Gulu la a Malawi okonda chakumwa lakwiya koopsa ndi malingaliro omwe mabungwe ena kaunena oti pakufunika malamulo oletsa a Malawi kumwa mowa pa nyengo zina.
Pothilira ndemanga pa nkhani yomwe ife a Malawi24 tinalemba yoti bungwe lina lomwe si la boma la Drug Fight Malawi likupempha boma kuti lichite machawi kuvomeleza ndondomeko yoona za kamwede kamowa yomwe pachingelezi ikutchedwa National Alcohol Policy, a Malawi anasonyeza kuti ndi osakondwa kuti anthu ena akufuna pakhale malamulo a padera oona za kamwedwe ka mowa.
“Linotu si dziko la chipembedzo chinachake, musayese ndi la Chislamu kapena Chikhristu. Tisiyeni tizipyoza mowa wathu,” wina analemba monyangala.
“Aaah mukufuna mudziko muno mukhale anthu ochepatu chifukwa tonse a mowa tisamukila ku mayiko amene kuli mowa,” wina anaopseza motelo.
Wina popowa kulankhula zambiri, anangonena kuti: “zopusa zimenezo!”
Koma mkulu wa bungwe la Drug Fight Malawi amene akutsogolera mabungwe amene akufuna kuti pakhale malamulo okhwima pakamwedwe ka mowa, a Nelson Zakeyu ananena kuti cholinga chawo ndi chakuti boma liteteze anthu ku mowa, makamaka a chichepere.
“Boma likuyenela kuvomeleza ndondomeko zatsopano izi zomwe zikukhudzana ndi kamwede, kagulitsidwe ndi kapezekedwe ka mowa. Cholinga chake ndi choti titeteze anthu ku mowa, makamaka achinyamata amene akuonongedwa ndi mowa,” anatero a Zakeyu.
Koma mawu awo sikuti akondweletsa a Malawi amene akuoneka kuti amakonda chokumwa chawo moopsa.
Chokani apa ma soberman inu.Beer imwedwe basi, asakufuna asiye!!
drink beer to save water
Ndalama zomwera mowa zimakhala zake.munthu akhoza kumwa mowa nthawi yimene akufuna as long as drinking joints are open
Boza
lie malawi24
Mukweze kwambiri mowao osatikuletsa anthu kumwa, monga momwe amapangila ku sasafulika
Asiyed ine ndikugwilizana nazo chitukuko chikubwelela mbuyo kamba mowa fuck Malawians
Mmalo molimbana ndi njala, matenda nsanje kuonjezapo umbuli. Basi akukamba za mowa. Ndimadana ndi ZAUSILU
Mabungwe kusowa chochita.ntchito zoti akhoza kumagwira zikuwasowa
Zibwana ai muzatilemba ntchito kodi mukaletsa mowawo. Zopusa zanuzo tatopa nazo inu amabungwenu
kkk mw moto kuti buuuu. musamwe mowa koma iye akumwa mowa odula. kkkkk ife tizimwa kachasu emweyo. nakhanso aligulu lamowa. mw watani
Ine sindimwa mowa,koma mukukambazi ndizankutu.amamwera zawo osati za boma ayi,vuto lanu ndi chani?mmalo moletsa mathanyula,zantiii
Kumowa kuli phindu lanji?ena aumati atamwa atagona akumalota akukukuta chinangwa apa akudyelela pamphasa kkkkkkkk zopusa basi
Mukulimbana ndi mowa zaziii mmalo moti mulipemphe BOMA kuti lipemphe kumaiko akunja macampany ochuluka kuti ulova uchepe mungokakamila kulima heee koma amalawife.
bawa nd deal
Timwe tlezele tisaxukexo.
Ndiye matsire amachita madzulo?Leave beer alone! Wachitukuko ndi wachitukuko.Inu simuwaona ma sober ali pa bawo mmawa,umphawi uli thoo
tathanani ndi mavuto monga #kamlepo_kaluwa wagwa pakati pathupa kkkkk mowa tizamwa mpaka kale kkkkkkk mongamso kubanda mpaka kale kkkk
I support the move. Ena amapezeka atalezera as early as 9:00am chonsecho nkazi ndi ana agona ndi njala panyumba. Alteast pakhale malire ma hours omwera mowa. Lets borrow a leaf from Tanzania. Nthawi yoti mzikalima mumapezeka kumowa, njala ikabwera u blame government chonsecho inuyo simulima.
Nde Atipase Zochita Zenizeni. Akufuna Ana Achuluke Mizimu Etii?
Maphunziro ndiye kuti chani, kodi tosefe tikaphunzira tnchito zake zilikuti sibola kumwa mowa. Muli makampani angati muno simukuona anthu ali ku joni akuthawa chani? Sikuti akuthawa mowa koma umphawi zikakukanikani mukunamizila mowa anyapala inu kkkkkkkkk….!
Mukufuna tiyambe ufiti eti??
Don’t drink&drive.
Just raise the tax and make it more expensive. …change the package no packing in small packs…..then that way beer consumption can be reduced. …
omwe ayambisawo ndi masoba en Kodi macompanies omwe amafula mowawu ali ndi fans yochuluka bwanji yomwe imagwira ntchito? Ndiye akaseka macompanies amenewa fans imagwira tchitoyi mutani nayo? sikuchulukisa kuba ukufuna? fuck yu all omwe mwabweresa fundo iyi chifukwa simukuganixira ovutika Koma kuzikunfikira chuma.
Posted in: Corruption. 4 Comments
We as Malawians, we ask President Peter Mutharika to send on force leave the seven cashgate concerned cabinet ministers. Recently Malawi Electoral Commission has suspended its top bosses to pave way for justice and this must apply to civil service and cabinet ministers or else Mutharika must resign as well.
On 29th August 2016, George Chaponda minister of Agriculture and Irrigation was chased and stoned in Mulanje by angry citizens. People started Stoning him and the function was disrupted and Chaponda had to run into his vehicle to save his dear life. People of Mulanje have rejected their own son in his homeland as they consider him to be a betrayer and a cashgate thief. Let us learn hold hands and learn from our brothers and sisters in Mulanje for unity and say ENOUGH IS ENOUGH.
These people are political thugs, they are politically corrupt to finish every little resource Malawi ever had.
Political corruption is the use of powers by government officials for illegitimate private gain. This corruption include bribery, extortion, nepotism, influence of murder, robbery of public funds etc. This government of DPP facilitate criminal enterprise such as drug trafficking, money laundering, and misuse of government power for other purposes, such as repression of political opponents and general police brutality.
Above all DPP and Mutharika are influencing bad politics, threat to elections process e.g (Mchinji elections undermined), bribing MPs to pass bills, bribing Judges and authorities in defending them over corruption (Cashgate), favouring them e,g(20 May 2014 Elections), diverting funds for food, health, development and delaying salaries for civil servants.
In politics, corruption undermines democracy and good governance . Corruption in elections and in the legislature reduces accountability and distorts representation in policy making; corruption in the judiciary compromises the rule of law; and corruption in public administration results in the inefficient provision of services http://www.dzukamalawi.wordpress.com
Nzuru zimenezo ndizopusa kodi zachokela pati zimenezo? Mmalo molimbana ndi njala imene ikumvekai
Mmmmmmm yemwe angavomele zoletsa madzi amtengo wapatali azakhala mdani 4eva kkkkkkk
Let all who get drank,
drink to the bumpar level of excessive safely!
AFTERMAN.COM
Misala chani
Kufuna kutiona kupusa et muzikauza azikaz anu mbwelelazo
Mkasiisa mowa marijuana alowepo
Apanga bwino, si mpaka akumaposo enuwake omwe adaziyambitsa..
inu boma silingakwanitse apolice adziyenda pansi kukagwira omwa mowa
kodi kuletsa kapena kukhazikitsa time yomwera
Zandivesa chisoni athu ambili omwe a kukana ku lesa mowa omwe amatiso opa mulungu mulungu salola mowa salola chiwelewele ndiye mmakhala pasogolo ziko lopa mulungu ikasowa mvula tipephe mulungu zokwatilana amuna ai inu athu a mulungu tichepese mowa ai mowa okha musiye chimo ndi chimo mowa chigololo zonse ndi chimo
I like bhawa more than anything tiwonetsana amabungwe zopusa eeti!
Mpofunika kuti boma liyike malamulo makamaka pa nthawi yomwe ingathandize kuti anthu azikhala ndi nthawi yokwanira yogwira ntchito malo mongokhala malo omwera mowa nthawi ndi nthawi,umbanda womwe wakula kwambiri Ku Malawi nchifukwa choti anthu ambiri sagwira ntchito chomwe Iwo amalingalira ndi kuba akatero akamwere mowa .Koma pa kakhala malamulo zidzathandiza kuti anthu azigwira ntchito chifukwa malo azisangalalo akhala atatsekedwa taganizirani mayiko omwe tayandikana nawo monga Tanzania Ali ndi nthàwi yomwe anthu amakagwira ntchito akaweruka ndipamene amapita malo azisangalalo (boma liyenera kuyika nthawi yomwe anthu angamamwere mowa osati nthawi ili yonse)
I don’t drink beer and recommend drunkenness,but what i have observed is that our country,malawi,is now becoming more satanic .Why people don’t mention about kicking out homesexuality [mathanyula] and other wickedest sins from our country that claims to be a God -fearing nation?
Eeeeeee mwakwiya etiiii
Kkkkkk zidakwa kulira
Pamowa pokhapo musaelekeze bwanji mulese mpunga guyz?
Mutseke Mowa Chamba Ai Apo Pokha Tdanapo Mwamva
Kodi amamwera ndalama ZANU? Tazingobani m’bomamo..nkhope zokwinyikazo
letsan basi .akale nd 3 hrs yomwera .2-4pm.mwina malawi nkutukukako iish
ah kma mabungw enjw bas mukukhal bzy nd zamoa muktan kuthan kae nd njal kvta kwamages maz ah ndie mwapez kt chophwek nd bawa thanan kae nd mfans omwe ikupha malubnoh
Kunena zoona timamwa mowa pofuna chisangalalo Panthawi Imeneyo ndiye Munthu wakonza kuti umwe mowa masana kuti kukada uzipita nde akuletse Kuti Koma Kude Kaye kapena kuti umwe lachiwiri aziti ai koma Friday Ufulu wanga uli pati? Ku Malawi Ukapolo Sunathe.Ma Bungwe Osowa Zochita. Iyi yokha Simupeza Nayo Donation, Funani Ina.
I cannot Support that move of stopping the Beer because iam here iam from the profits of beer so those who are depending on it muwapatsa zochita? Inunso Mwaiwala zoti mwaphunzira Kuchokera Mukachaso?Malamulo Adziko Lino Amakomera Ndani Kodi?Mukachita bwino musaononge ntajiwa a nzanu. Mutisamale!!!
Akalesa Bawa ndyeno tizipanga chain enafe ndi maswazi akazi sititenga timatenga Bawa asalese ayi apeze chiganizo China koma
mwati kulesa chani? masewera ameneWo musayelekeze ndati musayelekeze
Mmmmnmnnnn sizngatheke zache zasatan zinabwera kale asiyen anthu amwe
Tikasiya mowa mutipasa azikazi anu kapena ana anu kt tiwakwatile?nanga okonda fanta muwatani?azinjoya okha?osakalimbana kae ndi zombe ku lower shire bwanj,maguja anu mwanva!
Hahahah Ndie Mwat Mufuna Muthese Bawa,? Tangoyesan Muone Tpange Mademo
Mowa God will punsh u
Ndiye mulindichikhalidwe choipatu!!angoni inu
Iyeyu sanamve kuti Nowa analedzera after kutuluka mchombo muja munthu wa Mulungu amene ndiye inu mukukamba chani apa mowa ndi wakale kale inu musanabadwe mudzausiyanso kambani zina apa
mowa uletsedwe ukupangitsa anthu kusasamba komaso unve
Pali Anthu Ambiri Omwe Amagwira Tchto Yopanga Mowawu Ndiye Mukawuthesa Muwathandiza Bwanj??
ACHITABWI MABUGWE
enafe kuchipatala ana tiuza kutiuza kuti tikadzangosia mowa tidzafa mutitha ndiza bwanji, mmene mumamwela mowa ma mp ma loya pa bwandilo mudzasia kubwela?
Ngati mwalephela kulamula dzikoli pasani anzani. Anthu anayamba kumwa mowa inu musanabadwe ndiye mkumati tiletse mowa za ziiii
Koma achita bwino kulesa mowa,zili bwino,
Ngakhale mulese koma kumudzi kwathu kokha sizingazatheke
Nde bwenzi kamuzu atatsegulira company ya carlsberg za ziii popeza akulu akulu ali m’bomamu timamwa nawonso sitingawatchule amapapilanso kwambiri, a Bakili anatsitsanso mtengo wa mowa musaiwale izi nde ziti
Amalawi munazolowela ulesi.
Amalawi munazolowela ulesi.
Amalawi munazolowela ulesi.
Akamanva kuti kuputa mavu,nkhomola NDE uku,akuona ngati tidzimwa chani?
Aletsa bwanji bawa pomwe iwoso amayakaso hvy? ndenanga ife bwa????
Pofunika pakhale nthawi yomwera mowa osati nthawi iliyonse
Kunsowa zokambirana parliament mo basi
Alese kaye timabungwe tangoti mbwe Ku Malawiko
Mukamva kuti kupusa ndiye kumeneku.mukaletse mowa kuti wakulakwirani chani?osalimbana ndiokupha alubino bwanji? Yeserani muone timatcha maliseche muonanso……
peter akufuna azingoyaka yekha basi!
peter akufuna azingoyaka yekha basi!
Koma Koran ndi Bible zilimo mwati zimenezo. …tiyeni tigwire ntchito apa kuzolowera ulesi basi. ..mowa mowa ndekuti chani? ZOPUSA! !!
Mowa,nyama,kankazi kali pambali..ndye angoni amenewo. Ife sitingasiye chikhalidwe chathu
AULESEDI NGATI AMAKHUTA MOWAO UNGOLESEDWA BASI
Chamba ndi makobili alesa bwanji?Halmitone
mowa muli economy
mowa letsani!!! nose amene mukut mowa ndinu vitsiru simudziwa matendawa amafala kwambili kumowa? y mahule saima pa stage ya bus kusaka amuna? amapita kumowa coz amadziwa ndikumene kuli vitsilu vizawo. mowa ndigwero laumphawi mudzaziona tintchito/biznz mukudyadilato tikadzatha. mowa aletse bas, kaya tizimwa mobisa~ usat uzingopezeka palipose ngat frozzy ayii!!
inu ngati simumwa zanu. enafe mowa timaukonda. mukuti tikaweruka kuntchito tonse tidzikaunjikana m’mabawo? musandikwiyitse
Suputi at its best
andionjeza bwanamkubwa
ine ndiziziphikira kachasuyu bas
kkkkk km Malawi wayambisa ndindani mbwelela zimenezo? hahaha kaya zanu izo ife tizikamwa (KACHASOA) ok
Mowa sulepheretsa chitukuko ndipo ambili olemera ndiwomwe akumwa mowa mukamati mowa umasawukitsa inuyo zangokuvutani nkhani simowa kopusa kwanu mumati zikukuvutani kamba ka mowa
Oky lensani chigololo not mowa!?!!!
Bwanji osakwiya ndi abale anu amafa akamwa mowa osadyera aja?zazie
Ayambe athetsa kuzima kwa magetsi ndi kusiyasiya kwa madzi
ndalama zimene amamwela mowa sizikukhuzani amabungwe inu,zingoadyerani azungu kunjako,muli ndintchito zambiri zoti mupange mzikomuno.Mowa anayambisa ndi makolo athu kale ndie inu lelo ndi lelo mulese,tapangani kae za albino amene miyo yao ili pa ciopsezo osati zamowazanuzo
Ngati akufuna athetse Beautify Malawi Trust chifukwa utchisi plus defforestation zafika povuta
aaaaa chamba eti! osaletsa sex bwanji? wts th different
anthu amenewo asatenge malamulo akunyumba kwao awaike mdziko muno, bola #chanba nzoveka ndiye atilese kumwa #mowa afuna tizitani tiyambe #ufiti, muuzane mwanamizana mowa palibe uyo angaleke , ndibwerezeso mowa sitileka kumwa
Muletse Mowa, Walakwa Chani?
Mowa ndioipa inu even the bible or qouran imaletsa
Letsani mowa akumwa ndi ana omwe. Mapeto ake mukulephera fulfilling conjugal rights
anthu osamwa mowa amakonda izi..UHULE..NKHANZA..MABODZA.kungotchurapo zochepa,nde apa anganene zanzeru?beer ndi deal.
Umbombo Bwaa
eya ndinaiwaladi @ jose,munthu wanzeru sangadane ndi mowa.
ndiye tidzimwa chani tikasangalala ?
Kkkk asova waulesi gwaulesi sizikugwilizana
Asiyeni Amwe Aiwale Umphawi Wao
Asiyeni Amwe Aiwale Umphawi Wao
Zaboza Waulesi ndi Waulesi mowa Tinayamba. Kumwa kalekale kamuzu alipo ndiye mukuti chani
Mwakhuta eti
nawoso ndzidakwaa aletsa bwanji ndziko lit analesa mowa komw samamwa mpaka lero!! bungwelo kuliso zidakwa heavy lesan tiwone osamalimban cashgate ku hillko kupusa etiih kukamwa woyankhulawe
im nt a beer bt galu aliyese ali nd tsiku lake!! chtukuko akucta kma kulesa mowa dis can’t b gd way to solve the prblem we hv nawoso aleke kudyera masuku pamwamb pa anthu osawuka nd makape a mabungwee
Muyambe mwamanga Kaye azibambo onse osamwa mowa chifukwa iiii nduaumbombo kwambiri amathawa ana kukamwa tea mu tea room wamkaka ndi sikono.
Mukufuna kuti wonongera sogolo lathu ife zidakwa….
Inuuu asiyeni aMalawi nawo azizipepesa.Abale maiku enawa antu angoledzela daily koma angopitilizabe kulemela. Mowa siugaletse chitukuko chadziko. Ngati lililosauka ndilosauka basi. Pezani njila ina yoti antu achite kuchepesa upawi. Asiyeni antu osaukawo nawo azizi pepesako
Kuletsa mowa? iiiii usawi chichi? Tiyenda maliseche muona mutidziwaso. Walakwa chani mowa wabwinobwino?
mukanalesa mmbuyomu bwenzi anzanga ambiri asanafe komanso Edzi nsanaitenge kkkkkkk
Which NGOs?they found brewing beer,drinking beer,hardworking….Remember We Are Old Now Aged 51.So What?
mowa asasiye kupanga mukasiya tizitani?
Kkkkkk drug imadula hevy koma anthu amaipezabe nde mowa oti wa polisiso amamwa lawyer amamwa ka ndi Mr President ndunena pano ma grass awiri amwa kale nde mwati mwaletsa? Hahaha
ngati kumaloto!
maybe ngati mungakwanise I rest case
Kumwa ndi kumwa basi. Short way mungotipha basi,osati mukwanis
Unless Mr Peter stops drinking we can’t stay away from liquor.
Maganizo abwino asiye ndikupanga ndithu coz anthu ambiri aonongeka ndimowa maka ana achichepere kwa ine ndikuti muyesese asiyilethu ndipanga vyimowavo paja ndikaviona ndimakhala ngati ndaona bb la agalu
Mulesa bwanji Vinyo kt asamamwedwe,bwanj osaletsa opangawo kt asamapange ?,,,,Komanso ngat mumatipasa ndalama zokamwera mowazo Tisiya
Zikuoneka kuti anthu tonse tikukambapo zamowa pamalo ano, tingapanga mpikisano ulankhula kosatherapo ngati titakumana pamodzi (debate). Zidakwa zikuoneka kufika potukwana KKKKKKKKKKK
Nkhani imeneyi msaivereso ndithu
Mukundikumbukirabe anthu adzidzandithandiza chiyani Tsopano
ukamati wa ku zomba chani
Zotengeratengerazi muziona nzotengera zake. Khanundu eti
Paja chambanso ndi cholesedwa koma timasutabe nde you think mowawo tingakanike kumwa?? hahahhà mukunama amabungwe ife simungatiletse chimene tkufuna coz dolla ndi yathu! i rest my case
thy hv to start wt sex
thy hv to start wt sex
eti eti aise…si bho! anyamata a chakumwa timatcha basi
Apa pokha amabungwe mukutidelera,pankhani yamowa yokhai pafunika referendum timve maganizo aaMalawi.Chifukwa mowa ndi source of income kwaanthu Ena.Ndiye mukaletsa zizangoonjezera umbava ndi umbanda,chitetezo chovunda kale.
Hello my name is john I want to give a testimony about my HIV virus that was cured by a great spell caster. Since last 4years I have being a HIV AID patient. I never think I will live long again and am so grateful to Dr sule who help me cured my HIV AIDS last 3 weeks. I was in a great pain so I told one of my best friends; he told me that there is a great spell caster that can cure my VIRUS. I asked him if he had his contact, he gave me his contactl, I contacted him he talked to me and he perform the necessary things and sent it to me through corrier delivery company and deliverd to me at my place and he told me that after two weeks I should go for a test. Which I did, when the doctor told me that am now a HIV negative I couldn’t believe myself I went to see another doctor the result was still the same, I was human on planet earth, so I emailed him and thanked him. Please if you are having a similar problem please visit him/contact him via whatsapp +2348162447651
mowa mukuletsa chifukukwa chani kumowa2 timapewa zambiri komaso mbamva zichuluka
Ndakaika ngati zingatheke unless mutawapezela chakumwa china chokhala ngati mowa komaso choledzeletsa otherwise mutiuza ndinu zochita
aaaaaaaaaa koma zitheka malo mot mulimbane ndi anthu amene akupha alubino mufuna muletse mowa mayazi kulibwino ngat zakunyasani osangosamuka bwanji ndi
Mukupanga masewera eti mulese mowa zausilu eeeee ndye pavuta mukufuna tizigona sober tizilota njoka amabungwe pliz mulese ana anu ndzizukulu zanu ndapota nanu
tangovomelezani kuti dziko lathu lasaukisisa basi,walakwachani beer?
Mabungwewo ayambe amanga mahule onse kenako kuletsa chamba akakwanisa aletse mowa
Koma pali anthu ena moti akapanda kumwa mowa amadwala boma liwanganizila bwanji amenewa?
Inu mukuzinamiza kuti Mmalawi ndiye odziwa kumwa mowa? Boza pitsno pa Zambia ndi Kenya mukawone anthu okumwa mowa. Ngati Malawi ndi dzilo LA anthu okonda mowa bwanji samawinako chokho cha ziko lomwe lamwa mowa kuposa maiko aku pajatu ndi kumwera limene imakonda kuwina ndi Zambia kapena Kenya
Asiyeni anthu asangalare ndi mowa palibe chifukwa
Inu thanani ndi anthu skins
Mukaletsa mowa ndibwino muletsenso anthu kusakwatirana cz enafe mowa nde akazi akunyumba
My name is Bogadi kgaogano and this a testimony of how i became HIV NEGATIVE, i have been suffering from HIV for the past four years, i have spend a lot of money finding cure for HIV/AIDS until i found this true man who cured me completely with his powerful herbal medicine, i have tried different means to get this virus out of my body, all the possible ways i tried did not work out for me, i came across doctor olumo through some amazing testimonies concerning how Dr Olumo has cured different people from various kind of sickness like HERPES,HIV/AIDS, CANCER, with the help of his powerful Herbal Medicine, so i was encourage and i contacted Dr Olumo i told him about my Sickness, He told me not to worry that he was going to prepare some Herbal Medicine for me, after some time in communication with Dr Olumo he finally prepared for me the herbal medicine which he sent to me through courier service and he also gave me prescriptions on how to use it, after taking the Herbal medicine for some days, i went for test to confirm and the result was totally negative ,i went for test again in a different hospital still the same negative , Today i am fit and healthy to live life again, I am so happy for the good work of Dr Olumo in my life, if you are having a simillar problem kindly email HIM on { [email protected]} OR CONTACT HIM WITH HIS NUMBER OR CHAT WITH HIM ON (WHATSAPP) (+2348138956767) together we can live an HIV free life.
Mabungwe ena ndi zisende zomwa madzi ometera, zidepete zenizeni, zisilu zotheratu. Pa mavuto onsewa omwe a malawi akukumana nawo mwapangapo chani? Kuphedwa kwa albino, mathanyula, njala mwapangapo chani. Ndiye lero mumvekere kuti mukufuna kuthesa mowa umene loti ndi nowa amapapira. Olo mutandithira doom kamwa sindingasiye kunyopola bawa.
Read the post before making full comment. Sakukamba zakuletsa ku mowa. Akukamba za nthawi yomwera mowa. Anthu ena amapezeka atalezera as early as 9:00am. Nanga ntchito za chitukuko akagwira nthawi yanji? Nanga chakudya cha ana ndi nkazi panyumba akafuna ndani? Imagine mwamuna waledzera 8:00am koma nkazi ndi ana agona pa line ku admarc for 2days fighting for 5kgs maize! Kumaganiza polemba ma comment ena. Borrow a leaf from Tanzania. Analetsa kumwa mowa morning hours and ku Tanzania kulibe njala…wamva m’bale??
Inde ndava
Uletsedwa kumwa mmawa i support the idea.
Ask other countries they are getting rich bcoz of beer inu koma kuba amalawi aaaaa
Ndalama zomwe akuba andalewa misonkho yake yambiri imachoka kumowa nde mukuona ngati angalore kuti mowa authese…cash gate nde mowao
Asowa zokambilana ama bungwe amenewa akalmbane ndmowa zilnd phindu lanj cifukwa ena mwaio asyasya mowa nde bas atpatse phuma enafe?timwabe mikala bongo
zidayamba masiku awo….. Padziko pali anthu opatulika, inu ndindani kut mukaletse mowa? Pamanu…… Mwxiiiiiii…….
Aaaa musaletsedi mowa enafe kuti tisiye mowa ndiye banja litha coz mukhala ngati mwatipatsa mankhwala olela.
Mowa usalesedwe anthu ena akangosiya kumwa mowa ndimathelotso amoyo wawo
Yap Yap Yap Yap Yap! Mmajamo Mmajamo Kkk
Zautsiru
Zoletsa mowa-zo nde zausiru..! Ngat mwakalamba mungomwalira basiii..!! Zoletsa mowazo nde zachamba kwambrii…!!
ngati akufuna kulesa mowa atipase ana awo akazi tiwakwatire mmalo momwa mowa tiziwakwata kkkk
Maganizo ochepetsa kumwa mowa apangidwe. Amene akwiya ndi zimenezo ndi adani a chitukuko cha Malawi. Dziko silingatukuke ngati muchuluka zidakwa, a ulesi, a bawo, ntchuwa ndi a miseche, atambwali a ndeu, akuba, a katangale ndi ziphuphu. Zinthuzi zimaendera limodzi. Tiyeni tigwirane manja tiletse ndi kuchepetsa maka mowa. Mowa ndi wabwino pa nthawi yake. Osati kuchoka m’mawa mpaka m’mawa wa tsiku linali. Hmmmmmmmm…. Zoona????
Nanuso inu… au tryng tu potray that in thoz rich countries the things u mention doesnt exist????? Jst blv in wat ua my brother.
We are talking about Malawi. If you have nothing to say just keep quite. It looks you are big hearted and always fighting oeople including your own wife. Change your mindset!
Madimbo. ..wakamba zanzeru
Ngati muli ma sober man zanu zimenezo :V chakumwa chimwedwe mwaufulu apa alah
masoba man ndiamene zikukubowani ndimamwela ndalama zanga mwanva
Kuletsa its really shows how primitive malawian we are sizikufanana ndi kupedza nzeru yopezera chuma cha dziko, i can agree atati mowa wa spirit okha but not mowa onse zachamba eti
Iwe #Madimbo?,,,,,mukutichitisa manyazi mwamva eti,,,kodi muzazindikila bwanji kalowedwe kandalama mziko mwanu? Pamenepo ainiwakenu mukuti mwaganiza mwanzeru pamenepo uku ndiye kusowa chochita amalawi uku,,kutha nzelu,,
ine ndimamwa and i live a happy life, ana anga amapita ku school ya bwino so whats wrong with drinking, am a cross boarder business man and i pay tax,hahaha ngati simumwa zanu zimenezo,,
Ukunamatu iwe kuyaka,ku blaka ndizmene tmakonda.iwe ndmfit et?mowa muletse,koma mudzindphera mtundu wanga ma albino sichoncho?galu
Kusowa zochita eti
Mugule mawunyolo ochuluka kuti mukwanitse kutimanga
Eeh,mutiphweteka .ndife anthu amowa
Mowa kwa omwe amamwa ulibe tchito.ubwino wamowa ndikuchotsa munthu pa umunthu wako,kukusupula kumaso,pena utaumwa opanda kudyela umafa. phindu kumowa lili kuogulitsa bcoz it get a proft
ngat mungaletse mowa ndi bwino kut Marijuana mulolezeso tizisuta mwaufulu… Nanga monga kwa munthu wamuna azitan. Kumowa timapewako zambiri.. Mukundiuza kut kulesa mowa aliyese azakwanitsa kulipira ma college mene mwakwezawo.?
Ganja yemweyo wakwana koma bawa ndiye mayaz njeee mpakana tikumatchirani
Mukangoletsa tipanga ziwonetselo muwonatso (NDALAPA NGWAMBILI MUNDIPATSE CHIBUKU NDICHIMWE
Enafe A Chipatala Ananena Chekecheke Thwaaah, Ukangosiya Kumwa Kam’mapewa Uzasiya Nthaka, Nde Amabungwe Atithandiza Bwaa Pa Human Rights Yathu
Letsani nyasi zimenezi ndithu. Tinamwa zinatikwana.
Koma guys kumakhala serious eti. Malawi ali kale ndi mavuto ambirimbiri. Ena mwa iwo ndi awa; njala, kusowa kwa mankhwala, umphawi, #Kamlepo_Kaluwa, kusowa kwa ntchito, kusowa kwa madzi ndi magetsi angozima. Pongofuna kutchulapo zina. Ndye amabungwe nkhani ya chakumwa ichi cha mtengo wampesa sinkhani ayi. Tiyeni tithane kaye ndi mavuto eni eni monga kamlepo kaluwa yemwe watigwela pakati pathu. Zikomo. #wodandaula
Ndimayesa chi khristu chimati mowa ndi tchimo, nanga bwanji a khristu akuyikira mowa kumbuyo? Hypocrites!!
AMabungweadali ndi maganizo abwino kma tikati tione kwathu kuno padakhala kuti Employment siyimavuta ndikadavomerezana nao kuti Mowa uzimwedwa kuyambira 17:00 PM kma tikatiso pabwere lamulo limeneli Umbavaso ukula chifukwa tchito kwathu kuno ndiyosowa.
Ayerekeze aone
Mayiko anzathu mowa umamwedwa madzulo ku m’mawaku anthu akagwile ntchito munthu angakalime ataledzela mowa asaletse ayi
Ngankhale malemu sakadalora zopusa ngat zimenezi, mukumaganiza zopusa ngat zimenezi chifukwa simumamwa bawa.
Letsani wazugubu zama 5litazi uja
OK!! Mabungwewo akuti ndibwino kuletsa mowa osati mathanyula? Asiyeni a mowawo, oweruza siinu koma MULUNGU
kuletsa kumwa mowa sizingathe,koma kukoza bwino masiku omwela mowa zitha kutheka.monga kumwa mowa friday,surtuday,sonday bola cifukwa malawi waonongela cifukwa cha mowa.
Mowa waononga bwanji Malawi?
Zachamba Basi
Mukuletse mowq mukufuna tife ndi matenda cchoncho?
No ways
what are they gonna do with Chibuku & carlsberg employees? nanga onse ogwila kuma bottle store s across the country
Kkkkkkk koma kumeneko, lest see. with the world of lies.!
Kodi amagula ndani? Kodi boma linagulapo mowa kupatsa anthu? Even we can have drought have u ever heard kuti kumowa kwalowa drought? Letsani katangale wanuyo. Kodi ufulu uja wapita kuti? I thought everyone has a right of choice. Mwasowa chochita. Drought yalowa mubrain momwe.
Ha ha ha ha!! demonstration iji yoyenda mbulanda, idzachitike basi mpaka azagive, kuti tasiya zoletsa mowa iyaaa!!!
Aaaa palije wangaleska moba mumalawi. Moba tizamumwa mpaka kuchigotez cha chalu ise.
TISEKE KWAKANTHAWI KOCHEPA
Nkazi wina amafuna kumuyesa
mamuna
wake…. Analemba ka note
nkukasiya pa bed
iye nkumbisala pasi pa bedi…
kanalembedwa motele:” Ndanganiza zopita kaye
kwathu
kukapuma kwa miyezi iwiri,
Musale bwino!”
Mamuna uja atawona kapepala
kaja analemba mawu ena kuseli kwake. Kenako anatenga
phone yake……(mamuna pa phone)
“honey
Ndikubwera pompano
Ndizakutenge,
pumbwa uja wapita kwawo ati mpaka miyezi iwiri
Ndiye tinjoyatu!” mamuna uja
atasitha zovala ananyamuka
kumapita.
Nkazi anatuluka pansi pa bedi paja
misozi ukuvumba m’maso
ngati mvula. Anatenga kapepala kaja
kuti
awone zimene mamuna uja
analemba kuseli
kwake……. Kunalembedwa kuti: “STOP PLAYING
SILLY GAMES HONEY, MIYENDO
YAKO
IKUONEKERA KUNSI KWA
BEDIKO. TELEKA TEA
NDIKUKAGULA ZOMWELA
Alese mowa kma umathanyula azilola? Akuziwa kt even mugabe game imeneyo sangailore? Mbuzi imeneyo.
Sitinayambe kumwa pochita kumenyera ufulu ngat zqumathanyula zqwozo
Potirizani amabungwe inu mowa usamwendwe wamba wamba or uchotsendwe kumene
kuxowa zoletsa?
Mukaletsa mowa nanga ifeyo ogwila ntchito kumowafe mutitani Zopusa basi muyelekeze
m’malo moti athetse njala akulimbana ndi mowa,koditu iwowa alakhula fundo zomve akamwa mowa,ndiye akaletsa mowa azayamba kutukwana,
Mbwelera.Com
amalawi akiya omwewo
Muone athu Aku malawi ambili ndi osauka ndikupanda zeru mumangokhalila Kachaso ma presedent ose a kumalawi anali zidakwa mutukuka bwanji azanu amagwira tchito kuti atukuke inu magwira kuti mukabwe Kachaso fuck malawi
kkkkkkk Ndiye ife! tizitani?popeza Enafe! Zovulavulazi Sitimazitha kwenikweni. Musatikhomelere please kkkkk.
Enafe sitimamwa mowa komano nkhan iyi siyowona amabungwenu ngati zochita za sowa pezan zina not kuletsa chakumwa cha anzanu mdziko muno muli mavuto ambiri bwanji kulimbana ndi mavuto amenewo kuti athe musalimbane ndi mowa’.
amamwera kukamwa kwanu mulibe ndi manyazi womwe
Zoona aganiza bwino aletse bas
ndpo asayelekeze zopusazo
Bola muletse ndale
Kuletsa mowa ndiye amene amaphunzitsa ana ake ndi ndalama zogulitsa mowa ali pavuto. Ana saphunzila school. Vuto lalingono lipangitsa mavuto akulu. Tangolimbanani ndi ana amene mumawapeza kumowawo basi.
Eyyy amabungwenu,,,tamangani malo osamalira ana amasiye
Tayesani kupeza njira zothesera katangale/ziphuphu
Tampezeni njira yoti okalamba ndiolumala akhale mwamtendere mdziko mwawo
Tatenganipo gawo loteteza abale athu achi alubino!!
Mowa wayambira kumtunda kukasilizara kapolo nde muyambira pati????
Ngati asowa zochita ayambe ulimi
Aletse kumene kuledzera ndi matenda zimvereni chisoni.
Matenda anji?Malungo kolera?Mankhwala ake ndi chani?Mbwerera apa ayi.
Kumeneko kulilira kabanga? Kkkkkkkkk
It is a good idea to have regulated period of drinking beer because I have seen some drinking joints that open like groceries. It is surprising that people patronize such places as early as 7am and you wonder when such people make money for drinking and fending for their families. It is therefore important that such wasted time should be devoted to developing our national economy.
Nonse osamwa khalani chete nkhaniyi sikukukhubzani.komanso sizingatheke kuletsa mowa mapeto ake Angonife mutishosha dala.
Amalawi Ake Akwayawo Ndani Nawe…Watifunsa Kaye?
zamanyiii ayilikize ife wathu ndi mowawo
Ife tikasangalala ndie kuti tamwa mowa ndie mukaletse sizitheka simenezi
Aletse mowa chifukwa Chani? I Tchulani zifukwa zomveka bwino 100 zoletsela mowa
Kkkkkkkkk mwasowa zochita amabungwe eti
Mavuto ndiambiri dziko muno bwanji osathetsa mavuto enawo ndizosatheka ife nde ayini a bawa paka tsiku lobwera yesu
Guys 12grand mundipasa phone yanji?
NOKIA 5110
kkkkk asa
aletse mowa siwabwino aletse chifukwa amalawi ndianthu osaganiza kale bwino pachibadwidwe chawo amakanika kuganiza zinthu zoti ziwathandize paokha ndiye akaonjezera mowa zimaonongekelatu amachita kukanika kulipira fees za ana awo ku xul kuona ana ambili anafika fom 4 xul,,,, koma akukanika kupanga cos chifukwa bambo pakhomo akuti zake ndalama ndizomwera mowa choncho ana anthu amenewa omwa mowa ndizimene zikumakhala mbava zikuluzikulu chifukwa sizikupitiliza maphuziro zikumangoyambaso nazoso kumwa ngati abambo awo …
Uyankhula mbwelela bwanji munthu wa mowa umamu dziwa iwe munthu wamowa akamapita ku mowa amakhala kuti chili chose wapanga kale zaku nyumba kwake nde pali anthu omwetsedwa mowa ndi amene uku nena iweyo amakhala kuti kwawo sana pangekali kose amango bwela ataledzela panyumba nde aja amawa danda ula kuti akungo ledzela sikuti amakhala amwela zawo ai
inu Malawi ndi dziko laumphawi kuti muonetsetse makomo ambili kukacha amamwa tea opanda mkaka bola ali ndi sugar kusonyeza umphawi akakhala bonya ndiye ndiwo zimene zasamala makomo ambili kumalawi ndiye pa lyf imeneyo muzimwelapo mowa kumati mukunjoya ?
mulibe mfundo inu iyaaah ife tmakhala ndi nzeru tkamwa bawa iwe sukuziwa…….uyambe lero kumwa wamva
ndinu ana inu ndi mpake mukuchemelera mowa muzitifusa ife tinayamba kumwa mowa chibuku chili pamtengo wa K15 tinasiya uli pa k150 mowa ulibe chitukuko chilichose mowa umakupatsa courage zauchitsilu umatha kukupatsa mwano kumayambitsa ndewu chosecho ndewuyo sungawineso umakhala unagobola kale ..mowa umakupatsa chilako chogona ndi mkaz chosecho mphamvu zokwelera mkaz ulibiletu unagobola kale …muzaziona ndinu ana simunakhwime pa mchombo mwangoyamba kumene kuuva kukoma mowa
Mmmmmm
kkkkkkk ine ndine m’Malawi koma ndimamwa mowa & zonse ndimakwanitsa ndimaposa osamwa mowawe.kungoti ambili kulakwisa kanenedwe am ngoni and ndiyenera kumamwa mowa ndikakhala free
ndalama yako sungapange nayo mpikisano ndiine ndalama yanga iweyo singakupindulire olo nditakhala ndi ma million..chimodzmodz ndalama yako iweyo olo utagwila ntchito yokumba chimbudzi ndikukulipira ndiyako ine singakupindulire panjira iliyose
Kodi mukuti chani inu akatsonga?
Mowa athetse lero, ndi angati apezeke pa ulova ku makampani ofulula mowa? Ma Trading Centre opanda ma Bottle Store ayima? Ngati zomwera zinakutherani, khalani chete apa!
ndikuti musamakonde komwa mowa muzafa osauka choncho mulilimo ndiye maliro a inu anthu osauka amazuza ife andalamafe..
inu achina #mwantisi mukutupa ndi mowa koma mukuuchemerera ife tatopa ndikukumba manda ..
iii koma mowa aletsed, ulibe phindu
aletse ineso ndizayenda mumsewu zionetsero zovala mowa aletse Basi ..
Ife tizimwabe, mwanva? Osalesa mabungwe bwanji?
panja mtundu wakatsonga umakhala wamakani,zakumtundu kwanu osamabweletsa kuno kupusa eti, unava kut olemera samafa? Maxson Mbendera,Bingu,kungotchulapo ochepa,Mabus amasiyewo munyadira kut muli ndi chumawo? Demmmeet
mmm gyz kuyankhula kuti musiye mowa chifukwa mukamafa mumazuzitsa ife anthu a pheee ndiye kuti ndikulakwa ?
Ndipo ndifebe okwiya kamba kamanong’onong’owa…Malawi hav so many problems as of now rather dan ds isue yoti somhw ikuthandza boma financially…gues how much chibuku breweries…calsberg..ie southern bottlers contributing to nation develop in sports..health & da like…how many pipo ar stil employed from ds companies coz of mowa brewering…somehow opanga fundo zoyendetsera dzikowa akumakambirana ataladzera beyond or iwowo akufuna atasiya nde aganiza zotero…komabe sitiwalorera kudza nd mfundo za ziii…tidakakondwa nao mowau…coz za bible izi
Aku letsa mowayo mumu uze pantumbo pake akaletsa mowa tizi panga chani zaku n.nyelo zimenezo aletsemowa aku phuzila ku esa zida koma sizitheka muziti ama bungwe akufuna ma hule ose awa pezele mabanja nde abweletse ma hule atsopano munmalo azi sangalalo osati tingave zomwe nkhutu ku ve ina iku bwela ndi fundo zopoila akamati dziko anthu aku sangalala amanena chani mesa mowa wo popanda mowa ndepanga khale dzikoso zandi nyasa ndima phuzo ndaikawo ngati angathe kuona andi hale ku inbox mwana ophusayo
are u crazzy.know God today my brother
umenewo nde mowawo!
Za chamba eti
Aletse fanta ndi coca cola zimakhala nda cid nkati
Hehehe kma ndiye amabungwe mwasowa zochitatu.kma mumadziwa kuti enafe kt tigwire ntchto bwinobwino timayendera mowa or kt tigone turo tabwino ndi mowa omwewu ndiponso kt tilankhure zomveka pa guru ndi mowau?aaa stop that nosense..
u must be aborn again.dont be proud of bear my man think about life after judgejent
Tiyenda mbulanda iyaa fodya et
mmmmmmmmh Zafika apa…..dd jesus not turned water into wine?what is wine?
Tell thm zausilu basi
A Stevie Kaliati!Zikomo. takumvani.kma ine mowa ndi tea wanga
kkkkkk tayerekezani kuletsa mowa muone…… timuuza winiko kuti tiyendenso maliseche pamseu iyaaaah
ndifunse nawo guys..kodi kwa amene samamwa mowa ndichani chimene amanjoya nacho?
Ufiti
Kikikik owo??
wanditha man , I don’t consider mowa a sin , but things pipo do after kumwa mowa hahaha
@Sam nde wati kut uyankhule zomveka umafunika kut umwe¿¿¿¿¿………nde apa ukuyankhula zaziiii tiziti sunamwe et? (just joking)
Andrew!kkkk Bawa ndi deal
Ur ryte stv, seems walemba utangolawa kkkkkkkkkkkk
Ur ryte stv, seems walemba utangolawa kkkkkkkkkkkk
Masachet lesani kumene
Chitsiru
Kkkkk…koma yhaaa
Manyi ako!
aletse mowa chifukwa chan? amakupempheni inuyo ndalama zomwera mowa? mmalo moti mzilimbana ndi za mphindu mkulimbana ndi za ziii ngati izizi,, kusowa chohita etiiiii
sanalakwe
khwimisani kapezedwe ndikagulitsidwe ka mowa basi koma zoti anthu asiye kumwa mowa sizingatheke…..