President Peter Mutharika has commanded government to name the Karonga-Chitipa road after his brother, Bingu wa Mutharika.
According to press reports, the order has been issued following completion of the multi-billion Chinese funded road.
Office of the President and Cabinet has made the announcement that following the decree from APM, the road will now be named after the president’s late brother.
The road joins Lilongwe Stadium to fly Bingu’s name under APM’s orders.
Thanx brother Peter 4 remembering me!
Amalawi ambirife ndife mbuli going by ma comments ndaonawa, tikuona ngati Binguyo anachita kutigayila nsewu uwu pomwe inali ntchito yake, chitukuko zitimayela kupempha kuti Boma litichitire iyayi. Aliyense wodulidwa msonkho wooneka kumaso kwa anthu agwirizana nane kuti izi ndi ntchito za misonkho yathu, ngongole anatenga Bingu zizabwezedwa ndi misonkho yathu choncho ndifeyo tikupanga izi osati yemwe tinamulemba ntchito kuti ayendetse.
zaziiiii zopanda ndimuchere omwe
zabwino izi…..
@ Yohane Kanjala Chiweko,very good 2 points tangosiyana chipani ine wamafunde koma nsewu uwu ndimagwilitsa ntchito tsopano ndiwapamwamba sadandilakwile a DPP pomupatsa mtsogoleri wawo wakale ulemu
Thanks brother
Tru
Apapokha ngakhale sine wa DPP,akhoza zedi sadandilakwile,let’s stop opposing in the sake of opposition
Autchule kuti Cashgate Highway
Better: China Highway
I second APM. Pabwera ma president angati omwe awanamiza anthu akuchitipa about Karonga-Chitipa road??? Ndiyekhayo anakwanilitsa nde yaa He deserves it.
Za ziii zopanda nzeru
idiot of so called president full of autocratic tendencies just like his departed brother!
Bola Anakati Chakufwa Chihana Highway,ngati Mmodzi Omenyera Ufulu Anthu Dziko Lino,andinso Ankachokera Kuno.When Will Malawi Respect Chihana.Mzimu Wake Ukudandaula As A Hero,koma Osamukumbukira Olo Mpang’ono,why U Selfish Pple
Kkkkkkk mzimu wake wakuuza kuti ukudandaula?
ine ndilibe pulobulemu lol
Nseu umenewo ndinakumana ndi vuto . Pa namujesi tisanafike misuku t off truck inalephera kukweza nkubwerela reves 50 meters. Izi imachitika nkuti chazulo lake truck ya southern bottles itagwa nkutaya ma botolo onse pamalopo .
ongopanga name the whole Malawi basi……
vuto palibe autchule ,takumbukani nthawi ya bakili atanena zokonza nsewuwu mu nyumba yamalamulo phungu wina ananyoza kuti nsewu wachitipa ulibe phindu kumbal
After ur leadership we Will change the name of this road .to hell with u
KKKKKKKKKKKKKK Atumbuka zikukuwawanitu hahahah koma ndaseka…..Bingu deserves it!
Ndibwinodi kutelo
Tabweletsani fundo yoti mutukule dziko mukukakamira zinthu zoti kwaifeyo is no profit even one kwacha
Zinazi ndizochitisa manyazi kkkk munthu wakulu kulilila nseu kutiaupatse dzina lake akamakhala amalota chani wayambaso zabrother wake zafrag zazi mphindu ndichani azautenge aziyenda nawo muchikwama ngati zikumunyasa kuti zina ulibe chifukwa akhala oyamba kupanga zimenezo kkkkkk
zausilu.let him burn in hellfire!!!!
Alakwitsa kutchula dzina la bingu, msewu. Umenewo ukanatchulidwa mu dzina la chihana, ndi chifukwa chiyani ndikuti litchulidwe mu dzina lachihana? Kumelekeza zomwe anachita kumalawi mu 1991s, mwachisazo ku southafrica kuli zinthu zomwe zimayitanidwa mu mayina anthu amene anamenyera ufulu wozilamulira koma anamwalira wosakhala m’tsogoleri wa southafrica monga oliver thambo kuli oliver thambo international airport, peter mokhaba ndi moses mabida kuli moses mabida stadium komaso peter mokhaba stadium, kuliso chriss han ndi water sisulu kuli water sisulu university komaso chriss han university,
Bingu deserves to be remembered through that road that was one of his achievement kwa iwe ukuona bvutowe tchula dzina la nseu ndiweyo tione ngati zingafike mpa fb pomwe
M1 nde ukhala kamuzutu
Better Mpandadzina road!
Again this displays myopic reasoning by the so called Malawi leadership (if at all there is any). I repeat it is the president’s responsibility to develop his country, mandatory for that matter. No need to clap hands for him or her for performing a dutiable function. Even Kamuzu was over praised in similar fashion and strangely we also have Bakili Bridge.
Women, do you have to praise ur husbands for bringing food on your table when it is their responsibility? Ankati chani pofunsira?
Men, do we have to clap hands for our wives for breastfeeding our babies?
Apatu Mlomo waombera mmanja Matako potulutsa zam’mimba!
Am behind that only for Peter!
Dats very very true BINGU HIGH WAY
he deserve it its one of the greatest achievement we should be proud of as Malawians. those who had never had a chance to go to chitipa before the construction keep your comments for your self. I really second that
Thanks bwana mutanenso kachiwiri. mtima wanu ukhale okodwa. mwandisangalatsa heavy.
Good development indeed , he deserve it . not all can be happy tho but let it be so..let’s respect each other..
Comment imeneyi ndi za mseu zomwezi kapena mkuluyu amakusakani kale Mr Chiumbuzo?
George Matenga osangotukwana zizizonse, aliyese ali ndi ufulu oyakhula mbali yake
Ởlo kumudziwa bwana kumangowa pemphelera anthu oterewa.
i like your attitude mr chiumbuzo God bless you for taking no offence.
I second you Chiumbuzo. Otukwana musatope ndikuwapemphelera
A George pa anthu omsewa mwatukwanapo nokha manyazi bwa,,?munakakhala kuti munadusapo nseu usanamangidwe sibwenzi mutatukwana,ine ndiwa jb koma pokhapa asiyeni a DPP ayenela kukondwa ndi chitukuko chawo ,delete your comment boss mzocheza izi
Mkuluyu mwina ali ndi vuto nankha mseu mmesa ndi chitukuko cha ziko nde chotukwanila ndi chani?
Anapeza mseu ayambapo kunyoza anthu ena eeeeish
Bulshit!!!!!!!!! mmalo mopanga zotukula dziko basi uzikati nsewu dzina likhala chani……voetsekiiii man
Koma Bingu anapatsidwa kale ulemu ndi Five Star Hotel komanso Stadium nde mseu munakaupatsa dzina lina.Olo mseu unakapanda kukhala ndi Dzina sitinakadandaula
They must use ethical Malawi names not after his brother or anyone so if i become a president that mean anything i do for my Country/Malawi i must mention it after any of my relatives?
Good news
anamanga yekha no vuto for that i wonder some people arguing mumafuna atautcha chani
The last sentence confusing the story
Are these roads related?
non of my busness
Senseless!Karonga Chitipa road is fine by me!just that
It’s Ok.
Wina aliyense tchito zamanja ake zimuchitire umboni.Nanu akumpoto mukazapeza Prezident wanu muzatchulako maina ake azitukuko zimene wapanga
Mayina onyatsa achilomwe ama foreigner wochokera ku Zim ayi kuno tidzachotsa dpp yikachoka fooook
Iweyo udachokela kuti ndizina lakoli?
Kuburundi ndiye.???kunoso mayina aliko, nt lachilomwelo aaa takana ise
asaaah mayina kunyatsa ngati ndiwo zamtapasha
After this government these names of thieves wil be changed they deserve nothing in Malawi
Kkkkkkk dzina lamunthu akuti traffik
Nonsese !!!!! i see no good in this work.
I’ll change it to “Orton Chirwa” or “Kanyama Chiumia” highway. These thieves want us to read their dirty names eveywhere.
Kanjira kwa2so kakufunika zina limenelo
Dooko la Nsanje will be Bingu Port. He initiated it! Not so?
Peter is moving with time that when he leaves whe shall all contemplate
Welcome Development.He Deserses It.
Zakumtoso zedi
Ndie??umafuna autchule malawi 24 Joice Banda?
wat for? that’s an insult!
better he named it after his brother others could have mentioned their name
This guy is really a waste of time
OK
ungokhala sleepiness chaponda road
it should have been named perhaps after the late speaker of Parliament munyenyembe im only suggesting!
A Munyenyembe palibe chinapanga iwo cholozeka kuti mpaka dzina lawo mkugwilitsidwa ntchito
Kkkk mpaka Munyenyembe,,
bingu wa muthalika deserve this take it or leave t
sorry for munyenyembe no history or development ask Lucius for tribute
Well read me well don’t browse
Asa1