Namadingo blasts Bushiri in new song

336

When the days were good, Namadingo sang a praise song for South African based flamboyant Prophet Shepherd Bushiri. Now he has decided to throw subliminal jabs at the man of God whose ministry is under fire in South Africa.

Namadingo blasts Bushiri in new song

Namadingo blasts Bushiri

In his new release Dziko liri pamoto set to be featured in his to-be launched album, Namadingo has laughed off modern Prophets accusing them of fooling people.

In the first verse of the song, Namadingo is generalising his accusations. However in the second verse he throws pointers at Bushiri.

“Mtsogoleri Yesu samalimbana ndi anthu, sali ngati chipani cha ndale, safuna ma vote Yesu,” sings Namadingo.

His message might in a way be referred to Bushiri whom the ruling Democratic Progressive Party has accused of working with politicians and operating as a politician.

When Namadingo was contacted to comment on the song, he refused.

Share.

336 Comments

 1. All i know is my Major will remain a great divine encyclopedia. He is a wonderful man of God….God is always happy with his Ministry…May God Almighty continue to bless Major 1…Give him long life so that multitudes would b saved in Jesus name….Satana Malawi 24 wandilira

 2. inuyo a news ndi amene muli ndi vuto munthu sanatchule munthu munyimboyi komanso olo atakhala zoti bushiriyo watchulidwamo iyeyo ndindani kuti asanenedwe malingana ndimbiri takhala tikuzimva kuchokera ku south Africa zoti akumalipiritsa anthu ndalama kutingoti amuone ndi prophet wantundu wanji olipirisa anthu ndalama?olo atamamunena ife tilibe nazo ntchito za bushiri zatikwana omukhulupilira azimukhulupirira ndizisankho zawo mxiiie….bushiri this bushiri that who is he after all nosense

  • Takhala tikumudziwa Namabingo kwanthawi yaitali kuti ndi munthu yemwe ali woyimba wabwino ndipo amatumikiraso ku ECG bwinolomwe. Chomwe angasankhe iyeyo chikhale chomwecho kaya kupitiriza kutumikira olo ayi, sakakamiza. Ena asapezerepo mwayi apa woti adzikamba zonyoza, kutukwana ayi chifukwa ameneyo ndi satana otukwanawe. Bwanji osatakwana azibusa akwanu komwe mumapemphera ngatidi mumapemphera? Mumapereka dzimaulemu kwa a zibusa anu, ma shehe anu ndipo palibe yemwe amaatukwana koma maso kwa Bushiri adakulakwirani chiyani? Angapange zabwino kuthandiza anthu ovutika ndi chuma chambiri koma inu kopanda manyazi kutaya nthawi nkumanyoza, sizikutengerani mtunda. M’malo moti mudikire maungu aphike anthu mudye ndi kuyamika nazo Mulungu inu koma kuvutika ndi kutukwana pano.Mtundu wanji opanda manyazi. Adakulembani ntchito ndi ndani kapena? Bwino nazo mungadzavulale nazo izi. Aneneri a Mulungu ndi owoopsya.

 3. Malawi 24 nda news paper yolemba and samalani nawo ngoyambanitsa and iwowa akanachita manyazi coz prophert bushiri ali pheee zake zikuyenda and ndimadabwa kuti phhindu lanu ndichiyani kuti mugulitse kwambiri.choti muziwe nditumiki wamulungu and woyimbayo sizinkukhuza ayi,asatana inu.

 4. Please achibale msiyeni #Patience ndimunthu odekha pazandale zanu zomwe mukupangazo, musamputile mkhondo ndiluso lake lomwe adampasa Mulungu… if you are trying to insult Bushili do it by your self and not somebody’s behind

 5. Kkkkk kkkkkk nkhani yake kufuna kutola chikwama? koma anthu muli ndimavuto ndithu, mwayamba kutama nkhono wanyama kusiya MULUNGU? Ndakutsika aise ndigwilizane ndaliyense amene akunena kuti awa ndimathero ako amaimbidwe. ndingoyamika MULUNGU kuti akumationetsela maso mphenya iwe anzako akumaitsika iwe wati ukwere? kkkkkkkk

 6. Inuyo a news ndinumukunama monthly sanachule Bushiri kungoti simugona naye Tulo bushiri ndipo mukuchedwa si Size yanu pangani zanu ndi Dpp mungoba chimanga shame.

 7. whether Bushiri wants to join politics or not its within his rights and freedom. why panic. long ago church leaders were running governments as well, maybe for the better. look at ur messy bullshit u r having now

 8. Malawi 24, plz improve on ur writing skills. The title of the story sikugwirizana ndi zomwe mwalemba m’kati. The song is very general. Ma article okhuza analyis ya nyimbo perekani kwa yemwe anaphunzirako literature plz.

 9. Malawi 24 takambani za Chaponda mwina mukadakhala opatsidwa ulemu.koma iyi ya anamadingo ayi ngati mwayamba kusatsa malonda yavuta zomwe timaziwa ndizakuti muli ndimavuto andalama.koma kumbari ya Bushiri ena awomboledwa – kuchilitsidwa- kutsitsimuka ku ifa- pa anthu100 amalawi 4% ambiwo amakhala azathu amaiko akunja inuyo mumapempha ndalama kusiya olumala,ndi odwala mukawona chopeleka chija eeeee mukadakhala inu tidakava kuti ku ofesi kwanu kwayaka moyo.ife ma DvD anamadingo timawaziwa musakokere agule ndi anthu ochepa 10,000 osakwana

 10. U Malawi 24 guys zabodza timakana mwamva, lembani zina pls.Muzakhala okondwa akadana eti? Mvetselani nyimboyo kachikena. “Might in a way be referred”, kungoganizila basi!!!

 11. Mmmm…..the world will neva like the truth. Namadingo walakwa pati,,,mukudana ndi choona and let me remind you that even jesus christ suffered coz of the general truth you hate. Namadingo nawe, unangofulumiza kutulutsa nyimboyi timafuna nafe amve motto buuu…. no man is above man and wait for the word of the almighty and not this village boy…. za chuma zipite uko…..

 12. He never mentioned bushiri in the song and even if he did i would an am siding up with him .. Paja ndalama zikayankhula chilungamo chimakhala chete,,,,many hav been blinded by money but judgement day awaits us all. Be carefull

 13. kodi Bushiri mmamuika pampando wanji? akangoimba nyimbo munthu yokamba zomwe zikubwera mmutu mwake nthawi yomweyo mwayamba kufanizira zochita za Bushiri ndi nyimboyo why??? Bushiri mmamutenga Mulungu wanu?? kapena Profeti wanu?? kapena Satana oyambirira yemwe akuchita ufumu wake ndi zinthu zamDzikoli???

 14. ine ndayinvera….
  Walemba izi..its anyc s0ng..sanatchule munthu..or kuyakhura chining’a AYI!!!!….akungofuna kutisokomeza..komans0 kupeleka bad pic..kwa patience

 15. That is the problem of being a Malawian. We are good at judging others. Why most of the Malawian musicians, amakonda nyimbo zamaboza?
  Mchitibwe umenewu tizingosaukirabe. Zaka 60 tiri pa ufulu wozilamulira tokha koma kumalimabe ndi Khasu. A Malawi azanga masiku olimbana ndi anthu anapita kale. Zintchito zathu ziziwonetsa kuti ndifedi a Khristu kapena Msilam owopa MULUNGU.

 16. Chiwerengero cha anthu opalamula omwe akudikilira kukumana ndi ifa ya kachete chete chafika pa 2, Joseph Mkasa ndi Namadingo koma Amalawi tili mmaso kuti oyimba apalamulawa akhalebe ndi moyo, asafe mwa nkhaza ngati muja anapotokoredwa khonsi ngati Matafale muja,

  • Judge not according to the appearance, but judge righteous judgment. John 7:24

   Read the Bible, God TELLS us TO judge. Matthew 7:1-5 speaks against self-righteous (hypocritical) judgment but in v5 it still tells us to judge, and in 7:16-20 2x it tells us to judge, in Matthew 23:23 Jesus was furious with the Pharisees because they did not judge.

 17. Every tree is known by its fruits,this is an old saying found even in the Bible but we refuse its wonderful implication in todays world kkkkk “anthu anga akufa chifukwa chosadziwa!” I rest my case,the name of Jesus bless you all!

 18. this is a rubbish prophet lia full of stupidity ine ndimaona zonse za boza za bushiri munthu wabwino sangakhulupile uyu ayi ndi munthu waboza ngati mumakhulupira uyu mumataya nthawi zedi tumizani whatsapp ndikuoneseni zina. za boza zomwe akupanga

 19. keep it up patience!!! dont listen to fools who are blaming you of insulting bushirg for GOD’S sake u didnt mention anybody’s name this means its them insulting him in their interpretation,,,, umatha iweyo dont let rumours drag u down

 20. The problem we malawians hve z ngati unazolowela miseche ukangowona amzako akucheza pafupi ndiwe umangoganiza kuti akukunena ,2 ukazolowela kuba aliyese amene ungamulembe ganyu umamuganizilas zoti amakubela, so dnt judge, wajudge woludikila wozajudger wokha zisiyeni zikulile limodzi.

 21. Malawi is the land full of non precious rocks and its inhabitants most of them don’t know what they are saying but act as if they know,their freedom fighter fought off the white people just the same week they came to Malawi even before they had developed their country.most of them don’t work hard and if you do and get blessed to them you are a sinner or a witch or you are satanic.my people are so dumb that they comment on everything that they see on internet .their leaders are busy stealing while they suffer .yes they have freedom but its only for self suffering.musicians seek fame even if they were supposed to bring unity,they read only part of the bible and sing as if they know it all, the bible says its not for us to judge if you see that lam going astray Gods way pray for me not sing about me in one of your songs. You know what if we had gold ,diamond or even copper this country would have been at war too many dumb people acting like mr know it all

  • Hahahahahahaha! Masudi wayankha bwino kwambiri m’bale. Iyeyo akudzitenga wolungama kwambiri? A Malawi kumvetsa chisoni. Akuti iwowo ndiye anthu opemphera kwambiri omudziwa Mulungu kupotsa ena onse pa dziko lapansi. Mzawo akachita bwino zonena komanso nsanje thoo! shame…

 22. PENAPAKE ANTHU KUMAVETSETSA NAMADINGO SANAIMBE NYIMBO YONYOZA MUNTHU WANU WA MULUNGUYU AKUTI ATAFUSA NAMADINGO WAKANA KUTI IYE SANAIMBE MUNTHU. MALAWI 24 ANGOGANIZILA KUTI NYIMBOYI WAMUIMBA BUSHIRI KWAINE MALAWI 24 YALAKWITSA PONAMIZA NTUNDU WA AMALAWI ZA NKHANI YABODZAI. INU AMALAWI 24 AKUUZANI NDANI KUTI NYIMBOI WAIMBA BUSHIRI PAMENE MWINI WAKE WAKANA? AMENE MUKUNYOZA MUNTHU WA MULUNGU WA NTHAWI YA PANSI PANO NDINU OSATI OIMBAYU MUSAMUIKE MAU MKAMWA

 23. #Namadingo close us our eyes then praise in ur heart u ar gospel lie why u can mention someone in ur gospel song that’s not gospel song just praise devil bro no one is blind nowadays mr!!!

 24. Did he mention Bushiri in his song? Uku ndiye kuyikana mau mkamwa komanso kudanisa wanthu. Ma prophet ndi ambiri, ndipo ngakhale atakhala kuti akumunena Bushiri koma chifukwa choti sanamutchule dzina iwe ndiye ndani kuti ukaonjezele dzina la munthu mu nyimbo yakeyo?
  Atola nkhani a pa Malawi eish!

 25. There is a difference between attacking a person and speaking the truth. Unfortunately money is carrying more weight than the truth. Only few people nowadays speak the truth and refuse to be silenced with money.

 26. Achedwa nazo zimenezo angopitiliza ntchito yotumikila poimba yomwe timamulemekeza nayo not judging others tonse ndife olephela pamaso pa mulungu

 27. DO NOT JUDGE!! What someone is doing in this earth!! No one knows who is perfect’ ONLY GOD KNOWS!!
  Count yourself first!! Then don’t point a finger at someone else!!

 28. Achitsiru a Namadingo,mwadya idya ndalama za Bushiri pano mukuti chani,za ziii.why can’t you just concentrate on your singing career other than kulimbana ndi munthu.inu mumazitenga a ngwiro kapena kuti oyela mtima.kumbukilani kuweluza sikwanu koma kwa Namalenga.

 29. When you r on top you become a topic and when you r a head you become a headline,why kumalimbana ndiazitumike for what kkkkkkkk every pastor in this country whether you u r of my church or not l love u so much and may good Lord increase his anointing upon you up to the maxmum in jesus name

 30. I wonder if namadingo has mentioned Bushirs name here anyway ,what God has blessed no man can curse and when God calls one to be His Servant no any approval is needed from any man,man never wishes good things to his fellow man,mmmmmm man !!

  • Bushiri is not of God, he is of Satan. If there is one thing I would have the brothers and sisters of Africa learn, it is this… just because someone SAYS they are a Christian, or SAYS they are a preacher of God, DOES NOT mean they really are. “Ye shall know them by their fruits” – first thing ever, check if they preach the right Gospel – salvation by faith ALONE in Jesus Christ just like in Romans 10:8-13. Not “repent of your sins to be saved” or “baptise to be saved” or “there must be a change in your life afterwards”. Faith alone, not of works. Ephesians 2:8-9 Romans 4:5. Then make sure they use a real Bible, in English that is the KJV (old one, not NKJV) and there’s a long study about that but you can see the free movie New World Order Bible Versions on Youtube to explain that.

   Fake miracles/healng – fake preacher. Preaching only positive things, clearly a fake (Isaiah 30:10-11, 2 Timothy 4:2-5) – the best sermons are those which challenge you and even offend you. Preaching ecumenism, fake (John 14:6).

   People, the Bible says “study to shew thyself approved”. “prove all things” (prove = test). Never just watch a man say “I’m a man of God” and believe it, TEST IT via the BIBLE. If there is a disagreement, the Bible is always right.

 31. Namadingo ndi nkasa zao ndi zimodzi.gospel yamasiku ano akumaimbira munthu osat mulungu ai.Koma anthu amene timawelenga baibulo tivomelezane limanena kut anthu azakhala okonda ndalama siizi nanga.Abale mwa ambuye tieni tingotsata choona chomwe tikuchiziwa.Amen

 32. When the days were good, Namadingo sang a praise song for South African based flamboyant Prophet Shepherd Bushiri. Now he has decided to throw subliminal jabs at the man of God whose ministry is under fire in South Africa. Namadingo blasts Bushiri In his new release Dziko liri pamoto set to be featured in his to-be launched album, Namadingo has laughed off modern Prophets accusing them of fooling people. In the first verse of the song, Namadingo is generalising his accusations. However in the second verse he throws pointers at Bushiri. “Mtsogoleri Yesu samalimbana ndi anthu, sali ngati chipani cha ndale, safuna ma vote Yesu,” sings Namadingo. His message might in a way be referred to Bushiri whom the ruling Democratic Progressive Party has accused of working with politicians and operating as a politician. When Namadingo was contacted to comment on the song, he refused.

 33. mumupanga attack paka liti Bushiriyu tiyeni timukonde munthuyu , SA ndidziko lotukuka ndikale koma anthu amamukonda kuposa ife a Malawi ndiye chifukwa chake akuthandiza chuma cha SA kupita patsogolo m’malo motukula dziko lake la MALAWI.

 34. He Said Wat He Knows. He Was Close 2 Him And I Think He Know Him Better. I Wonder What Gospel Is Frm Yo Man Of God , I Only C Miracles. Musatinamize Nafe Bible Timalitsata ,the Gospel Is About Repentance Not Good For Nothng Miracles. Know Wonder On The Final D We Wil C Pple Going Tu Hell Coz They Trusted Men More Than God’s Words. Yeshua Once Said B Happy Coz Yo Names R Written In Book Of Life N Not Coz U Perfom Miracles Or Demonds Obey U. C U On D Day Of Seperation, Btwn( Wheat& Weed).

 35. Mmmm you 24 i dont think namadingo can do such thing to Bushiri following his interviz with times tv he said Bushiri is more than a friend to him ngat wayimbad then something z happening lets wat and c.

  • Nothng wrong with attacking the workers of iniquity. Ever read the Psalms? Read Psalm 58, 69, 109, 139. Even Paul named false preachers in the New Testament. Elijah mocked the believers of Baal. Bushiri is not a man of God, he is a child of Satan who is leading millions to burn in Hell forever through false gospel, so he can make loads of money at their expense.

Leave a Reply