Blue Eagles have pleaded with the Football Association of Malawi (FAM) to ban Surestream Stadium in Blantyre from hosting big games.
Team manager for Blue Eagles Gabriel Chirwa made the remarks on Wednesday after the Lilongwe side suffered a 2-1 loss to Wizards football club.
Chirwa said the state of the ground is not fully fit to hold big games, singling out the parameter wire fence which he said is damaged and needs renovation.
He further said that spectators were hiding balls when they went out into touch, a development which affected the tempo of the game as there were numerous delays.
“Let me plead with FAM next time when they plan for other games they need to select good grounds, and if they cannot then Blue Eagles will not accept to play at Surestream Stadium again,” said Chirwa.
During the match, Wizards’ Hendrix Misinde scored either side of half time after Blue Eagle’s opener to boot the Lilongwe side out of the 2016 Carlsberg Cup.
Kuluza ndi kumeneko but if we want to improve soccer in Malawi Let us start with grounds starting from this small leagues up to stadiums pa stadium ku makhala ngati podyera ng’ombe and we are happy with that . It just shows that something is wrong with us
IF THERE IS ANOTHER GOOD GROUND FO SUPER LEGUE HERE IN MALAWI,,,SURESTREAM IS ONE OF THEM….ANGOSOWA ZONENA AKULUWO
Pepani anamalira….. Kumeneku kudali kuyankhula kwa aaenimbumba.
Mmmmm mbwiye zangovuta basi tazidikirani fisd cup
Angoyamba Kumene Aziona Chakachino Kaporo Stars Ikubwera Kuzakuthilani Utsi Konko
pa nankhaka nde mpachaninso pamenepaja?zavuta zavuta basi
Words of a dying horse. Nsangopita tilankhulebe basi.
Ground limenelo ma team akulu akulu ankasewela pomwepo ndiye akufuna likhale lotani ? Just accept defeat
mvula ikagwa kuchuluka zoliralira..zakuvutani basi
Nankhaka Ndi Surestream Zasiyana Pati
Aaaaaaa Choka iweee coach wabodza anzanu a Widzadz wo amasewerera mmwamba, ?mwaluza mwaluza basi kuzolowera nyanga basi !odziwa kuvina sasankha nyimbo ,mlimi sasankha khasu
Ground silimenya mpila asanamizile anaphedwa basi.
Ndiye Kuti Wizard Imamenya Pa Fit Ground Eti?Ndiye Kukubwera Akulu Awo Weekend Ino Komweko.Adzakupaleni Mamba Kachikena
Kkkk kma ukamenyedwa ndmwana umachulutsa zolankhuka kwabasi eee chifukwa munandgwira ndchfukwa anapeza mpata ondmenya kkkkk kuvomeleza basi sikuti musitha dzina ayi
Kkkkkkk ndekuti capita osadwala?
Iiiiiiii ndizovesa chisoni
Agwa nayo basi. Kkk
Ngati ground unfit chigoli chinachija munachinya bwanji?? Za ziiiiiii mxiiiiiii
Nao mateam akulilongwe akaluza kuchuluka zonena mwatulukabe, muzingodikira BB ikugazeniso simuupeza pumulo week ino
Heheeeeeee kulira kwa munthu wankulu kkkkkkkkk
Uku kunali kulila kwa ayini mbumba
Ilo Ndi Bodza Pamaliro Pamakhala Zambiri Zonena.
Zavuta bansi
thats true anawa anawinira kulizolowera ground lawolo
Coz mwaluza,if my memory z gud,u played on de same ground last league and u won de game nothng u talked
Pa nankhaka ndi ground limenelija pabwino mpati?
palibe aluza aluza bas osat stadium unfit palibe Khan nkoseko kusavomereza kut aluza
Bwanji matiuza lero yet he spoke on wed?
Hehehe zavuta bax
it waz gud if they (eaglez) say this in the first place b4 the game, akulira ndi nkozo wawo angovomeleza kut aluza bac
Aaaaaaa Chifukwa Choti Aluza Nde Aziti The Stadium Z Unfit, Nanga Akanawina Akanati Chani Aaaaaa Za Ziiiiiiiiii
Mukaluza mumachuluka zoliralira
Pali Standium yomwe ingafafane ndi MDC tangonganizani Balaka Standium, Dwangwa Standium, komanso ku Mtchalo Standium ingafanane ndi MDC Standium?:D:D;( mukunamatu inu standium ili bwino kungoti ndikomvuta kubvomeleza kuluza azanu azisewela basi!!