Reports that Sylvester Stallone who is popularly known as Rambo is in Malawi have turned out to be false, Malawi24 can report.
One of the country’s publications reported that Stallone arrived in Malawi on Tuesday afternoon through Kamuzu International Airport and later went to Likoma for tourism.
However media reports from the United States of America show that on Monday the actor was in Michigan in America attending an event.
On Monday evening the 70 year-old actor was also spotted having dinner with his wife and two daughters in Hollywood, according to United Kingdom’s Daily Mail.
A travel expert Malawi24 spoke to expressed doubt that the movie actor could have been in the country by Tuesday afternoon.
“Stallone is in the US. It would be through magic for him to be in Malawi when less than 24 hours earlier he was in Michigan, a distance of 13,000 km,” he said.
Stallone is one of the most popular actors of all time and is best known for his role in the movie Rambo.
Rambo azadye nao makose huhuhu!!!?
or atabwera kuno sizoti angafike kwanu,,,,tilibe naye ntchito tkumuziwa since childhood
Zopanda ntchito
Amalawi kutsalila ngati machende ankhumba
kkk…amafuna azamchite Rambo Peter….kkk..hahaha..
Akuzapanga ma interview a U General Commander wa MDF,,,,, si paja a Ignacio Maulana pano nd mkulu wa BEAUTIFY MALAWI,,, iiiiiiiiiiiiiiiiiiiiii ndinaywala paja ndi mkulu wa NFRA
Yes it doesent change
Ma Admin aku Nyasa osowa job kukhalira miseche basi
A ntaba ndi a Dausi akana kuti Rambo sanabwere koma otsutsa akukana kufuna kuonongs mbiri ys mtsigoleri wadziko lino
Koma mpaka ine kwawuza ana anga kuti Rambo wabwera ku Malawi eeish sinzakukhulupiriraninso asaaa,,,ana anga aziti a Bambo aboza munandinamiza inu eeish
To do what in this rotten country.
Besides what business would he have had if he were to come to Malawi anyway? Wishful thinking.
We don’t care either
Adzatani kumalawi Rambo? Chambachamba eti,
Akuti abwela kwa #KAMLEPO kuzamudilisa kukonzekela kubandulana ndi #PETER
Hunting elephants with a knife
Adangoona Nakamula mwina!
Rambo ? mapa anu mwamva nde mumamunamiza ndan,
Kkkkkkk bodza Malawi24 iiiii
wat change can he bring anyway? whether he is here or not is useless to ordinary Malawians. Go get a lyf!
Ndamuona ku Ching’ambo
Inenso pa msika waching’ambo
WHICH IS WHICH?
Kaya tiziona basi
musatinamize dzuro ndakumana naye kumbayani amagula chinangwa
Philimon Qoto, Memory Ndhlamine, Lackwell Botha hes not in Malawi
Zosatheka
aalidi konkuno dzulo anali ku nyanja kenako anazapita kuchigayo nde pano akusaka nyumba ya lent
Ine ndamuona mu limbe akulawa nthumbwana,akuluakulu..wafikadi phiriyu’
Jounalism in amalawian style kkkkkkkkkkk
Lack of professionalism, no truth in the world
Mkabudula mwako walemba zimenez
Does my brother looks like Rambo?
In malawi to do what?
i hate shit,dont play wirh pple
Whether he is in Malawi or not it doesn’t change the price of buledi.
Kkkkkkkkkkkkkkk
buledi lolest
kkkk
kkkkkkkkkkkkkk
Osati masikono? chifukwa ndi buledi yemweyo ndiwosowa madela ena kkkkkk
Kkkkkkkkkk
Ena akuti van damme wabweraso kumalawi eti ndi zowona.
News24 Kamulepo ndi RAMBO wa ku Malawi
Are you desperate in need of watching Barclay’s premier League live matches for free, movies, wrestling and many more ????, call or whatsapp me for cheap installation on 0881687272, 0999172498 ——MAXLIN CONSULTANTS—— ——EXPERIENCE THE BEAUTY OF FREE TO AIR 4 LIFE——–
ndimulungu zopusa basi agalu inu ife tinakufunsani kuti mutiuze
ndimulungu zopusa basi agalu inu ife tinakufunsani kuti mutiuze
ndimulungu zopusa basi agalu inu ife tinakufunsani kuti mutiuze
Are you desperate in need of watching Barclay’s premier League live matches for free, movies, wrestling and many more ????, call or whatsapp me for cheap installation on 0881687272, 0999172498 ——MAXLIN CONSULTANTS—— ——EXPERIENCE THE BEAUTY OF FREE TO AIR 4 LIFE——–
Akulu, Barclays are not the sponsors of EPL this season nde it’s no longer Barclays Premier League
But for people to understand it better its nice to put it that way boss
But for people to understand it better its nice to put it that way boss, thanks for your thorough observation.
Searching….
ndmuwona ku singa bay ameneyo osakana apa muzichta kukanizila ng’oooooo! Ine ndmuwonabe
kkkkkkkkkkkkkkk sorry Malawi 24hrs bodza lanu anthu wena adamangidwa, kuphedwa, Kudana, komanso kunyozedwa because of your reports
Malawi 24 You Are Full Of Shit You Want People To Call You Agile Yet You Are Failing to come with khani yabwino takutoperani tsopano. Pang you waiste my data. The Country were jolly to think what next 2mrw and you post a nonsense story kutipanga Cashgate kumeneku ngati simukudziwa ta uza dolla pofuna kubva za chambazi. M’maso mothinamo mxm zopusazo ai atherwise page imeneyi mungotseka kenako mudzalira nayo.
Maboza akula ku 24 Malawi kkkkkk
Ndamuona Ine Lero Ndi Maso Anga Awiriwa Atatenga Mfuti Mu Film Ya Rambo 4 Ndiye Inu Mukuti Sali Kuno?
ndekuti jet lee Achina van dame Achina swazneger chack norlis alikunoso Flames 23 can confirm this
uja anapanga yachichewa aliku Malawi bt wa yachizungu is not in malawi
Ngati Gidesi anapita ku US what more Rambo kubwera ku M’Mpanje ?kkkkkk!!
Rambo yemweyo kuti wa!wa!wa!
Kkkkkk Malawi 24 manyazi bwa mulibe?
Patrick Wazisomo Vinthenga plz don’t make me spit my tongue out wit laughter
No comment………….
Ndi zoona Rambo wabwera ali mdziko muno. Ndinakumana naye lero masana pamsika wa pa Chimbiya ku Dedza. Mawa akuti akapezeka pa Bembeke ku Dedza komweko.
Whever he is here or not but am here
Can you prove it
apolice kuzomba akusaka mkulu wina yemwe wazipha pozimangilira kudenga lanyumba lake. komwe wathawira sikukuziwika
Afikira kt??
This page is fake and fuck
Atola nkhani a24 pitani kuxool mukaphunzile bwino nchitoyi
Mwina anagugula ndiye mm’alo mwa Mali anawona ngati Malawi inenso kudabwa kuti angabwele kuno ameneyo ngati anamuwna pa airport mwina anasokela kuno koma anzathu aja aku jamaica amafuna adzaziwonele wokha kuti kunonso chimalimidwa
Kikikikikikikikikikik
Rambo wakuncheu uja koma wafikila kwa AKILA ENTERTAINMENT
chamba
Mumakwiya anthu akamanena kuti atola nkhani ndinu aboooooodzzzzaaa
The actor died few years ago. Now you are saying that he is in Malawi….
Awuze agalu akutsalila ngati matongo ankhumba
Man auzeni chichewa choveka bwino kuti akutsalira ngati machende ankhumba
His death two years ago was also a hoax!!Google,you’ll see,he’s alive.
His death two years ago was also a hoax!!Google,you’ll see,he’s alive.
Anafa mu movie kkkk
iwe Rambo sanafe unamva kut zimenezo
boza yanthunthu imenei rambo sanafe guys
kuno kt kaya kuno kuti kaya kuno kumalawi 24 news kumalawi kuno chilungamo chathawa bodza lifika kuziwa kulbe
Rambo akabwele kumalawi chaamba olokulota samalota
Could possibly be one nicknamed Sylvester Stallone working for nyasa times who was on vacation in the US.
Koma m’mene alembera Heading yo..t means kut alikuno..!! “No,silver stallone is not in Malawi”..Tha means positive…..,,coz sentence ikatere No…ndi not zima khansulana……….
Chizungu munaphunzila kuti akulu?
Ndinangobadwa nacho bas..kkk
Bakili Muluzi anaonongadi zithu ndi free primary education, zalakwika pati apa?
Nde poti..mukufunanso free..university..nde zifika pa worse tu….sinanga bakili ananonga…ngat thaw yakamuzu..mumakwanitsa kulipira fees…chisecho..1 kwacha…..peter akat university ikhale yaa free..muzamunyozenso ngat Bakili..anthu..pabwino..mulibe……,,nde fees tikwezansotu….
Bwana Ali uyuli yambani ya kwacha
Ayao osamalowolela za english palibe chanu dziyakhulani dyekwedyekwe wanuyo bas
Panopa yakwacha..ndikuchita bwino..mot..nkalasi andisakhanso u Leader
Ali Uyuli,tawelenganiso chiganizotu chikuvekabwinobwino,
Kkkkk…willy dyekwedyekwe..mpaka et….ok
Ha ha ha ndimangoseka. ,,some comment..ndekut Awilly inu…ndi Black America….or white Man?
Kkk ine ndiwaku Newcastle man UK
I can see…..,,,I like Debate…de sentence z right..coz..if it starts with No!…it means dat…someone was told lie to de nation that someone..,who z Rambo z here… ,,so to respond that kind of false stories we can start ndikutsa Which z( No)….then nd ndikunena kut muthuyo sali kuno…which z..(he z not in Malawi)..
Nonse..Mwakhoza..koma Rosemary…nde wapambana nonse..coz..she was de 1st one..to respond my comment…Rosemarry ..lets meet inbox..I hav ur Gift…
HAHAHA mpaka Grammar zomwezi
Kkk..Man..Tikungopitiliza bodza ..lomwe layamba kale…..,,Nafe tizinamizako azanthu..aaah……ife nde tizingonamizidwa..ha ha ha
Kkkkk zakhansulana basi.straght,forward sentence,koma mungokhala ngat nchiphwitikiz plz
Chizungu sitimvera sound, we follow rules
Chizungu sitimvera sound, we follow rules
A! wanatiphalire wa zbs,lekani tipukekwa zodiaki para ngunenesho.
Mbuzi za atolankhani kufuna kutchuka ndi nkhani yosafufuzidwa kkkkkkkkkkkkk
Kakakakakakak hahahahaha eeeeeeeh koma pamalawi amwene mmmmm kaya tsopano!!
Kkkkk
Nde tizikhulupilila nkhan zomwe muzipanga post choncho???
cholinga mukufuna mbulu asakhare ndinkhawa,amunyokabe
anthu aziti bodza ilo kuMalawi.
It seems the writer has failed recognise that visitor,sorry,vuto si inu kma anakutumani kuti mulembeyo
Abwere or asabwere palibe ndipindulepo ine ndiye msandisokose yaagh!!!.
Zaboza Ali nkokuno boma likubisa kuti musithe koma he is here no smoke without fire am not a fool
Basi ndasiya kutsatira page yanu yabodzayi
Timve Ndani Pakati Pa Malawi 24 Ndi Nyasa Times?
nde ena atukwana tukwana pa khani imeneyi lero akamanva kuti njabodza zamanyazi Z…
Inuyo ndiye zitsiru mesa manena ndinu
Kutengeka kuno nzilizonse kukabedwa ndrama zaboma ndiye osayakhura kathu mxiem
zodiak sinalembe nawo zopusazi. That’s y sometimes……………….
Anthu openga inu,kodi umbuliu uzakutherani liti?Rambo angabwere muno dziko boma osadziwa?aaaaaaaa!koma abaleeee,zamanyazi
Mungo namizana muli phee, news paper inanso idanamiza amalawi koopsa namanena kuti team ya south africa under 23 yachita ngozi ku brazil chimene chidali chibonya cha goo kuchokela kwa munthu wa ndevu.
Koma malawi24 bodza lanu mulibenalo manyazi.
Ndintchito zanu atolankhani athu aChimalawi kupeka nkhani kufuna ma comment ambiri
So what???
ndinu zitsilu kwambili that’s mukukalambila konko maiko ena ntchito simungaithe
Malawi 24 ndiyopenga zeed
Malawi 24 you were amongst those fubricating the hoax and because its proven to be a lie,you are puttig yourself out of the liars.
not forgotten Malawi Punch kunama onsewa basi
Yes Kkkkkkk amakopelana amenewa. Akanama mmodzi ndiwonse.
They saw me. And they thought it’s him.
Ok.
musawone mzungu wazimphamvu atavala maglass atintedi muli Rambo ameneyo..
kikikiki,Dont Sekesing Me
Kkkkkkkkkkkkk
kkkkkkkkk koma you
Contradiction to you writers which means you just pick up story from nowhere.Shame…
Kkkk mr Gawani.
Mbudzi zaanthu izi akhuta migayiwa mkumazitcha ma journalists kkkkk
koma zinazi
doing wat in that shit country
Kkkkkkk
Just Apologise For What You Told Us, Osamabwetuka Ngati Inu Simunalengezenawo!
wakufusani ndi ndani?ameneyo ndi msilikali wodziwika kwawo ndiye sangabwere kuno ngati bakha dziko osadziwa.
Mpaka bakha
Kkkkkk
Kkkkk koma abale
that’s why I have been saying that these journalists 4m Malawi24 are idiots, simandivera satha chizungu can u see there
that’s why I have been saying that these journalists 4m Malawi24 are idiots, simandivera satha chizungu can u see there
misala ya Malawi 24
Plat kak u nayi24news
Koma bwanji muma ulutsa maboza?
Even whole world would have known
timve ziti kodi
eish Most of Malawian we like to spread fake story’s that’s not good…have the whole information before telling someone please…
Mesa Mumati Akugona Ku #likoma? K K K Ugalu Bwanu’
lkkkkkkk
Watıpusıka kale wanyınu tımva zıtı