Police in Nkhotakota district are keeping in custody Robert Bizayi, 35, for raping a 5 year-old girl in the district.
According to Nkhotakota Police Public Relations Officer Sub Inspector Williams Kaponda, the suspect over the weekend was caught red-handed raping the child.
“The mother of the victim prepared breakfast for her two kids and when she called them to eat they were nowhere to be seen,” said Kaponda.
The woman started looking for the child and she found her being sexually abused by the paedophile.
Medical examination conducted at Malowa Health Centre revealed that the victim had been raped.
The rapist will appear in court soon to answer the charge of defilement.
He hails from Ndevu village, Traditional Authority Mwadzama in Nkhotakota district.
KOMA VUTO NDICHIANI KODI ?
Akazi onsewa akusowa amunawa kumalimbana ndi ana osalakwa ufiti chiyani? Akazi mpaka afika pomayenda kote neked kt mwina apeze owapatsa tulo milandu ngati iyi oro atati 4life sanamulakwire #ROBART
Chop off his penis 4gud,so that he will come 2know the benefit of his action
Mmupitise kwa Judge Micheal Mtambo akaonane komweko. Matama akewo akauthera. Akuzionetsa ngati angakayime mu ring ndi judge Proffessor Mtambo. Akafunakuziwa zambiri za Judge Mtambo afufuze kwa Raph Kasambala, Pika Manondo Kapena ndani uyu uyu uyu eyaaa Mc Donard Kumwembe. Kapena akachezera limozi kumene mabwanawa apita. Akamfotokozera zonse. Mtambo asakuderere mwanayu izamuonetse!!
Chimchira Chopanda Manyazicho Chinafunika Chikana Pita Ku Mchinji, Mtsikana Wa 20 Wakakamiza Boy 9.Ndeuyu Wa 32 Anafunika Apite Mu 2o Ndikuwadikira Kwa Zaka.Kunkhwima.
Ngati chinali chamba nde chikupweteketsa!!!
Mumuphe kuti ena atengelepo phunzilo
Mwina Ndiwamisara
Malawi Akupta Kt Guyz
Bull!you have the certificate and now you dont want ur children to have it what a shame?tocut the cost why dont u stop nosence travelling and put the exams on board stupid idiots.shit
Mwana otelo sasesato thawi zambiri samanva kunukhaaaaa
Zamanyazi akotakota
wagogera ka nsapato kamwana… Mkwidzingeni basi.
Afele kundende ameneyu!
mselu bwaaaaaaaa
selu bwaaaaaaaa
Amangidwe basi ameneyo
Uchitsilu wake ndi munchiuno mwake mwampangitsa kugwila mbendela ,chepetsani amalawi mahule achuluka
Asamusekere angomudura mbolo yakeyo basi asazachindeso galu ameneyu kukhwima chani?
Chamba basiii iyaaaa……m.
Atchpirenj hule
He deserves to die dat idiot
Ha ha ha pamwana
Kma zinazi; mwna wazaka 5 kma abambo mutu wao net work yilibwno bwno kma? akungownonga ana a eni ake za chamba basi znazi!!
eee waonjeza
Zanyanya iii ogwirira akuchulukirabe
Koma nanu anthu a ku Khotakota,mpakana munthu oipa ameneu akapezeke in police custody,how? Mwaphweketsatu bwezi titi tizimva kuti ali #mmanda bola.
n’chiyani kodi aMALAWI?
agwililira aziphedwa chifukwa nde chikusanduka chisimo …..kupusa aziBambo enawaa
Kwa Manje kuno 400 imatheka kumeneko akudula??? bwanji? minyamatu imeneyo
Analowetsa koma..?kapena anangogunditsa?kkkkk kma anthu ena inu kungoti chilakolako nchovuta ndiye basi aaah osangomenya ka m’manja bwanji..?concerned much with this stupid behavior…..
And then he’ll walk out free, #shame_on_thee
eishiiiii nchiyan kodi a Malawi?
Zoziyamba dala.
Amenewo ndiye manyi osamupha ndi mfuti koma anyongedwe bassi zaka zonsezo kugwiririla mwana wa zaka 5 palukundupo chimbolo chokhwima osamva chisoni zawumve basi
nyele zanuzi muva nazo kuwawa zachamba eti
Koma amalawi ndemwana wazaka 5years amakoma chani pot olo ndisikhu omwe amakhala kut sanathe inu ndevu tho kugwilira mwan olo manyaz mulibe kod kumakhala kukhwima kapena chani…….
Ganja
Apolice gwirani azibambo opusawo asamatuluke mukagwilamo
Defile and rape ar different ….
Azimai osewa mukumalimbana ndi ana bwanji
kumeko ndiye kigwirira osati mdala wa zaka 80 uja ayi !!!! amene uja anagwiriridwa ¥¥¥ uyu akafere kundende komweko chifukwa ndi mfiti ¥¥wakupha
Anthu akusowa umunthu….May God end this kinda world..kukhwima kapena chani?????
Azibambo enanu mbolo mungonyamulila m’manja!
kodi akazi akuluakuluwa ndekuti akuvuta? am so puzzled with this issue
Raping??????
Azibambo Enawa Ku khwima Eti!!