Convoy for President of Malawi Lazarus Chakwera

Chakwera wakuwizidwa

Anthu m’boma la Lilongwe anaiwala kuti mtsogoleri wa dziko lino Lazarus Chakwera anali pa chisoni pomwe anamukuwiza kuti “tipatse mafuta” nthawi yomwe amachokera ku mwambo oyika m’manda malemu John Tembo. Lachitatu pa 4 October, 2023,… ...