Nduna yoona zofalitsa nkhani imenenso ili mneneri wa boma a Malison Ndau auza atolankhani ndi mabungwe ena amene amafuna kuti iwo apepese ati kamba koti ananena bodza pa za umoyo wa mtsogoleri wa dziko lino kuti iwo sangapepese.
Mabungwe ena omwe si a boma anakhala akuyimba milandu a Ndau kuti apepese pouza mtundu wa a Malawi kuti a Peter Mutharika ali ndi moyo wangwiro ku Amereka. Koma a Mutharika atabwela ananena kuti io nyamakazi inawasautsa ku Amereka kutanthauza kuti amadwala.
Koma poyankhulapo pa nkhaniyi, a Ndau amene amanenela boma ndipo anaopseza kuti anjata anthu amene anali kutchukitsa kuti a Mutharika anali akudwala anayankhula kuti sangapepese.
“Ine sindinaname iyayi, ine ndimanenela boma ndipo ndinanena zimene a boma amadziwa. Ku boma timadziwa kuti a Mutharika ali wangwiro ndipo sitinaname konse,” anatero a Ndau.
“Choyenela kudziwa ndi choti a Mutharika ali ndi moyo wawo umene pena umayenda opanda a ku boma kudziwa, nkhani ya matenda iyi sitinauzidwe poti sanali matenda enieni,” anaonjezelapo a Ndau.
A mabungwe anapsela mtima a Ndau ati chifukwa ananena kuti Mutharika ndi wangwiro koma mwini wache ananena za nyamakazi. Koma ngakhale zili choncho, a Mutharika ananena kuti nyamakazi imene inawavuta sinali vuto kwenikweni.
“Kanali chabe ka nyamakazi kamene kanavuta, ndipo ine ndikudziwa palibe munthu anafapo ndi nyamakazi kupatula mwina ku Zodiak,” anatelo a Mutharika polankhula ndi atolankhani lachisanu.
A Mutharika anakhala ku dziko la Amereka misonkhano imene anapitila itatha. Iwo anaonjezela kukhala kwawo ndi masabata awiri. Izi zinapangitsa anthu kuyamba kufalitsa nkhani.
Zinatchukitsidwa kuti a Mutharika akudwala. Iwo atabwela mdziko muno anaonjezela mphekesela izi pokanika kugwilitsa ntchito mkono wawo ma dzanja la manja.
zoona palbe wamuyaya
Eish
Ngati anakana kupepesa …… Ndee mukuganiza uyu angapepese
Guys musavutike mu africa savomela kupepesa
Show
gyz mukuwonabwanji tingomupha peter chifkwa watizunguzarrtu
kukhala m’malawi gyz sikophweka m’malo momawona zamagetsi tili bzy nd za munthu m’modzi modzi gyz think twice zichite kutha mwezi nkhani zosatukula dzikoziiii ???????????
Amw mukumu kakamiza munthu kudwala mukumva ululu ndinu?sakuti samwa lila ai koma kuti musa chite kumupangila sibwino
amupepese ndani?Zopusa
Time will come that you will need us!!!
Sometymc i blame myslf y i was born in teritory of malawi bcoz of same issues like this akuti apepese kaya akufuna apepese chani kaya , kukakamira zinthu xopanda phindu basi God forbid n mercy on u Amen
Atumbuka akut matenda bisan nyifwa tizamulira tose nde ngat a president ankadwala kumene anali palibeso zopepetsa apa stupid well done Mr Ndau
What comes around goes around zivere mtolo wasala madzi amozi uyu msiyeni analipo anthuanthu siawa
ndikupepeser ndine
Tizingomphempherelana
Olo asapepese idon,t care
Kikikikikikiki!wat a governmnt,apology 4 wat?kudwala ndi kudwala basi.so he thnk he z so strong,apology nt needed at all
Kkkkkkkkkkkk akapepesa ndiye mutani?kufuna ulemu basi, muuze akwanu akupepeseni
Ukukana kupepesa ngati ndani iweo? koma ukutidziwa bwino bwino kuti ndife ayani?uona polekera come 2019 khala choncho usapepese!
Ukufuna akapepesa ndiye utanino iweo
Palibe chomwe ndingapange atapepesa,koma nkhani ndiyakuti ali kumeneko kutumikira ife a malawi,nde asamabise chinachilichonse chizikhala poyera tonsefe ndife amodzi nde that guy akuyenera kapepesa ku mtundu wa a malawi chifukwa chosanena zithu zoona.
Apepesa bwanji munthu amauza mtundu wa a malawi zomwe DPP govt inamutuma.
Tizaona ngat suzapepesa 2019
Tizaona ngat suzapepesa 2019
Tizaona ngat suzapepesa 2019
andalewa kungowasiya sakuva madandaulo ayife koma thawi yovota timafunika
Dzimenedzo ndiye mdzauchitsilu,kodi nkulu wako uja alikuti? Ngati adapita iyeyo nangaiwe ndiye ndani?kodi ukuganidzakuti ungadziombole ndi chuma chako?chibwana chimenecho,mulungu wakuchilitsani kuti mube komaliza akubwela adzakutengeni,ngati nthawi yakwana palibe kupsatila,payele payele basi,kapumeni mwaba mokwanila,
Ngati umatha kolodza anthu akwani president siwakwanu anthu agule iwe
Iwe ukunena mozitama ngati suzafa? uyambe wafunsa anthu akwanu kuti abale ako ena ali kuti before kulankhula moputsa chomcho wamva #James nkhumba yamunthu iwe. Ndipo uyambe kufa ndi iweyo before APM
Iwe Nkanda choyamba ndikuti panyopako, ngati umalodza anthu ndikwanukomweko mfiti iwe. Ukuwona ngati kuti iye atamwalira angavutike maikidwe, ameneyu dziko lonse kuziwa kusiyana ndi mphawi ngati iwe odya zotoleza ngati nkhumba. Uwona, ufa ndi cholera akubwera posachedwapa tione ngati anthu angamve zoti fisi winawake wamwalira. Usazayambilenso kulankhula mopusa, panyopako basi ndapita ndikukagona uyetse kuzanditambira ndikutchola pomwepo.
KKKKKK kkkkkkkk zivele wekha fan pirta ok
Mwina akuziona ngati chitsulo. Palibe kupepesa PETER ndi odwara basi, olo zibagera sangalimbe nazo. Wa miyoyo nine amaliliranso kupepetsedwa utsilu eti?, mwaiwara kuti manda aja akutidikira a moyofe. Utsogoleri muzawasiyira ena ku dziko kuno akulamulira iwe{peter} uzapita ulibe kali konse.
Koma ameneyu! amayenera kupepesa basi. Kodi iyeu mese ndi mbusa? Kapena ndiwasataniki eti?
Ukayambe wafusa chakwela kt anali ndani asana bwere ku ndale
Anthu a kugona mu mdima wopanda magetsi anayamba wapepesa who is he to people If he is failure to deliver even little thing to Malawian citizen shame on you
Ukadwala ikhala nkhaniso.Mulungu amaona sungabitse chinachilichonse.sungabitse matenda pamene ukudwala.Tithokoze Poti Chauta Anatipatsa Moyo.Anthufe timatenga moyo ngati wathu mwini wake alipo.moyo 2 sagula ngakhale ukhale ndindalama zochuluka bwanj sungagule moyo.Heart is a precious
that’s why i don’t support any political party,
Kaya Zawo Izo
Zinavuta anzanu izo
Mutharika ananena pa press conference kuti if there is any1 to blame is him,not mgeme or Ndau.ma journalist aku Malawi simumamva olo pang’ ono.APM is the 1 to apologize not ndau or mgeme,koma mukumuopa that’s y mukulimbana ndi mgeme.
Palinxo xopepesa pamenepa kkkkkk kma guyx u nid 2 think wisely b4 u talk,,, musapepese biggy,, ximenezo kwao konko pamtundu pao
But you dont owe any one apology .why should you apologise ?
Honourable wa analeledwa pachilolo kwao,ziwani izi kamba ukamzampeza ali mumtengo alipo anamukwezamo,tikutsisani 2019 madolo alero ndimakape amawa.
Angati tinawina tili ku opposition nanjino pano tili m’boma kale ndiye 2019,tingalephere kulamulilaso sumadziwa ndale iwe ukatenge social ngati umaphumzila
Kkkkkk #Ruth tamuwuze munthu opanda mfundoyi mwina saziwa
Iweyo umadziwa chani?u youth mulalo wakowo komko pano ayi,kuzolowera kuyimba ng’oma kumitsokhano yandale eti? Malo mogwira ntchito otukuka ndi Honourable inu mkumatuwa ngati nsomba yabakayao.
Ine social sindikatenga koma iweyo zilibwino popeza ukuyenda nayo mkabudulamo
Kkkkkkkkk. Ayaluka. The sky is a limit.
tawasiyani awa paja ndichoncho ena ajanso amkatelo ndikut munkhito SAPEPESA!!!
apepetsa ngati anaba bwana ndau
Chelsea 2 Man u 0
Musaiwale kuti khoswe akakhala pa nkhate sapheka
Apepesa bwanji chilungamo alibe. Andale ndiye bola kumangosapota mpiratu kkkk
OK Mukhitosotu anatelo kenako China China chitika.
Zimenezi Nd Zopanda Job Yomwe Pa Aktelo Dziko Lamkanka Ku Lilamla Adzibisa Matenda Nd Kape Ameneyo
Kaya zawo ife kwanthu nkulila basi magesi anyanya hevy
Kd Osamuuza Chakwela Kt Apepese Kt Akuthamagitsa Anthu Achipan Chake Bwa?
choncho malawi can it be developed,let look kodi munthu wanjala nkutukula dziko? amalawi amavutika popeza money koma akaipeza kugula chimanga(food) but zikumapezekazo kuti magetsi kulibe. ndiye tiyeni tidzikambirana nkhani ngati za magetsi kuti titukule dziko lanthu osati zosathandizazo.lets change malawi
Ndani anaulura zisitsi za bwana wake munthuyo adakali kugwira ntchito. Pokhapokha mchere watha.
Okufa lero safa mmawa azipepese yekha
Bwanji sanapepese atanena kuti anthu azidya ,mbewa makoswe ngumbi udzudzu nkhanu ndi dziewala.nkumaseka kkkk ndi joke ndiye ndau amatha joke nayeso
Amangidwe cz paja anena kuti aliyese ochita bodza pa fb pa nkhani ya mtsogoleri wathu adzinjatidwa
kukula mtima basi akakuchosa ndiye uzilira ?
Chilungamo chimapweteka,andau akudziwa choona koma sanganene.
Palibe kupepesa apa mwatende amabungweo atende yao ngawa ya mmwejo iyayi
Kodi supepesa chifukwa chani? Iweyo makani? Fotseki ndiwe ndani kuti usapepese? Ngati ulimwano tionana 2019 sharp.
Sitikuopa 2019 dilu ndi chimanga tizalamulilaso ngati tinatenga boma till ku opposition ndiye tikakanike kuwina 2019 manyazi mulibe
Just wait and see,mukati dilu mchimanga, munena chapa msalu,ife timafuna chakunkhokwe
Chilipo masiku ano kumangouzana chilungamo basi wachita bwino
Kupepesa dzi chani azi patse ulemu amuthalikawo asadzi tukwanitse koda kale ngati kuno sindikufuna ndi tsuke nkamwa prz kodi n.yeyo ndi chitsulo akati adzi uza anthu kuti apepese kuntundu wa amalawi muthalikayo ngati wadzipopa ango ima po ela ndikuuza anthu kuti ali bwino osati nkhani zama #buzi akunenazo fuck muthalika upange zaineyo bwanji ineso ndimodzi amene ndima uza anthu bolani mr ndau siama uza anthu kuti iweyo ukudwala koma ine nde ndima uza anthu kuti iweyo wa mwalila nde azungu kwamerika akupanga prastic sajaly akufuna amu veke waku banja la amuthalika iweyo ndi fake piter muthalika kana ngati ndiku nama nyamakaz ya chani vuto la atsogoleli okwatila pokha pokha mukapatsidwa npando ndi choncho banja ukalilowa uta kula kale zima telo ndinkani makolo amango wasiya ana akamapanga chibwezi kuti a chotsane uviligo amakana zodwala dwalazo kaya zako izo adah
komandiye opitalawo olalatidwatu,mpaka meepo ofilipo?
Mupepe
osadanda Ndau ndkupepesera ineyo
Apology not needed, Muntharika and the rest of his crews knws kuti ndi zooona. Aliyense amadwala and adzadwala, chokanira ndi chiyani. Yamikani Chauta kuti wakupatsani moyo, tsiku la wina aliyense likakwana basi ndi ulendo basi. Kumvomereza ndi kwabwino abale.
apepese chani ndipo kwandani
Tiyeni nazoni
Funso ndi loti kodi abwanao sakudwala full stop? Apepese ngati sakudwala koma ngati akudwala palibe chopepesa. Nokha mukuona nkonowo tu kuti muthuyu ngodwala tasiani zopusazo tu.
paja mumkati atisiya ndiye uyankhidwa ukafunsa choncho
Uwayankhe tu iweeyo ine unditumizila pa sma.
Kodi Godfrey Danreck.ukuti chain..?Peter ali ndi vuto dzanja lamanja kapena ayi..?
Usapepese ndau olo apepese zitipindulira chani
anakulera mopusa,uzautaya mchele 2019 mumat munakhalitsa kuamericako 4 the benefit of malawians palibe ndimfundo yogwila ntima pa presidential press tiyembekeza kut mutiuza mfundo zenizen!zachison kwambiri childish gvt
Agogo ako akauze azaimilile 2019
unaleredwa mopusa,uzautaya mchele 2019 mumat munakhalitsa kuamericako 4 the benefit of malawians palibe ndimfundo yogwila ntima pa presidential press tiyembekeza kut mutiuza mfundo zenizen!zachison kwambiri childish gvt
Apepesa bwanji pamene anenaokha kwa atolakhani kut,amadwala nyamakazi.
Kodi Nyamakazi Simatenda?Ok Nyamakazi Yomweyo Mpaka Admited Kuchipatala Kuamelika?Asamangidwe,amangidwe Iyeyo Waononga Ndalama Zathu.
Chilungamo ndichofunika asakuke mtma atipepese amayesa ife ndiogona.
Kkkkkkkkk kaya tiziona ZIKANA NKHALA MBUZI TIKANATI SIZINAPITE KUBUSA MASIKU ATATU .
ANKATHAMANGA NDI NCHELE NKHUMBA ISANAFE PANO AKANAKUDYA DEYA MWINA ADASUTA KUM’MUSI YA…..KKKKK …WAPEPESAKALE M’MAGANIZO KUTELOKO M’MANYAZI .
Recycled craps!
WAYITHA KOMA AKUTHAMANGITSA
A Muthari nd mstongoleri wadzi iwo akalamakhula asamakhale akupanga point zala kuti koma ZBS AI! And a Ndau musaiwale kuti izakwananso thawi inja imene mudzawafune anthu kuti akuikeninso pamene mulipo. Mtsongoleri Is not God kuti iye sangadwale AI kaya inali nyamakazi kaya zinali zina ife sizikutikhuza. Pano zibisani zonso nafe tizabisa mthawiyo muzatifuna
zopusa