BREAKING: Villagers join Chanco students against police in Zomba

Advertisement

…as students block US second lady Dr. Jill Biden convoy 

Irked b the noise perhaps villagers around Matawale and Chinamwali  areas in the city of Zomba have joined another grouping of Chancellor College students who are in a cat and rat chase with police officers in the city.

As we reported, the students are protesting against the decision by the University of Malawi (Unima) to raise fees for generic and mature students.

Villagers joined the battles.
Villagers joined the battles.

Some of the students had to run away to villages around the city in fear of being arrested by the police.

But police who followed the students around met the wrath of villagers who claimed to have been disturbed and therefore rallied behind the law enforcers in the running battles.

The demos started yesterday.

As this post was made, the students blocked the way for a convoy that was carrying the US Second lady Jill Biden who is on a three day visit in the country.

The college has since been closed.

 

Advertisement

240 Comments

 1. Kunangonditalikira naneso nkanalowerera kwa ma students dziko lokondera opata ili ena kumakhala ngati ndi marefugees dziko lathu lomwe

 2. Hello I’m Samuel Okizou by name, I’m giving a testimony about Dr.Sule the great Herbalist, he has the cure to all manner of diseases, he cured my HIV disease, though I went through different website I saw different testimonies about different herbalists, I was like: “Many people have the HIV cure why are people still suffering from it?” I thought of it, then I contact Dr.Sule via email, I didn’t believe him that much, I just wanted to give him a try, he replied my mail and Needed some Information about me, then I sent them to him, he prepared the CURE and sent it to me via UPS courier service, they told me that it will take 3-4 days before I’ll get the parcel, 3 days later I received the package and I started taking the medicine as prescribed by him, after 7 days of taking the medicine I went for check-up, I was tested HIV NEGATIVE… IF YOU ARE SERIOUS YOU WILL BE CURED!!! contact Dr Sule on whats-app +2348162447651.

 3. Uyu uyu akanakhara kuti makolo ake amkapita kumunda around 4 a.m kukalima maganyu kuti ana adye and apeze yogulira ndiwo sakanapanga choncho.iwo anadutsa moyera umphawi samaudziwa.Muganizire mwana oti amalimbira xul,form 4 kukhonza bwino a unima ndikumutenga koma asakudziwa kotenga fees and loan osatengedwa.Yester a friend told me kuti Next academic year sindibwera 400 000 ndiyambiri.KWA MUNTHU OTI UMPHAWI AMAUDZIWA sizikanakhara choncho.AMBUYE ATITHANDIZE!

 4. Kodi mbewa ndi zitete pa kilo zikugwa pa bwanji? K500? Ife vuto palibe kwathu ophunzila kwambili anafika std 6, zoti amalipilanso ku xool kaya college sitikudziwa ndiye xool us please! We are very busy kusaka mbewa ndi zitete boma latipatsa tender nde nditha kulipilira ana a chancol onse fees mukambayo. All Chancol students just list your names below, Ofuna ntchito yosaka mbewa kapena kupha zitete(Agulu mamina) mubwele kwa Wenela we are recruiting on monday next week!

 5. Dzuka please Malawi DPP imapha Ana asukulu iyi mmalomothandiza atsogoleli amawa awa Malawi uli busy Manu gweee kusekelela Mbuzi 577 billion muthalika ndi nzake akutiwonongela malawi wathu you??? Why Malawi ?kod ndi kupeleka? Zowona malo okusiyila agogo aja uzilipila?kwenikweni ndichani Malawi? Kapena tiziti ndiwe watulo? Plz Malawi dzuka DPP WATIONJEZA…….. 2

 6. Bola kuti ikhaledi demo yeniyeni mngomuphapo mupolisi mmodzi kuti ayifere ntchito yopanda malipiro ngati iyi that can be better to send message to the malawians as a nation kungomthyolako khosi mupolisi mumodzi just to put him/her on a map

 7. Kupusa,usavege ,umbuli,ndiye apolice ntchito yawo ndichan ?,apolice sangalolere zopusazo kut zizichitika ndipo achita bwino kuwathila machaka,Panopa zulo lija mmene imat 02:00pm ana onse apa achanco awathamangisa pa xool yi,ndipo ana 12 awasekera Ku Zomba police station ,ena akagona mmuz kuopa kumangidwa pamene pa waluza ndan?,angavutike ndan?,munaopo ana apa college of medicen ku BT.akupanga zopusaz mwapambana bwanji inuyo,kwacha ikagwa palibexo kuchitilira mwina zinthu zimakwera mwandikwiyisa heavy,azibale anga Ku Zomba ko azikhala mwamantha coz ov u stupid students chanco ,chanco cuannn..

  1. Vuto ndilakuti apolice timamwa nawo m’ma bar athu a lokolowa ndiye tidziwatibula out of work! Amene alibe ndalama ndi amene akulilawa, opeza bwinonu mukulimba mtima nanga simukaba misonkho ya amphawife.

 8. Kupusa,usavege ,umbuli,ndiye apolice ntchito yawo ndichan ?,apolice sangalolere zopusazo kut zizichitika ndipo achita bwino kuwathila machaka,Panopa zulo lija mmene imat 02:00pm ana onse apa achanco awathamangisa pa xool yi,ndipo ana 12 awasekera Ku Zomba police station ,ena akagona mmuz kuopa kumangidwa pamene pa waluza ndan?,angavutike ndan?,munaopo ana apa college of medicen ku BT.akupanga zopusaz mwapambana bwanji inuyo,kwacha ikagwa palibexo kuchitilira mwina zinthu zimakwera mwandikwiyisa heavy,azibale anga Ku Zomba ko azikhala mwamantha coz ov u stupid students chanco ,chanco cuannn..

  1. Kodi chikala amkalilira nyanga nyumba itapsya adamuimba munyimbo ya mulungu uja ndi inuyo kapena agogo anu?

 9. The Govt Of Malawi Is Now The Govt Of The Rich.Kulimbikira Kukweza Zinthu Chosecho Anthu Nd Osauka, Akuona Ngat Ndalama Anthu Akazitola Kut.The Poor Wil Get Poorer While The Reacher Wil Get Reacher.What Kind Of Govt Is This?

 10. The Govt Of Malawi Is Now The Govt Of The Rich.Kulimbikira Kukweza Zinthu Chosecho Anthu Nd Osauka, Akuona Ngat Ndalama Anthu Akazitola Kut.The Poor Wil Get Poorer While The Reacher Wil Get Reacher.What Kind Of Govt Is This?

 11. nanunso apolice mumalowerera zinthu zozawakhuza, do u tink u can afod 2 pay 4 a huge amount of fees de government unconsiderably,thinkinles is presenting 2 pple, that is torture. say u want 2 reduce graduates due poor jobs we know this.

 12. Where R the so called civil society organisations ? they r busy eating & giving a deaf ear to the cries of chanco students , this is the battle that must be fought by every citizen of good will . they have forgotten that they were on gvt bursaries . now that their belleys have protruded with tax payers money don’t like poor sons & daughters of this trouble stricken nation to be educated . shameless coucil leaders .

 13. Prease aukhaida help us with Gun prease we are tiered with opresion any body who is poor will join us peace is now fell osauka kumangosaukabe.

 14. Chonde amalawi zinthu ngati sizilibwino nenani.Wins as soup on bone semi boma lathuli lalephera tiyeni tione zina Mwaiyiona nkhani ya Land bill IJA ikuyendera basis tonsefetu tigulitsidwa..take care Malawi.

 15. Pagulupa ndikutha Kuona kuti Pali wina wathawa Ku Zomba Mental Hospital apa. Zokamba zake zikukhala ngati wangobwera Ku Malawi kudzacheza, akhatha abwelera kwao Ku UK. Pamene mudzi mwao ndi Mwachiuziramunso. Pepani ndamumvetsa munthu Yu. Wadya zitete ndi mbewa zochuluka lero.

 16. What I Know Is This;
  .
  Kulimbana ndi BOMA ndi chimodzimodzi ((KUKOKA MALISECHE AKO MWAKHANZA-ena akuwonerera ))
  .
  Who can feel the Pain?

 17. Koma izi zomati mukajambula chithunzi nkuyikapo chi ujeni chanu ichi cha Malawi 24 mpaka chithunzi chonse osawoneka, ine nde zimandinyansa koophya…

 18. Wat cmez next z tu riquest doz hu statng voiyz but malawi will nevr empwer az own.tizingochedwa zopanda pake insted zabwino.osazikonda ma lycter pliz.

 19. Bravo locals. Amene akukweza fees’wo adophunzira pa ngongole ku university, worse still they’re not paying back the money. Now akufuna kupha education kuti only ana awo ndiamene aphunzire. Shame on you a council

 20. #Oppression is one of the bad themes circulating in all corners of this #NYASAland (malawi) what a presidency? Lucky are those who did their University Education during #Kamuzu’s era, You people lets think #wise on this, paying fees at #TTC (PET)?, Aplying for university #Loan? Where are the good #OLD DAYS? free university #Education. this is a total #OPPRESSION TO THE #POOR and I 100% agree with you #Students at #CHANCO the #chilunga. LETS SHOW THEM THAT WE DON’T WANT #OPPRESSIVE acts.

 21. tawerengani chibvumbulutso kt muziwe zoona zake zenizeni za nyengo pamene tikumane mzotsautsa kuposa kukwezedwa kwa xl fees

 22. more fire chanco student!!ndalama zachulukitsa kodi ndiacivo servant angati akulandila k4handred southand mboma?sionse aliopata zanyanyatu apa koma dzikoli muli presedent ngati alipo nde ndibwantasatu!policeyo thibulani atikwana mazoba amenewa amalimbana ndi za ziii mmalo mogwila mbava

 23. Solidality at its best..i dont have any relative ku University but i still find this fees hike as inhuman tikatengela m’mene life yalimbira pa Malawi pano. Am in support of what you guys are doing!!!

 24. Azanga taonani mchilombo chinthuchi ngati chidachoka chili du osachitapo kanthu ana akuvutika chonchi.suja anatsekaso ma college? Sizi

 25. Kod ndi chan agalu inu Ku zombako ,,?zot kwacha yagwa simukuziwa ndiye mumafuna kut fees ikhalebe mwakale momuja?,chimene mukuswera magalimoto ,komaxo kulanda malonda aphawi aanthu osalakwa ndichan?,boma likachitapo kanthu muzit boma la peter ndilokupha eti ,,?mwandikwiyisa kutachere chanco inuyo kutan?,manyi ambuz akuthire machaka apolice osagona pa duty tiyen nawon

 26. Everytime i read about these senseless fees hikes happening in Malawi i feel really bad for my Nation. Everywhere in the world students are fighting for zero fees in all institutions of learning and to the contrary in Malawi they are raising up the fees rediculously.

  This is a real kind of brutality the government displays when it has failed its citizens. The reason why we have too old madalas in most key government positions, who are always sleeping while on duty, is because we have denied our own youth a better education through exhorbitant school fees. Malawi with its current leadership is really in a state of mediocrity….we can nolonger afford to live like foreigners in our own land. VIVA THE REVOLUTION….VIVA MY FELLOW UNIMA STUDENTS…

 27. @George coz of ur fucken shit “shame on Anthu ofuna cheap EDUCATION” u r very stupid in block letters!! how can u sy that??

 28. This has take to de old good days of de late DU CHISIZA Jr On his play called, STOM ON LITADA. DE XOOL FEES IS UP,DE PRIZE OF SUGAR,WATER, TRANSPORT,RENT ALL IS UP BUT MY SALLARIE MY PAY, MY WAGES!!!

 29. @ George,shame on you “Zoba” if you don’t have anyting to say on dis issue jst shurt up ur facken toilet! wandinvetsetsa!!!?

  1. inenso wandikwiyitsa heavy Zoba ameneyu!! @Henry look at his prifile picture “MBALAME” [email protected] George usadzayambilenso wanva?? ngati ndakulakwila “ZAKO” ine sindipepetsa wandinvesetsa??????

 30. APA solution ndiyophweka. Chosani subsidy ya fertilizer, malata ndi cement zomwe ndi za campaign, ndalamazo zipite Ku fees ya college. Akamaliza sukuluyo azagulira makolo awo kumudzi fertilizer, cement ndi malata. Simple.

 31. Akuba ndalama akungokhala phee kudya ngati ndi zawo! Atengetsetseni agalu amenewa akulimbikitsa kuba pa Malawi. Tsogolo lingakhale labwino kwa onse ngati mukweza fees kuti ana anu okha aphunzire?

 32. One effective way of reducing literacy rate in Malawi is hiking public university fees otherwise by 2020 ndekut Malawi adzakhala ovaya coz we are priotising school as the best way of getting income….chodabwitsa ndichoti 3/4 yama lectures a UNIMA masters degree yawo amakatengera kunja through schoolarships coz kwawo kuno amakanika kudzilipilira okha nde nchifukwa chani akufuna ana anzawo adzivutika? Come on lectures

 33. A Malawi kukula mopepera thus why anthu akuluakulu amene ndi amuna a ndevu zawo akulilira zinthu zotchipa. Remember the Mutharikas are here to teach Malawi on how to rely on our own. Olo anyanyale asayiwale kuti ma lecture zawo akulandira komanso a policewo alandiranso ma allowance. Akanyanyala palibe amene atavutike okha abwereranso koma zotsitsa fees iwalani. Ana a mabwana ndi amene akuyambitsa zisokonezo zimenezo chifukwa iwo akuziwa kuti akapita kwawo akayamba ma private. Shame on Anthu ofuna cheap EDUCATION. fees must be hiked basi

   1. Waa! Iwe ukutchula ya ababa ako pagulu? Psyiru iwe eti? Uyesa iyeyu mwana wa amama ako kapena shamwali wako? Buluka!

   1. Please show us apicture ya mbuzi ya munthu tiyiwoneko.Kodi imakhalanso ndi nyanga ngati mbuzi timadya ija?

  1. achisilu mwana uja Ali standard 5 uja muzakwanisa kulipira inu mbuzi yamunthu mukuganiza kuti izakhala pa bwanji ngati pano yafika pa 1.4 million

  2. Ngakhale dzina lakolo it doesnt sound that you are a malawian ukulankhula motumbwa ukuyidziwa maximum wage ya pa malawi pano ngati munthu amalephela kupitiliza maphunzilo chifukwa chosowa K45,000 ndiye pano akuti K600,000 ndi angati angakwanitse mbuzi ya munthu iwe

  3. Majority chani apa?? Ku chanco aliko anthu angati?? Mukanakhala anthu enieni simukanathiridwa teargas. Ndiponso Chanco angoyitseka tikuonereni. Tione ngati simukapepesanso ngati nthawi ya Bingu ija. Fee hike yomweyo basi. Kuzolowera zochipa

  4. Kodi when the fees is hiked do we get a new syllubas …..or special attention. ..kapena azikatiseta ku toilet komwe. …cause fees is hiked. ..accommodation 36 000 per month …..so if you can afford we can’t …we not asking for it not to be raised but we want a reasonable hike. ….not 300% hike …….so lets be reasonable…..

   1. Iwe psyiru usamatchule uniform ya ababa ako pachimtindi wamva? Psyiru uyu akuthabula maganizo ake!

  5. Kkkkkk! Amuna andevu za kunamizira umphawi kkkkk. A amalawi kugona too much Peter akudzutsani. Olo mupange makani Mutharikas akalankhula palibe kusintha. Asafuna akhale palibe akukakamizidwa

  6. How many pipo in the govt amalandira 400000? Ngati munthu akupanga withdraw ndi 275000 what more 400000? Use ur brain to think critically.

  7. Ndamudziwa George Yu Ndi Uja Amanyamula Chithunzi Chapitala Pa Misonkhano Yake Yambiri Ma Plan Adamuthera Kale Kale Akungodikira Tsiku Lakufa Basi

  8. Ngat ukuziona udolo mwapadera Mulungu achite nawe komaso mtundu wako onse ukhale ukuyenda ndi thembereroUmadziwa salary yomwe amalaw timalandira Namapwala iwe?Kapena uli m’gulu lopeza ndalama za magazi?Ndi dziko ili osamalimbana nd zinthu zot ambir akulira.

  9. Nanga Dzina La Munthu Wakuda Limakhala George Daniel,ndi Mzungu Munthu Wakuda? Akulu Akulu Munthuyu Ndi Bulutu Ndi Makolo Ake Omwe AKAPATSIDWA T SHIRT NDI CHITENJE AMAONA NGATI DZIKO LIKUYENDA BWINO,NYANI WACHABE CHABE BAMBO AKO ADAKANGOPANGA MASTURBATION ZIKADAKHALA BWINO.ADALAKWA KUCHINDA AMAKO NDIKUBEREKA CHITSEREKWETE NGATI IWE

  10. Mmmmm chimakhala chani? kuchikondetsetsa chipani or nsanje ndi ana anzanu pot mwina mtundu wanu simupita ku university?

  11. Mmmmm chimakhala chani? kuchikondetsetsa chipani or nsanje ndi ana anzanu pot mwina mtundu wanu simupita ku university?

 34. Tiyeni nawoni musawasiye ndipo peter atule udindo wake pansi walephera kulamulira mtundu wa amalawi. Nanenso ndikanakhala komweko ndikanalorera kulifera dziko langa. Adzichita kutiposa anthu aku Zimbabwe kulimba mtima, ife ndikumakhala ombwambwana. MO FIRE MALAWI.

 35. Mapaz awo amenewo,,akngojweza znthu ngat ndalamazo azitipatsa ndi iwowo,,,,atren fire,we r human beings nt wild animals,,,,,,sssshhhhhhiiiittt

 36. INE NDIKUWONA KUTI DZIKOLI LALOWA UCHITSILU BWANJI TINGOBANDULANAMO KKKKKKKKKKKKKKK ANTHUFE TIMAFUNA KUMASEWERA NDI APOLICE NDIKUKUMBUKA MMBUYOMO MPIRA KU STADIUM UKUMAYAMBA 01:00 nde umatha nsanga anthu akundilande amati tikafike nthawi zino kunyumba tiyeni nawo apolice zinali zosangalatsa ndithu kusewera ndi apolice basi nde kuzombako ana anu sewerani nawo a policewo zabwino zonse

 37. what ave realised is that we malawians we are stupid instead of joining hands with the students we are jst staying doing nothing angakwanitse feez imeneyo ndi amalawi angati??? munthu alephere kumaliza school chifukwa cha feez?? mmalawi kungompatsa t-shirt ndi chitenje nthawi ya campaign wamutha azingokuyikila kumbuyo even ma decision oti amukhudza iye mwini aah! malawi at 52.

 38. what ave realised is that we malawians we are stupid instead of joining hands with the students we are jst staying doing nothing angakwanitse feez imeneyo ndi amalawi angati??? munthu alephere kumaliza school chifukwa cha feez?? mmalawi kungompatsa t-shirt ndi chitenje nthawi ya campaign wamutha azingokuyikila kumbuyo even ma decision oti amukhudza iye mwini aah! malawi at 52.

  1. Guys ndili ku matawale panopa bt ma students sakupanga bho..imagine kumaswa magalimoto a fans yosalakwa..kulanda madasi poor pipo..osapita ku ptc bwanji..

  2. Iweyo unawaona mafana amenewa akamapanga ma demo kuti amaononga katundu wa anthu wamba?? Ndi tizithandizira u savage umenewowo ife? Awakwezere fees ifike pa 1 meter kumene zinazo akapepesere anthu omwe akhala akuonongeredwa katundu at the handa of these students mxiew

  3. Am not against you bro but if u say we Malawians are stupid, u can’t call your mum, dad, aunt or ur uncle stupid, I knw for sure all these relatives of yours I have just mentioned are also Malawians that means they are inclusive.

  4. Every word that we speak has an impact on our lives, some curses are just self imposed, there are a lot of words that we can express our failure or weakness rather than calling urself stupid. The solution is never to repeat the same mistake that we did to endorse power to these guys. I tell u and believe me speaking these insults or provocative words won’t change anything only a few people have an access to Facebook. So I don’t think this is the right place to express our anger than just doing actions

 39. Infact the issue of fees hike has concerned thousands of people by realizing that more can not afford the family to spend for single child but it would be calm resolution had it been all letters sent by the University of Malawi Student Council(UMSA) was considered it would’nt happen the way it is,now the pilice arrested even some chinamwali dwellers for trial probably they are going to deffend themselves as innocents whilst they mostly not happy with why students are conducting riots.

 40. in this government there is people who are too corrupt the result of it is this fees hiking from no where,,,,,,,dpp must go n fees must fall.

 41. too bad.that means mwana wamphawi saphunzira aphunzire ndi ana anthu olemera ngati tikukanika kulipira ana ku open K10,000 timalipira katatu fees mutchulayo tikwanitsa ine kwangotalika mkabwera makatedi sizoona zimenezi amene amapanga ma decision amenewo okweza fees ana awo saphunzira ku malawi kuno uphunzitsi uja mwayamba kulipilitsaku collage ntchito ya ana amphawife kwatsala ku army mku police koma kuti mutitengeso zaulelezo ayi mwandikwiyitsaso mwamva

Comments are closed.