…as students block US second lady Dr. Jill Biden convoy
Irked b the noise perhaps villagers around Matawale and Chinamwali areas in the city of Zomba have joined another grouping of Chancellor College students who are in a cat and rat chase with police officers in the city.
As we reported, the students are protesting against the decision by the University of Malawi (Unima) to raise fees for generic and mature students.
Some of the students had to run away to villages around the city in fear of being arrested by the police.
But police who followed the students around met the wrath of villagers who claimed to have been disturbed and therefore rallied behind the law enforcers in the running battles.
As this post was made, the students blocked the way for a convoy that was carrying the US Second lady Jill Biden who is on a three day visit in the country.
The college has since been closed.
Kkkkkkk achita boo kapolice unit kamenej
kkkkk
Kunangonditalikira naneso nkanalowerera kwa ma students dziko lokondera opata ili ena kumakhala ngati ndi marefugees dziko lathu lomwe
Hello I’m Samuel Okizou by name, I’m giving a testimony about Dr.Sule the great Herbalist, he has the cure to all manner of diseases, he cured my HIV disease, though I went through different website I saw different testimonies about different herbalists, I was like: “Many people have the HIV cure why are people still suffering from it?” I thought of it, then I contact Dr.Sule via email, I didn’t believe him that much, I just wanted to give him a try, he replied my mail and Needed some Information about me, then I sent them to him, he prepared the CURE and sent it to me via UPS courier service, they told me that it will take 3-4 days before I’ll get the parcel, 3 days later I received the package and I started taking the medicine as prescribed by him, after 7 days of taking the medicine I went for check-up, I was tested HIV NEGATIVE… IF YOU ARE SERIOUS YOU WILL BE CURED!!! contact Dr Sule on whats-app +2348162447651.
Let’s fight harder!! Ndamva zoti army ikubwera, let’s dont give up.
Uyu uyu akanakhara kuti makolo ake amkapita kumunda around 4 a.m kukalima maganyu kuti ana adye and apeze yogulira ndiwo sakanapanga choncho.iwo anadutsa moyera umphawi samaudziwa.Muganizire mwana oti amalimbira xul,form 4 kukhonza bwino a unima ndikumutenga koma asakudziwa kotenga fees and loan osatengedwa.Yester a friend told me kuti Next academic year sindibwera 400 000 ndiyambiri.KWA MUNTHU OTI UMPHAWI AMAUDZIWA sizikanakhara choncho.AMBUYE ATITHANDIZE!
Insanity…
Kodi mbewa ndi zitete pa kilo zikugwa pa bwanji? K500? Ife vuto palibe kwathu ophunzila kwambili anafika std 6, zoti amalipilanso ku xool kaya college sitikudziwa ndiye xool us please! We are very busy kusaka mbewa ndi zitete boma latipatsa tender nde nditha kulipilira ana a chancol onse fees mukambayo. All Chancol students just list your names below, Ofuna ntchito yosaka mbewa kapena kupha zitete(Agulu mamina) mubwele kwa Wenela we are recruiting on monday next week!
Dzuka please Malawi DPP imapha Ana asukulu iyi mmalomothandiza atsogoleli amawa awa Malawi uli busy Manu gweee kusekelela Mbuzi 577 billion muthalika ndi nzake akutiwonongela malawi wathu you??? Why Malawi ?kod ndi kupeleka? Zowona malo okusiyila agogo aja uzilipila?kwenikweni ndichani Malawi? Kapena tiziti ndiwe watulo? Plz Malawi dzuka DPP WATIONJEZA…….. 2
Bola kuti ikhaledi demo yeniyeni mngomuphapo mupolisi mmodzi kuti ayifere ntchito yopanda malipiro ngati iyi that can be better to send message to the malawians as a nation kungomthyolako khosi mupolisi mumodzi just to put him/her on a map
Kupusa,usavege ,umbuli,ndiye apolice ntchito yawo ndichan ?,apolice sangalolere zopusazo kut zizichitika ndipo achita bwino kuwathila machaka,Panopa zulo lija mmene imat 02:00pm ana onse apa achanco awathamangisa pa xool yi,ndipo ana 12 awasekera Ku Zomba police station ,ena akagona mmuz kuopa kumangidwa pamene pa waluza ndan?,angavutike ndan?,munaopo ana apa college of medicen ku BT.akupanga zopusaz mwapambana bwanji inuyo,kwacha ikagwa palibexo kuchitilira mwina zinthu zimakwera mwandikwiyisa heavy,azibale anga Ku Zomba ko azikhala mwamantha coz ov u stupid students chanco ,chanco cuannn..
Vuto ndilakuti apolice timamwa nawo m’ma bar athu a lokolowa ndiye tidziwatibula out of work! Amene alibe ndalama ndi amene akulilawa, opeza bwinonu mukulimba mtima nanga simukaba misonkho ya amphawife.
Kupusa,usavege ,umbuli,ndiye apolice ntchito yawo ndichan ?,apolice sangalolere zopusazo kut zizichitika ndipo achita bwino kuwathila machaka,Panopa zulo lija mmene imat 02:00pm ana onse apa achanco awathamangisa pa xool yi,ndipo ana 12 awasekera Ku Zomba police station ,ena akagona mmuz kuopa kumangidwa pamene pa waluza ndan?,angavutike ndan?,munaopo ana apa college of medicen ku BT.akupanga zopusaz mwapambana bwanji inuyo,kwacha ikagwa palibexo kuchitilira mwina zinthu zimakwera mwandikwiyisa heavy,azibale anga Ku Zomba ko azikhala mwamantha coz ov u stupid students chanco ,chanco cuannn..
Kodi chikala amkalilira nyanga nyumba itapsya adamuimba munyimbo ya mulungu uja ndi inuyo kapena agogo anu?
Who has won now? Shame on them
So sad
The Govt Of Malawi Is Now The Govt Of The Rich.Kulimbikira Kukweza Zinthu Chosecho Anthu Nd Osauka, Akuona Ngat Ndalama Anthu Akazitola Kut.The Poor Wil Get Poorer While The Reacher Wil Get Reacher.What Kind Of Govt Is This?
The Govt Of Malawi Is Now The Govt Of The Rich.Kulimbikira Kukweza Zinthu Chosecho Anthu Nd Osauka, Akuona Ngat Ndalama Anthu Akazitola Kut.The Poor Wil Get Poorer While The Reacher Wil Get Reacher.What Kind Of Govt Is This?
Big up to the villagers and don’t stop keep going strong.
nanunso apolice mumalowerera zinthu zozawakhuza, do u tink u can afod 2 pay 4 a huge amount of fees de government unconsiderably,thinkinles is presenting 2 pple, that is torture. say u want 2 reduce graduates due poor jobs we know this.
Malawi 24 , you write things which your not sure of.
akudziwa kuti fees timakatenga kunyumba komweko
big up to the villagers big up
I can smell a fight pa gulu lino
Makolo azelu amapanga choncho
koma ya! Abel Chinsisi Nyamazani Maseko
Job well done, akutionjeza mwapiya ameneyu
eti adha
Kkkkkkkkk kunachema et
Where R the so called civil society organisations ? they r busy eating & giving a deaf ear to the cries of chanco students , this is the battle that must be fought by every citizen of good will . they have forgotten that they were on gvt bursaries . now that their belleys have protruded with tax payers money don’t like poor sons & daughters of this trouble stricken nation to be educated . shameless coucil leaders .
Prease aukhaida help us with Gun prease we are tiered with opresion any body who is poor will join us peace is now fell osauka kumangosaukabe.
Chonde amalawi zinthu ngati sizilibwino nenani.Wins as soup on bone semi boma lathuli lalephera tiyeni tione zina Mwaiyiona nkhani ya Land bill IJA ikuyendera basis tonsefetu tigulitsidwa..take care Malawi.
apolice nawo ali vwiiiiiiiiiiiiiiii kupusa eti?? osaganiza kae kasalary kanu kaja bwanji?? anthu mumalandr 40pin,,, ndie taganiz iwe wapolice pamenepo ungakwanitse?? ur stupit
I wish l was there to join u gyz am tired with dis stupid so called government
mutinamiza inu… kkkk,
this gvt has no vision mo fire my b loved students beat those idiotd policre officers
They are guardians for chanco students
Pagulupa ndikutha Kuona kuti Pali wina wathawa Ku Zomba Mental Hospital apa. Zokamba zake zikukhala ngati wangobwera Ku Malawi kudzacheza, akhatha abwelera kwao Ku UK. Pamene mudzi mwao ndi Mwachiuziramunso. Pepani ndamumvetsa munthu Yu. Wadya zitete ndi mbewa zochuluka lero.
KKKKKK Yooooo
What I Know Is This;
.
Kulimbana ndi BOMA ndi chimodzimodzi ((KUKOKA MALISECHE AKO MWAKHANZA-ena akuwonerera ))
.
Who can feel the Pain?
Boma limagonja man ndidaona academic freedom itatheka mpakana kape wina cardiac arrest
Not villagers but thugs cos villagers are always quick to realise the nasty consequences that comes with such.
Hahahaa Km kumeneko
yaa go ahead
Koma izi zomati mukajambula chithunzi nkuyikapo chi ujeni chanu ichi cha Malawi 24 mpaka chithunzi chonse osawoneka, ine nde zimandinyansa koophya…
Wat cmez next z tu riquest doz hu statng voiyz but malawi will nevr empwer az own.tizingochedwa zopanda pake insted zabwino.osazikonda ma lycter pliz.
Bravo locals. Amene akukweza fees’wo adophunzira pa ngongole ku university, worse still they’re not paying back the money. Now akufuna kupha education kuti only ana awo ndiamene aphunzire. Shame on you a council
Sorry guys, its part of life.
#Oppression is one of the bad themes circulating in all corners of this #NYASAland (malawi) what a presidency? Lucky are those who did their University Education during #Kamuzu’s era, You people lets think #wise on this, paying fees at #TTC (PET)?, Aplying for university #Loan? Where are the good #OLD DAYS? free university #Education. this is a total #OPPRESSION TO THE #POOR and I 100% agree with you #Students at #CHANCO the #chilunga. LETS SHOW THEM THAT WE DON’T WANT #OPPRESSIVE acts.
Mukhalira zomwezo makape
koma kumenekooooooiiiii
Paja ma villagers ndi amene amasaka fees
Ma parents nanuso wonesani kukwiya kwanu ngati mmalephela pocket money mukwanisa bwanji namatetuleyu tiyen basi tiyetiyetiye
tawerengani chibvumbulutso kt muziwe zoona zake zenizeni za nyengo pamene tikumane mzotsautsa kuposa kukwezedwa kwa xl fees
more fire chanco student!!ndalama zachulukitsa kodi ndiacivo servant angati akulandila k4handred southand mboma?sionse aliopata zanyanyatu apa koma dzikoli muli presedent ngati alipo nde ndibwantasatu!policeyo thibulani atikwana mazoba amenewa amalimbana ndi za ziii mmalo mogwila mbava
Solidality at its best..i dont have any relative ku University but i still find this fees hike as inhuman tikatengela m’mene life yalimbira pa Malawi pano. Am in support of what you guys are doing!!!
Azanga taonani mchilombo chinthuchi ngati chidachoka chili du osachitapo kanthu ana akuvutika chonchi.suja anatsekaso ma college? Sizi
Kod ndi chan agalu inu Ku zombako ,,?zot kwacha yagwa simukuziwa ndiye mumafuna kut fees ikhalebe mwakale momuja?,chimene mukuswera magalimoto ,komaxo kulanda malonda aphawi aanthu osalakwa ndichan?,boma likachitapo kanthu muzit boma la peter ndilokupha eti ,,?mwandikwiyisa kutachere chanco inuyo kutan?,manyi ambuz akuthire machaka apolice osagona pa duty tiyen nawon
iweyo ndiye mbudzi yothelatu wamva munthu opanda nzeru iwe nsunu wako sunukanyoko wamva ndi boma ntchito yake ndichan
panyapako aise zoti unapitako kusukulu ndikukaika….pamene ulipo or mwana omulipilira fees ulibe kape zobaaaa
Kkkkkkkkkkk mamemba sopano
hike the fee basi asafuna asiye
Palibe kuchitira mwina fees ikwele bax
Lord we dare still
i hav noted dat countries which hav corrupt presdnts tend to hike everythng unnecessary,ndaonera #zuma ndi #mutharika
#team_ZICHECHE Sitithandiza!go chanco!
Pamenepa pokha APM wapala ndipo akapitiliza vote yanga sadzaipeza come 2019
Aliyese apa akukatha dpp dpp yavunda basi
Amene amkakambirana zokweza fees chonchowo tiwathidzimule
Everytime i read about these senseless fees hikes happening in Malawi i feel really bad for my Nation. Everywhere in the world students are fighting for zero fees in all institutions of learning and to the contrary in Malawi they are raising up the fees rediculously.
This is a real kind of brutality the government displays when it has failed its citizens. The reason why we have too old madalas in most key government positions, who are always sleeping while on duty, is because we have denied our own youth a better education through exhorbitant school fees. Malawi with its current leadership is really in a state of mediocrity….we can nolonger afford to live like foreigners in our own land. VIVA THE REVOLUTION….VIVA MY FELLOW UNIMA STUDENTS…
@George coz of ur fucken shit “shame on Anthu ofuna cheap EDUCATION” u r very stupid in block letters!! how can u sy that??
This has take to de old good days of de late DU CHISIZA Jr On his play called, STOM ON LITADA. DE XOOL FEES IS UP,DE PRIZE OF SUGAR,WATER, TRANSPORT,RENT ALL IS UP BUT MY SALLARIE MY PAY, MY WAGES!!!
kkkkkm kma pamenepo
@ George,shame on you “Zoba” if you don’t have anyting to say on dis issue jst shurt up ur facken toilet! wandinvetsetsa!!!?
Wandikwiyitsa ameneyu heavy
inenso wandikwiyitsa heavy Zoba ameneyu!! @Henry look at his prifile picture “MBALAME” enieni@ George usadzayambilenso wanva?? ngati ndakulakwila “ZAKO” ine sindipepetsa wandinvesetsa??????
#mike Otsapepetsa mbudzi tikumana pamene akupezeka ndikuziwa tionana kuchakumwa utipedza man,
jst understand him, ma comment ama yourth cadet a DPP samasowa!
Zonvetsa chisoni a police akuponya ma teargas chonsecho salary yawo sangakwanitse kulipirira mwana ku college .
APA solution ndiyophweka. Chosani subsidy ya fertilizer, malata ndi cement zomwe ndi za campaign, ndalamazo zipite Ku fees ya college. Akamaliza sukuluyo azagulira makolo awo kumudzi fertilizer, cement ndi malata. Simple.
Ntchito yake akayipeza kuti pa Malawi Makalata amadegiri akung’ambika osapeza ntchito.
Pamenepodi. Komabe ntchito sikulembedwa kokha. Athanso kupita maiko ena ngati Botswana, Moz komwe ntchito zikuyeselako.
nyumba yamwini sitiotchera mbewa. Xenophobia , blacklisting ndizomwe zikufuna kuyambika mmaikomu
Atiwonjeza kwambiri
Apolisi opusa osathyola anthu myendo mbuzi za apolisi
Akuba ndalama akungokhala phee kudya ngati ndi zawo! Atengetsetseni agalu amenewa akulimbikitsa kuba pa Malawi. Tsogolo lingakhale labwino kwa onse ngati mukweza fees kuti ana anu okha aphunzire?
A Malawi a Malawi tizamva liti anthufe ngati mkufuna tengani boma tione
I think it’s the nigga thing to hate the police
What is Chanco?
Apolice mufela za eni.koma lero lokha tithana nanu
One effective way of reducing literacy rate in Malawi is hiking public university fees otherwise by 2020 ndekut Malawi adzakhala ovaya coz we are priotising school as the best way of getting income….chodabwitsa ndichoti 3/4 yama lectures a UNIMA masters degree yawo amakatengera kunja through schoolarships coz kwawo kuno amakanika kudzilipilira okha nde nchifukwa chani akufuna ana anzawo adzivutika? Come on lectures
more fire…kkkkk poly,bunda,com where r u..zikanakoma zikanakhala kuti all institutionz are in it together…
A Malawi kukula mopepera thus why anthu akuluakulu amene ndi amuna a ndevu zawo akulilira zinthu zotchipa. Remember the Mutharikas are here to teach Malawi on how to rely on our own. Olo anyanyale asayiwale kuti ma lecture zawo akulandira komanso a policewo alandiranso ma allowance. Akanyanyala palibe amene atavutike okha abwereranso koma zotsitsa fees iwalani. Ana a mabwana ndi amene akuyambitsa zisokonezo zimenezo chifukwa iwo akuziwa kuti akapita kwawo akayamba ma private. Shame on Anthu ofuna cheap EDUCATION. fees must be hiked basi
mbolo yako Galu
Waa! Iwe ukutchula ya ababa ako pagulu? Psyiru iwe eti? Uyesa iyeyu mwana wa amama ako kapena shamwali wako? Buluka!
mbuzi yamunthu
mbuzi yamunthu
Please show us apicture ya mbuzi ya munthu tiyiwoneko.Kodi imakhalanso ndi nyanga ngati mbuzi timadya ija?
DPP
wasted sperm
Olo mutukwane…..mukutukwana chotukwanidwa kale kkkkkk ndinazolowera
achisilu mwana uja Ali standard 5 uja muzakwanisa kulipira inu mbuzi yamunthu mukuganiza kuti izakhala pa bwanji ngati pano yafika pa 1.4 million
Ngakhale dzina lakolo it doesnt sound that you are a malawian ukulankhula motumbwa ukuyidziwa maximum wage ya pa malawi pano ngati munthu amalephela kupitiliza maphunzilo chifukwa chosowa K45,000 ndiye pano akuti K600,000 ndi angati angakwanitse mbuzi ya munthu iwe
Kodi chinatukwanidwa kale, iiiii koma man
Palibe chazeru ukukamba majority rules athu tatopa nanu nde bola president akhale winiko
Kupusa
Fuck them athyoleni miyendo agalu amenewo ngati akufuna yotchipa apite ku chipinda cha bambo ake ndi amake akatsekure yake,,,,, mbuzi za anthu,,,,ukutukwanawe mbalame yopanda profit pa world pano,,,
chitsilu ichi galu
mbuzi.
Majority chani apa?? Ku chanco aliko anthu angati?? Mukanakhala anthu enieni simukanathiridwa teargas. Ndiponso Chanco angoyitseka tikuonereni. Tione ngati simukapepesanso ngati nthawi ya Bingu ija. Fee hike yomweyo basi. Kuzolowera zochipa
Kwathu kuno timati CHINDELE CHAKUFIKAPO
Name ;George Daniel Origin ; Burundi current Location : Dzaleka Dowa
Kkkk
Kodi when the fees is hiked do we get a new syllubas …..or special attention. ..kapena azikatiseta ku toilet komwe. …cause fees is hiked. ..accommodation 36 000 per month …..so if you can afford we can’t …we not asking for it not to be raised but we want a reasonable hike. ….not 300% hike …….so lets be reasonable…..
Goe machende ako kodi zikukusangalasa zomwe akuchita mbuzi zankoyo
Iwe psyiru usamatchule uniform ya ababa ako pachimtindi wamva? Psyiru uyu akuthabula maganizo ake!
meee!
Ikwere basi
#flypar zikundikomera heavy
Chizeleza
Fwetsekee zako wamvaaa!!! Nditha kulolela2 kufa money zanga kupita kwa ng’anga kuti akulodze Galu iwe
Cadet
Kwanu akati wophunzira ndiwa std 3 stupid
#george ninga~up, kos~kol maliz, useles otsabeleka faaa, uliibe chilichose
Kkkkkk! Amuna andevu za kunamizira umphawi kkkkk. A amalawi kugona too much Peter akudzutsani. Olo mupange makani Mutharikas akalankhula palibe kusintha. Asafuna akhale palibe akukakamizidwa
uli ndi tsoka iwe.ndi munthu wa mtundu wanji iwe?
Chitsiru chimenechi akuti chi George kaya….
#Noel-DangayaDikirani ndidye kaye chamba……guys musanditukwane ndine wachamba……Chitsiru chili ndi mwini kkkkk
haha..muowozeni..woooooooooooo!!!
How many pipo in the govt amalandira 400000? Ngati munthu akupanga withdraw ndi 275000 what more 400000? Use ur brain to think critically.
Ndamudziwa George Yu Ndi Uja Amanyamula Chithunzi Chapitala Pa Misonkhano Yake Yambiri Ma Plan Adamuthera Kale Kale Akungodikira Tsiku Lakufa Basi
Wa maplan sangalilire za ulere
as far as am concern u r big fool.hw dare u say that
panyapako iwe wamva
Bwanji akamakweza feez yo salary xo yamakolo izikwela molingana ndi feez?
Konyelera kwako kumtumbo. pitiliza kukhala ndi chilakolako chofuna kuchinda mayi akocho.
Ngat ukuziona udolo mwapadera Mulungu achite nawe komaso mtundu wako onse ukhale ukuyenda ndi thembereroUmadziwa salary yomwe amalaw timalandira Namapwala iwe?Kapena uli m’gulu lopeza ndalama za magazi?Ndi dziko ili osamalimbana nd zinthu zot ambir akulira.
Nanga Dzina La Munthu Wakuda Limakhala George Daniel,ndi Mzungu Munthu Wakuda? Akulu Akulu Munthuyu Ndi Bulutu Ndi Makolo Ake Omwe AKAPATSIDWA T SHIRT NDI CHITENJE AMAONA NGATI DZIKO LIKUYENDA BWINO,NYANI WACHABE CHABE BAMBO AKO ADAKANGOPANGA MASTURBATION ZIKADAKHALA BWINO.ADALAKWA KUCHINDA AMAKO NDIKUBEREKA CHITSEREKWETE NGATI IWE
Chimuthuchi ndichachamba kwambiri ingakhale comment ya munthu olongosoka imeneyi
utukwanitsa makolo akotu iwe!!!!
R.I.P
Musamdandaule watuluka dzulo ku mental
mumbo – jumbo!!!!
Mmmmm chimakhala chani? kuchikondetsetsa chipani or nsanje ndi ana anzanu pot mwina mtundu wanu simupita ku university?
Mmmmm chimakhala chani? kuchikondetsetsa chipani or nsanje ndi ana anzanu pot mwina mtundu wanu simupita ku university?
Tiye naoni kkkkkk
KKKKK UFUNA UCHITE KUYITSATILA KHONDOYO
Kwambiritu Paul Kay
Kwambiritu Paul Kay
Udzanditenge ukamapita
Udzanditenge ukamapita
Aaaaaaa ukanandiuza dzana wachadwa ka
Aaaaaaa ukanandiuza dzana wachadwa ka
OK kanizani ndeu yomweyo
OK kanizani ndeu yomweyo
Hahaha iwe mesa wachedwa nanga
Hahaha iwe mesa wachedwa nanga
Bola mano asakathe
Bola mano asakathe
Alipo onse 32 Paul Kay
Alipo onse 32 Paul Kay
Malawi dzuka
Chance has been closed,hope they will demonstrate in their respective homes
Tiyeni nawoni musawasiye ndipo peter atule udindo wake pansi walephera kulamulira mtundu wa amalawi. Nanenso ndikanakhala komweko ndikanalorera kulifera dziko langa. Adzichita kutiposa anthu aku Zimbabwe kulimba mtima, ife ndikumakhala ombwambwana. MO FIRE MALAWI.
Lets all join hands to fight the oppressor
Pano chanco yatsekedwa.
villagers have done well,people are tired with this government.
maseWero abwino
ofunika kuwafaila chitedze amenewo makape oyimba sukulu zaulele
am on ma way to zomba!
We got a horse race, a dog race, human race oooh ” what a Rat Race” …
Mapaz awo amenewo,,akngojweza znthu ngat ndalamazo azitipatsa ndi iwowo,,,,atren fire,we r human beings nt wild animals,,,,,,sssshhhhhhiiiittt
ziliko
Dont giveup #Chanco, gogogo mwayintha2 kuzolowera kuba anthuwa
tajoina kun0 ku chnamwal ndpo zuchta kuk0ma meeen
kodi akupangadi ku matawaleko
eya,mpaka anafika pa shop ya shehe,m0t atseka ma grocery kwa supe k0nse
mmmmmm owo koma nde zavutatu. nde ati auzidwa kuti azipita aitseka kaye
oh sinamve kma mwinad!!,,akut amenyanso wa police pa matawale
apa alemba kuti amuthyolera mfuti
eeh kma ndy zavutad,,,
pa newspa za zodiak akunenadi atseka chanco komanso amulandadi mfuti ndi kummenya wapoliceyo
apa ndy teargas wavuta,chnamwali chphokoso chokhachokha
INE NDIKUWONA KUTI DZIKOLI LALOWA UCHITSILU BWANJI TINGOBANDULANAMO KKKKKKKKKKKKKKK ANTHUFE TIMAFUNA KUMASEWERA NDI APOLICE NDIKUKUMBUKA MMBUYOMO MPIRA KU STADIUM UKUMAYAMBA 01:00 nde umatha nsanga anthu akundilande amati tikafike nthawi zino kunyumba tiyeni nawo apolice zinali zosangalatsa ndithu kusewera ndi apolice basi nde kuzombako ana anu sewerani nawo a policewo zabwino zonse
nazoni tiyeni azadeweza
First they were told by parents to go demonstrate……..So their parent refered to as “Villagers” have joined them….Go Go Go lol
Bwerani tidzalime chamba abale anga sukulu niyawo aboma ngaa yanu hahahahahah
Pafunika ndunayo ndi ambassador yo, kuwakong’ontha, adziwe kuti anyamata odya Mbewa ndi Zitete alibe zibwana.
Hahaha ndakomoka
kuwagagad,kuwazupula
Ndakomoka ine hahaha
bakha iwe usandisekese kkkkk
Hahahaha…..you made my mayne
kikikikikikikiki
tiyeni nalo bomali tilitengese latidzuza ziko lokhala lathu peter?must go
what ave realised is that we malawians we are stupid instead of joining hands with the students we are jst staying doing nothing angakwanitse feez imeneyo ndi amalawi angati??? munthu alephere kumaliza school chifukwa cha feez?? mmalawi kungompatsa t-shirt ndi chitenje nthawi ya campaign wamutha azingokuyikila kumbuyo even ma decision oti amukhudza iye mwini aah! malawi at 52.
what ave realised is that we malawians we are stupid instead of joining hands with the students we are jst staying doing nothing angakwanitse feez imeneyo ndi amalawi angati??? munthu alephere kumaliza school chifukwa cha feez?? mmalawi kungompatsa t-shirt ndi chitenje nthawi ya campaign wamutha azingokuyikila kumbuyo even ma decision oti amukhudza iye mwini aah! malawi at 52.
Zoonad wamkulu smukunama mmalawi sadzathekanso mpaka kalekale
u hv a point koma inu mwachitapo chani?
M’malawi kungolandila t-shirt, K100.00 komaso chitenje basi udziwe kuti dera limenelo watenga.
Guys ndili ku matawale panopa bt ma students sakupanga bho..imagine kumaswa magalimoto a fans yosalakwa..kulanda madasi poor pipo..osapita ku ptc bwanji..
@levi phiri thats it man malawi at 52.
kuswa m a galimoto ndye muzit akupanga
Iweyo unawaona mafana amenewa akamapanga ma demo kuti amaononga katundu wa anthu wamba?? Ndi tizithandizira u savage umenewowo ife? Awakwezere fees ifike pa 1 meter kumene zinazo akapepesere anthu omwe akhala akuonongeredwa katundu at the handa of these students mxiew
Am a Malawian and am proud to be a Malawian but withdraw your statement saying Malawians are stupid.
Am not against you bro but if u say we Malawians are stupid, u can’t call your mum, dad, aunt or ur uncle stupid, I knw for sure all these relatives of yours I have just mentioned are also Malawians that means they are inclusive.
Denis true malawi ndife zitsiru usalese tikuvutika pozavota kuvotabe omweo imagen ndife ozindikira pamenepo
Every word that we speak has an impact on our lives, some curses are just self imposed, there are a lot of words that we can express our failure or weakness rather than calling urself stupid. The solution is never to repeat the same mistake that we did to endorse power to these guys. I tell u and believe me speaking these insults or provocative words won’t change anything only a few people have an access to Facebook. So I don’t think this is the right place to express our anger than just doing actions
Komano inuyo u claim to be educated koma pena zomwe mumapanga zimakhala zaumbuli
great news other universities shud also join
Infact the issue of fees hike has concerned thousands of people by realizing that more can not afford the family to spend for single child but it would be calm resolution had it been all letters sent by the University of Malawi Student Council(UMSA) was considered it would’nt happen the way it is,now the pilice arrested even some chinamwali dwellers for trial probably they are going to deffend themselves as innocents whilst they mostly not happy with why students are conducting riots.
Kkkkkkk kma kumenekooooo!!!
in this government there is people who are too corrupt the result of it is this fees hiking from no where,,,,,,,dpp must go n fees must fall.
Go Ahead, Kumangodziwa Kuzuza Anthu Osauka, More Fire Dont Put It Out.
More firee!
too bad.that means mwana wamphawi saphunzira aphunzire ndi ana anthu olemera ngati tikukanika kulipira ana ku open K10,000 timalipira katatu fees mutchulayo tikwanitsa ine kwangotalika mkabwera makatedi sizoona zimenezi amene amapanga ma decision amenewo okweza fees ana awo saphunzira ku malawi kuno uphunzitsi uja mwayamba kulipilitsaku collage ntchito ya ana amphawife kwatsala ku army mku police koma kuti mutitengeso zaulelezo ayi mwandikwiyitsaso mwamva
tiyeni musasiye akuzolowera
Ena Akuthamanga Ulere Enawo Akulandila Ma Allowance!
De fees hike wz too much,gd for ana adadi,burden to de less priviledge!officials adress them to calm de situation
mxiew!!!! akufuna ana awo okha ndamene azikhala ndmaphunziro apamwamba et!! nawooo amanewo angapitilire kumatiphwekesa
mr jono.it does no matter everyone.we r at work.to put food on the table.let daed burry daed.ifeyo not our busness
20 July.
ajaila kwambiri sizomati where are heading to zoso ayi
Tiyeni osabwelera mbuyu ationjeza
thus Malawi….
Shaa enawo ndiye angofuna kubaaa pobela
Tiyeni naoni amenewa anaphuzira sukuli zaulele lero akufuna azioneka ngati madolo aku Malawi osasiya
go chanco go!!!! am on ur side.
had t bn dat am there i wud hav joined them
Hit them hard,,,OBOMA wadziwa bax kut despite donations..Malawi Gvt is still oppressing the Poor
E e e kma yaa
Is what i was waitng those students they are coming from the village their parents must be angry aswell keep it up villagers
Waiting for another one at the polytechic
Yah…timalize kaye mayexo
nza bho bho
Malawi Malawi where r heading to? koma zanyanya enawa anaphunzira ulele.
TYen nawo akujaira amenewa akutitola hevy
TYen nawo akujaira amenewa akutitola hevy
Petulo Sakutiganizira Amalawi
Tiye nawoni kkkkkkkkk koma kumeneko
Kkkkkkk Malawi wanga