All eyes on Nomads new Nigerian signing

Advertisement
Amos Bello

They have perhaps found a new haven  in Nigeria, and now Mighty Be Forward Wanderers have permanently signed another Nigerian by the name Saheed Oluwa Shinaayomi.

Amos Bello
Amos Bello to be joined by fellow Nigerian at Nomads.

The striker has been cleared by the Football Association of Malawi (FAM).

FAM’s International Transfer Matching System Manager, Casper Jangale, has since confirmed of the clearance.

Shinaayomi has been under the watchful eye of Shiba Football Academy.

The Nomads now have Japanese Genki Nakamura who is yet to play in competitive games due to delayed work permit procedures but Nigerian Amos Bello has already been key to the Lali Lubani side so far.

The Nigerian deals have been masterminded by Nigerian legend Jay Jay Okocha according to sources.

Advertisement

154 Comments

 1. kkkkkkkkkk congratulations neba. kunja mpaka? mukuitha but problem ndi yoti ma player mukugulao kukabwafu ndi nsulupi gunners aliko ambirimbiri moti amadya thabwa kusowa malo osaziwa ku noma aliko malo awo.koma osadanda ndi chikhalidwe cha2 a Malawi ndi zija zomati sindingakwatire wa chimizi ndagwira wa mtauni ukunena mayi opanga maganyu ochapa kapena ogulisa masamba mtauni osasamba komanso Osaoneka bhoo ndi zomwe akupanga a noma.kkkkkkkkkk umatha neba

 2. Omse othawa Boko Haramu in Nigeria bwerani ku noma akusungani bola mungonama kuti mumasewera mpira basi akutengani,Boko Haramu wecom to Nyerere team yamakape mxieeew! Kodi china chikungodwaladwala chija mumati (nagamura) kapena Jeke? mchani paja ine ndaiwala!

 3. Nomads are really killing malawian football,malawi has not even reached that stage of buying foreign players! instead of kufufuza ma player m’midzimu shame!!

  1. Amalawi amapita kunja kukasewela mpila bwanji? Kumeneko kulibe maplayer midzi mwao oti angasewele ? Kumanganiza , kodi amalawi mumadziyang,anila pasi bwanji? Mudzidziwa kuti ifenso amalawi tikhoza kungula ma player kunja ngati tilinazo zoyenelezazo

 4. Neba uli ndi vuto zampira zimakukanika bola uzikapitiliza kulima kampopi bas,inu ndalama mulibe player wakunja mumpatsa chani,adikire mukagulitse kaye fodya ndi lit limenero

 5. Anoma Simungakwanise Kugula Player Kunja Zosatheka! Akubwela Okha Osati Mudzitinamiza Kuti Mukuchita Kugula. Mumakanika Malawi Momwemuno Koma Kumalephela Nde Mungakwanise Wa Ku Nigeria? Akuthawa Boko Haalam Amenewo.

 6. ma player aku nigeria simukugula akungobwera pa free agent nde mukunama kuti mwagula ,simungakwanitse kugula mulibe ndalama zogulira ma player aku nigeria amagulitsa ma pounds osati ma dollars kapena makwacha

  1. Nkhawa njee ife manoma tili ndi ma player ambili Ena akumenya Ku nyasa bullets,osadanda nyelele woyeeee

 7. ma player aku nigeria simukugula akungobwera pa free agent nde mukunama kuti mwagula ,simungakwanitse kugula mulibe ndalama zogulira ma player aku nigeria amagulitsa ma pounds osati ma dollars kapena makwacha

 8. Congrats goes to the noma hierarchy for making it to another player signing. much to come from these guys. saheed oluwa shinaayoni most welcome. amos bello has the property of changing the game field structure.the striking force has an end point and you are the answer.genki hope you will feature agame soon.jafali chande welcome and we hope much to come from you guys. we hope to look forwad for the league lifting. ana tsogolani ife tibqwea mmbuyo a eni ake ulendo

 9. Kkkkkkkkk 9m yomwei mpaka ma player akuja iyi nde tmat misala

 10. Neba paja samatha kugula,,koma kutola ku Dzaleka Refugees

  Ingopita ukatole Ena koma zogulazi tisiyire Ife.

  Ndalama tilinazo nde osatidandaula ayi,,iwe udzingosilira basi

 11. most welcome saheed oluwa shinaayomi, manoma is the only team in Malawi that can accommodate you because there is full of wise and intelligent people.

 12. Wina alila, pena kumagula akunjawa, mwina nkupangako mbiri,, nanga kumangoti Mike Mvula wapita ku zimbabwe kukayesa mwayi,,

 13. Nyelere morefire .Ngakhale maiko ena akumagula ma player kunja koma national team yao imachita bwino .sizotengela umphawi wako ndiye.Munayamba liti kugula zinthu kodi? Tili ndi anthu ochuluka bwanji kwathu kuno omwe ndiakunja ;Akulephela amenewo kuwadandaula mukadandaula olowa mwa chilungamo inunso mudzakhala olephela phaka kale.Bale akulephela malonda eti? Yambani ya Ganja kuti ziyende.

 14. Sign more and more muone ngati ma players anu a local azimenya zoziwika, azipanga chikuwawe becoc their salaries ndizosiyana u will agree with me mutalephera kutenga league yet the team is full of stars

 15. Sign more and more muone ngati ma players anu a local azimenya zoziwika, azipanga chikuwawe becoc their salaries ndizosiyana u will agree with me mutalephera kutenga league yet the team is full of stars

 16. Zikumuwawayo akagule ake ku Spain or ku England….koma MANOMA akuphula ku Nigeria

  Ife tasankha kumeneko ndipo tikugula ncholinga..

  Winawe udzazindikira za cholinga chathu titakubandula 4-0

 17. kodi amuule bwanj sanje bax mukadakhala inu.. ,, manoma woyeee! zosowa izii kumalawi kuno club kugula player wakunja….we r putn malawi soccer on a map bt t luks lyk pple dnt knw that especially u neba

  1. deal z on…gam on simukuziziwaxo tisiilen mukhalira zomwezi Noma movin forwad beforwad ndiyokhayo basi amene zikumupweteka akaziphe

 18. Enanu mukuyankhula za chingambwe bwanji maplayer athu ali ku moshko mutafuna makaka chaka chake ndi chino born as a noma suppoter die as a nyerere fun

 19. Ngati ndi nsanje nde zikuvutani coz sitinati tikubweretsabe Ena..

  Ndibwino kuyesayesa kusiyana nkungokhala…Cholinga nchoti team ichite bwino.

  Iwe amene ukutiwe tikutaya nthawi ndi ndalama,,takagula ako pa Mozambique pompa ubweretse tikuonere

 20. Komanso anthu musadandaule za ndalama coz ndalama sizanu,,Ife tikudziwa komwe kuli ndalama…

  Aliyense amene alinazo ali ndi ufulu kutero..

  Tisiyeni tili ncholinga musalimbane nafe..

  Zikumuwawayo akagule ake ku England or ku Spain,,koma Ife tikugula ku Nigeria

 21. Kikiki mwaganiza bwanji bwana Ted Kamundi?

  We are importing players because we want to achieve something and we will..dont forget the league has just kicked off

  Don’t judge us ndi ma game 4 okha…

 22. Komatu asamale ndima terrorists aku Nigeria anzathu a Wandalaziwa. We want to safeguard our girls here paja timagulu taoti kuba ma beib ndi luso lawo. Vetting should be done.

  1. Akungowononga team zitsiru zimenezi mxiiii.Munya muwona chaka chake ndi chino 8pts clear.Dzichedwani ndiku oda Ma oga anuwooooooh.Adzikuphunzitsani ufiti wakwawoooo

 23. Zili ngati kugula malaya pakaunjika ma 4th hand koma osawavala ndeumangounjika kuchipinda unagula poti anatchipa ndeamangotha ndinjenjete too late what a waste of money .kma nyelele ndi nyerere bas nzeru zimathera kuuna who told u chakunja chilichonse ndi chabwino

  1. Its not Waste of mony coz its not urs! Ngati ma puleya akunya samathandiza nde ndi ziko liti lomwe silimagula?? England izikagula whta abaut Manoma? Kuyamikila ndikwabwino athu ameneaja atiphunzisa mpila

  2. manyaka wo mapuleya woti kwawo amasewera mu songani veterans kukanakhala kuti ku england akungolandira zilizonse bwenzi manyakawo sakanabwera uko bwezi achina wadabwa atapitanso

  3. It’s the way to go south Africa imatenga ma player pa flames pano y not us kutengako akunja. malawi players will learn something from these guys hence improve the standard of play in our country.

  4. Mpila muzauziwa liti a Malawi.ma south africa amagula kunowa amagula zinyatsi.chimenecho ndiye chamba muziuza makape osati ife (foseki)

  5. Anoma sikuti mukugula ayi kma muli ngati bungwe la red cross lothandiza osowa nde inu zinyatsi zasowa mateam zikubwera kunoma redcross nde poti team yanoma sinayendeko kumayiko akunja amangowola eti mbiri . Manyaka amenewo angasinthe mpira, chasintha ndichani pa nakamura ,atsu ,bell zazii

  6. Anoma sikuti mukugula ayi kma muli ngati bungwe la red cross lothandiza osowa nde inu zinyatsi zasowa mateam zikubwera kunoma redcross nde poti team yanoma sinayendeko kumayiko akunja amangowola eti mbiri . Manyaka amenewo angasinthe mpira, chasintha ndichani pa nakamura ,atsu ,bell zazii

 24. Constitutionary clubs are given quotas to sign foreign players. So its not strange to have two, three foreign players that can of benefit to a team as well as our national league to conquer with Hestings Chimenya’ comment. However, there is a gteat need critically study such players to avoid regretting in the future for abandoning our good raw talents and deceived by the glittering gold.

  1. Muzingophwanya ndi ma draw??? Osazimvera chisoni bwanji??? Anzanu they didnt sign any foreign player but they are on top of the leageu….zimene mukupangazi ndi chimodzi modzi kumanyadira kut unakwatira nzungu koma ali osabala

  2. #Ted_kamundi Mukutichititsa Manyazi Ndi Umbuli Wanuwo Muziwonerako Mipila Yakunja Club Sikhala Ndima Player Adziko Lake Lokha, Tapangani Google Maplayer A #Tp_Mazembe Kapena #Arsenal Austin S Phiri

 25. Its Useless to import more players from outside tsono athuwa ndie adzingokhala pa bench.vuto lina la wanderers ndi limene silimakhutira ndi maplayer amene ali nawo,they are failing to use the current players ndie adziwonjezeraso ena,mind u timu ikachuluka ma star siziyenda aliyese amadzimva,lets promote our own players for us to have agood national team that we all support,look at england all its national players are local!

  1. Mr Muha sometimes it’s good to learn knew things from others we hv good players yes but they still lack kenakake which we can learn from these international players, that’s the way to go if football is to mprove in our country.

  2. @Ernie The-deejay to say our own players don’t kno football is an insult to them. I hav watched this Nigerian guy Bello and to say the fact he is no different from our local players. Don’t tell me that they are here to teach our players how to play football. If that was de case, they would not hav come here to play but to coach. We hav talent, all we need is exposure and hav good agents that can negotiate deals for our players

  3. @Ernie The-deejay to say our own players don’t kno football is an insult to them. I hav watched this Nigerian guy Bello and to say the fact he is no different from our local players. Don’t tell me that they are here to teach our players how to play football. If that was de case, they would not hav come here to play but to coach. We hav talent, all we need is exposure and hav good agents that can negotiate deals for our players

  4. Hear me right Joseph am not saying malawi players gat not talent, we have that’s y we export but we still other talent from some other countries so we learn 3 or 2 things.

  5. There’s nothing new we can learn from. As a matter of fact, they are here to learn football. If they were good enough to teach us football, they would hav gone to ply their trade in Europe

  6. thats true mr man,they r not good players,for example look at wanderers where it stands on the tnm log table,had it been that they r good enough they would have gone at least to south africa!

  7. if we talk of countries like spani, England even south Africa the have all the talent in there country but the still import players even from Africa y do u think the do that and y not malawi to import players my brother? the way i have seen Belo his a class of his own than our players though i haven’t seen Genk play.

  8. Yes they all recruit players from all parts of the world. Even if you look at players that shine in EPL most of them not from England. But i hav never ever heard people in England saying those foreign players are there to teach local players football as u said in one of ur previous comment. For ur own information the FA came up with a policy that every team should hav a specific number of foreign players (quota) with an aim of safeguarding local talent.

  1. ok bro dats a good quest uknw wat if noma sign thos guyz every body in niger must 2 knw dat in malawi ther is a team known as noma dats why de team becm famous ihope u get me

  2. Man Ted Thats A Stupid Question Do U Think A Player Can Sign For Another League Without His Home Football Asociation Knowing ? ! The Nigerians Know That There Is A Team Called Wanderers In Malawi Thats Why They Are Coming

  3. The only way For a local club to be on the world map is to win super league & then participate in CAF. Not just buying players from dululu fc from nigeria

  1. Pali ma reason ambiri: mwachisanzo ngati kwabwela osewela awiri payamba anabwela mozi kenako winanso wabwela ndekuti ku dziko lakwao aziwa kuti amalawi amakomda mpila

  2. Pali ma reason ambiri: mwachisanzo ngati kwabwela osewela awiri payamba anabwela mozi kenako winanso wabwela ndekuti ku dziko lakwao aziwa kuti amalawi amakomda mpila

Comments are closed.