Inu nonse okonda kutsuka mkamwa ndi mau aululu, samalani tsopano. Lamulo likuchitani tintini.
Bambo wina wa zaka makumi atatu ndi mphambu zisanu ndi imodzi (36) wagamulidwa ndi bwalo la majisitireti mu boma la Machinga kuti akagwile ukaidi wa kalavula gaga kwa miyezi isanu ndi umodzi (6)chifukwa chotukwana.
Malinga ndi malipoti a Polisi, bamboyu a Lloyd Wazili ati anatukwana chikunja Mayi wina.
Ati bamboyu anapeza mayiyu atayima pa malo ena. Iye ati analonjela Mayi uja ndi mawu opempha kuti akagone naye. Koma mayiyu anakana ndi kumupempha kuti achoke.
Bambo Wazili mmalo moti achoke, ati anayamba kutukwana Mayi uja. Iwo anatchula ziwalo zobisika za Mayiyo ati chifukwa anakana kuti akagone nawo.
Bambo Wazili anagwilidwa ndi Anthu a zachitetezo a ku midzi amene anawauza a Polisi. A Polisi atabwela ndi kunjata Bambo Wazili, anachoka nawo chothawa ati chifukwa anzawo a Bambo Wazili amafuna kuthila makofi apolisiwo.
Ena mwa anzawo a Bambo otukwana mochititsa manyaziyu ati mpaka anatsatila ku Polisi komweko ati akamutulutse mzawo. Koma anagwidwa ndi kutsekeledwa.
Pa bwalo la Milandu, oweruza agamula a Wazili kuti akagwile kwa miyezi isanu ndi umodzi (6) kamba kotukwana pamene anzawo anayi amene anagwidwa akuti akatulutse a Wazili ku Polisi, awauza apeleke chindapusa.
I dedent wont conthises mutharika all presedent in malawi is wrong is asalantilly now live for god is seve pleblems hi she fogtern cocision only god can jug pleblems thank you
Ndatopa ndi kumva andale akuyankhula modzikudza nayenso mutharika akuyenjeza tinangobetsa mavoti athu njala ilimbwelekete ku malawi nanga tisankha ndani
Oba ndalama zachimanga nanga??
Send more police in our area tili ndi wa police m’modzi kuno kuti ayiyambe yomangawo amenyedwa
Nde zitinso izi? Malawi will never seize to be a laughing stalk. Malawi bomboclaat laws.
Guys nanga wakuba chimanga zaka zingati?
kkkkk ena akuba ndalama za LDF Osamumanga koma ukatukwana umangidwe? Malawi sadzatheka ndithum
Mwayamba kunama eti,mwalephera kumanga chaponda.
Ayambe nankumwa
Matthew Paul Chibambo, Davie Kush Kuchilunda, Axholile Ymf Yeezintoh, Santos Clever Bouy Kanada Kagulu inu
Eva Nthete, Ine Ndi Xabi Mauwo, Gomondah Gomondah Africa Skybuzzy, Matthew Paul Chibambo, Davie Kush Kuchilunda, Boy Nangwa, Santos Clever Bouy Kanada, Evans Nappyboy Kalumphalinga
Palinso wina watukwana kuno ndipite naye kuti?
Ndiye mmene mwalembera mutu wankhaniyi ndi nkhani ili mkatiyi zikusiyana
Asena ali m’madzi chaka chino chifukwa akati ayamika bwino mpaka atukwane kaye
ekkkkk lhave ahigher certificate speacial for swealing so is up judges to think about pple like us
Aaaaaa manyi ndatukwana come mzandimange kkk
Munyanya kutukwana ngati anthu any a……….
Kkkkkkkkkkkkkkkkkkkk
Kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk
Ndie muyambe mwamanga nduna zonse zaboma + president coz ndi amene amaziyamba ndie mumati tisatukwane???? Tikukwana ngati zithu sizili bwino, kodi malamulo mungoonjezera onjezerabe bwanji? Aope ndani zimenezo. Lodi anthu ake ndi inu mukulemba bible part 2 aja ndinu eti? Mitu ngat mbuzi kuyambira yemwe anapanga lamuloro mpaka wa police amene angammange munthu otukwana. Mixm
dzikoli lili m`manja mwa agalu
Majestrateyo mboli ya make
Kkkkkkkkk
shaaaa!kikiki
Lamulo ligwire ntchito basi to make new Malawi
Mumange ine peter ndi nduna zako vigin zanu
Kusowa zochita Ku Malawi kuno Noun is a name of anything ndiye amumangila chiyani
Akusiya mbava amanga otukwana doesn’t make any sense….
Wakhaula,,,uhule onyamulira pansalu
Nde kundendeko kudzaza asena okhaokhatu. Kapena muwamangira ndende ya wokha?
kkkkk kkk koma yaaaa
Amaonjeza ameneo
Kkkkkkkkk koma guys malamulo enawa
Nanga paja boma limadandaula ndi kuchepa kwa ndende za m’dziko muno. Nanga uku si ndiye kutha malo ko? Poti ndi ntchimobe mwina adzingolipitsa.
Ichi ndeno chamba what to freedom of speech
Aphungu nosee akumalawi panyapanu
chikhalilenosho kusukulu
munapita zaka zankhani nkhani
koma zelu mulibee kuyambila
pita muthalikayo nyamakee
aliyese amene ada4meleza zalamulolo
bolo yabambo akee
hahahaha koma adha…. komadi anthu ena amanyanya kutukwana, ofunika apolisi achonchi azipezekaso kuma bus stands…. komaso china anthu akumabaso chimangawa ofunika kuwamanga osamaona za mbali imodzi
happy new months friends my name is Priscilla Mbangwe doctor abumen help me to cure my HIV/AIDS virus with an herbal medicine, am sharing this to the world to save some lives, believe me there is a cure, you can contact dr abumen on his email address [email protected] and you can also call or whatsapp his number which is {+2347085071418} please share to save lives.
Osamanga okuba ndalama za chimangawa bwanji…
Zopusa
ZANTI, KULEKA KUMANGA WATHA KUBA NDALAMA M’BOMAWA PANO NDALAMA ZATHA WAYAMBA KUBA CHIMANGA. CHAKA CHINO TIKOLOLA CHATHU. NDIYE MUKATELO ADZIPANI DZAKUBADZI AONJEZELA DZIMANGA PASALU.
osakamanga a maizegate bwanji, nanga kutsuka mkamwa mpaka 6 months!
Abwere kwathu kuntcheu ndipo aszamanga pafupifupi mudzi ose
Mumangeso ine
Akalowe basi kutukwana timatukwana pa fb osati pamaso asova
Next george chaponda
Panyero panu
Uri bwino bambo
Lower Shire, mangochi, machinga nkhatabay palamulo ili lokha nde mwanama, muwamanga n mudzaimika Nokha manja.
Ife anthu akunyanja sitimatukwa koma kutsuka mkamwa
Bweran kuno Kumangochi kuli anthu oziwa kumuvula munthu koma atavala muwamange ngati sazakuphulisani just try, Lamulo liposa mphamvu koma si Lamulo lake ili mmm am telling you start from the beginning again reform it, then I think it will work, but for now muona chiwelengero cha a police chikwera okufa pa Lamulo limenero.
iya kutukwana nde chani wasiyanisayo nda mene watukwana
Wina waba ndalama zachimanga uko koma
Zopusa basi osamanga mbava yayikuluyo achaponda bwanji
Makamaka inu aku Nsanje plu a Lomwe
Ine ndili kuno ku botswana ndimakonda kutukwana boma mudzandimangetu mubwele kunoko
Zaziiii!!! osanena kuti osapita ku church amangidwe bwanji?
Nanga uja wakolola chimanga chachiwitsi uja kumanena kuti wakolola poopa winawake amaba chimanga sikunali kutukwana ?
Lamulo ligwire ntchito
Nanga awa abwande aba chimangawa akakhala dzaka dzingat ku maula?
Mukulephela Kumanga Mbava mukulimbana ndizopanda pake ngat zimenez,paja tikachitchula mu chzungu ndekt sunatukwane eti,
Zopusa zimenezo kutukwana nanga inu mumatukwana in english tipange nanu bwanj ine nde ndi tsiku lililonse kutukwana mubwere mudzandimange tione ngat simukadziika nokha ku prison mbuziiiiii za a2
Kubweraku timva..aliyense oyenda ndawala amangidwe bwanji akuyenda ndawala akupita kut mwina akupita kokaba ameneyo kkkkkk Aphungu kusowa zokambirana atatopa ndikumwa tea wamkaka kuyamba kukambirana zopepera….zanziiiiiiii
use of insulting language ndi mlandu wakalekale siunapangidwe lero koma vuto inu simumadziwa!!
kkkkkkkk mwaganiza bwanji man?mpaka wandawala amangidwe
Hy #Manes usakhale ngat okhulupilika apa wamva..ukati vuto ndi inuyo simudziwa iweyo kuzivaka kudziwa zithu kwambiri..oky let me ask u…Miyezi yapitayo Aphungu amavomereza kut pakhale lamulo lovomereza kuchotsa mimba tsono ngat Amalora lamuro lomweso lili ntchimo kwambiri nde ukanene kutukwana ?? Mulandu ochotsa mimba ndi kutukwana zoyenera kukalowera kundende ndi ziti ?? osamangobakira zithu zofoila aunt #Manes mwanva ?? Am not saying kutukwana ndikwabwino ayi komano nkhalidwe ngat limeneli munthu amayenera kuzipanga control ekha not kumangidwayi..
Zoonadi zafika Pena tsopano malamulowa amenewatu bwanji.
kkkk eti chemwali #Nancy nde wina aziti Boma lachita bwino pomumanga munthuyo aaaaa Kutukwana kumangokha kusowekera umunthu wako otukwanawe..ndikachiwanda koti ngakhale ku police ko azikatukwanabe kkkkkkk
Wadyapo…. ………..get it up nigga
…No,give me where it is written in the constitution of Malawi…just kutukwana basi, mpaka miyezi yonseyo???
kkkkkkkkkkk “kutsuka mkamwa ndi mawu aululu”
Kaya alipo yemwe sanatukwanepo kaya,,,,,koma ngati alipo atole mwala …..
Koma pa flamez kusowa chochita kapena chani?
Kkkkkkkkkkk
Nkhanizi zimakhaladi zoona koma? Nanga uyu daily mmangomuika yekhayekhayu bwanji pankhani zomangidwa komaso zosiyanasiyana mawaso mumukaso pankhani ina
Amangolakwa yekhayo nthawi zonse
Osamanga akuba chimanga ndi ndalama zaboma bwanji mukulimbana ndizopanda ntchito
Zilibwino kwambiri, maybe our children will be raised in a conducive environment and grow up to be responsible and real persons
Otukwana ambiri ku Malawi ndi ambuli, osaka abwannoni, opanda mwambo, alibe chalichi, kuba basi, sanapite ku thezo. Ndiofunika kuwatumiza ku gule wankulu akawakunthe, abweleko alibe mano. Mungopangisa Malawi manyazi basi.
Kkkkk
Kuyambira apresdent mpakana nduna zonse za boma ndinu zitsiru coz simungamaononge nthawi yanu pokambirana nkhani zopusa ayi, inu mungamange munthu kamba kotukwana zoona? Bwanji simukummanga uyu wakubayu? Ndinu zitsiru eti
nanu atakumangenipo apa.iwe ndi osauka ngati ine ogona ndinjala ngati ine ungamalalatile anthu opata ngati chaponda?uganize bwino blow.
Kkkkkkkk koma za ulendo uno
Kodi kutukwana ndi chani? Amalawi chatisowa chilungamo. Buku loyera, Mateyu, limatchula mwachindunji kuti, .. amene adzakwata… Mwambi umati, wakwata kwa mphezi… Koma wina kuti atchule zomwezo mukuti watukwana. Pachingerezi timatchula kuti penis, vagina, clitoris, testis. Why. Kapena munene kuti wamangidwa chifukwa chonyoza bwa? Once again, what is kutukwana?
Eti bradaaa mmalo mothesa corruption, zaziiiii
Just shows that you don’t know the difference between a name, abusive word and an insult. Kukwata, mbolo sikutukwana. Koma kumakhala kutukwana ngati pali kunyoza. Ukhonza kumutukwana munthu pogwilitsa ntchito mwendo, dzanja, mutu kapena thako. Komanso mau olaula sikutukwana, kumakhala kutukwana molingana ndi momwe wagwilitsira ntchito mauwo.
Eg..mboli yako,nyin yako,mavuzi ako etc …kkkkkkk
I know more than what you know, and more than this. You may be the one full of emptiness. That’s why kumapetoko ndafunsa kuti, osati amumanga chifukwa chonyoza bwa? Unawerenga ndikumva funso limeneli? Kapena unangowerenga chabe? Kodi iwe sudamvepo munthu akunena kuti, uyu watukwana pamene munthuyo anangofotokoza potchula ziwalozo? I am against such misconceptions.You can follow the English version of the same story, where expressions like “insulting a woman” have been used. So, your argument doesn’t hold water at all.
Iweyo usazembe apa uli against ndi nkhani yoti wina wamangidwa chifukwa chotukwana ukuona ngati ndizosatheka kumangidwa chifukwa chotukwana don’t try to be very clever walemba wekha zamveka bwino zomwe wanenazo osazipanga contradict.
Critics and authors are able to express one idea using various devices. Some can use irony, others can use paradox and many more depending on their choice. They don’t explain the particular style they have used. In this way, it becomes the duty of the audience to interpret the way they want. So, whether you construe or misconstrue, is none of my business.
Paul james ngezi inayo yandipita use simple phrasalogy kkk dausi
Happy, macheza awa, kkk.
Nangano a cash gate ,. Maize gate wa, awachita bwanjiiii !!!! Tione!
eti man akulimbana ndi zaziiiii
A court ntchito yawakanika, alimbane ndi maize gate.
Kukhwimisa malamulo pa anthu osowa pomwe yawo milandu ikumangogonera , what a crazy Malawi!! Am tired of MW.Guys ndipanga passport bas.
Kkkkkkkk Ngati zayambika zimenezo, pakubwelapa mudzitimanga kuti tafusira mtsikana wamwini,
kkkkkk waganiza bwaji dolo
Eishiii koma ziliko.
iiiiiiii nde tili madzitu chilichonse ndi unyolo masiku ano,apa ndingopesa American ID bas
Alephera kumanga Chaponda amanga otukwana kkkk ma judge aku Nyasaland
Ku nsanje kukwatira amati kukwata moti adzinjatidwaso? Mwachitsazo christopher wakwata nasibeko
Za ziiii ndende mukuzazikamo otukwana pamene okuba zaboma akunjoya muleka kumusekela uyu waba chimangayu. Zipangani
Kodi muthuyo watukwana ndani ?
Ndiye utani ukamudziwa, popeza magistrate wagamula basi kuti alakalowe muchitokosi.
Zaulendouno
Section number chani ikuteroyo?? kusowa zochita eti??
Kusowa zochita eti stupid
Kkkkkkkk
Kkkkkk!mxiiii,nditsukiletu nane apa,admin ndiwe ‘dyabu”Sena’ 😎
Kkkkk chichewa cheni cheni, dyabu
Zachani..?
anatomy sititukwana….!
Apite ku Nsanje kapena ku Ntcheu sati kutukwana ai koma kutchula chiwalo, kutsuka mkamwa. olo pomunyadila mnzako amatsuka mkamwa chimodzimodzi
zazii …..mumanga omweo opusao ife tikutukwanani sitinati
SECTION CHIYANI IMENEYO
Great!