Members of Parliament (MPs) on Thursday passed the Copyright Bill to protect works of art from being pirated in the country.
The new law will see people found guilty of digital piracy paying a minimum fine of K5 million.
Copyright Society of Malawi (Cosoma) board member Rudo Chakwera has since applauded the bill arguing that it will promote art in the country.
Despite authorities getting tough on piracy, the malpractice has over the past years refused to stop being a thorn in the fresh of Malawian artists.
Some artists have been seen moving on personal campaigns of confiscating computers that are used to pirate art music in the country.
While fighting for piracy in the country, Malawi artists blamed government for not putting measures that could curb the malpractice.
Agalu inu eti and mwasowa chochita eti? Ife tizibenabe and muwonanso…..with no fear
Kodi Anthu enanu mukudana ndi bill ya piracy bwanji? Ndiinu amene mukumana lumukumaba eti? Mukhauladitu simunati coz ife wil fight for our Artists coz ndikale munayamba kuwabela.Ngati mumafuna kumabena chonde imbani zanu
Hahahaha well sell more to get fine money
H
Kenako umva ukabereka ana opitilira awiri msonkho hiyaaaa Malawi at its best ine kukumbuka voti yokhala yanga kundisenzetsa stress kkkkk
Yalakwatu apa
Piracy is also cashgate but in another form, komanso yaing’ono, ndiyeno gwirani kaye mbava mukugwira nazo ntchitozo kenaka bwerani ku piracy, timayamba kuthana kaye ndi mavuto aakulu then timakathera ku ang’onoang’ono, mwaiwala kodi? mesa ndinu anthu ophunzira inu, don’t run away from your responsibilities, mwatani kodi ma profesor ndi ma doctors? Tiziti school yanu ikugwira ntchito yake apa? Ndakaika!
Mungoti wopezekayo ndi ulendo wa kumanda
Mungoti wopezekayo ndi ulendo wa kumanda
Iyi yokha makape inu munyera manyi,sitisiya
Demeti gwirani kaye mbava…..pc n ma blank cds zonse zanga n kuburnako ndikusaka cash kukana kuba basi muzibwera ndi nzeru zopusazo……. Zopusa basi
that is better alemereko oimbawa
5mili kuitchula mosavuta
Wawa ine siningaleke yayi, ndipitiliza ku burner nithu
cash gaters should get lyf imprisonment then
konzani kaye economy yadziko, gwirani mbava za cashgate zonse zibwenze ndalama, pangani zoti ntchito zisamasowe mdziko muno, kenaka muzilmbana ndi piracy..
Ntchito yi ndinayamba nthawi ya Kamuzu mpaka pano koma sindinapezepo 5 million. Inu ndiye mukuti chiyani?
Ayamba kusewerako ukooo ku Parliament basi atseke mmesa budget inadutsa???
Closed yesterday boss
Futso nali Kodi frash usb zinabwelelanji .
Kkkkkkkk iiiiiiiiii mavuto alipo!
Ndakana ntundu wa alomwe.matafale evison analosera kale lero mmalawi usalire.
Ndakana ntundu wa alomwe.matafale evison analosera kale lero mmalawi usalire.
Kkkkk, apolise ndi omwe azisangalala ndi lamuloli
Iwe MP zala zakozo zinagwilako 5 million?
Im telling u MPS muzilowa nyumba iliyonse poti lamulo mwakhazikitsa ndinu.
Chingambwe eti
zopusa
5 Million kkkkkk. mukuona ngati ndalama imeneyi yophweka eti. osangowapha bwanji.
koma agalu a DPP zulo akuti tizilipila malo okhala athu lero akuti ma cd bwanji osangowaletsa ogulitsa ma blank? koma anyani inu eti zitsilu zina ndiye zimavotela minkhwere imeneyi zawutsilu basi
Kumalawi nkosalira.ndizime nezo.choongu wanu uja ndiameneyo
muukha madzi ndiyetu kwatsala 3years
Yambani mwatsutsana ndi nkhanza zolipiritsa anthu malo okhala awozi…..muthane ndinkhanza zolipiritsa mankhwala nzipatala zaBoma….mukatero lowani ku ma Pirates koma failing that…..mwanya tizicopabe…….ndipo mawebsite nde zikumatengedwa bwino while muli ku Studio ife tikumapezeka nazo.
Maka aphungu oyimbanu ndiomwe mukubweretsa mfundo zopusazi….kodi mmalowera kudzathana ndi ma Pirates? Mwauponda
munthu ukagula galimoto akhoza kuinyamulitsa cabbege or mbatata chifukwa ndiyake,same 2 obena akagula cd ndiyao okhoza kupanganayo chomwe afuna siagula basi?komanso patakhala cuti palibe obena nyimbo&videos zingafike bwanji mu flash{usb}?
Ayambe alesa ma phone a ma memory card, ma usb disc, ma radio a usb, internet, akatelo zitheka
Obena nonse mundiimbire foni ndikuuzeni nyimbo zabwizabwino zobeneka popanda chewuchewu. Nyimbozi ndizaku france. Yea! La Musique Francaise! Hear from U soon.
APM msonkho mpaka nkhani za kuchipinda she
Nkhondo ilipo chaka chino
Dziko lokonda ndalama ngati ili kaya, Ma albino akuphedwa koma chomwe muchitapo palibe,,,, koma maso ali pa ndalama basi osati kuteteza miyoyo ya anthu, ntchito ikhale kubela amphawi basi, Zachamba.
izizi simungazithe,letsaniso whatsapp ndikucha ma bluetooth m’ma foni,technology munkaifuna ndiimenei
Tikanajudula ife izi tione ngati lamulo limeneli ligwire jobo yake bhobho
zioneka ngatizitheke chifukwa munthu ndiwovuta zikupangitsa ndi neti kutsegula failo ya anthu oimba mungotuluka nonse kuchita kuzitsankhila nditenge uti amene watchuka kwambiri kapena amakutsangalasa ndimutsunge ndikumavela tsiku ndi tsiku koma dizofunika kuganiza bwino.
Ndaumwanso ndikamugwira,ulinzingat?Wakumowa.Zikomo tiwadyere obenawa.
room yoburnayo including rent and ma PC sizifika 50 sauzande.n u saying they should be paying that money. muidziwa 5 metre inu??? amalandilatu ndmunthu opanga retire.#kkkk
Up to 5mita?……A total lie. ..
Amatithandiza ife! Amenewa zanu za Originazo mumakhala nyimbo zochepa zokha 10 pena 9. while njondazi zimatimatila nyimbo 70 mu DISK Imodzi yotchedwa Mp4 mtengo wakeso wabwino.Ndiye ife tikudabwa inu! kuti mukutokota zichani? Sangasiye ku bernaku ifeso! sitisiya kuwagula Musolver.
Kuyambira mawa whasapp yanuyo sizakulolan kutumiza kapena kulandira media,bltoothyo ndiye sizapezekanso mfoni yanuyo ndatha anthu ine man!!
Thats agood news! Let entertainers and musicians enjoy their talents obena nonse pezani zochita zina!
Komatu Stuff Yambili Mmatulutsa Ma Artist Nu Imakhala Yosaphikika Kweni Kweni_ Pipo We Cant Be Spending Too Much Money On Half Baked Cds__ Start Coming Up With Great Stuff Tikagula Tisamanyinyilike! Takumvani
Eeeeeeeh
Zokambilana zakuthelan eti kwasala timva mukut otsitsa pweya azilipila kkkkk musowa maluzi ali posepose
kkkkkk kkkkkk eya
Kkkkkk mukuunjeza ka
U know?
kkkkkkkk pirates mesa imathandiza kupeza nyimbo zomwe umakonda,panyimbo ten yakusangalasa imodzi nde ukagule cd yake yose.hiiii ayike panet tizipanga download ndikugawana mumablth athuwa mesa si pirates.ndalama yavuta ndani angalamule zake,munthu ochokela kufumbi,opanda ungwiro?kaya kuli kupwetekana,ndani atamugwira pc,desktop aziyika kuchipinda.
Iwe Richard ulesi eti? Osaimba zako bwanji chimutu!!!
Kkkkkkk technology is moving so fast zokhara ndima CD zikupita kokutha we share music on whatsp etc for free not izy to control
Mukunama ma phwanga Ife tizibenera mu toilet
Ife tikakudyerani kuti? Akunamizana ku parliament ‘ko sitisiya ndimisonkho yanuyo,paliponse msonkho mpaka mtoilet
Kma ngati uli Umphawi
nde omwe amapanga burn ma cd muwapezera vep?? koma boma lilibed dolar et???
Hahahahaha nkhani iliko chaka chino ndiyotolera ndalama zoona mpaka 5million
Boza basi,woyimbayo alibe 5m kkkkk mtipeza