They have perhaps found a new haven in Nigeria, and now Mighty Be Forward Wanderers have permanently signed another Nigerian by the name Saheed Oluwa Shinaayomi.
The striker has been cleared by the Football Association of Malawi (FAM).
FAM’s International Transfer Matching System Manager, Casper Jangale, has since confirmed of the clearance.
Shinaayomi has been under the watchful eye of Shiba Football Academy.
The Nomads now have Japanese Genki Nakamura who is yet to play in competitive games due to delayed work permit procedures but Nigerian Amos Bello has already been key to the Lali Lubani side so far.
The Nigerian deals have been masterminded by Nigerian legend Jay Jay Okocha according to sources.
Neba Sudzayamikanso Waiwalakale anakulizila Amos Bello Pokulephelesa Mnyozo Pa Kwanupo?
Hence the phrase money talks…..lol
Hence the phrase money talks…..lol
kkkkkkkkkk congratulations neba. kunja mpaka? mukuitha but problem ndi yoti ma player mukugulao kukabwafu ndi nsulupi gunners aliko ambirimbiri moti amadya thabwa kusowa malo osaziwa ku noma aliko malo awo.koma osadanda ndi chikhalidwe cha2 a Malawi ndi zija zomati sindingakwatire wa chimizi ndagwira wa mtauni ukunena mayi opanga maganyu ochapa kapena ogulisa masamba mtauni osasamba komanso Osaoneka bhoo ndi zomwe akupanga a noma.kkkkkkkkkk umatha neba
Omse othawa Boko Haramu in Nigeria bwerani ku noma akusungani bola mungonama kuti mumasewera mpira basi akutengani,Boko Haramu wecom to Nyerere team yamakape mxieeew! Kodi china chikungodwaladwala chija mumati (nagamura) kapena Jeke? mchani paja ine ndaiwala!
zabwino zonse manoma
Noma ndkawawa
Noma kundivesa kukoma mmmmmmm
Noma kundivesa kukoma mmmmmmm
Nomads are really killing malawian football,malawi has not even reached that stage of buying foreign players! instead of kufufuza ma player m’midzimu shame!!
Noma nd deal
Amalawi amapita kunja kukasewela mpila bwanji? Kumeneko kulibe maplayer midzi mwao oti angasewele ? Kumanganiza , kodi amalawi mumadziyang,anila pasi bwanji? Mudzidziwa kuti ifenso amalawi tikhoza kungula ma player kunja ngati tilinazo zoyenelezazo
BT he should not be like the rate Lino Asu!!!
Eeee…Mbola, Noma Yalowetsa Boko Haramu m’Malawi Basi…Lol
Eeee…Mbola, Noma Yalowetsa Boko Haramu m’Malawi Basi…Lol
Neba uli ndi vuto zampira zimakukanika bola uzikapitiliza kulima kampopi bas,inu ndalama mulibe player wakunja mumpatsa chani,adikire mukagulitse kaye fodya ndi lit limenero
we have faith on the so please stay out of dis,,,,,,we ain’t gonna buying dem for nating
In nomars w ply prefetional ftbll tzw w afft 2 by forein player kkkkk kuli nyelele m noma ndithu wina a mwa temeki
In nomars w ply prefetional ftbll tzw w afft 2 by forein player
Chi team cha anthu andalama,osat i chingambwe ftball club.kkkk!
noma mukuyitha
Kkkkkkkk!!! A rebellious subject why can’t they obey buy Malawian product
Kkkkkkkk!!! A rebellious subject why can’t they obey buy Malawian product
neba sukusilira?
Anoma Simungakwanise Kugula Player Kunja Zosatheka! Akubwela Okha Osati Mudzitinamiza Kuti Mukuchita Kugula. Mumakanika Malawi Momwemuno Koma Kumalephela Nde Mungakwanise Wa Ku Nigeria? Akuthawa Boko Haalam Amenewo.
Y waisting that heap of money for nix? Hahahaaaaa nyelele kusamva
wow so wonderful, Y nt us? even uefa clubs z all about importing foreign players.big up nyerere!
ma player aku nigeria simukugula akungobwera pa free agent nde mukunama kuti mwagula ,simungakwanitse kugula mulibe ndalama zogulira ma player aku nigeria amagulitsa ma pounds osati ma dollars kapena makwacha
Nkhawa njee ife manoma tili ndi ma player ambili Ena akumenya Ku nyasa bullets,osadanda nyelele woyeeee
inu simukukate bwanji? Mulibe ndalama zowalipira?
ma player aku nigeria simukugula akungobwera pa free agent nde mukunama kuti mwagula ,simungakwanitse kugula mulibe ndalama zogulira ma player aku nigeria amagulitsa ma pounds osati ma dollars kapena makwacha
Congrats goes to the noma hierarchy for making it to another player signing. much to come from these guys. saheed oluwa shinaayoni most welcome. amos bello has the property of changing the game field structure.the striking force has an end point and you are the answer.genki hope you will feature agame soon.jafali chande welcome and we hope much to come from you guys. we hope to look forwad for the league lifting. ana tsogolani ife tibqwea mmbuyo a eni ake ulendo
bwinoTu boko halamu
bwinoTu boko halamu
Lol
Lol
Kkkkkkkkk 9m yomwei mpaka ma player akuja iyi nde tmat misala
Apa ndiye Manoma yafikaponsotu mpaka ma Nigeria n’s 2 mukukhwana kooopsaa
You are welcome Saheed to the warm heart of Africa
noma imakwana
Neba paja samatha kugula,,koma kutola ku Dzaleka Refugees
Ingopita ukatole Ena koma zogulazi tisiyire Ife.
Ndalama tilinazo nde osatidandaula ayi,,iwe udzingosilira basi
most welcome saheed oluwa shinaayomi, manoma is the only team in Malawi that can accommodate you because there is full of wise and intelligent people.
Nyelele zimandivesa kukoma
Iweso neba ugule wako anthu amuwone usamangotha zankamwa.
Conglatulations to Nomads futbol club 4 adng 1 more foreign plyr lk him 4rm Nigeria
Kkkkk
mayaz anoma prayer mmodzi sanga
menye yekha gemu mwava
Vuto kampopi fc wazolowera kutola dzianthu dzothawa nkhondo Ramadan Nikiza
Noma fireeee
kma amamenya malo ati
Tikuonjezela mafuta mu thank basi,,
ndalama ndiwanu super league ndi wa2
Zilibwino wina akhaula
Money talks noma 4ever
MAKAPE ABULLETS ALILA MXIEEEE! !!!
Wina alila, pena kumagula akunjawa, mwina nkupangako mbiri,, nanga kumangoti Mike Mvula wapita ku zimbabwe kukayesa mwayi,,
Ife phee kudikira kuzapha matchatnchu ndi maboko harram akewo neba!
nomore buying nomads we huv so many skillful players
bg up manoma………
Arent they scraps,do they have a name in nigeria -!?
shud I seh Money Money talks.. Chinekeo! Bullets jealousywoooo..
Nyelere morefire .Ngakhale maiko ena akumagula ma player kunja koma national team yao imachita bwino .sizotengela umphawi wako ndiye.Munayamba liti kugula zinthu kodi? Tili ndi anthu ochuluka bwanji kwathu kuno omwe ndiakunja ;Akulephela amenewo kuwadandaula mukadandaula olowa mwa chilungamo inunso mudzakhala olephela phaka kale.Bale akulephela malonda eti? Yambani ya Ganja kuti ziyende.
Nxt tym we will buy another one from EUROPE,kkkkkkkkkkkkkk manoma imadoda dada!!!
What’s wrong with u neba??chimtima ngati phwala pazilizonse?? shame on you MAULE!!
winanso ameo nde munyelaaaaa,mumva mpepo dis yr,nyeleleeeeeezooooo,asadawa ndi mmene tilili.
Sign more and more muone ngati ma players anu a local azimenya zoziwika, azipanga chikuwawe becoc their salaries ndizosiyana u will agree with me mutalephera kutenga league yet the team is full of stars
Sign more and more muone ngati ma players anu a local azimenya zoziwika, azipanga chikuwawe becoc their salaries ndizosiyana u will agree with me mutalephera kutenga league yet the team is full of stars
One more Boko Haram
Zikumuwawayo akagule ake ku Spain or ku England….koma MANOMA akuphula ku Nigeria
Ife tasankha kumeneko ndipo tikugula ncholinga..
Winawe udzazindikira za cholinga chathu titakubandula 4-0
MIGHTY BE FORWARD WANDERERS
THE WISE PEOPLES CHOICE!!
kodi amuule bwanj sanje bax mukadakhala inu.. ,, manoma woyeee! zosowa izii kumalawi kuno club kugula player wakunja….we r putn malawi soccer on a map bt t luks lyk pple dnt knw that especially u neba
Mwagula Kuti?
Anthu omvetsa chisoni ndithu……
deal z on…gam on simukuziziwaxo tisiilen mukhalira zomwezi Noma movin forwad beforwad ndiyokhayo basi amene zikumupweteka akaziphe
Enanu mukuyankhula za chingambwe bwanji maplayer athu ali ku moshko mutafuna makaka chaka chake ndi chino born as a noma suppoter die as a nyerere fun
Bola adzilandila money yofanana
Ngati ndi nsanje nde zikuvutani coz sitinati tikubweretsabe Ena..
Ndibwino kuyesayesa kusiyana nkungokhala…Cholinga nchoti team ichite bwino.
Iwe amene ukutiwe tikutaya nthawi ndi ndalama,,takagula ako pa Mozambique pompa ubweretse tikuonere
we have money that’s y we are able to buy from Nigeria
We need to boost our own players those pple r develop already. What waste of money.
Komanso anthu musadandaule za ndalama coz ndalama sizanu,,Ife tikudziwa komwe kuli ndalama…
Aliyense amene alinazo ali ndi ufulu kutero..
Tisiyeni tili ncholinga musalimbane nafe..
Zikumuwawayo akagule ake ku England or ku Spain,,koma Ife tikugula ku Nigeria
Kikiki mwaganiza bwanji bwana Ted Kamundi?
We are importing players because we want to achieve something and we will..dont forget the league has just kicked off
Don’t judge us ndi ma game 4 okha…
Nigeria yomwe ndimayiziwa ine osewela wabwino amapita ku Europe osat kumalawi kuno.
Manoma bwera ndikubeleke
Komatu asamale ndima terrorists aku Nigeria anzathu a Wandalaziwa. We want to safeguard our girls here paja timagulu taoti kuba ma beib ndi luso lawo. Vetting should be done.
Amwene kaduka sapindula
Akungowononga team zitsiru zimenezi mxiiii.Munya muwona chaka chake ndi chino 8pts clear.Dzichedwani ndiku oda Ma oga anuwooooooh.Adzikuphunzitsani ufiti wakwawoooo
Kkkkkkkkk uyooooooo!
Agift Chitedze
josey
Tiuzeni za signing fee yake,paja Bello mukuti ndi 8 mita?
Beware o4 boko harram …neighbour..ukukaishosha wekha.
Nkhani yabwino athunso maplayer amakamenya ku RSA ngakhalenso ku Zimbabwe
Sizinayambe lero zimenezi….Manoma ndi choncho
Tom Aidoo in my mind..
Team idzikhala ambitious!!
Just be ambitious but @ the end never achieve anything…………. Anything to smile about??
Deal yabwino
Zili ngati kugula malaya pakaunjika ma 4th hand koma osawavala ndeumangounjika kuchipinda unagula poti anatchipa ndeamangotha ndinjenjete too late what a waste of money .kma nyelele ndi nyerere bas nzeru zimathera kuuna who told u chakunja chilichonse ndi chabwino
Its not Waste of mony coz its not urs! Ngati ma puleya akunya samathandiza nde ndi ziko liti lomwe silimagula?? England izikagula whta abaut Manoma? Kuyamikila ndikwabwino athu ameneaja atiphunzisa mpila
manyaka wo mapuleya woti kwawo amasewera mu songani veterans kukanakhala kuti ku england akungolandira zilizonse bwenzi manyakawo sakanabwera uko bwezi achina wadabwa atapitanso
Pena tizitha kuyamikila,, kodi ntchito ya ndalama ndi chani?? Tisamangosalila pa chilichose
It’s the way to go south Africa imatenga ma player pa flames pano y not us kutengako akunja. malawi players will learn something from these guys hence improve the standard of play in our country.
Mpila muzauziwa liti a Malawi.ma south africa amagula kunowa amagula zinyatsi.chimenecho ndiye chamba muziuza makape osati ife (foseki)
Anoma sikuti mukugula ayi kma muli ngati bungwe la red cross lothandiza osowa nde inu zinyatsi zasowa mateam zikubwera kunoma redcross nde poti team yanoma sinayendeko kumayiko akunja amangowola eti mbiri . Manyaka amenewo angasinthe mpira, chasintha ndichani pa nakamura ,atsu ,bell zazii
Anoma sikuti mukugula ayi kma muli ngati bungwe la red cross lothandiza osowa nde inu zinyatsi zasowa mateam zikubwera kunoma redcross nde poti team yanoma sinayendeko kumayiko akunja amangowola eti mbiri . Manyaka amenewo angasinthe mpira, chasintha ndichani pa nakamura ,atsu ,bell zazii
ndalama ukuidandaulao yako? Suuzwa mpra………vomelezan bas kut maulee ma bigyyy
ndalama ukuidandaulao yako? Suuzwa mpra………vomelezan bas kut maulee ma bigyyy
Is good news 4me
He’s most wlcm
matimu ena sangathe kkkk NB singathe ,,,,,Nomah aphuzitseni mpira chaka ichi
Constitutionary clubs are given quotas to sign foreign players. So its not strange to have two, three foreign players that can of benefit to a team as well as our national league to conquer with Hestings Chimenya’ comment. However, there is a gteat need critically study such players to avoid regretting in the future for abandoning our good raw talents and deceived by the glittering gold.
matimu ena sangathe kkkk NB singathe ,,,,,Nomah aphuzitseni mpira chaka ichi
NB z dvlpng local players than wasting money 4 nothing.
Nomads Hv Vision This Season Matimu Tidzingophwanya
Muzingophwanya ndi ma draw??? Osazimvera chisoni bwanji??? Anzanu they didnt sign any foreign player but they are on top of the leageu….zimene mukupangazi ndi chimodzi modzi kumanyadira kut unakwatira nzungu koma ali osabala
Zakozimenezo Kkk
#Ted_kamundi Mukutichititsa Manyazi Ndi Umbuli Wanuwo Muziwonerako Mipila Yakunja Club Sikhala Ndima Player Adziko Lake Lokha, Tapangani Google Maplayer A #Tp_Mazembe Kapena #Arsenal Austin S Phiri
Kkk Tamusambisen Mmasoameneu
Its Useless to import more players from outside tsono athuwa ndie adzingokhala pa bench.vuto lina la wanderers ndi limene silimakhutira ndi maplayer amene ali nawo,they are failing to use the current players ndie adziwonjezeraso ena,mind u timu ikachuluka ma star siziyenda aliyese amadzimva,lets promote our own players for us to have agood national team that we all support,look at england all its national players are local!
kkkkk nde national team yakumalawi ndimahybrid
nde achina Gaba abwereko ku RSA…?
kkkkk nation team yake iti kkkkkkk bg up manoma ma local plyer kuchuluka mwanooooo alixiwe thabwa
Kkkkkk this game is so funny, let m b v referee….VIVA MANOMA ZIKUMUWAWA AKAPENTE PHIRI
Mr Muha sometimes it’s good to learn knew things from others we hv good players yes but they still lack kenakake which we can learn from these international players, that’s the way to go if football is to mprove in our country.
@Ernie The-deejay to say our own players don’t kno football is an insult to them. I hav watched this Nigerian guy Bello and to say the fact he is no different from our local players. Don’t tell me that they are here to teach our players how to play football. If that was de case, they would not hav come here to play but to coach. We hav talent, all we need is exposure and hav good agents that can negotiate deals for our players
@Ernie The-deejay to say our own players don’t kno football is an insult to them. I hav watched this Nigerian guy Bello and to say the fact he is no different from our local players. Don’t tell me that they are here to teach our players how to play football. If that was de case, they would not hav come here to play but to coach. We hav talent, all we need is exposure and hav good agents that can negotiate deals for our players
Hear me right Joseph am not saying malawi players gat not talent, we have that’s y we export but we still other talent from some other countries so we learn 3 or 2 things.
There’s nothing new we can learn from. As a matter of fact, they are here to learn football. If they were good enough to teach us football, they would hav gone to ply their trade in Europe
thats true mr man,they r not good players,for example look at wanderers where it stands on the tnm log table,had it been that they r good enough they would have gone at least to south africa!
if we talk of countries like spani, England even south Africa the have all the talent in there country but the still import players even from Africa y do u think the do that and y not malawi to import players my brother? the way i have seen Belo his a class of his own than our players though i haven’t seen Genk play.
Ok if that is the point,do they import those players to teach them football as you indicated in your previous comments?
Ok if that is the point,do they import those players to teach them football as you indicated in your previous comments?
Ok if that is the point,do they import those players to teach them football as you indicated in your previous comments?
Ok if that is the point,do they import those players to teach them football as you indicated in your previous comments?
Ok if that is the point,do they import those players to teach them football as you indicated in your previous comments?
Yes they all recruit players from all parts of the world. Even if you look at players that shine in EPL most of them not from England. But i hav never ever heard people in England saying those foreign players are there to teach local players football as u said in one of ur previous comment. For ur own information the FA came up with a policy that every team should hav a specific number of foreign players (quota) with an aim of safeguarding local talent.
Ine ndiwa B4ward basi
kod neba league yake yomweyi ya 9 milion ?
Zimayamba ndi ife manoma
welcome saheed
Muziwika bwanji pamene maplayer akunjawo mukungowamenye mu nsanamamu?????
Shinayoom dzinalo nde ngati Nakamula bola osanyikapo apa
i think is a good idea for sign lot of foreign players wanderers wld bcm very famous football club in other countries so i proud for those nigerians players
How will wanderes become famous in other countries?????
ok bro dats a good quest uknw wat if noma sign thos guyz every body in niger must 2 knw dat in malawi ther is a team known as noma dats why de team becm famous ihope u get me
Man Ted Thats A Stupid Question Do U Think A Player Can Sign For Another League Without His Home Football Asociation Knowing ? ! The Nigerians Know That There Is A Team Called Wanderers In Malawi Thats Why They Are Coming
Wakhoza khala pansi! Wina amene angayankhule ngende?
Wakhoza khala pansi! Wina amene angayankhule ngende?
Then u r implying that they don’t even know other clubs Wanderers competes with?
Then u r implying that they don’t even know other clubs Wanderers competes with?
The only way For a local club to be on the world map is to win super league & then participate in CAF. Not just buying players from dululu fc from nigeria
good news, tisamangoziwa kugulisa nafe tizigulako. in so duing tiziwika ziko lonse
How?
Pali ma reason ambiri: mwachisanzo ngati kwabwela osewela awiri payamba anabwela mozi kenako winanso wabwela ndekuti ku dziko lakwao aziwa kuti amalawi amakomda mpila
Pali ma reason ambiri: mwachisanzo ngati kwabwela osewela awiri payamba anabwela mozi kenako winanso wabwela ndekuti ku dziko lakwao aziwa kuti amalawi amakomda mpila
Otsatinamiza apa