things, clearly a fake (Isaiah 30:10-11, 2 Timothy 4:2-5) – the best sermons are those which challenge you and even offend you. Preaching ecumenism, fake (John 14:6).
People, the Bible says “study to shew thyself approved”. “prove all things” (prove = test). Never just watch a man say “I’m a man of God” and believe it, TEST IT via the BIBLE. If there is a disagreement, the Bible is always right.
Waganiza bwanji ameneyu??
Guys pipo u just say bushiri this that please I know him A to Z if u don’t know him don’t talk about him fuck bushiri and I said son of a devil bushiri
I agree with u n I’m behind yo back
TO ME ITS 100% RIGTHT
U guyz i like ur comments n i agree wth u
Namadingo zangomvuta ngati akufuna ndalama angopempha,
Nyimbo za uzimu sizankuluwiko.
You sound bitter & I can sense some jealousy from you people
You sound bitter & I can sense some jealousy from you people
You sound bitter & I can sense some jealousy from you people
You sound bitter & I can sense some jealousy from you people
You sound bitter & I can sense some jealousy from you people
You sound bitter & I can sense some jealousy from you people
You sound bitter & I can sense some jealousy from you people
Sisqo
Yeah man
Ndiye Akabwenze Galimoto Akuyenderaro
Ndiye Akabwenze Galimoto Akuyenderaro
Fucking
Namadingo ndi nkasa zao ndi zimodzi.gospel yamasiku ano akumaimbira munthu osat mulungu ai.Koma anthu amene timawelenga baibulo tivomelezane limanena kut anthu azakhala okonda ndalama siizi nanga.Abale mwa ambuye tieni tingotsata choona chomwe tikuchiziwa.Amen
https://www.facebook.com/drchaponda/
Mwayamba kuyimba zawanthu. Zopusa. Lalikani uthenga wambuye
God is the best judge only.Lets let Him judge us.
Namadingo zangomvuta ngati akufuna ndalama angopempha,
Nyimbo za uzimu sizankuluwiko.
Ukayimbanso udzasowa!
Fightings can not solve the problems rather we better pray for each other.
Namadingo zangomvuta ngati akufuna ndalama angopempha,
Nyimbo za uzimu sizankuluwiko.
End of Namadingo’s Journey
Namadingo zangomvuta ngati akufuna ndalama angopempha,
Nyimbo za uzimu sizankuluwiko.
Aneneri Onyenga Tiye Nawo Namadingo Osaopa Stand 4 De Truth
Iwe ndiwe omphweteketsa eti? Grace chinga alikuti?
Kaliba Kufera Chilungamo Ndikukhala Ndi Moyo Dziko La Chinyengo Cha Nzeru Ndi Chani
Kulimbana Ndi munthu ndikutaya nthawi osamangiyimba za MULUNGU zo bwanji?
I hop natin will happen to him cuz am still cryin for Grace chinga
Namadingo zangomvuta ngati akufuna ndalama angopempha,
Nyimbo za uzimu sizankuluwiko.
When the days were good, Namadingo sang a praise song for South African based flamboyant Prophet Shepherd Bushiri. Now he has decided to throw subliminal jabs at the man of God whose ministry is under fire in South Africa. Namadingo blasts Bushiri In his new release Dziko liri pamoto set to be featured in his to-be launched album, Namadingo has laughed off modern Prophets accusing them of fooling people. In the first verse of the song, Namadingo is generalising his accusations. However in the second verse he throws pointers at Bushiri. “Mtsogoleri Yesu samalimbana ndi anthu, sali ngati chipani cha ndale, safuna ma vote Yesu,” sings Namadingo. His message might in a way be referred to Bushiri whom the ruling Democratic Progressive Party has accused of working with politicians and operating as a politician. When Namadingo was contacted to comment on the song, he refused.
Namadingo zangomvuta ngati akufuna ndalama angopempha,
Nyimbo za uzimu sizankuluwiko.
Can you send me a song please on 0995548266
Mr Masudi..listerni the song 1st….
koma walemba izi..mmmmmm
Nyimbo yabhoo..ndipo sanathule munthu….
even chining’a mayaz
Kodi anthu timamva Bwanji??? iiiii
Share pliz 0882483587
Ndigawireniko abale +27784394121
0027739554962 share
+258842160637 share
Titumizireni ngati muli nayo please +27604811488
Ine ndayimvetsera koma siikukamba izi zikukambidwa APA
08844466660
0884466660
0996430080 pliz ndiimvereko
ndigaireni +260976420700
Tamawululanani kumeneko iyaah!
mumupanga attack paka liti Bushiriyu tiyeni timukonde munthuyu , SA ndidziko lotukuka ndikale koma anthu amamukonda kuposa ife a Malawi ndiye chifukwa chake akuthandiza chuma cha SA kupita patsogolo m’malo motukula dziko lake la MALAWI.
at atnve kut tlemba zotan kkkk, malawi 25 mukufuna ttukwane bushri or namadngo? kuyesa zda uku.oymba amaymba koma kumafunika kunvetsesaaa komaso olalika amalalika kumafunka kunvetsesa ngat suvetsesa olakwa umakhala iwe.kufusa kwabwnoso
whoever is doing what in this world, we have Christ the perfect judge..
Namadingo zangomvuta ngati akufuna ndalama angopempha,
Nyimbo za uzimu sizankuluwiko.
He can blast him on songs and internet but Bushiri is not anointed by songs or internet . this can only be God . power
Namadingo zangomvuta ngati akufuna ndalama angopempha,
Nyimbo za uzimu sizankuluwiko.
He Said Wat He Knows. He Was Close 2 Him And I Think He Know Him Better. I Wonder What Gospel Is Frm Yo Man Of God , I Only C Miracles. Musatinamize Nafe Bible Timalitsata ,the Gospel Is About Repentance Not Good For Nothng Miracles. Know Wonder On The Final D We Wil C Pple Going Tu Hell Coz They Trusted Men More Than God’s Words. Yeshua Once Said B Happy Coz Yo Names R Written In Book Of Life N Not Coz U Perfom Miracles Or Demonds Obey U. C U On D Day Of Seperation, Btwn( Wheat& Weed).
True true he knows bushiri beta
Namadingo zangomvuta ngati akufuna ndalama angopempha,
Nyimbo za uzimu sizankuluwiko.
Mmmm you 24 i dont think namadingo can do such thing to Bushiri following his interviz with times tv he said Bushiri is more than a friend to him ngat wayimbad then something z happening lets wat and c.
Namadingo zangomvuta ngati akufuna ndalama angopempha,
Nyimbo za uzimu sizankuluwiko.
I thought u praised him in “sindinjenjemera”? Mukudziwana
Namadingo zangomvuta ngati akufuna ndalama angopempha,
Nyimbo za uzimu sizankuluwiko.
Big up patience expose them
Namadingo zangomvuta ngati akufuna ndalama angopempha,
Nyimbo za uzimu sizankuluwiko.
Ankaoneka awa zoyimba zawo zija kuti sia gospel….lero siizi..?
A Namadingo nimathero akuyimba amenewo. Mesa mukulalika uthenga wa Mulungu. Mwayamba ndale eti. Zimvutani achimwenetu. Bushiri wali ndi funs ndiye mudana ndi ambiri.
Sizikugwirizana
mwayamba kupembedza bushiri mwasiya mulungu ,..tsoka pa inu ndithu
Is man of God a ghost or a human being??
Man concentrate pa nyimbo zako bax,ufoira2 kumene walowera ixe!
nde tgailen nyimboyo
Namadingo Musamayimbe Zoti Musangalatse Kagulu Kena Ka Wanthu mahule Ndi Mbala ZOse Zili Mmalawi Muno Basi Kukayimba Za Iye Why Not #Chaponda? Naweso Ndiwe #Satana!
Izi Zalowaso Chaina? M’nyimbomo Akuti Chani Za Bushiri?
Namadingo akuyenera kutelo olo muli inuyo gyz kupeka nyimbo kwayamba kukuvutani zakutherani next step yanu munyimbo mungatani?
only major 1 can do that not all the minor 1
keep it namadinga ,satanayi mwina asiye kupha anthu
Anapha ndani? Mukamaona matsoka musamadabwe. If you hate him, keep it in ur heart than corrupt other peoples minds. Unapha anthu ndi iweyo….no wonder ukulimbana ndi munthu wosamdziwa.
Very true
Anamupha ndani bro
Grace chinga
only major 1 can do that not all the minor 1
Namadingo zangomvuta ngati akufuna ndalama angopempha,
Nyimbo za uzimu sizankuluwiko.
nde mwati watan mu nyimboyi? mesa ndi mwana wa bushiri?
Pano ndri phee kuyifila koma ndye ili khenge. Mmm siza gospel nso izi .
Titumizileni tiinveleko nanga ticommente nsanainvele?,0999673863
tigayile 0888496838
Share on whatsapp bra 0884868487
N me too on whatsapp 0882236682
N me too on whatsapp 0882236682
Ok guys !!
amene waipeza andigaire apa +27 780 368 360
tiponyereni 0999722926
0788277452
Share me plzzzzzzz 0994215760
ada share mi plz tiifileko 0880011392
shere me aswell +27610860979
If pocible pliz share +265882343356
zonama izi…
namadingo ndi more ………. Tiyenaxo
Namadingo you dickhead why derailing from the right path?
Namadingo zangomvuta ngati akufuna ndalama angopempha,
Nyimbo za uzimu sizankuluwiko.
Comment Reserved
Namadingo zangomvuta ngati akufuna ndalama angopempha,
Nyimbo za uzimu sizankuluwiko.
God annointed Bushiri before he was born. Now listen, it is bad to fight against the servant of God. Now my prayer is that God should continue blessing Bushiri.
Ndi wanu2 atumbukanu
which God??? open your eyes bro..
Munaliko before he oz born kti muzitibwatika za anointment yakeyo???
lol mboni yanu ndani man?
Satanic
#Blessings wake up……
mulugu asakudalitse iweyo koma yeyo man ndichifukwa a malawi tikubeledwa chifukwa chogona
Iwe. Brenda Sambakusi umati satanic ndiko kuti iweyo ndiwe wa satanic?. Umaziziwa bwanji za satanic. Vuto munthu uka khala mbuli zochita zako zimakhala sanje basi. Zoona kwimbi lose LA anthu limamukonda iweyo ndiwe ungaziwe za Bushiri. Umbuli umenewo Let God judge him not you.
Inuso ndinu ambuli mumapembeza Bushir kusiya Mulungu
Wellington Munthali vetsera nyimbo uve ngat patience watchulapo bushiri….
Kuyamba lero mulandire yesu,,,umphawi wanuwo ndiomwe umakupangitsani kukhulupilira Bushiri
Ndikunena ndi iwe Wellington Munthali
A Wellington Munthali ndinu abambo achikulire ndithu koma zoona kumapembedza Bushir kusiya Mulungu zoona?ndinu ovetsa chisoni
Koma kunena kuipa kwa munthu its only God who knows dat dis is wrong or is good. But not us for sure. You are not God to know dat dis is Satan or is Christian. Tisamalodzane dzala tose ndife ochimwa , Mulungu yokha ndiyo amadziwa zonse basi. @ Brenda.
Zaukape basi zoona mkumalimbana apa mwiniwake akudziwa zoona komwe aliko ndinuoseketsa bwanji ndikakhala ine ndikungodikila Xeno kuno basi
Namadingo zangomvuta ngati akufuna ndalama angopempha,
Nyimbo za uzimu sizankuluwiko.
Apa zangondionetsera kut..all of u…Nyimbo ikunenedwayo simunayinvere…..its a nyc s0ng..ndipo sananemunthu ayi
kapena chining’a..Mayaz….
Walemba izi akungofuna kutis0komeza….ndikubweretsa chinthuzi choyipa kwa patience…
Poison Amalawi Ndchncho Uxamawayiwale Ali Uyuli
Kkkkkk big up Namadingo lalika mu nyimbo,,ife timve
tamusien mulungu agamule. ife ndian.
Thanks @Ali Uyuli for your comment especially for telling us the truth. The fact is that Namadingo in his song has not mentioned the name of the beloved prophet Bushiri. Only that these journalists of this maize gate and cash gate nation would like to tanish the image of innocent people. So repentance must start with the Malawi 24. Lastly, we must learn to respect one another. Nobody worship Bushiri only God. Bushiri also fear God in heaven. After all or even Jesus Christ was also rejected by his people in his home village so who is Bushiri ? God bless Bushiri.
Bushiri is Servant of god not God
Takura naye bushiri tikumudziwa ndifem mtumiki wina ariyese amadziwika ndi zipaso zake
I thout thz pple r together
Namadingo zangomvuta ngati akufuna ndalama angopempha,
Nyimbo za uzimu sizankuluwiko.
amene ali nayo nyimboyi atigayire pa whatsapp 0995214302
Walowa ndale let Major 1 alone.
Namadingo zangomvuta ngati akufuna ndalama angopempha,
Nyimbo za uzimu sizankuluwiko.
i thought namadigo and bushuri r close
Namadingo zangomvuta ngati akufuna ndalama angopempha,
Nyimbo za uzimu sizankuluwiko.
Namadingo waphonya nseu m’malo molalika kudzela m’maimbidwe inu mwakangalika kutonza anzanu YA DIZILO AIKAMO PETULO
Kaya, odi ndisuke mkamwa ndizipita kuntchito ine. Ife tipindula chani ndi nyimboyo
Tanenani
Satana agonja basi tiye Namadingo
A 24wa ngopeka awaa
Judas sold Jesus
Namadingo zangomvuta ngati akufuna ndalama angopempha,
Nyimbo za uzimu sizankuluwiko.
whats happening?enafe sitinayimvere nyimboyo,kodi akutinji mu nyimboyo?
I thot he’s a gospel artist? and why is he attacking ppo in his songs instead of praising the lord or preaching
Namadingo zangomvuta ngati akufuna ndalama angopempha,
Nyimbo za uzimu sizankuluwiko.
Nothng wrong with attacking the workers of iniquity. Ever read the Psalms? Read Psalm 58, 69, 109, 139. Even Paul named false preachers in the New Testament. Elijah mocked the believers of Baal. Bushiri is not a man of God, he is a child of Satan who is leading millions to burn in Hell forever through false gospel, so he can make loads of money at their expense.
amene amalimbana ndi #bushiri amangotaya nthawi yawo coz I’ve never seen BUSHIRI akulimbana ndi munthu..!
Unawona kt onyenga akulimbana ndi munthu?
A Namadingo Mungofuna Kutchuka Basi, Let Bushiri Alone
Namadingo anatchuka kale bushiri asanabwere
Anatchuka kwa iweyotu ndi anthu akwanu not us. Namadingo……..okupsya koma?
It is not good for the Man of God to be involved in all these squabbles around. It would be good if he moves out from these equations
Namadingo zangomvuta ngati akufuna ndalama angopempha,
Nyimbo za uzimu sizankuluwiko.