Civil society organizations (CSOs) in the country have advised President Peter Mutharika to strongly condemn death threats directed at the Chancellor College lecture, prof. Blessings Chinsinga.
In joint statement released on Thursday, March 24, the Centre for Human Rights and Rehabilitation (CHRR) and Centre for Development of People (CEDEP) say death threats against Chinsinga are not a laughing matter.
The lecture reportedly started receiving the threats after his presentation at the fourth stakeholders meeting that was organized by the Public Affairs Committee in the commercial city of Blantyre. He said there is a group of people who are planning to assassinate the lecture for being critical of the Mutharika government.
But the two CSOs have demanded assurance from the Mutharika administration on the protection of members of opposition, civil societies, journalists and all politicians in the country
Utsogoleri ndi mphatso yochokera kwa Mulungu.Sudandaula ngati ena anzeru akudzudzula pazina zolakwika koma utakhala kuti utsogoleriwo udachoka mphamvu ya satana umangotangwanika ndi zolankhula za ena mmalo moyendetsa utsogoleriwo mapeto ake zotsatira zake zimakhala ngati tikuzionazi.
Prof Chisinga & other political analysts are not evil they are advisers who help the driver of the country to access & see his car if it has a fault or not; If it has a fault Prof Chlsinga & others can always help him correct the fault thru their political knowledge;Those who criticise the government are the ones who wish the President well- they are not enemies; Enemies of the President should be his own personal advisers- they lie to him to keep their jobs;
exactly!
Barking up to a wrong tree!
ukati utchuke mkulakhula umakumana nazo ndiye kumalakhula mukudziwa kuti mulindiphamvu
Iye alindimwai kut some1 has warn u,but others lik dick matenje,aron gadama thy had no opportunity to be tould about their death.so plz speark lik aman
Iye alindimwai kut some1 has warn u,but others lik dick matenje,aron gadama thy had no opportunity to be tould about their death.so plz speark lik aman
Mesa polankhula umalankhula wekha zopanda ncherezo ndie uziteteza wekha
He will condamn after you your death! kkk
Chinsinganso ndi ndani pa Nyasa pano?Politics is a dirty game,iye akusiya zaulecture zakezo kufuna kuoneka dolo pankhani zandale,lero washosha mavu,alimbe nazo yekha,a State President palibe chikuwakhuza.Chinsinga adani ake akuyenera kuthana nawo yekha.
Ku CHANCO kuli ma professor ambiri amene amayankhula pachinachake chokhuza mbali yawo chikachitika,ndiye professor Chisinga ngati wayankhula zabwino akuopa chani? Apa zikuonetseratu kuti ndiye kuti wayankhula zobweretsa udani pakati pa anthu,therefore akuyenera kulandira ziopsezo ngati zimenezo.Remember Blacks Song #MULOMOWU#
Chanco was closed because of the same person in 2011
Leave him chisinga amalaknhula maganizo ake
Following
Ukaziputa limba akulu anatero. RIP in advance!
ku chanco kuli anthu ambili omwe amayankhulapo pa nkhani zokhudza dziko lino.Ndichifukwa chani akuopsezedwa yekha ngati zili zoona?
Ziwanda zoyipa zamathanyula
What about threats from prophets?
At the beging, I was trusting Olemekezeka a Chinsinga komano kungoyambira nthawi yakampeni 2014, I lost my trust on him. Anayamba kukomenta zokondela Mcp mbali inayi akumanyoza Peter Mtharika ndi Alomwe kuti ndiomwe anamuvotela. Panopa Olemekezeka J Kabwila nawonso akamanena za President akumanyozanso Alhomwe kuti President ndi Ovoteledwa ndi alhomwe osati aMalawi. Ndiye anthu awiliwa ndikudabwa kuti koma Mcpyi ndi chipani cha aChewa kapena aMalawi? 2, kodi Alhomwe si aMalawi? Koma Alhomwe akuwanyozawa azawafuna Alhomwe 2019? 3, kodi kunyoza Alhomwe chieukwa President ndi Mlomwenso sikugawanisa anthu mziko muno?
HOW SPECIAL IS HE ?IS HE AFRAID OF DEATH?AFTER ALL IT’S ONLY ONE FROM MANY LECTURERS YOU WILL NOT BE MISSED BY US WHO LOST PARENTS LONG TIME AGO
Ndimandana ndi anthu olankhula zobweretsa zisokonezo m’dziko!!! Panopa uli pa survival of fittest, uziteteza wekha , yamba kuthamanga, ukamva kulira kwa mfuti ndiye kuti siyako koma ukamva ziiiii pa thupipo mziwilatu .
Mufuna kuyamba kupha chifukwa akudzudzulani? Iphani Chinsingayo koma mwazi wake ukhala pa inuyo.Kodi mwayiwala kuti pamene mulipo pampandopo adakuikani ndi anthu? Ndiye poti paja mudachita kubera mavoti ndiyealiyense odzudzula dpp amaphedwa.
He must not only condemn but must also make sure
Litle boy chinsinga always trying to put himself at ahigher level kkk
Kupha sikusova vuto mukufuna muyipise president awonanaye chochita yekha osat kupangila
zayambika pamene ena anagwidwa kamba komakambirana zokhudza kulanda boma pa Whatsapp anthu munadzudzula boma kuti silienela kugwilitsa ntchito zokambirana za mma phone nanga amenewa chiopyezo akumalandila kuesela mu njira yanji? kodi chifukwa awa ndi lecturer ndiye zigwitsidwe ntchito?
It’s a matter of you yourself being part of the solution to Malawi’s economic problems rather than ask one to condemn threats. How do you expect someone to adress an issue which you you are part of? Hangup your Ties & Executive suites for work suites & get to work cos today’s world needs Technicians. White collar are a burden.
No point omar…
you still need the white collar man
Bele, Malawi just has too many than we need & can afford to maintain. It’s the worksuite that we need @ 99% to build everything even the the economy itself & just a handful of the white collar to do the paper work.
Typing comment,,,,,,..,..,,,,,,.
malawians whats your problem? Kupha otsutsanananu? Stupid if u kill Chinsinga know that there is some 1 greater than u he’s there 2 protect him n other opposition leaders so beware of ur dirty mouth
malawians whats your problem? Kupha otsutsanananu? Stupid if u kill Chinsinga know that there is some 1 greater than u he’s there 2 protect him n other opposition leaders so beware of ur dirty mouth
amayankhula motumbwa
hw special is that guy kuti mpaka president apange condemn
hw special is that guy kuti mpaka president apange condemn
Kodi anthu samafaaa abale eee chisinga.
Eee chinga
Lilipo ziko la anthu osafaaaa
Kodi anthu samafaaa abale eee chisinga.
Eee chinga
Lilipo ziko la anthu osafaaaa
kikeest
kikeest
Simakoswe anthu enawa ngati mumava a DPP ndi Dziko ili
Simakoswe anthu enawa ngati mumava a DPP ndi Dziko ili
Simakoswe anthu enawa ngati mumava a DPP ndi Dziko ili
Simakoswe anthu enawa ngati mumava a DPP ndi Dziko ili
Kkkkkk so the demand now is for the president just to “condemn” the threats! Havent you heard that actions speak louder than words? In other words, actions are more stronger than words? I wish the CSOs put much pressure on police and not on the president to act swiftly the way they pressured the police on mzuzu violence saga
Kkkkkk so the demand now is for the president just to “condemn” the threats! Havent you heard that actions speak louder than words? In other words, actions are more stronger than words? I wish the CSOs put much pressure on police and not on the president to act swiftly the way they pressured the police on mzuzu violence saga
Akazitenga ngati dolo asowe basi, angazadelere ma big kkkkkkkkkkkkkkk
Akazitenga ngati dolo asowe basi, angazadelere ma big kkkkkkkkkkkkkkk
3
Any event happens in Malawi is always attached to Politics. Why?
Any event happens in Malawi is always attached to Politics. Why?
3
K k k k kkkkkkk malawi, the warm heart of africa.Iiiii koma zinazi monga mulinandalama kuti mulimbana dollar koma mukanda chebe
K k k k kkkkkkk malawi, the warm heart of africa.Iiiii koma zinazi monga mulinandalama kuti mulimbana dollar koma mukanda chebe
AChinsinga tangoyambani ndale osamangolalata kunja
How does Mutharika come in?
How does Mutharika come in?
Being a president means a father 4 everyone, ndie ngati mukufuna kupha means usogoleri wanu ngwakupha, mwinanso mukumapha ma albino aja ndi inu bt jst bcoz u r a ruler its lyk u r on a hide-out, mavuto ali mziko muno chitsilu china whom pipo called a ruler nkumapanga target zofuna kupha!!? wat a ruthless leader, shame on malawi my home land, we will meet 2019…
Being a president means a father 4 everyone, ndie ngati mukufuna kupha means usogoleri wanu ngwakupha, mwinanso mukumapha ma albino aja ndi inu bt jst bcoz u r a ruler its lyk u r on a hide-out, mavuto ali mziko muno chitsilu china whom pipo called a ruler nkumapanga target zofuna kupha!!? wat a ruthless leader, shame on malawi my home land, we will meet 2019…
Good writer!
Kodi inu anthu and ale paliponse mwakala mumangoganiza zakupa basis
Kodi inu anthu and ale paliponse mwakala mumangoganiza zakupa basis
Govt must at forefront protecting the citizens. Freedom of speech isnt excercised in our country. How can pipo like Jappie Mhango apraise death threats. This in logical with democracy we got. Chinsinga deserves an apology if Govt is to build betters politics in youth his lectures. Killing pipo must come to an end.
ndiye zachamba zimenezo!
him shld be killed ana amwano more over our population now is reaching 17million. kumwalira iyeyo sitingadandaule
Just as your disappearance could be immaterial
Just as your disappearance could be immaterial
really man
really man
Kkkkkkkkk artificial way of controlling population?
Kkkkkkkkk artificial way of controlling population?
Seriously????
Seriously????
Vondo? Eeeeish an evil person!
[READ MY STORY. ON HOW I GOT MY HIV CURED].
Truthfully, i was tested HIV + positive for the past 8 years. I keep on managing the drugs i usually purchase from the health care agency to keep me healthy and strengthen, i tried all i can to make this disease leave me alone, but unfortunately, it keep on eating up my life. So last Two Months i came in contact with a lively article on the internet on how this Powerful Herb Healer get her well and healed. So as a patient i knew this will took my life one day, and i need to live with other friends and relatives too. So i copied out the Dr Collins the herbal healer’s contact and I contacted him immediately, in a little while he mail me back that i was welcome to his Herbal Home whereby all what i seek for are granted. I was please at that time. And i continue with him, he took some few details from me and told me that he shall get back to me as soon as he is through with my work. I was very happy as heard that from him, as i was just coming from my friends house, Dr Collins called me to go for checkup in the hospital and see his marvelous work that it is now HIV negative, i was very glad to hear that from him, so quickly rush down to the nearest hospital to found out, only to hear from my hospital doctor called Browning Lewis that i am now HIV NEGATIVE. I jump up at him with the a test note, he ask me how does it happen and i reside to him all i went through with Dr Collins. I am now glad, so i am a gentle type of person that need to share this testimonies to everyone who seek for healing, because once you get calm and quiet, so the disease get to finish your life off. So i will advice you contact him today for your healing at the above details: Email ID: [email protected] or you can also add him up on whataspp +2349036950737. CONTACT HIM NOW TO SAVE YOUR LIFE AND DOCTOR ALSO CURE ALL KIND OF DISEASE AND SICKNESS: [email protected] AS HE IS SO POWERFUL AND HELPFUL TO ALL THAT HAVE THIS SICKNESS.
Fuck dat shit
ku shosha vumbwe kulinga ulind nkhuku ukaziputa limba
U cso why
Stupid politics if you killed him what will you benefit?Remember,this life is not ours,our God is watching you.
akayankhulanso walakwa
Osamalankhula ngati pamalawi pano mulipo nokha mzeru mwamva
Chinsinga wataninso? Treason? Anzao ankati Chinsinga akanena zosawakomera, amamuuza Mbowela waku Mzuni anene zowakomera, basi!
shit politics in malawi
Amalawi simumasekelera akamavutika president lero mukufuna thandizo lake musiyeni akafuna anenapo kanthu osati kumuwumiliza paja alibe problem musayiwale kkk
Bt y?
Agree with concerns komanso akulu awa nawo ali ndi vuto lomangofuna kumveka mmanyuzi. Nthawi yake inali ya Academic Fredom ija otherwise pano angobwebweta zachizombazomba eh ngati malemu Davis Kapito.