BREAKING: Comedian Izeki dead!

Advertisement
Izeki
Izeki
Izeki dead.

Malawi’s renowned actor and comedian John Nyanga popularly known by his stage name Izeki has died, Malawi24 can confirm.

Nyanga died at Queen Elizabeth Central Hospital in Blantyre where he had been admitted to for the last few weeks.

Nyanga, who rose to fame performing with Kwathu Drama Group and as part of the ‘Izeki ndi Jacobo’ moniker with his friend Eric Mabedi, passed away this afternoon.

Bon Kalindo has so far confirmed the sad news.

Nyanga will be laid to rest on Tuesday in the commercial city of Blantyre.

 

Advertisement

1,447 Comments

 1. Malo moti ukhale mbaliyanga uzidyanane kauze apolisiwo pakhomo pache sipano apolisi azingodusa vi vi pali mankhwala achabe pano taluza munthu wochita Zinthu zotsangalata tikatsegula wailesi timafuna mau aizeki
  .
  ……… ndinzake jakobo timati wailesi yasangalatsa
  ..
  .jakobo akwanitsa ntchitoyi yekha nzimu wa izeki uwuse mwa ntendere nafedwa wankulu ndi jakobo potaika nzakw tingoti pepanii jakobo

 2. Ndiwe Galu kwabasi. Mmalo mwakuti ukhale mbali ya ine. Iweeeeeeeeee. Siwanena kuji ndisamba? Ndisambadi. Uwonaso magalimoto a Police azingodutsa pano kuti viii, viii, osapawona pano. JOHN UWUSE MUMTENDELE. UNAYIGILA NTCHITO. R I P

 3. its quite 2sad kut anthu azisudzo nd osangalatsa dzko azipita kulichete,kwa iwe kwatha tilingalire ife otsara kut taphunzirapo chani anyway lets accept. R . I . P . U were born to intertain people of malawi

 4. Umadya bakha ndinamugwila nanga madzira ake umadya ndikubwelesera tomorrow morning tilisowa luso lako R I P

 5. Umadya bakha ndinamugwila nanga madzira ake umadya ndikubwelesera tomorrow morning tilisowa luso lako R I P

 6. Akazanga uyu ndi mfiti uyu ati ali ndi airport pa senzanipa ati amalandira alendo jakobo ndi ndege alipo mmmm izeki kuusa kosatha munthu osauka kukhala ndi mbalume galu iwe usazabwerenso pano zipita ndikucheza nda akazanga mnyumba shaaa izeki tizakusowa pakati pathu

 7. Utipuletipule pamenepo, ndi masosege ako amenewo, msana khotawo, osawuka kudziwa mbalume……..
  We will always miss him, the great talented Mr John Nyanga (aka Izeki).
  Innalillah Wa Innalillayh Rajiuna (truely we came from Allah/God, and to Him we return.

 8. “kungocha mmawa mwa bvumbwe muno basi kwa ine kudzamwa mkaka……iwe tampatsa zakudya jacob yo timukame mkaka……” kkkkkk. Rip baba Zex

 9. “kungocha mmawa mwa bvumbwe muno basi kwa ine kudzamwa mkaka……iwe tampatsa zakudya jacob yo timukame mkaka……” kkkkkk. Rip baba Zex

 10. Atćheya!! Atcheya ndi dolo eishiiiiiiiii mukuxiwa kuti atcheya amadwala ? kàyà achira nthawi yañji anyàmata ápatauni.

  kuumodzi mwa mikumano ya phwañdo la Ñdakatulo MR JOHN NYANGA kutimvetsa ķukomà .

  AMBUYE LANDILANI MZIMU WAKE.

 11. Eshii! koma moyo uwu!! Izeki, adzandisekesenso ndani? Pokumbukira luso laku lakuti, tili mwamba mwadzidzidzi tinangomva oyendetsa ndege akutiwuza kuti, ndege yapanga airrock nonse tsikani muikankhe.Kkkkk ! Poti kunalembedwa r. I. P.

 12. chifukwa chani a Malawi timakhara ngati achikondi wina akamwalira koma akudwala izeki atapepha chithandizo ndindani mwa inu anamupasako

 13. Ambue ndnapta kuamerika kukaona mwana wanga uja anandtana,,,,,kma znatichtkra munjra tkubwera mmmm zoopsa kwabasi,,,,,,tafka pasasafilika ndege yatha mafuta,,,,,,kma yambani kukankha ndegeyo!!!!! RIP BIG MAN

 14. “Njingayi Ukubwelekayi ukaonesese kti ukafuna kugwa uzikatsika kaye kenako kuiyimika pa mtengo, kenako uzikagwa bwno..ikabwele bwnobwno”” wl mis U John Nyanga!! R.I.E.P

 15. Wafika nzanga, eee, ndati iii ndikamuwone nzangauja kwina akandagaile nkaka ooooo wachitabwino , kodi iwe tamuze Jakoboyo azidya ameneyu Jakoboyu uyu timukame nkaka wambili ameneyu jakobo

 16. I wll naver 4 gat u once again asking alot of money from bst frind jacob ……. Jons andipha ndithu akut tikangokumana azindimenya chibakila chimozi 10 kwacha may ur soul rest in peace Malawian national is ur witness

 17. eeish to blieve z imposible even ateenager know ths man indeed gud thngs doesnt stay long nothng to sy ITS A UMAN JOURNEY bt brother RIP

 18. mundingongoze pamenepa ndangongola ndingongole yanga imeneyi kuvala nsapato sikunyada bola fees yapezeka mulungu akulandire nasunge mzimu wako

 19. This man was really talented.Nganga wafika apa! “Basi saizi yanga ndimeneyi” Kulemera basi kulemera! I will remember u as multitalented person who entertained the Nations.May your soul rest in peace.

 20. I started watching you at Zomba Chanco great hall while my dad was working in the MDF at Cobbe Barracks,I met u physically and will never forget u.The whole nation of Malawi is your witness.RIP

  1. It’s non of ur business Tobias,there was not even a reason for u reply me. I don’t know u bro,sorry for wasting ur tym replying me.

  2. It’s non of ur business Tobias,there was not even a reason for u reply me. I don’t know u bro,sorry for wasting ur tym replying me.

  3. It’s non of ur business Tobias,there was not even a reason for u reply me. I don’t know u bro,sorry for wasting ur tym replying me.

 21. Akulu koma munatchuka mma radio ngakhale mu Tv koma kukuonani pamaso chidebe chenicheni……….inu kaya kulodzedwa kumavalanso chipewa cha police kuno bwana arrest the guy mmmmmmh……sindidzakuiwala iwe u were such my jester

 22. Mwapezeka bwanji ndi katundu waboma(chipewa cha apolisi) pomwe siiiwe wapolisi,, bwana arrest the guy, mmmmmh we will always remember you Mr Nyanga

 23. You walk,then you turned left,you walk kaya kwinaku ukasochera uzikafunsa konko,Ana amuna odyera pakamwa,matenda ndikanadandaula nawo ndi ma shingles atangobandula mlomowu zanga zada,R.I.P you were such atalented actor!

 24. “ine ndinali kunja ndinakwera ndege,napita ku America moti nda kumana maso ndi maso ndi MADONA ati afuna andipange adopt”. Rest in peace Izeki…

 25. Munthu Kuvala Zovala Zake Izi Kkk Munthuyu Akufunika Reform Iyambire Pompa, Munthu Amatha Uyu, Olo Utakwiya Kungomva Mau Ake Umayamba Kumwetulira Wekha, May His Saul Rest In Peace,

 26. Jacob unali kuti m’mene izeki amapanga zimenezi. i think ukanakhala pafupi sizikanatheka. May his soul rest in peace

 27. palimbe wina amene anga zapange monga iye sangalasi wamalawi tithokoze mulungu pazabwino zose wachita akalimoyo zimu wake ukause mutendele john nyanga

 28. R .I .P. Kapumuleni ku zowawa za dziko la pansi. Ngakhale a Jacobo atakhala 10 pa mtengo wa 10t sangayende malonda. One of his comedies.

 29. Sad,my mind goes bc to a Tv prog.my story!u were alone doing everything while sick u fought a fight kapumuleni kuzowawa za dziko lapansi

 30. Iwe m’mutu mwakomo khata pita ukayike ku nyumba kwako mmmmmmmm ngati boza lero izeki kuvomereza khata ya jacob yija amayikana RIP izeki

 31. Chaka chino ndichowawa kwa amalawife anthu abwino komaso aluso akupita kumanda. Mwezi watha grace lelo izeck rest in peac u two. Tikusowa.

 32. mukuona kuti mmudzi monse muno palibe ali ndi chimbudzi. tsopano inu kumanga chimbudzi kuti akutameni ndi kubiba?” gret izeki RIP

 33. Izeki zimu wake uwuse mu mtendere

 34. Rest in peace JOHN NYANGA,chikondi chadziko lapansi chimatha pamene wokondedwa wayikidwa m’manda,tidzakusowa kamba kalusolako….ambuye mlandileni JOHN….

 35. Atate atate tung’ono tung’ono ndito timanenepesa nthawi imeneyo akuyitanila malonda telkom ithink inali chama 2002 tizisowa nthabwala zake RIP Atate atate

 36. ” ndimangomva pa maradio kuti Jacob,,Jacob!! a Jacob ndi inu eeti,, mmmmh koma radio imalemekeza chinthu chonyasa eeti,, kkk…. surely we belong to Allah n to him shallow we return !!

 37. Anali akamuna awa akati Fabiyano ulipopanobe eish sindizakuiwala mpaka nane tizakumanenso poti ineso nthawi ndikudikira zandikhuza kwambiri limba mtima mbale wanga Jakobo

 38. Rest in peace u hv suffered for long tym dia John. sindizayiwala comedy unapanga posachedwapa kuti nkhope yako ukanakhala nkazi sukanafusilidwa taaa .u made my day seriouly

  1. Ndiwo zitasowelatu mukhoza kudyela nchele. In this context, izeki was ndiwo fine. Now that we are laying him to rest, jacobo akhoza kupeza nzake wina amene akhoza kukhala ngati mchele koma saangafikepo pa izeki olo pang’ono. Izeki was the greatest. Jacobo is nsima yosala imene tikhoza kudyela mchele.

 39. My number +27780774642 zadwino zose azanga akukwale zingwagwa ndi chitawila komaso kwathu kulunzu zanga balamani ndazi kacepa kwaponda

 40. God loves when he see people entertaining each othert but the happiness you used2 share with us in your life time is unfgettable malawi will always remembr u may ur saul rest in peace,yes right there in paradise.

 41. I don’t understand untill now, would you just brief the statement guys. Did you say JOHN NYANGA(Izeck) Shame! Very very sad indeed, I will never find such a talented man in Malawi. If it is a time lets just say the scripture comes true(ALL IS TIME). I believe the nation will miss you and talent, we be missing you in fresh but your sprit will be still around the nation. R I P

 42. Eshiiii its abad newz to Se u izek again we will ms u but god powerful we gonna meet again may ur soul rest n internal piece

 43. U had a special talent 2 our nation,so we as de Malawians we wil mc ua jokes, ‘kod iwe Jacob!Chimbudz nd odi umayamba cani?’ may hs sour rest n peace.

 44. John Nyanga ndakudandaula ndipo ndakulira pa imfa yako, unali munthu wabwino iwe, ndikukumbukila bwino ndili wamngono pa 29 Nov 1999 unabwera kwathu kudzamuona brother wanga akudwala

 45. Izeki u were atrue comedian, u had no one to compare with, u used to bring tears of joy to us but today u bring us tears becouse of ur death. May ur soul Rest in Peace.

 46. Its sad to lose one of greatest comedian in southern africa. He was funny guy to watch even u didn’t get the language he spoke but his action was ininterpreted in so many languages across the world may his soul rest in peace

 47. These remaind me that really this is not our home ,with the talent you had your name never die ,sorry for family and entire nation May his Soul Rest in Peace

 48. Izeki was a rare comic gem..he wud step on stage,a mic in his hand…people wud burst into uncontrollerable laughter ..he was indid a powerful commedian..Rest Well Mr Nyanga..”Kod iwe Fabiano,pakati pa nkhumbazi ndi iweyo,ofunika ndi ndani?”

 49. RIP John Nyanga. I think you have had your best time on earth. Ife tizangoti “TAMATAKASANI. MUZITAKASA. KODI MADEYA SIMUWAZIWA.”
  “I AM THE ROAD. YOU WALKO YEEEE YOU WALKO. I AM ROUND ABOUT.

  UKATAYIKA NDIZAKO. KUNO SIKWANU.”
  Izeki Malawi sazakuyiwala. You are the legend of all times.

 50. A Jacob matama avekere anali kunja ku Zimbabwe, Izeki akuwaphwetsa kuti ulendo wa kuja sakwera Bus, kunja amakwera ndege basi kkkkkk, ndikulira awuse muntendere original joker.

 51. My condolences to the entire Nyanga family/ friends/ relatives & the Malawi nation for losing a great personality in terms of stage-plays & comedies; the Lord giveth, & the Lord taketh away;…you will always be remembered…MHSRIP !

 52. Ndidangobva mau ake okha zimaonetsad kuti moyo wake unasinthadi sanali chimodzimodzi afike ndimtendere pa fukato cha Abraham amen.

 53. ” Jacobotu Ameneyo Ndiye Kuti Wadya maungu Ophatikiza Ndi Ma Pumpkins’. KOMANSO Ukuciona Bwanji Cimamuna Cacifupi Cakuda Cili Biiiii!! We Shall Always Miss Your Servises, Rest In Peace Mr. Izeck (nyamayasakaza)

 54. 2016 Wadza ndizotani? Why are you taking away the people who bring us some relief, when our face is casted down? These are the Big names of all that are known for something good; unlike you and me.Rip.

 55. Imfa ya anthu akeimkomera awalandira m’mumba zokozeka. So gud to finish up in aspritual note. May yr. soul rest in eternal peace. Izeki unali obweletsa chimwemwe pamiyoyo yambiri. RIP Zeks

 56. You died a hero!may the grace and love from the most high jah guid ya till the day we shall meet and lough again.tsamaya pila

 57. He has finaly sleeps away ,we will remember him as a great thinker who used his art to convey messages that changed many pipo particularly the youth,izeki will continue talking to us through his work ,,,to God be the glory he has finished the race well ,legends may die but their work lives forever ,,,lets celebrate his life ,,,,,,,,rest izeki ,,ise tikusowenge nadi

 58. Ambuye anapeleka Ambuye yemweyo watenga. Ngati anthu amapuma ndikuti mukapume ankolo munazunzika. Zowawa zinachuluka. Koma mapemphero athu achepetse mkwiyo wa Mulungu popeza kulakwa nkwathu kukhululuka ndi kwake. RIP Izeki

 59. Nidzakumbuka izeki because was best ever…..Kukhaka awiri simantha, Tonde WA nkkhumba,kunja, njinga,lilime lamkango… And many more. Izeki anari doro sadzapezeka wina oposa John nyanga….chikha timasankha oyenera kufa tikadasankha enawa.

 60. If only words and tears could bring u back Izeki..walimbana nako kulimbana kwabwino.. Wapita utamuziwa Yesu.. Zifundo zake zikhale ndi Mzimu wako..we thank God for the blessing u have been to Malawi.. Unali munthu yemwe umatha kubalalisa nkwiyo makomomu ndikuzazamo kuseka kosatha.. May u sleep in the Lord Izeki till we meet again.. We will sadly n deeply miss u.. U will always be our Hero!

  1. He was the one we love,he makes pp hpy all the time he waz our hero to mw,am so hpy dat God show hm the way he new God so much.

  2. Amen.. Knowing that he died preaching Jesus is our greatest comfort.. Pumani mu mtendere Izeki tikusowani physically but in our hearts n TVs u will live forever..

 61. anawa tizawauza kuti kunali mr you wlk eee u walk turn left………….. May the Good Lord be with the family and frez in this hard times

 62. we love Mr Nyanga may god guide your way sorry for our heartless course munthu sayamikiridwa akakhala akupuma koma akagona shaaaa the whole world will respect more over REST IN PEACE TATE IZEKI.

 63. Kod ndifuseko enafe xool stinapiteko kod akat “likes ” amatanthauza chani? Ine ndi dyomba ndiphuzitseni uthenga uwu ndiwachisoni nde tikamapanga ma like zimatanthauzanji kwa ineo nane ndidziweko lero pls!!! Anjiganyeko nombene mbate kumanyilira INNARILLAH WA INNA ILYH RAJGHUNAH

 64. “kuyesera muno ndi muno osagudwa ,azimayi kumaangodutsa, kuti uzigudwa amakupanga aJacobo awiri one kwacha, hahahahahahaha,,kkkkkk,,,ndiyiwale bwanji ine, REST IN PEACE IZEKI ,,respect.

 65. asa pa Hethrow ambuye izeki ndege itakanika kulira airlock what happened ? Mwasiya history in malawian comnedy u shall be renembered ambuye aulandire mzimu wanu uuse mumtendere dothi ku dothi fumbi ku fumbi dziko lapansi sikwathu

 66. My ccter hw ar u? My condolences sure Izeki wamwalila? Muuuuuuuuu amatikondweletsa abambo aja ndithu yaba too bad indeed.Ndangowelenga kumene pa face-book yaba caipa.

 67. carrying a blacket on your shoulder saying ndi chi jb as our fomer president used to carry a piece of cloth on her shoulders ! You have finished the race bro , lets meet on other side of life.RIP !

 68. Rip Zex Ndiye kuti chani? Simungamalembe dzoveka iyai…. Kodi ifa simuyidziwa? Dzulo lija simati wafa,, Eya wafatu wamwalira ndiye mukuti awunse mutendere nanga sikunyadira kumeneko? zowona munyada zowona ZEX maphangombe kuti wafa?

 69. Eeeish poti ndikufuna kwambuye kunanakhala komapelek belo ndikanapeleka koma ndingoti kwanu kwatha kwasala kwa ine REST IN PEACE MR IZEK

 70. ‘pakhala change?’ change cha chiani? ‘chabwino ayi pasakhale’ gd bye Zex!! luso salandana komanso sasiilana….wapita nalo…RIP!

  1. nkhani yomvuta kuyivetsa every one knw time like this ist diffent than ather dyz.to u izk takuluzani mupite mwambuye,ugone how next 2mrry R .I .P

 71. CHAPONDELA!! Muwonetsetse uyu wamkulu JACOB m,mkame mkaka wambili or machen 4 atuluke pali iye apo , ISEAC ISEAC ine nili ndi ng,ombe iwe ulibe kalikose, galu wa chabe chabe, uyelekeze anyamata anga akuponde, RIP madala

 72. zex Gone but not forgotten wangosogola ase tikupeza ife tili ndichisangalalo chifukwa unalibe mlandu ndi muthu,ndikachita bwino iweso ngati unachitabwino tizakumana pa nyanja Ya mandala ndikupereka chikondi cha Philadephia kwa iweyo mpumulo wa Bata ndi chisomo chayesu zikhale nawe

 73. When i remember, ku SouthAfrica sikunja, kunja sikupta Munolulama kkkkk. Kwamulungu ndikumene tinachokela ndikumene tizabwelenso.

 74. Malawi’s renowned actor and comedian John Nyanga popularly known by his stage name Izeki has died, Malawi24 can confirm. Nyanga died at Queen Elizabeth Central Hospital in Blantyre where he had been admitted to for the last few weeks. Nyanga, who rose to fame performing with Kwathu Drama Group and as part of the ‘Izeki ndi Jacobo’ moniker with his friend Eric Mabedi, passed away this afternoon. Bon Kalindo has so far confirmed the sad news. Malawi24 will keep you updated

 75. Malawi’s renowned actor and comedian John Nyanga popularly known by his stage name Izeki has died, Malawi24 can confirm. Nyanga died at Queen Elizabeth Central Hospital in Blantyre where he had been admitted to for the last few weeks. Nyanga, who rose to fame performing with Kwathu Drama Group and as part of the ‘Izeki ndi Jacobo’ moniker with his friend Eric Mabedi, passed away this afternoon. Bon Kalindo has so far confirmed the sad news. Malawi24 will keep you updated

 76. Malawi’s renowned actor and comedian John Nyanga popularly known by his stage name Izeki has died, Malawi24 can confirm. Nyanga died at Queen Elizabeth Central Hospital in Blantyre where he had been admitted to for the last few weeks. Nyanga, who rose to fame performing with Kwathu Drama Group and as part of the ‘Izeki ndi Jacobo’ moniker with his friend Eric Mabedi, passed away this afternoon. Bon Kalindo has so far confirmed the sad news. Malawi24 will keep you updated

 77. Malawians it’s very painfull to lose this Man, IZEKI, RIP,ndizovuta kuyiwala nthabwala zanu man, Pepani a kubanja,tonse tikumulila Izeki

 78. malawi will always rememba u izeki kaya ife nde tizasiya chani palibe chomwe timatha ata rest in peace my condolence to jacob i knw its hard to blive koma mlungu yekha ndamene akudziwa

  1. kkkkkk a nyonzoh nel c demba ufiti ndikakhala ndimatha kanayambira ku state house mkukagwa mwina mkutchukako kkkkkkk

 79. John Nyanga will be missed for ever in the comedy fraternity and also in the communities around and beyond. We have learnt a lot from his comedies and other educative messages. MHSRIP

 80. kod aonesa pa tv kut wamwalira? pakuti pa fb ndi pa radio sibdikukhulupirila kut anganene xoona Chfkw aka ndikachitatu kulenga xakufa kwa prophet Z

 81. R.I.P Prophet Z (lemba losiriza) Koma inu a Malawi 24, mwayambaso? Mesa mwanena kale? Ndiye tizingomva yomweyi muja mudachitira pamaliro a G. Chinga? Anthu opusa!!!! Kambani ina.

 82. Ndili okhuzidwa kwambili, imfa bwanji imasiya mbava, mbanda, komanso zigawenga nkukatenga anthu ofunika. Mzimu wanu uutse muntendere.

 83. RIPIZEKI U HAVE INSPIRED A NATION,WE NEED A STATE FUNERAL FOR HIM,FOR ALL THE LAUGHER HE GAVE US,MUNTHU OSANGALATSA ENA NDOFUNIKA LIKE A FLOWER

 84. Acomplete stage drama maestro who would make people laugh lungs out gone too soon, you fought a good fight our dear brother, you have finished your race, go in peace our entertainer of decades,till we meet again in Gods glory,we wil miss you but memories will remain for ever

 85. abale,ndkoneka ngat wankaziet?,kma wankaz’o atamaonka ngat ine ameneo angakwat’we ngat?,banja limvutatu,akwat’wa kma akwat’wla cisoni.Let him rest n peace

 86. Maula! Maula! Tzkakupasla sma pawndo! Iwe chpewa cha apolsi unachpeza bwanj? Kupanda manyaz kumachvala kuno. Ayi bwana, arest the guy! Do smothn’! Tel the european that we r serious!! Ine ndkangomva jacob ndnu? Koma abale wailes imalemekeza chonyasae!! Chafuklaa? Yes bwana! Tabwera kuno, incase! Panga makan anyamatanga akuponde uone!! Wh@ atalent guyz!! Zntchto zanu tzsowa & rip

 87. TIZAKUSOWANI MR . MUMTIMA MUDZIWAWA NKAKUMBUKA NTHABWALA ZANU..

  (Sopano akulu , ndifunse nawotu tisanachoke, ndekuti munampanga zinazache eti,?) Shaaaaaaaaaaaaa

  R I P.

 88. Muwuse Mutendere Man Izeki Tikusowani Pamene Ndikakumbukira Muja Mumapereka Map Kwazungu Opita Ku Chileka Aaaa R I P

 89. Maybe my comment wont be important for the majority of people here. Some of u will ignore it, most of u wont bother to read it and it will go unnoticed along with other comments or maybe ill be critisized for this, its okay but i just want to let u all know I am selling potatoes!!! Anyway RIP

 90. Kaende bwino muntu wamulungu angale naiwe pamwe nabangeli bake,tizakapezana kwamene uko naife tibwela mumbuyo ✋

 91. poti kunalembedwa kuti tonse tizafa nd2 chabwino, koma ndidakakonda anthu aluso ngati inu mukadati musamapite. Malawi has lost one of its great son again, so pitty.

 92. Very sad,He may be gone forever but to us Malawians he will live forver in our hearts.He was blessed with his talent.As Lucious said in one of his songs”akanati azisankha…tikanatumiza enawa”….Oooh we have lost a very our beloved Izek…..so sad!

 93. Mukafuna kungwa panjinga yangai muzitsika kaye inuyo ndikungwa mukamaliza kungwako muthaso kukwera Zexy tizakusowa mpaka kalekale RIP

 94. Iwe mmalo moti ukhale mbali yanga zikakuvuta uzizangongola kwa ine apolice oky iwe ndi galu kobasi… never forget u mr man zex RIP

 95. If its true then Malawi has lost avery important person. These are the pple who deserve State Funeral. He made the nation proud!. Honestly the inborn talent that u had is Ireplaceable. Very difficult to find such tallent again.. Am saying If its true that he is gone, then he deserve State Funeral. Maiko amnzathu akamwalira anthu ofunika ngati amenewa maliro awo amalemekedzedwa… an example is that of PAPA wemba who after dying on stage his nation offered him state Funeral. Ngati wamwaliradi chifukwa olemba nkhani akumalawi mwatchuka ndi uchifuamba okhupha anthu kuzera mkulemba nkhani zabodza….. Koma ngati ziri zoona kuti wamwalira Izeki will miss ur comedies, ie, Reform, maliro, kunja, ku stadium(independence day), Njinga and many more… RIP. we shall miss u in our family for u were and u still enteryain us even in ur absencia.

 96. Zitheka bwanji mumthu ot siwapolis kupezeka ndichipewa chapolis arest de guy show de ulupian dat we r serious zoona? Wapitad wat kind of tree jacob he touch eeeeeeesh so bad

 97. Wy Malawi?????? De tears 4our dearest gospel singer Grace Chinga dey r stl fresh n 2day we r hearing de death of 1of our best comedian John Nyanga.. Mmm run out of words. MHSRIP.. WAT A PAINFUL YEAR IN MALAWI!!!

 98. Sindidzawaiwalira pa comedy ya candlex mu nthawi imeneyo pa chichewa choti, azimai ena Mulungu sanachedwe nawo powalenga anangoti papapa tiye uko candlex ili komko mukaoneka bwino ndi zodzoladzola. Pamene ena eeee Mulungu anafatsilira, kuwachunachuna .

 99. Zex have been our greatest source of inspiration and courage, in fact, he was such talented man…….deep down in our hearts we will always keep your image_…….Rest In Peace Sir

 100. Koma amenewo akapume ndithu, mzimuwawo uwuse mumtendere pano ndikulira Jacob amudulatu mkonowamanja apa, alira bwanji Jah

 101. pali mitengo yachabe pano apolisi sapaona pano ndisamba uonanso katundu akalowa walowa basi! hallo jane taphika thererelo ndikubwera ndizakukonzekonze! Kulemera basi! Ause ndi mtendere,izeki

 102. Too bad to lose him anali olimba mtima. “Wakufa sadziwika” he used to say when rumour mongers killed him then. To miss him.

 103. I Rememba It Wz 2003 Dat Tym I Oz In Std7 @ Njedza Primary I Met Wit Izek & Jacob Face 2 Face @ Mulanje Pak Day Ov Education May His Soul Rest In Peace

 104. After all the rumours that have been escalating about your death, u are now finally gone. U made the world big, and the whole world shall remember you. Rest in Peace, Zecks.

 105. I have bn followin him since 1986 when Charles Severe was alive during the Crowd Puller Kwathu DG.Rest in peace Jacob,sorry – IZEK.

 106. i still remember his jokes.One of the jokes still makes laugh:….he was to see his friend’s new born baby boy..then he lift him up..in his arms and..say the child is already old..look the face….lol RIP

 107. Its so unbelievable tht u r gone Zex, u hav died a Legend ma men, God blessed u wth un Amazing Talent so its high tym u hav 2 Entertain Angelz up in Heaven, REST IN PEACE 2 U SIR ZEX, much respect 2 u Sir

 108. Death has distort a good entertaining pair .WHO WILL PART ERIC MABEDI ?.ANYWAY MHSRIP. Mwandipatsa za school fees, nsapato, zitenje . Ndiwo kulibe. Nanga yaabambo yapathumba. WHAT A TALENT?.LETS JUST PESERVE MY FELLOW MALAWIANS, WE HAVE REALLY LOST A NATURAL TALENT.

 109. Rest in peace big man ngakhale nkazi ndi ana anakuthawa lero ati akulira dziko lapansi nde limenelo nzako jacob amakukonda ndipo azakukondabe,Rest in perfect peace my neighbour.

 110. may his soul rest in peace!!!…mukandpelekeleko mon kwa grace chinga!!!!

  1. De man of God should rest in peace indeed but am very sole 2 Jacob u were bros for real. De nation of Malawi wil mc Zeks mo ndimkamva kukoma akamapanga ma programz pa Joy radio. MHSRIP