
Ophunzira wa ku UNIMA walamulidwa kukagwira ukaidi kwa miyezi 22 chifukwa chakuba
Bwalo la Chief Resident Magistrate ku Zomba lalamula ophunzira wa ku yunivesite ya Malawi (UNIMA) Martin Kachigayo wa zaka 26 kuti akagwire ukaidi wakalavula gaga kwa miyezi 22 chifukwa chomupeza olakwa pamulandu okuba kompyuta komanso… ...