Two people have been arrested at Dedza border for possessing fake South African Rands.
The fake Rands amounted to R19, 000 (K1.1 million) and the two wanted to use the currency to steal from South Africa bound Malawians passing through the border.
District police spokesperson for Dedza constable Cassim Manda confirmed the arrest on Wednesday.
Manda identified the two as 46 year-old Themba Nyirenda and 41 year-old Bernard Nyirenda, both from Chiyona-Nyirenda village in the area of Paramount Chief M’mbelwa in Mzimba district.
Police suspect that the men wanted to exchange the forged notes with Malawian currency from Malawians going to South Africa who pass through Dedza border.
Meanwhile the two have been charged with the offence of importing or possessing forged notes.
Lol
Eish imali aikho bafwethu kunzima asikisi guys kuzolung’a life goeson mbiya jisawisye pane paliponse khobidi nde ikufunika ma styles ndionse chabe kuti anthu akakutulukira ma style ako ndizimenezi umayaluka komabe never give up
Kuyesera mwai tulo take timeneto wake up
They did’nt kill any person
kumachenjera pa Town
ndakubadi athu amenewo kuno anayamba kale kutero.ndikuwadziwa athuwa ali ndi machine
Shame .
Zawo Zimenezo! Wakundende Basi!!
Kkkkkkkkk. Madala mumati kukanjoye ndi Rand kumpanje mukainjoyela ku maula
Zazi basi ndala mayaku Malawi sindi lamainu zongoli mba nazake zazingati zimenezo
Atayeni.Sadabe And Dollayo Simakwacha.Vuto Nchan?
I trust Malawian ppl I didn’t think they had a corruption Even them. But they Help thm selves. because they didn’t robbery any Banks here in South Africa
Aziwa bwanji kuti ndi za fake pa border,kufuna kuwabera?
Za ziiiiiii
Za ziiiiiiiii
Not good
Ndikubwera ndizanga tizaone ngati mungandimange
Nde amazisintha mabwanji, ngat R19000_mk1.1million? Kma anganya inu kunamaaaaaa
Agalu achabechabe mwina anali ku Lesotho
Kkkkkkkkkkkk makape
Kkkkkkk R19 000=K1,1 Milion nde sitilemeratu kkkkkk
Its happens
Kumalaw kumadana ndi munthu oxisakira km ngt inu odalira xolandila Kumalaw kumakuyanja makape nonse amene mukut achita bwino amumanga
Inu ngt mul ndi nxer osapanga bwanj zt xikuthandixe?
Asiyeni naonso amafuna ndalama pitani mukamange a cash gate aja mwangoona kuti ndiosauka ndiye mwapeza nkhani naonso akufuna afane nanu
Amenewa ndiye kuti anayamba kale kubera anthu.
kusowa chochita a police akumarawi mbava zamu boma akuziwona koma kumaka gwira muthu woti wavutika yeka kusaka dora zama rand ndizisiru poti dziko ramarawi naroso ukavu ngunandi.phepani naremba no ma full stop chifukwa wanikwiyiswa!!!!!!
These people deserve the full mighty of the law they damage the image of malawians, send them to mawula
Ambiri sakuwaziwa ma rand a fake ineso amandikanira ma R200 koma anali owona.
Ndinawauza ine, kuti business yimeneyo muyisamare koma kusamva
aaaaaaaah ndiye full of shit osamamqnga ma China amagulitsa za faking
aaaaaaaah full of shit osamamanga ma china
Okuba amenewo
M’bodza osadandaula inu ndende za malawi ma suspect amangomunyemela iliyose police nkukuthawitsa mu ndende iyeyo nkumalengeza kuti mwathawa apo nkuti kokoliko pamodzi ntomato wake zili kumanja.
bolani inu kusiyana ndikupha alubino atuluke basi
Bakili was once found in the same situation, yet noone arrested him. Now why should these be in police cell? Stupid poor fox.
Iphani basi
Eish! My best martin why?
Leave them please! They have never harmed anybody. If u want arrest albino killers and cashgaters.
Miracle fake money
B
Madolo apa mw kkkkkkkk
kkkkkkk ma Tsotsi a pa Dedza
Well done police
why arresting such talented people who ought to survive in this economic massacre…..police simukuganizapo bwino
Ma guy bwanji kodi? Malawi police does not play if it wants to catch. Jbg ikulenga.
Ziotchedwe tizione otherwise zigwiritsidwaso ntchito.
Kill those idiots immediately
Kkk amangidwe komanso m’mene akuonekeramo sangapange ndalama amenewo ali ndi ma bwana awo muwafufuze bwino aulure
Nkhani ina kodi kulibe?
kufuna kulemera mwachangu kkkkkkkkkkkk
Iyii Frams Nde Idaguga Ibwelele Titumizeko Maxbullets Ikathetse Minyozo Mmmhuhhhh hy
mukazatuluka ma man muzapangeso zina koma zizakhale ma Dollars.
Mukufuna mutisokoneze timaipeza mozunzikatu ife Rand mwamva
Kkkkkkk kumeneko kufuna kukolola? Maganizo opusa eidiot
Akalowe Agalu Amenewo Maluzi Ake Amenewa Kumapanga Zibwana Ndi Money
a Malawi,ngati ku South Africa angamange anthu awo atapezeka ndi makwacha a fake? (which they rule out to be useless) Kufuna kuoneka abwino all the time. #buyingfavours#
Ati kuchenjera kkkkk amafuna akawawombe ndani zimenezo.
Koma Kwacha(MWK) nde yamwaliratu; R19,000.00 mpaka kukwana K1.1m?
Takuchepelani?
Eya Man; R19,000.00 to K1.1M!!! Zimenezo zabwino?
Kkkkkkkk zachangu mapeto ake ndiamenewa kumangidwa kapena kupha azako
Kkkkk koma wandiseketsa bwanji.atsuka kale miphika kuti akaphike nyama,hahaha agwa nayo
Walangike watibila nyengo zitali, wapolisi wabekeso pa petroda ku Bt waliposo wanyake ine wakanisintha fek wanyamata apo, nakondwa wakolekapo wanji,
Myisova guyz
Amationa ngat makape kuno eti wakumaula bas
Anatani kugwila ntchito molimbika kuno ku joeni kuti apeze ma Rands amene amawafunawo.
T z their miracle money
Zimenezo ndizisiruMalawi inachangamuka sopano asatatulukenso akhalekonko moyowao onse
gunz kodi achinyengo mudziko lathuli ndi ayawo okha
Sorry
Kkkkkkkkkkkk anthu aku mpoto kuyesetsa kupita ku school kuti muzikabela a Malawi hahahahaha mwatondeka waka! Muzikapangila kwanu komweko ku mpoto osati ku Malawi
– Anthu ameneo choyamba aonetse ma passport awo kuti anafika bwanji ku Malawi
– Aponyedwe mudende mosayimbidwanso mulandu mulandu wakwana kale umeneu ndioponsa kupha ALUBINO
– Kamulepo Kaluwa ukuti chiyani pamenepo?
Kma ndie amaesa ngat kupeza Rand ndimasewela eti . Bx mukawasungino ameneo.
Kwacha ndie yatha R19 000 ikupanga K1.1 mita eish.
Ndalamayo fake ai koma bvuto lomwe lakura ndiloti boma liribe ndalama ndiye lapexerapo mwai wofuna kukolora pomwe sadalime podxiwa kuti ndalamayo yakwana Meter. Amalawi kukonda kubwezeletsana m’mbuyo wina zikamamuchitirako bwino. Ikadakhara Kwacha tikadati akubelani inu koma poti ndi RAND ndiye muwabwere. Mulandu Wa Cashgate sakuidziwa anyamatawo.
Mbuzi za anthu zimenezi,muzimange nyakula kt enaso atengerepo phunziro well done pa ntchito imeneyi apolice mwayetsetsa
Nde police cell ukayilowe nthawi yotentha ino kkkkkkkkkk welcome to the world of sikidzi nde ndende yakumalawiyo kkkkkkkkk…..Inu muli after fake money mapeto ake ndi ndende bac ubwino wake anzanufe tili after miracle money zikumangolowa ku bank ine ndili phee
Whats the difference? Iwenso uyenera ukalowe basi ndi miracle wakoyo kkkkkkkk! Wati bambo ake ndi a Money. Kwathu ku timamutchula kuti Mirako Moneyi.
Kkkkkk miracle money spender for life
kuno ku RSA timati kemisi
Shasha ndi Kemisiyo osati zafake zawozi kkkkkkkkkk
MUMAKWANA GUYS RAND IS NOT EASY TO GET THEM
Afalitsi omanga nyemba pamxhenga aja
N’ndimwewo
Anjateni amafuna kupitiliza kuononga ziko, chifukwa akanakhala masha-sha akanasitha pa kuchamano nyansi zaozo azisiye m’mozambiqe alone asena aja m’mene akanawamangila.
Akagwire 2yrs akufuna abere azake k1.1m mmene ikusowela ndalama pamalawi
no shot cut to be a reach man
imadya pomwe aimangilila
Kkkkkk koma nde zochititsa manyazitu chifukwa azikazi anu mwauza kuti tikubwela tili pa dedza kkkkkkkkkkk
Go a head….south african nde eni bokonda za fake
Asazatulukenso amenewo mxwiiiiiiiiii mbavaaa!!
Anyongedwe makape amenewo kuzi va jon kwambili ama ona ngati maliwi ndiwo gona agalu amenewo mbuzi ama ona ngati aiphula akasungunula 20.000×50=1000000 mwanyela pogona anthu muku choka ku sosibele mwapeza anthu akulila kale zamavuto anjala kukwela kwa fees anthu sakugwila ntchito aganize zama vuto aza chuma inu mwati ife nde mashakazulu matsotsi tii wonetse kkkkk aphwanga ndiku mnpanje kumeneko anthu akuphula njelwa zamoto nde sikuti land angango fikila kuiponya nchikwama nkhope yamandela anthu ku malawi amakhala nayo busy heavy nde ndima damukesi imeneyo akadziwa apitar muthalila aku manthana ndanthu otchuka ngati inu
Mpaka kunyongana xomwezi mmmmm
Simbava nanga zikha ule simatsotsi mashakazulu nanga adziwe kuti afika pa nyasa
Azibambo opusa osawasiya ena atengele chisazo
Ndi Ayao amene kkkk si enanso
Watch out ur mouth, aYao atani apa?
Kkkk
kkkk # Wassi…amene agwidwa ndi Rand ya fek
Bravo Guys! Malawi wadzuka keep it up make more fake rands titukuke basi. China wakutukuka ndi fake materials ife nkulekeranji? FAKE RANDA
Chowamangira ndichani mesa ndi ma Rands akadakhala makwacha bola ndikadati amangeni.
Boma ikulephera kumanga anthu adaba ma Billion.Umboni wonse alinawo kuti anthuwo adabadi koma akulephera kuwamanga nde munthu akagwidwa ndi Nkhuku mwati amangidwe Shame on UUUUUUUUUUU………….!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!#
Ndiye Amachoka Nawo Uku Kumazasintha Kuno Kuti Chani Mmesa Ndiye Kubako Am’bele Munthu Wavutika Chaka Chonse Kulima Pali Nzelu Pamenepo Muziganiza Man Mwamvae
Inuso tadziganizilani ngati Boma likulephera ndiye adzipititsa dzithu dzoipa kunalibwino akadatenga makwacha afake inuyo nkulankhula mmene mwalembera inuyo A shadreck K sokosi. koma simudalembe zazeru ai
Iwedi ndi sokosi ndithu
mdhala iwe mutu wako umagwira koma?
ameneyo sokosi yeniyeni yobvalira jombo
Sizikugwirizana ndi kuba ma billion’,
ulibe manyazi ndithu ndiwe mbuzi
pusy
Malawi wavuta uyu guyz,,basi guys ndikusamukira dziko la ku Mpoto kwa atumbuka ndatopa ndi a Malawi
Mohammed Tabrez
mbuzi ikakondwa ndiye kuti amalonda alipafupi dziwakuti mmawa ndiweyo
Sorry my fathers,mufumenge tose tikupenja ndalama
Sorry guys mudzayeseso mukatuluka ku jail
Akhaulitseni amenewo anthu oipa kwambiri musavutike kutaya nthawi ndikuononga ndarama zaboma powazenga mlandu tangowaponyani mundende agwire ntchito yakalavula gaga
I’ll bring mine next wk more than R30, 000 ndisasintha bho bo ena sakuwadziwa ma fake rands
Kkk ndiyekuti anazipeza bwanji
Teach them a lesson
Iiii izi ndie zoziyamba dala
Kwakhola kwa Mvakule yoyoyo
mwaiwelenga news kikikiki
Yewo kkkkk
Wati imwe walengeska adada wane awa
Chomene walengeska nadi mbwenu kujele basi
Aaa yai wafume waka ka wakapenjanga ndalama kikiki
R19,000 =K1.1 Million, Huh?
Rand gained too much value against weak dollar and Kwacha is just a victim of depression.Its temporal..
Atayeni…. iwoo ndi madolo coz sanapange kwacha yanuyo yopanda mphamvu
kikikikikikikikiki they thought we are stupid!
Ndi Atumbuka guys
your name sounds your thinking capacity
Empty brain
Open the link u blv me both they’re sons from same family Nyirenda
#Vick palibe zamitundu apa,,,,mesa inu ndinu mumapha ma Albino inu? No zeru ncthito kukumba mbewa basi
Mmmmm moti upange comment bho bho uliku mitundu,koma anthu ena amadabwisa
i like fake things but fake money no no no no, they must be sent to prison wth hard labour.
Yoo akalowe bası amenewo wakutınangıra mbırı ya yıthu ya jonı
Yoo akalowe bası amenewo wakutınangıra mbırı ya yıthu ya jonı
Ana Opusa Awa Bwanji Kungokhala Kumudzi Muzilima Gondolosi Ndi Nsasi.Mumaona Ngati A Malawi Ali Mtulo Hahaha! Amangidwe Akathanyuridwe Kkkkkkkkk
kkkkkk
Aaaaaa m’mene akuonekeramo adali Jon yake it? ndiabulu2 ongofuna kuyesa mwayi awa….
kkkkkkk, ngati kujoni ko sizimayenda bwanji osangobwelako nkukalima,, ndepamenepo mwapindulanji,,
kkkkkkkkk amalawi
Kkkkkkkkkkkk amaona ngati ku malawiko anthu ndi opusa kuti ma rands sakuwadziwa?akanadziwa akanangosiya ndithu malawi inachenjera pano
Uchitsiru umenewu. Pamenepa Boma lilandile ulemu ndithu. Gud Job. well done. Sikufuna kupatsana umphawi kumeneko? Akalowe agalu amenewa.