Mtsogoleri wa dziko lino a Peter Mutharika adzudzulidwa mwamphamvu ndi atsogoleri ena otsutsa ati kamba kotayitsa nthawi a Malawi ndi msonkhano wa atolankhani umene anachita lachisanu sabata yatha ku nyumba ya boma mu mzinda wa Lilongwe.
Malingana ndi mtsogoleri otsutsa mu nyumba ya malamulo, a Lazarus Chakwera, a Mutharika anangobweleza zimene anthu akudziwa kale mmalo monena mau a tsopano opeleka chiyembekezo kwa a Malawi.
A Chakwera anapsela mtima a Mutharika ndikuwadzudzula ati kamba kobisa nkhani ya matenda awo amene.
“Iwo asaname, anakhalitsa mu dziko la Amereka chifukwa cha matenda awo osati kuti amagwila ntchito zina zaboma, koma taonani mmene anayichitila nkhani ija. Anangowawula basi,” anadandaula motero a Chakwera.
A Chakwera ananena kuti khalidwe la a Mutharika lobisa matenda ndi limodzi mwa zifukwa zimodzi zimene a Malawi akufunila lamulo lopeza nkhani ku boma lija pa chingelezi akuti ATI bill.
“Tikanakhala ndi lamulo limeneli ndipo likugwila ntchito yake moyenela, a Malawi sakanavutika chonchi,” anatelo a Chakwera.
Kumbali yawo a John Chisi amene ndi mtsogoleri wa umodzi anadzudzula a Mutharika ati kamba kouza atolankhani kuti ngati akufuna ayimbe munthu mlandu pa kubisa za kumene anali amayenela kuyimba iwo basi.
“Boma si munthu mmodzi iyayi, boma ndi anthu ambiri. Iwo akunena bwanji kuti tiyimbe mlandu iwo wokha. Iwo akuziyetsa ndani kodi?” anatero a Chisi.
A Chisi anati mawu a Mutharika anali oloza ku chipani chimodzi zimene zili zosaloledwa.
A Mutharika adalankhula ndi atolankhani lachisanu patatha masiku asanu iwo atafika mu dziko muno kuchokela ku msonkhano wa UN ku dziko la Amereka.
vuto anthunu fodya mukusutila kumatako choncho boma clingayende!!!!
Dpp Woyeee
mbuzi koma iyi
Tizayakha
A opposition dziwani kt ndinu amene Mukunthandidzila kt dziko lisamayende bwino osati dziko lidziyenda bwino.mukhale patsi mukambilane nokhanokha Muli ndimantha mukuchita kusonyedzelatu kt payi mundale mulibe mutu mwanu koma kusongonedza malo moti mukhale patsi mudzipanga manifesto kt mudzatani kuti muwine 2019. Palibe.Muli.0% a opposition.kkkkkkkkkkkkkk.bola dzanthu.
Ameneo ndiye osusaboma akumalawi. Nthawi yowona kuti boma linapangapo zabwino inapita kalekale munthawi ya Tembo zomwe zasala panozi mdimanyaka a opposition
kkkkkkk ndikhale mbuli pa khaniyi
mabodza mumvera malawi 24.ife pano tikukamba za mpira osati za zii.
eeee zawo izo akudya okha ife tikudandaula zanjala kut kod tipulumusa bwanji ana athu #ManeMaker
Uchitsilu Waotsutsa Kusowa Zotsutsa, Asatan ,mubusa Wanj Otele Odya Matewela Awana,
osusabomainu mukufunamunthu adzichitachani? kuti muzisangalala tatopananusopano
No food for lazy man.sisinyoko! pusi!
Amene akuvomelezana ndi president ndi anthu osaganizila mtundu wa amalawi, otsutsa boma akunena zoona, nanga blackout zikukusangalasanitu, ife azanu tatopa nazo. n
zitsilu zotsutsa,mwamulephela petter,komanso akupanani mpaka tizipanitanuto tikutha,munya munthu wake sipetter ndipo 2019akutibulaniso
AKUMANA AGALU OKHAOKHA ALENDO PANDALE
Kkkkkkk zovuta kuvesa
W9
Koma anakanena kuti basi ndasiya u President munakasangalala anyapala inu
Kkkkkkkk koma ziliko
Mr chakwera ithink ubusa uja was ua best ground not politics cos mfundo zanu zina zikumaveka chitnchalichi siyani pitani muzikalandira zamasika
So what ???
yankhulan bwino a sam olo atati watula pansi udindo kubwera wina azakhalaso oipa nde mmalawi ameneyo kudziwa kunyoza bas sitizatukuka ata
amafuna tingoona kuti wachila komaso anthu andalewa poyakhula simasowatu pazithu ZOSE amanena kuti adachita ku USA zambri ndibodza lokhalokha ndipo athu amene ali hig grade ya bodza asanamize amalawi anali hospa
Chakwela ungocya ndale kulekana mkumawazunguza anthu mitu
Chinde tisawa NYoze tyeni tigwirane maja dzko ndilathu ili
zoti inu anthu akumpoto muzatenga ku president dziko muno muiwale ndi wa lomwetu upresidentu kkk mtumbuka undinyesa ine mxieew.
Akanati asapangisenso bwenzi mutamunenanso.eeeiish a Malawi this is too much…,,,
Gyz don’t lose time for nothing mind our business
Palibe zobakila apa Galu ameneu achingotula pansi utsogoleli palibe cha mzeru akuchita mu dziko mwathu muno Hgologolo ameneyu. mbava .
Pathako Pake Lazaro Chakwera Ndi Chisi Wake Amusiye Mutharika Alamulire Dziko Kod Chakwera Akulephera Kuthetsa Mavuto Ku Mcp Kungokhalira Kutsutsa Zirizonse Basi Ndale Zauchitsiru Akupanga Lazaro.
Mr Chakwera bwererani, tiyeni tizikangolambira Mulungu, you can’t make the presidency of this nation, believe me
venda akugulitsa 11000,boma 12,500,anyika basi
nonse ndinu zibwete, mwateng dzikongt ndilamakoloanu eti? zachamba bac kukhlila kulongolola ngt ndiakazi koma ndiazibambo, mbuzi zaman kunsi. kkkkkkk mwandkwan.
Akt kumati azawo nkholokolo pano zabwerera mudziwe lake nkholokolozo ndiye kaya azichotsanso bwanji?kkkjkkkkjkkkkkkk ophunzira saposa phunzitsi achina jumbe,chatinkha ndiena otero ndimizwanya pandale sikungoti wakhuta umvekere fwe fwe fwe,onse pano akuthawa amakuyamikira pano aja,amvekere bwana thananawoni nkholokolo zimenezi,court kungolamula pano kuli mziiiiii,tinanena kt fatsani bwana muphunzire ndale ena amatinyoza,ife ndale zapamalawi taziphunzira 22yrs sipano ndikale multiparty abwera
Ngat ukukanika kuendesa bwino chipan iwe chakwera ungaendese dziko iwe?????? Musaone ngat zofuna zamalawi ndizofanana ndizankhosa za assembless ai kt mungazkwanise
Ichi anena ichi anena otsutsa boma adagwa chagada
Nonsesical
Kupusatu Uku nde mukadziwa matendawo magetsi asiya kuzima chimanga chitsika
Fear God respect Men of God
Mapazi awo atsutsawo
Thankx. Tamva nawo
Uyu akusaukitsa Malawi…Malawi akufunika president wachinyamata Ngati mmene analili a chair Dr Bakili Muluzi kuyipupa
Hey! nanutso mwaya thawi potsutsa.Mkamasutsa mziona ndi nkhani yake.Mwatibowa Mkufuna Chani Kwamsogoleri.Mzipanga Zanu.Kkkkkkk
INU OSUTSA MUMAYESA ANENA KUTI, WATULA UNDINDO MWALEMBA MU MADZI. ANAKUTAYILANI THAWI YA CHANI? PEPANI PA N’GONO POKA NDINU MBUZI.
Chifukwa munanama kuti wafa then mwati walumala pano meadows chonena iii musova
chakwera ndi anzakowo dzimitu dzanu furish
Pamalawi otsusa awa ndi mbuzi zeni zeni zedi awa olo boma litanena chithu chothandiza bwanji asusa basi
The problem is Malawi opposition do not know what to do as opposition. They need to be taught what it means to be an opposition party. It’s very dangerous to leave God and go for earthly things. From church to politics……. Very bad
Nanuso fundo muribe nkharani pasi chakwera anthu ambiri anamuvotera and 2019 apezaso mavote migoromigoro musanimizire zamipinga man tiyenitiyese munthu wamulunguyi
Sizizatheka chakwera kulamupa dziko la malawi God sent chakwera here to win the souls not politics and its very dangerous to a person kugwa mmanja mwa mulungu ndikukayamba ndale
Chaxweraso sangathe
mukunama nosenu
Atleast We Saw both of his Hands working ….Spicing up the whole event he challenged Chilemba into a Fight ….
Mmmmm cd yake mmm yokalika
Tembo ánasiyila chitsiru ndye ķu çhurchko unķalarikira chani kumáti man of god ukufuna tate wanga adiwe esheeeeeeeeeeeeeeeeee jusus Christ of nazaret
Boma ilooooooo!
INE BOLANDINAMVAKUTI ALIBWINO MTIMAWANGA PANO ULI MMALO..
Hahahaha, ndiye?? Otsutsa inu, nthawi anaonongayo ndiyanu? Inuyoso mukamatsutsa zilizonse mudziwe kuti mmangotaya nthawi nanu
Kkkkk point taken
Kkkkkkkkkkkk ok
nonse anthu akumwera mudzatha mano mkamwa ngati mbuzi yanuyo! stupid apm n o pple 4rm southern
zopusa basi
ENANU MUKUNGO LANKHULA NGATI WAKULEMBANI GANYU BWAMPINIYO
MCP. Never come back in government mpaka chiweluzo mukanabwele 2004 anayimila agwanda chakuamba.pano zingobwebwetani azanu akudya makobiti
Rest In Peace Gwanda Chakwamba
That was a fools paradise
Kodi nakono akuti chani kumeneko
Amazitcha Amalawi Okonda Ziko Pomwe Ali Ansanje Kufuna Ng@ Atalamulira Ndiwowo Koma Sakuziwa Kt Sizingatheke…An2 Akulu Akulu Bt Actng Lyk Small Brainz_iwowo Osapanga Wawo Msonkhano Watola Nkhani Bwanj Mwina Ayankhula Zamutu
2019 CHAKWELA BOMA
Anakutaisani nthawi bwanji popeza Peter Munthalika wa osusa anamwalira koma uyu ndi wa a Malawi omwe anamva zomwe amanena. Inunso mumakamvela zolankhula wakufa munatiuza kuti wafayo. Pamenepo wakufa ndi ndani? Chakwera unalephera ku mpingo walepheranso ndale yang`ana china chochita basi kkkkkkkkkkkkkkk
Apa chakula ndi chamba mumasutila dziyeso ?
Atsogoleri otsutsa amasowa zokamba then amangobwebwetuka zopandapake bola atsutsa basi shame ok!
Munthuyu uyutu akungotichedwetsa
folllowing
zokamba mbwete mmafuna afe kapena?
You have nothing to say bcz you failed to lead the church members.
Mulibe nkhan, bola mudzingokhala kunyumba kwanuko mudzionela #zuku_tv (shat up
Inu Ndi Otsutsadi Ndi Chazelu Chomwe
All these comments just shows most commentators have blank heads, they don’t know what they are commenting on. Mind poverty at its best
Muxut chaniso inu nd poverty yanuyo
Ulesi iwe! Ukufuna pulezident akugulire zovala?
Ulesi iwe! Ukufuna pulezident akugulire zovala?
Ulesi iwe! Ukufuna pulezident akugulire zovala?
muzilephera kulimbikira pakhomo panu nkumafa ndi njala kuti ndi ntchito ya president kuthetsa njalaaa??? amalawiii
you don’t understand, that’s why #binwell akuti you have blank heads…….. makani thoooo koma mmutu muli mamina ……. olo mutalimbikira kugwira ntchito. koma ngati ndondomeko za boma zoyendetsera dziko zisali bwino, ambiri amagonabe ndi njala malawi nkumatha zaka 10000 osatukuka…….. just use your brain ……. ukuona ngati ukusangalala ukuvutika……. tiyeni tikaone agogo ako kumudzi ngati zawo zili bwino …….
Mumafuna kuti akuuzeni kuti watula pansi udindo ndipamene mukanaona kuti sanataise nthawi AMALAWI eti? Osamatero tatiyeni nthawi zina tizifuniranako zabwino.
muwakhululukire anapitirako kudya osati mfundo zothandiza dziko,takhuzidwa ndi mliri wanjala ndi kuzima zima kwa magesi
Mutakhala inu mungatheee ngati mukulephera kupeza mfundo zothetsera mavuto a m’banja mwanu ndiye a dziko mungakwanitseeee
Bertha kut mubwele mzaone banja langa mukhoza kusilira zamavuto izo iwalani the entire family relies on me boma lot ndalama timapanga ndifeyo iwo osazivutikira basi kulephera zamanyazi
Makamaka ataona kuti ali bwino bwino
Mumafuna kuti agawe ndalama kapena?kususuka basi!!:):/;(
bwana mwakweza kwambiri chimanga ine ndimalandira thirty nyumba fifteen balance mwana ku school
Mugolima chanu basi muzigulitsa 5pin
Achakwera ndi anzanuwo mukungotukwanidwapotu ulere apa… chonchi ndiye mulowa m’boma in,mfundo zake zimenezi?
whch bible verse says “mucye ubusa mukayambe ndale”??????? wat do u want 4rm our apresident 2 do 4 u …..lets gve hm afull support we ar all malawians & once ur wu cme we gve u also full support czchamba mukuyakhurazi apa “ichi mwakamba ichi mwakamba osaziwa kut znu ziiipa”
zonsezo ife akumuzi tingofuna chmanga chisike bas 12500 yachuluka were falled 2 buy it plz fanz lets talk abaut it
Pajat anathawa yautumik amei
Inunso mwandionongera nthawi yanga powerenga post yanuyi.
Kkkkkkkkkk mavota-vota anu amenewo
kkkkkk kuthamangira kukamba nkhani zopanda umboni. ndinati ine kwanga ndikumangoona.
Wanenay Ndan? Lazalo Wauphawi? Hihihi Wayamb Kale Kunjenjemela. Amaona Ngat Amwalira? Wauponda Judax Ndp Ayambe Kufa Lazalo Akhot Akamulamul Kt Apange Covention. Mu2 Umaseka Mchira Wazako Kt Ndwautali Pomwe Wako Wacht Kumangl Nkhata Pamsana?Ukhalir Yoxuxa Yomwey Adzako Tkukhalir Matako
Palibe chanzeru apa
NKHANI MULINAZO NDIZOMWEZO BASI,ZANDALE NDIKUKAMBA BOMA???
Chakwela Ndi Amzake Akutisokoneza Kobasi, Poyamba They Made Us Belive Kuti Msogoleli Wathu Wathawa, Then anatiuza kuti he is spending our money wherever he is, chomwe chinatikwiyisa kwambili, anapekanso nkhani ina kuti a dad akudwala sali fit kulamula, anazabwelanso kuzati adad atisiya, izi zinatizunguza bongo kwabasi, anatipangisa kuti timuitanise mwachangu, atabwela, anatijambulila mkono waku manja pafupi nationesa kuti mkonowo wafa(we are not even sure if it was really his hand) Kenako Anati Adad Apange Press Comf, Anapanga Timaona Munthu Uja Akuyankhula Mwa M’didi, Akuonesaso Manja Abwinobwino, Pano Nde Akuti Anangotitayisa Nthawi? Chimakhala Chili Chani Kodi? Kusowa Zochita Kapena Kusavala #mwado?
vuto ndi nsanje basi. nkhuli yolamula ikuwapweteka
vuto ndi nsanje basi. nkhuli yolamula ikuwapweteka
kkkkkkkk
vuto ndinuyo mukuombela manja zilizonse!
amakhala ali toBAcco
Kkkkkkkkkkkkkk dziko ndi choncho
kkkkkk kusavala mwado
nsanje basi
otsutsa akumadya mbanje kwambiri now plz olamula nxt time musazaloreso kuti otsutsa azilima bale bt chimangs coz akaluma mbanje zawozo akumakgalila kusota kufuna kut nafe tifoyire nawo
Ubwino wake amaononga nthawi yake osati ya abambo anu. Kundinyansa kwake agalu inu otsutsa!
they thot anena kut ndatula pasi udindo kkkkkkkkkkk
Kma Yaa, Kukhala Kuja Mwat Wamwalira, ku Bwela Ku Mudzi Osalakhula, Mwa Wapaga Strok, Nde Wayakhula Mwatiso Bwelera Eeah, Ana Ajoka Inu, Panja Mukamulemphela Munthu, Muma Kanyela Pakhomo Kt Aponde, Tsonot Satuluka Mpaka Manyi Anu Auma.
Mburi za ndale agalu
Nkhani ili apa ndi ya Mthalika koma ena mukumba za Chilima Guys zikugwirizana bwanji ? Mulungu akukhululukeni nonse
Zoona
Mmmmm Mmesa Ndi Otsutsa? Mgati Asatsutse Ndiye Akhala Bwanj Otsutsa?
Mpake mulidi otsutsa, mnsonkhano unachitika lachisanu inu lero ndimukukabwera ndimaganizo amenewa. Inu ndizitsiru zotsutsadi, kuteroku mumafufuza ndalama zomwe zinaonongekatu ndimisala yanuyo. Fatsani anthu azakuvoterani, akakuonani kuti muli ndinzeru koma apo bii mudzakhalira yosavomereza zotsatira zachitsankho kuti akuberani akhakhakha inu zako Chakwera izo.
Otsusa akumalawi samadziwa udindo wawo mwina mukanachotsa mawu oti otsusa muziti othandizira boma mwina akanaziwa udindo wawo.
Koma amafuna chani? Amve kuti satha kuyankhula chifukwa wadwala? Afiti. Jesus is coming soon. You gonna roast in surphur.
Koma yaah, ntchito iliko kuno kwathu.
Zoonadi palibe chanzeru tinatolapo ,zacjamba basi
Kapangitseni wanu mawa anthu ansanje inu
Kkkkkkkkkkk koma otsusa boma mulibe mzeru ndithu, kodi mmesa ndinu mumati apangise msonkhano wa atolankhani kkkkkkkkkkk
Otsutsawa lachuluka ndi dyela… makamaka uyu, uyu uyu mumati Chakwela yi… money hungry lions
Iwe ona zako upindura chan kooo kazisokora ndale sadya
Malawi24 bwanji mukayamba nkhani simumaliza? zomatipatsa ma link enafe zimatibhowa!
Ajames bwinotu ndibwera kunyumba kwako ndikagumura kamsasa kakokaja mmxxxmmmm
Opposition ndi choncho
Ine ndikudzudzula onse include leader of opposition nchito yawo sakuidziwa,Dziko sila peter yekha koma tonse ine problem will face 2gether.Chakwela aganize bwino ali udindo waukulu womuongolera president akalakwitsa osati kumuloza chala sadziwa polakwika
Ndale zapa Malawi wolewole
Aaa zaziiii mkuvutisa chabe anthu wambafe nonse ndi zisilu bwanji
Ameneyu anayenela kukhala body guard wa chilima because amaoneka okwiya nthawi zonse hahahahahaha!!!!
Ntchito yawo ndiku sutsa pls pple understand them
khani zandale zovutakuvesa, kulimbananazo mutu umangopweteka ngati masile a mkalabongo osadyela.
koma zatikwana zimenezi tsiku ndi tsiku nkhabi yomweyomweyo zaziiii!!!!!
koma zatikwana zimenezi tsiku ndi tsiku nkhabi yomweyomweyo zaziiii!!!!!
Pamya pawo otsutsao mesa zomwe ankafuna ananva?amafuna atanva zoti nkono wamanja uja wasiya ku gwira nthito?nmafuna munve zot wasiya kupuma n’dalayu eti?????mwanya!!
chitani manyazi
Ine Nduganiza Kuti, A president Sadataye Nthawi Ndi Press Conference. Osutsa Boma Asaiwale Dala Kuti President Amafotokozera a Malawi Za Ulendo Wake Wa ku Unga, Komanso Kutsutsa Poyera Bodza Lomwe Osutsa Bomawa Anabweretsa Loti President Sakutha Kulankhula wadwalika Pomwe Sizinali Choncho. Bomatu Sayendetsera Pa Press Conference, Dzuka Malawi Dzuka!!
Ambuye…Otsutsa boma akungosusa ndi zoona zomwe. They have been realised to be confusionists because their plans have failed. So no wonder when your hear them with their destructive criticisms!
ko.
Otsutsawaso asatitopese adikile nthawi yawo,iwowo akupangapo chani muxipani zawozo kumangochotsa anthu ndizimene amadziwa zaziii
Mongokumbutsa chabe thumba la chimanga LA 50kg ndi 12500 ”’,,ndiye paja akuluwa alibe pulobulemu tisova basi
Pajatu thumbali ADMARC imagula pa 11000 (220/kg) mmayembekeza kuti aligulisa pabwanji sir?
From 5000 to 12500 ndikuwona kuti monga boma silinaganize bwino ambiri mwayi ife ntchito yanthu ndi yopelekela matope ndiye adatiganizilako sir ,,mukuwona bwaji inu
Samalani ndalama yoperekera matopeyo mukagulile chimanga! Ndipo sichingatsikeso kuposa pamenepa ndie kuti sikumalawi.pompa chakwanila.
Katundu ukamugula modula umagulisatso modula,akakhala mavto sanayambe lero
Ntengo ogulira uja udaoneseretu kuti chimanga chikwera ntengo. mukawonesesa muona kuti ayikapo 1500 yomwe ikuonaso transportation, packaging, fumigation and other services. mukaona zosezi muona kuti boma silinapange profit yoti nkumakamba izi tikukambazi. koma poti ndife anthu ayi tiyeni tizikambani
komaso sir paja zipangizo za ulimi akuluwa anasitsa monga muja anatiuzira pa misonkhano yokopa anthu 2014
Zachisoni kwambiri dziko lamalawi
Ma corporate company sayendetsedwa kuti azipanga profit koma kuthandiza ma citizens, apopo musinthe maganizidwe anu Gilbert..
ife sanatitaitse nthaw tsoka kwa iwe otaitsidwa nthawi munthaw ngati imene ija.
akapanda kutsutsa akhalaso otsutsa
Inu nomwe mumakakamiza Mutharika kut achitise mnsonkhano wa a tolankha,lero mukut anangotaisa nthawi?Ndie mumafuna chani apuludzu inu?otsutsa akumalawi amenewo kkkkk zamanyaz ndithu.nchifukwa chake munaba ndalama za ku assembless of God etiii
Atokotere
kkkkkkkk muuze mbuz ya munthu ngat imeneyi chakwela ndiye kut chani
Ineso basi sndinena kanthu mwakwanila man
kkkkkkk hahaha
zankutu zenizeni! kodi kutsutsa ndie kuti chilichose usayamikileko? misunderstanding mxiiiiiiii
Mmmm
Kkkkk asamajaire anyani amenewa
Koma kumeneko kkkkkkk
hahaha koma zoona anangotayadi nthawi, nanga ndi chani chanzeru chomwe anauzapo mtundu wa Malawi? bwerela zokhazokha basi
Aaaa Zaziiii !
zanu izo
Eeee muuzeni kapeyu anangotitayitsadi nthawi pachabe dank osutsa mwachita bwino kumuzuzula
Koma kaduka ameneyi mufika nae kuti,kod akati kutsutsa ndichoncho? Munya,mukhala choncho ndi nsanje yanuyo agulu inu mixeeew.
anangotha nthawi kumene ,just speaking of zodiak,kungot president chlungamo by zodiak chidamuwawa zedi
Kod palibepo chanzeru chimene ananenapo
Iwe admin aku-trapa 2,ndikuona ngati wameza Chimtuwisa
Kutsutsa ndikupanda mzelu sizinatalikane kwen-kwen
Ankafuna kt osawafunila zabwino onse apange manyazi
Yanga sanataye
Kikikk Anangovutikadi Kupangitsa Nsonkhano..
ameneyo nd osusayo
kkkkk ndiye osusao nanga atani lingolowa dzuwa asadasuse sangagonetu tsiku limenelo
Such Z Lyf Aliyense Pa Ntchito Yake Kutsutsa Or Kulamula Osewa Nd Amodzi Amageya Mkaka
Nthawi zonse otsusa ndichoncho