Two arrested for having fake Rands in Malawi

Advertisement
Themba Nyirenda Bernard Nyirenda
Themba Nyirenda  Bernard Nyirenda
Arrested.

Two people have been arrested at Dedza border for possessing fake South African Rands.

The fake Rands amounted to R19, 000 (K1.1 million) and the two wanted to use the currency to steal from South Africa bound Malawians passing through the border.

District police spokesperson for Dedza constable Cassim Manda confirmed the arrest on Wednesday.

Manda identified the two as 46 year-old Themba Nyirenda and 41 year-old Bernard Nyirenda, both from Chiyona-Nyirenda village in the area of Paramount Chief M’mbelwa in Mzimba district.

Police suspect that the men wanted to exchange the forged notes with Malawian currency from Malawians going to South Africa who pass through Dedza border.

Meanwhile the two have been charged with the offence of importing or possessing forged notes.

Advertisement

144 Comments

  1. Eish imali aikho bafwethu kunzima asikisi guys kuzolung’a life goeson mbiya jisawisye pane paliponse khobidi nde ikufunika ma styles ndionse chabe kuti anthu akakutulukira ma style ako ndizimenezi umayaluka komabe never give up

  2. I trust Malawian ppl I didn’t think they had a corruption Even them. But they Help thm selves. because they didn’t robbery any Banks here in South Africa

  3. Kumalaw kumadana ndi munthu oxisakira km ngt inu odalira xolandila Kumalaw kumakuyanja makape nonse amene mukut achita bwino amumanga

  4. Asiyeni naonso amafuna ndalama pitani mukamange a cash gate aja mwangoona kuti ndiosauka ndiye mwapeza nkhani naonso akufuna afane nanu

  5. kusowa chochita a police akumarawi mbava zamu boma akuziwona koma kumaka gwira muthu woti wavutika yeka kusaka dora zama rand ndizisiru poti dziko ramarawi naroso ukavu ngunandi.phepani naremba no ma full stop chifukwa wanikwiyiswa!!!!!!

  6. M’bodza osadandaula inu ndende za malawi ma suspect amangomunyemela iliyose police nkukuthawitsa mu ndende iyeyo nkumalengeza kuti mwathawa apo nkuti kokoliko pamodzi ntomato wake zili kumanja.

  7. Bakili was once found in the same situation, yet noone arrested him. Now why should these be in police cell? Stupid poor fox.

  8. a Malawi,ngati ku South Africa angamange anthu awo atapezeka ndi makwacha a fake? (which they rule out to be useless) Kufuna kuoneka abwino all the time. #buyingfavours#

  9. Walangike watibila nyengo zitali, wapolisi wabekeso pa petroda ku Bt waliposo wanyake ine wakanisintha fek wanyamata apo, nakondwa wakolekapo wanji,

  10. Kkkkkkkkkkkk anthu aku mpoto kuyesetsa kupita ku school kuti muzikabela a Malawi hahahahaha mwatondeka waka! Muzikapangila kwanu komweko ku mpoto osati ku Malawi
    – Anthu ameneo choyamba aonetse ma passport awo kuti anafika bwanji ku Malawi
    – Aponyedwe mudende mosayimbidwanso mulandu mulandu wakwana kale umeneu ndioponsa kupha ALUBINO
    – Kamulepo Kaluwa ukuti chiyani pamenepo?

  11. Ndalamayo fake ai koma bvuto lomwe lakura ndiloti boma liribe ndalama ndiye lapexerapo mwai wofuna kukolora pomwe sadalime podxiwa kuti ndalamayo yakwana Meter. Amalawi kukonda kubwezeletsana m’mbuyo wina zikamamuchitirako bwino. Ikadakhara Kwacha tikadati akubelani inu koma poti ndi RAND ndiye muwabwere. Mulandu Wa Cashgate sakuidziwa anyamatawo.

  12. Nde police cell ukayilowe nthawi yotentha ino kkkkkkkkkk welcome to the world of sikidzi nde ndende yakumalawiyo kkkkkkkkk…..Inu muli after fake money mapeto ake ndi ndende bac ubwino wake anzanufe tili after miracle money zikumangolowa ku bank ine ndili phee

    1. Whats the difference? Iwenso uyenera ukalowe basi ndi miracle wakoyo kkkkkkkk! Wati bambo ake ndi a Money. Kwathu ku timamutchula kuti Mirako Moneyi.

  13. Anjateni amafuna kupitiliza kuononga ziko, chifukwa akanakhala masha-sha akanasitha pa kuchamano nyansi zaozo azisiye m’mozambiqe alone asena aja m’mene akanawamangila.

  14. Anyongedwe makape amenewo kuzi va jon kwambili ama ona ngati maliwi ndiwo gona agalu amenewo mbuzi ama ona ngati aiphula akasungunula 20.000×50=1000000 mwanyela pogona anthu muku choka ku sosibele mwapeza anthu akulila kale zamavuto anjala kukwela kwa fees anthu sakugwila ntchito aganize zama vuto aza chuma inu mwati ife nde mashakazulu matsotsi tii wonetse kkkkk aphwanga ndiku mnpanje kumeneko anthu akuphula njelwa zamoto nde sikuti land angango fikila kuiponya nchikwama nkhope yamandela anthu ku malawi amakhala nayo busy heavy nde ndima damukesi imeneyo akadziwa apitar muthalila aku manthana ndanthu otchuka ngati inu

  15. Bravo Guys! Malawi wadzuka keep it up make more fake rands titukuke basi. China wakutukuka ndi fake materials ife nkulekeranji? FAKE RANDA

  16. Chowamangira ndichani mesa ndi ma Rands akadakhala makwacha bola ndikadati amangeni.

    Boma ikulephera kumanga anthu adaba ma Billion.Umboni wonse alinawo kuti anthuwo adabadi koma akulephera kuwamanga nde munthu akagwidwa ndi Nkhuku mwati amangidwe Shame on UUUUUUUUUUU………….!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!#

    1. Ndiye Amachoka Nawo Uku Kumazasintha Kuno Kuti Chani Mmesa Ndiye Kubako Am’bele Munthu Wavutika Chaka Chonse Kulima Pali Nzelu Pamenepo Muziganiza Man Mwamvae

    2. Inuso tadziganizilani ngati Boma likulephera ndiye adzipititsa dzithu dzoipa kunalibwino akadatenga makwacha afake inuyo nkulankhula mmene mwalembera inuyo A shadreck K sokosi. koma simudalembe zazeru ai

  17. Akhaulitseni amenewo anthu oipa kwambiri musavutike kutaya nthawi ndikuononga ndarama zaboma powazenga mlandu tangowaponyani mundende agwire ntchito yakalavula gaga

  18. Kkkkkkkkkkkk amaona ngati ku malawiko anthu ndi opusa kuti ma rands sakuwadziwa?akanadziwa akanangosiya ndithu malawi inachenjera pano

Comments are closed.