APM names Karonga-Chitipa Road after brother

Advertisement
Albinos Malawi
Bingu wa Mutharika
Chitipa-Karonga road named after Bingu

President Peter Mutharika has commanded government to name the Karonga-Chitipa road after his brother, Bingu wa Mutharika.

According to press reports, the order has been issued following completion of the multi-billion Chinese funded road.

Office of the President and Cabinet has made the announcement that following the decree from APM, the road will now be named after the president’s late brother.

The road joins Lilongwe Stadium to fly Bingu’s name under APM’s orders.

 

Advertisement

79 Comments

 1. Amalawi ambirife ndife mbuli going by ma comments ndaonawa, tikuona ngati Binguyo anachita kutigayila nsewu uwu pomwe inali ntchito yake, chitukuko zitimayela kupempha kuti Boma litichitire iyayi. Aliyense wodulidwa msonkho wooneka kumaso kwa anthu agwirizana nane kuti izi ndi ntchito za misonkho yathu, ngongole anatenga Bingu zizabwezedwa ndi misonkho yathu choncho ndifeyo tikupanga izi osati yemwe tinamulemba ntchito kuti ayendetse.

 2. @ Yohane Kanjala Chiweko,very good 2 points tangosiyana chipani ine wamafunde koma nsewu uwu ndimagwilitsa ntchito tsopano ndiwapamwamba sadandilakwile a DPP pomupatsa mtsogoleri wawo wakale ulemu

 3. I second APM. Pabwera ma president angati omwe awanamiza anthu akuchitipa about Karonga-Chitipa road??? Ndiyekhayo anakwanilitsa nde yaa He deserves it.

 4. Bola Anakati Chakufwa Chihana Highway,ngati Mmodzi Omenyera Ufulu Anthu Dziko Lino,andinso Ankachokera Kuno.When Will Malawi Respect Chihana.Mzimu Wake Ukudandaula As A Hero,koma Osamukumbukira Olo Mpang’ono,why U Selfish Pple

 5. Nseu umenewo ndinakumana ndi vuto . Pa namujesi tisanafike misuku t off truck inalephera kukweza nkubwerela reves 50 meters. Izi imachitika nkuti chazulo lake truck ya southern bottles itagwa nkutaya ma botolo onse pamalopo .

 6. vuto palibe autchule ,takumbukani nthawi ya bakili atanena zokonza nsewuwu mu nyumba yamalamulo phungu wina ananyoza kuti nsewu wachitipa ulibe phindu kumbal

 7. Zinazi ndizochitisa manyazi kkkk munthu wakulu kulilila nseu kutiaupatse dzina lake akamakhala amalota chani wayambaso zabrother wake zafrag zazi mphindu ndichani azautenge aziyenda nawo muchikwama ngati zikumunyasa kuti zina ulibe chifukwa akhala oyamba kupanga zimenezo kkkkkk

 8. Alakwitsa kutchula dzina la bingu, msewu. Umenewo ukanatchulidwa mu dzina la chihana, ndi chifukwa chiyani ndikuti litchulidwe mu dzina lachihana? Kumelekeza zomwe anachita kumalawi mu 1991s, mwachisazo ku southafrica kuli zinthu zomwe zimayitanidwa mu mayina anthu amene anamenyera ufulu wozilamulira koma anamwalira wosakhala m’tsogoleri wa southafrica monga oliver thambo kuli oliver thambo international airport, peter mokhaba ndi moses mabida kuli moses mabida stadium komaso peter mokhaba stadium, kuliso chriss han ndi water sisulu kuli water sisulu university komaso chriss han university,

 9. Better Mpandadzina road!

  Again this displays myopic reasoning by the so called Malawi leadership (if at all there is any). I repeat it is the president’s responsibility to develop his country, mandatory for that matter. No need to clap hands for him or her for performing a dutiable function. Even Kamuzu was over praised in similar fashion and strangely we also have Bakili Bridge.

  Women, do you have to praise ur husbands for bringing food on your table when it is their responsibility? Ankati chani pofunsira?

  Men, do we have to clap hands for our wives for breastfeeding our babies?

  Apatu Mlomo waombera mmanja Matako potulutsa zam’mimba!

 10. he deserve it its one of the greatest achievement we should be proud of as Malawians. those who had never had a chance to go to chitipa before the construction keep your comments for your self. I really second that

  1. A George pa anthu omsewa mwatukwanapo nokha manyazi bwa,,?munakakhala kuti munadusapo nseu usanamangidwe sibwenzi mutatukwana,ine ndiwa jb koma pokhapa asiyeni a DPP ayenela kukondwa ndi chitukuko chawo ,delete your comment boss mzocheza izi

 11. Koma Bingu anapatsidwa kale ulemu ndi Five Star Hotel komanso Stadium nde mseu munakaupatsa dzina lina.Olo mseu unakapanda kukhala ndi Dzina sitinakadandaula

 12. They must use ethical Malawi names not after his brother or anyone so if i become a president that mean anything i do for my Country/Malawi i must mention it after any of my relatives?

 13. The last sentence confusing the story

  Are these roads related?

 14. Wina aliyense tchito zamanja ake zimuchitire umboni.Nanu akumpoto mukazapeza Prezident wanu muzatchulako maina ake azitukuko zimene wapanga

Comments are closed.