Mangochi Police is keeping in custody a 32 year polytechnic student for stealing assorted items such as Kamba, soap, bread at People’s shop on Friday in the district.
Mangochi Police Deputy Spokesperson Amina Daudi has identified the student as Victor Owen.
According to Daudi, Owen stole assorted items like 23 protex soap, 3 packets of kamba, 8 bottles of Cocoa, 2 loaves of bread and other items that he hide in his jacket.
“All the items are worthy K45 000 and he was caught by Shop maneger who informed the police,” Daudi said.
The suspect will appear in court soon to answer the charge of shoplifting.
Owen hails from Chikwati village, Traditional Authority Mwambo in Zomba district.
Apolice akuno kwathu ndi mbolo kukanika kumanga anthu omwe akuba ndalamawa koma kumalimbana ndi ma students kkkkkkkkkkkkk manyazi bwanji?????
kubaology, de student wz on practicals trying to do wat pitala, a jijo chaponda and entire malawi cabinet are doing ready for 2019, release de student life iz tough nowadays pa campus!
shame
Firstly i shud blme Malawnews 24 fr expozing such munthu, ngat wina waba #Njinga, mumayika Njingayo pa wall yanu, kaya acourt amugamura mulandu mumayika Chihamara.. Dnt do apapa mwanyanya poti ndi wa poly aaa aaa! Poly ndikachani m’masiya kuwajambura ma scandal eni eni ndikumalimbana ndi sopo.
Secondly plz ngat tinapanga #like page yanu sikut tasowa zopana like mmm! mmm! Koma timakukondani ndeee! provide us wth GudNews osati tizisusananso ndi inu No #benefits.
Third one be like #ZodiacNews, wat am tryng to say s…. Dig deep and bring it up timafuna (Zakuyazo!) zibwere pa m’mbalanganda.
Educated thief,,zoona mpaka kamba?
Nkutheka zingomuvutadi , nizandalama zingati timulupilile kuno ku tsidya la zambezi ?
Ndipo ndizaboza coz zithu wapazo sizinakwane K45 000 ndiza ndalama yochepa
Niza ndalama zingati timu lipilile kuno kutsidya la zambezi ? mwina zinamuvutadi .
Mukulephera kumanga president akuononga Malawi mukugwira mwanawa xool palinzeru apa ?
Ndiye njalatu man
Enawo simmawamanga mkuwaonetsa chotchi bwanji? Koma dzikoli ndilokondeladi mwamva Wayanba mpaka unyolo shame wapolicewe
mfana amumangayo ndi freind akupanga za law papoly ndie wapanga dala zimenezi ati akufuna amenye mapractical mu cout…wosadanda naye ndi genious komanso kwawo ndikwa wapolice wochoka mano wamumangayo sikungafane..
Pa poly Law yayamba liti?
What a fuck arrest by by the Malawi police service
I don’t condone theft but to say that the govt is behind the perpetration of this vice is totally wrong. I STAND TO BELIEVE THAT LACK OF PERSONAL PLAN OF ACTION is what uhbreeding this malpractice. If we wholeheartedly concur that wealth starts from bottom line we can’t see ourselves in theft scams. Ndiye poti mMalawi believes in overnight wealth nthito zake zikhala zokubazi basi.
Akusowa zochita mesa munatsekela school. Inuso ndinu mbava mukumaba pamisewu. Tima 200 kwacha. Kupusa uku kwenikweni
No us we are the one fighting for crime…. So uzaiwerenga for Wat.. Are u asuspect
Yaaaa he must be changed
Nde Malawi ameneyo wakuba kamba 4yrs Ku ndende wakuba ma billions Iwo ali free sakumangidwa mpaka lero….. Za ugalu basi
Kkkkkkkk student from Phwezi polytechnic
Sorie bro.wrong things r only wrong whn caught next tym kuzaiwelenga boouboo
Koma 32yrs kuba kamba?? Kkkkkk bola akadaba cash tikadati akufuna fees.
Kkkkkkkk,wayambiratu kuba nanga akamadzagwira ntchito zidzatha bwanji?? Kodi paja poly ikutsekulira mmawa nde amafuna akonzekere mokwanira.
Chonde admin muzitchulanso mpingo womwe wolakwayo amapemphera
U can’t even try to post important things here but rubbish mmm malawi just put developed things here how many thief’s u have been posted so far in these dayz politics shame u
He isntva Poly student…amanama choncho n sometimes says he is working ku sunbird!…ndi dobadoba mu zomba
Mmene watcheneramu basi kuba kamba wodya ana? Very shameful kukhala my husband xxxxxxxxxxxxx
kuba kamba 200 kumangidwa wina kuba Chimanga cha ma millions osamangidwa. Kkkk Kumalawi Konkuno
Hey niggars no comment
Kkkkkk
The problem is that this government stopped providing alowances. Life is tough at college with nothing in your pockets. The young man was desperate. For goodness’s sake release him
there was no need to arrest him but paid for him.
Ana mpaka 7months holiday
Can i ask u goverment…..wat makes him to steal?
Strugle is real
Nanga chaponda?
Ameneyo akakhala kundende zaka 100 kumusiya okuba mabilion
Koma za ziiiiii kaya kuti zimveke bwanji poor malawi small issues easy to handle za ntiiii osawamanga aja achimanga aja bwa aaa
Leave the guy alone this is nothing
He is from Karonga Polytechnic,not our [MIGHTY POLY]
That tells you how much the Government of Malawi has failed people,they made people extremely poor to such an extent that the people cant afford even a bar of soap…..Malawi government is a disgrace
Vuto ndiroti apolice akumawi ambiri mwaiwo alindi ma jc form 2 akaona ophuzira bwino ama chita mayazi:( mutayeni oyo agwanya inu
January awuse mwa mtendele maluzi abvuta mpaka kuba soap ndi kamba mmmm
Kkkkkkk
Ziko LA Malawi umbava uli paliponse kuyambila Ku ndale mpaka Ku mipingo mbava zokhazokha koma chodabwitsa mponda makwacha milandu yake simaoneka bwino koma kwakwatuke ngati ine ndiye unva life in prison y malawi!?
all in pocket
Mistaken identity
Mu2 woti ali kuch Holidy anasekera kalekale molo moti muziti mwamanga mwana wa aphri,a banda or a mwale chakusangalasan ndchonyasisa geli ya anzanuu basi
Koma nayenso…mpaka kutchenebwa kokabako
Were u trying to make a headline?
Chithuzi chimodzi koma khani zosiyanasiyana eish!!
Mxi!!!
Ngat Mukuchedwesa Kusegula School Mukuti Anthu Azitani Bwezi Atamaliza Pano Akudya Zake
Mesa paja ena akukana kt njara kumalawi kuno kuribe??..
Kkkkkkk koma anawa Ali pamavuto mpaka kubaso bread pepani mavuto so maliro koma mtulusen anali ndi njala
anthu akumalawi nd osangalatsa amapitaku xool kti adzakhale mbava look at our politicians,govnment officials,bosses in offices mbava zokhazokha
He is un…..
UFN
wokuba limamanga ndi lamulo
Akagabe ameneyo
Zabodza izo bwana sangabe iyai
Mulandu wakuba kamba dziko lonse kumvera Chaponda kuponda mamillion kumangopondereza
I see no problem because even ministers are found in different gates ranging from cash to maize
Bola kumangoba ma pencil ndi ma ruler, kulekana ndi kukaba ku peoples tawona m’mene wayalukira mwake. Ndiye achitanso kukuonetsa nkhope, pamene anzako pomwepa nkhope imabisidwa koma ana aku poly mbuzi zeni-zeni.
Kuba kumakhala ngat chilema mwina makolo ake ndi akubanso.kkkkkk haa! Haaaaaaa!
Peple’s gate
Amene sanabepo ayambe kumuzenga mulandu
Polytechnic gate
How would he become a chief cash-gater if he doen’t practice? Practice makes perfect.
Apolice very stupid,mukuoneka ngati odziwa job,amaGATE mukuwasiya kuti musiyeni,musazionetse udolo apa,afisiwa akuba mabillion bwanji simukuwamanga?
Wat u no u Policemen is to arrest people who stl small things lke this nt People who stl billions of kwacha lke stupid fools Chaponda and his frnds ne?.
Kkkkkkkkkk odi ukooo! Malawi wamoto mawa ndim’kucha ndimvaso zina
RIP
Monseur January kkkkkkkk
Malawi sadzatheka wina kuba chimanga chomwe chidakatha kuthandiza mtundu wa a Malawi ambiri osamumanga koma wakamba kumukakamira mulibe chisoni amfiti opemphera
so malawi24 you dont know what to report ok thats fine with you idont think people will be happy with this news
kkk sukuludi imatipewetsa zambiri eti, nanga sukulu sanatseka mwina thats y ayamba kuba.
Koma mapolicegate ndiye mukuziwa kukakamula milandu ing’ono ing’ono mwaiwala kut usikuuno mumabweleketsa ma uniform anuwo kwa mbava hayala…ndikatopa nanu ndikuuluran nanu mumangidwe
Intellectual
mukumanga munthu oba kamba? Osamanga awowo bwanji?
Stupid police mpaka unyolo kamba chaponda bwanji osakathila nawo unyolo mwanayo mutayiletu zopusazo ai
I knw he has done delibetely .He doesnt find peace outside bars
Kkkkkk Let God Forgive Him, Stealing Is Bad In The Eyes Of The Creator.
martias Gudu kkk
Amaphuzira subject ya ukadaulo pakuba ameneyo.
.. ..cashgator in the making
Money yavuta pa Malawi, what else do you want us to do?? ☺
tchuwa pa polly waba assorted nginiii?kani ukapysalawu ukumayamba ndima intellectual nkumakwela kuntunda uku!tchuwa!!!
KKKKKKKK NO COMMENT
let him go to continue studying
duuuuuuuuuuuuuuuuu.it seems lack of job opportunity
Why can’t u go n arrest chaponda watiponda chimanga not kamba fokofu men
Cho ncho mukamu lamula mpaka za 5 pamene chaponda akukanikani kumumanga mutayeni mwana wa pa mangochi sec yo azikampuzira.
Poly must be a college that tries to educate savages & nowonder it closes every year. Big shame on you supposed to be ladies & gentlemen & if you can not afford groceries how can you afford fees.
Watch your language man.One man’s stupid action doesnt translate to all of us.We r different pple from different backgrounds, with different philosophies
I expected such only from those the finger points at and did not mean to offend those who don’t feel offended.
kamba soapgate kkkkkk!ndiye kuyaluka ndizazitu.nanu apolice.
Open poly
Aki forsake a Malawi 24 ndinu abodza kwabasi. Munati manager was sunbird poyamba pano mukuti poly students fotseki
Manager sangakhale student?
Komeneko sikuba njala inampola basi
Kundende chifukwa cha Kamba kkkkkkk?
Mmm kkkkkk zovuta
he loves his kids(achina kambawo) and the whole of his family.he wanna live a happy family,he wanna leave something for his family as he is left with just days before going back to his precious-iconic varsity..sapatsa ongokhala mkumangogona pa den.kk lol!
Not for the kids. Valentine’s gift
………..m
.lmost.m.
kkk
ive seen this story also published last year if not 2015
ndiye akafikira pension .. nanga 32 sanamalixe school?
kkk sinanga mumakhalitsa ku xul ko.course ya 4yrz mpaka 7 yrz afta kutsekatseka.mudzikafira pension kumene kkkkk loo
hahahahahah kkkkkkkkkkk nanga 32years man ali second year nanga akatsekaso school..
He only wanted to taste the security systems if they are working, good they are working, can other students do the same in shops wherever they are.
Kkkkk koma zinazi
nde mwat anasunga mu jacket zinthu za 45 pin..?
When a person did simple fault has he did it intesified. Ah its only God knwz.
Pa flames Moyo wavuta amafuna zotenga kusukulu mwana.
koma kumangochi kodi kuliso poly?
ok
koma kumangochi kodi kuliso poly?
Maybe is his experiment of his studies
Samy Slimdude Sammie mwaona zochita xa anthu pa poly?
ASA mdala ameneyo si wa poly yathuyi …mmm.m tamukana
Musamukane …mwinaso ndi mesho???
??? Ku Poly Kulibe Bachelors in Stealing araaaa
Hahah aliso mu psu
ana apoly ndilibe nao mau anandibelaso phone day ya social weekend
Kkkkkkl
Leave the guy alone, go and arrest those ”hynas” politicians thy r stealing billions.And exposing someone like dat before appearing in court is not on. It’s just a petty crime.
Kkkkkkk analibe pokayambila kusukulu mayesa sukulu atsekulira
baaaaaaaaaaad
Chomwe chamupangisa tuchiziwa et ma man Allih Bien Allieh Allih Friday Martial Samson PE LE TE
Ay C Wa Poly Kma #UFn Kkk
Kkkkkk wakanda kwambili mun2yu
That’s why in our government’s there full of thieves they train before they are getting employed in the government
Chiyambi Cha Cashgate/maizegate Nchimenechi!
He did that because he had nothing to do @ home since the school isn’t yet to be opened!
xul akupita2 next week
Kkkkkkkk
Nanu apolice mukumanga mwana wasukulu moti waba chimanga uja Geoge Chaponda
Breaking News…
ndiswagistic
32 year old!?
Umphawi winawu mmmm
Department of Kubaology
Head of Department_Chaponda
Course-=Kubaology
Code = KB 1101.
can’t wait to apply. ….
Which faculty kkkk?
faculty of Chaponda
kkkkkkkkkkkk nde mwati chaponda??kkk
Breaking New…
Kkkkkk Malawi wavuta uyu
Zonsezitu chifukwa cha chaponda,
kkkk zugwilizana bwanji man?
Ufuna ndiyakhe ktu aise?
Ngati ndi Chaponda akuchititsa, iweyo bwanji sukupita ukabe kamba wako bwanji?
Silly comment.
Bad News. What Waz Going On To Him? I Think Some Times Education Play Vital Part But Sometimes Are Not There4 Reffer This To That Student
hahaha kamba
Which polytechnic? There are so many polytechnics in Malawi, there are Thondwe polytechnic, phwezi polytechnic, Unima polytechnic etc
He did it for fame i don’t think he was really desperate for those stuffs just imagine Kamba,soap???.
Dude,.The struggle is real…
Hey Chap you’re lying stealing bread,soap and kamba its not because of poverty never had it been he stole money i would have agreed.You can’t survive with Kamba,soap and bread.
Kkkkkk Malawi Wavuta Uyu
awa ndi ana koma osagwira okuba mabillion
opita ku xool ndamene amaba ndeosadabwa
32 yr old? kodi ndi galanta kapena?
atani munthu stressed xul yao anatseka
vuto ndi #chaponda… wayambisa zolakwika..
Kkkk some people are saying kut ndi assistant mangaer wa sunbird hotel so which is which?
Feesmustfall imeneyi
Feesmustfall imeneyi
A very poor boy boy. He can’t even manage a soap bar. Leave him alone
Chaponda watuma mwana…
I don’t blame him. Zinthu zafika ali ndimwana agwilitse
Chaponda effect