Beware pirates: K5 Million fine for burning CDs

cds

Members of Parliament (MPs) on Thursday passed the Copyright Bill to protect works of art from being pirated in the country.

The new law will see people found guilty of digital piracy paying a minimum fine of K5 million.

cds
Musicians could smile to this.

Copyright Society of Malawi (Cosoma) board member Rudo Chakwera has since applauded the bill arguing that it will promote art in the country.

Despite authorities getting tough on piracy, the malpractice has over the past years refused to stop being a thorn in the fresh of Malawian artists.

Some artists have been seen moving on personal campaigns of confiscating computers that are used to pirate art music in the country.

While fighting for piracy in the country, Malawi artists blamed government for not putting measures that could curb the malpractice.

Advertisement

61 Comments

 1. Kodi Anthu enanu mukudana ndi bill ya piracy bwanji? Ndiinu amene mukumana lumukumaba eti? Mukhauladitu simunati coz ife wil fight for our Artists coz ndikale munayamba kuwabela.Ngati mumafuna kumabena chonde imbani zanu

 2. Kenako umva ukabereka ana opitilira awiri msonkho hiyaaaa Malawi at its best ine kukumbuka voti yokhala yanga kundisenzetsa stress kkkkk

 3. Piracy is also cashgate but in another form, komanso yaing’ono, ndiyeno gwirani kaye mbava mukugwira nazo ntchitozo kenaka bwerani ku piracy, timayamba kuthana kaye ndi mavuto aakulu then timakathera ku ang’onoang’ono, mwaiwala kodi? mesa ndinu anthu ophunzira inu, don’t run away from your responsibilities, mwatani kodi ma profesor ndi ma doctors? Tiziti school yanu ikugwira ntchito yake apa? Ndakaika!

 4. Demeti gwirani kaye mbava…..pc n ma blank cds zonse zanga n kuburnako ndikusaka cash kukana kuba basi muzibwera ndi nzeru zopusazo……. Zopusa basi

 5. konzani kaye economy yadziko, gwirani mbava za cashgate zonse zibwenze ndalama, pangani zoti ntchito zisamasowe mdziko muno, kenaka muzilmbana ndi piracy..

 6. koma agalu a DPP zulo akuti tizilipila malo okhala athu lero akuti ma cd bwanji osangowaletsa ogulitsa ma blank? koma anyani inu eti zitsilu zina ndiye zimavotela minkhwere imeneyi zawutsilu basi

 7. Yambani mwatsutsana ndi nkhanza zolipiritsa anthu malo okhala awozi…..muthane ndinkhanza zolipiritsa mankhwala nzipatala zaBoma….mukatero lowani ku ma Pirates koma failing that…..mwanya tizicopabe…….ndipo mawebsite nde zikumatengedwa bwino while muli ku Studio ife tikumapezeka nazo.

  Maka aphungu oyimbanu ndiomwe mukubweretsa mfundo zopusazi….kodi mmalowera kudzathana ndi ma Pirates? Mwauponda

 8. munthu ukagula galimoto akhoza kuinyamulitsa cabbege or mbatata chifukwa ndiyake,same 2 obena akagula cd ndiyao okhoza kupanganayo chomwe afuna siagula basi?komanso patakhala cuti palibe obena nyimbo&videos zingafike bwanji mu flash{usb}?

 9. Obena nonse mundiimbire foni ndikuuzeni nyimbo zabwizabwino zobeneka popanda chewuchewu. Nyimbozi ndizaku france. Yea! La Musique Francaise! Hear from U soon.

 10. Dziko lokonda ndalama ngati ili kaya, Ma albino akuphedwa koma chomwe muchitapo palibe,,,, koma maso ali pa ndalama basi osati kuteteza miyoyo ya anthu, ntchito ikhale kubela amphawi basi, Zachamba.

 11. zioneka ngatizitheke chifukwa munthu ndiwovuta zikupangitsa ndi neti kutsegula failo ya anthu oimba mungotuluka nonse kuchita kuzitsankhila nditenge uti amene watchuka kwambiri kapena amakutsangalasa ndimutsunge ndikumavela tsiku ndi tsiku koma dizofunika kuganiza bwino.

 12. room yoburnayo including rent and ma PC sizifika 50 sauzande.n u saying they should be paying that money. muidziwa 5 metre inu??? amalandilatu ndmunthu opanga retire.#kkkk

 13. Amatithandiza ife! Amenewa zanu za Originazo mumakhala nyimbo zochepa zokha 10 pena 9. while njondazi zimatimatila nyimbo 70 mu DISK Imodzi yotchedwa Mp4 mtengo wakeso wabwino.Ndiye ife tikudabwa inu! kuti mukutokota zichani? Sangasiye ku bernaku ifeso! sitisiya kuwagula Musolver.

 14. Kuyambira mawa whasapp yanuyo sizakulolan kutumiza kapena kulandira media,bltoothyo ndiye sizapezekanso mfoni yanuyo ndatha anthu ine man!!

 15. Komatu Stuff Yambili Mmatulutsa Ma Artist Nu Imakhala Yosaphikika Kweni Kweni_ Pipo We Cant Be Spending Too Much Money On Half Baked Cds__ Start Coming Up With Great Stuff Tikagula Tisamanyinyilike! Takumvani

 16. kkkkkkkk pirates mesa imathandiza kupeza nyimbo zomwe umakonda,panyimbo ten yakusangalasa imodzi nde ukagule cd yake yose.hiiii ayike panet tizipanga download ndikugawana mumablth athuwa mesa si pirates.ndalama yavuta ndani angalamule zake,munthu ochokela kufumbi,opanda ungwiro?kaya kuli kupwetekana,ndani atamugwira pc,desktop aziyika kuchipinda.

 17. Kkkkkkk technology is moving so fast zokhara ndima CD zikupita kokutha we share music on whatsp etc for free not izy to control

Comments are closed.