Chakwera is Yudas Iscariot – John Kapito

Lazarus Chakwera
Lazarus Chakwera
Judas Iscariot Chakwera

Outspoken Human rights activist John Kapito has said opposition leader Lazarus Chakwera is a Judas Iscariot who, together with President Peter Mutharika, has betrayed Malawians.

Kapito, irked by Chakwera’s gluttonous decision to accept a hefty salary hike for his role as leader of opposition, was speaking during the commemoration of World Consumers Day in Blantyre on Thursday

“We are simply saying that Judas Iscariot was the one that sold Jesus Christ today, in the Mountain of Gethsemane. Mr. Chakwera himself has sold us because we gave him trust as the one of the people that can stand for us. When you are leader of opposition, means to be standing with the people that are being oppressed and his job was not to fight for himself; to say that because I lost an election, therefore I am going to make sure that I oppress the people.

He was supposed to be in parliament and start speaking on our behalf, and start defending us. But see what Lazarus Chakwera is doing in Parliament- he has sold us. Because once he was given a big Prado and a big salary, then he was given two body guards, he started behaving as King Herod”.

The activists who had once likened himself to a dog that only barks to scare off enemy also called President Mutharika a Pontius Pirate.

 

Advertisement

218 Comments

 1. I used to respect Kapito but now I think we need the youth who will know how to respect our country by using the words which will unite us.

 2. Chakwela is so stupit thas why he lost 2014 ellection ,reall man of God sangasiye ubusa nkulowa politics.which means ubusa wake ngwachinyengo

 3. Pls mukamakomenta. muziyamba mwaganiza nonse amene mukunyoza a Chakwera ndinu masipuni amnyumba simudziuwa kumene kumachoka ndalama achakwera akukuthandizani kuti zinthu zisaonongeke mopirira muyeso mukadakhala azeru mudakamapempha a Peter achepese kugwirisa ntchito ndalama ngati zabanja ndiza Boma mukugonera phala la mpunga mkumayamika munthu okuzuzani musiyeni m’busa ndiyekhayo amadziwa kudyesa nkhosa zake akuziwa kumene azapite ndi nkhosa xake mkukapeza msipu obiliwira,amene muwayamikirao alibe plan yotsogolera amalawi koma plan yamoyo wawo bcz sakudziwa komwe Malawi wachoka,angobwera kuno mkumazadya ma 10% adonation amaiko ena po a Chakwera akuziwa mavuto adziko lanthu

 4. Mr Kapito you are chairman of Blantyer water board & President Peter Mtharika gave you that job so you cant save two masters- you are saving the DPP which is feeding your family; If you talk bad of DPP you will loose your job- they have silenced you with a big sikono in your mouth; Pliz leave Chakwera alone he needs that money to run the new MCP; Ife tikudziwa kuti akuwuzani kuti akuchotsani ntchito mukanena zabwino za MCP ndi Chakwera; Mukuwopa kubwerera ku Area 25 Nyambadwe ikukoma?

 5. Kapito Tseka Pachimbuzi Pako Nsanga. Watopa Ndikukanda Konyelera Eeeti

 6. shame on chakwera he just think on himself ya a it’s indeed end time

 7. My focus z on L.Chakwer, my fell friends just read Proverbs 16v25 den scrutise it wel. Chakwer indeed he z Judas Iscariot

 8. Ukamati “he has sold us” ukuphatikiza iweyo, akazi ako ndi ana eit, coz enafa zot tinagulitsidwa tikukanatu..

 9. Anthu amene mukupeleka ma comment anu pano mukuchita kuonetseratu kuti zinthu simumazitsata bwino bwino,choipa ndichani kupanga za utsogoleri wadziko yet munthuwe ndi m’busa,kodi simunamve kuti David analinso mfumu yet mbali inai amapanganso zamulungu,Solomoni bwanji,nanga Yosefe ku Egypt kuja u minister wa agriculture anapatsidwa uja munamva ndani kuti kwamulungu kuli unduna wazamalimidwe,ineyo ndine msilamu koma Chakwera kukhala m’busa on the other hand mkumafunanso kutsoholera dziko pamenepo ndilibe napo pulobulemu coz choti mudziwe ndichakuti Chakwera ngakhale sakupanga za ubusa koma mmutu ndi mumtima mwake kuopsa kwa mulungu akukudziwa ndipo azayenda munjira imeneyo

  1. Che siffah, inu ndi mzilamu simungatsate Bible bwino coz u dont bliv in it. Listen, wanena kuti David mu Bible anali king at the same tym was serving God. Nanga pamenepa David anachita kusiya chimodzi ngati? David was doing thez 2 things at once unlike chakwera who has completely dropped serving God. Understand issues. Don’t understand tissues.

 10. Uyudas Upose Wakowo U Chair Wakumadziwo Ungoona Ngati Wamaliza Masamu Onse Unya Uwona Chibanzi Akudyetsacho Iwe Ubweza Cake Uwonasa Musiyeni Chakwera Kodi Anthu Sasiya Ubusa Oyamba Ndi Chakwerayu Za Ziiii Basi enenu Ufiti Uli Thooooo Koma Yet Ndinu Bishop Nde Bolanso Chakwera Olo Mutanyoza Bwanji Ine Nganganga Pambuyo Pa Chakwera Kupindika Nkhope Ndi Mtima Womwe Simwayi Sukulu Bwezi Muli Ndani Achikhala Kamuzu Sanayambitse Mamphunziro Pa Malawi Pano

 11. Uyudas Upose Wakowo U Chair Wakumadziwo Ungoona Ngati Wamaliza Masamu Onse Unya Uwona Chibanzi Akudyetsacho Iwe Ubweza Cake Uwonasa Musiyeni Chakwera Kodi Anthu Sasiya Ubusa Oyamba Ndi Chakwerayu Za Ziiii Basi enenu Ufiti Uli Thooooo Koma Yet Ndinu Bishop Nde Bolanso Chakwera Olo Mutanyoza Bwanji Ine Nganganga Pambuyo Pa Chakwera Kupindika Nkhope Ndi Mtima Womwe Simwayi Sukulu Bwezi Muli Ndani Achikhala Kamuzu Sanayambitse Mamphunziro Pa Malawi Pano

 12. Inu #yehova ndi wa mkulu. Tsogolo la aliyense mumalidziwa ndi inu, a Chakwera kusiya utumiki wanu mkuyamba moyo wa dxiko lapansi, xifukwa xawo mumaxidxiwa ndi inu. Ndipo xonsexi tiloleni xikhale mmanja mwanu. Titha kutukwanana apa mpaka tikalowa naxo ku Gahena.

 13. Inu #yehova ndi wa mkulu. Tsogolo la aliyense mumalidziwa ndi inu, a Chakwera kusiya utumiki wanu mkuyamba moyo wa dxiko lapansi, xifukwa xawo mumaxidxiwa ndi inu. Ndipo xonsexi tiloleni xikhale mmanja mwanu. Titha kutukwanana apa mpaka tikalowa naxo ku Gahena.

 14. KAPITO ndiye mbalaso ya munthu ndipo ndiwa Satanic ananyamulisa anthu Manyi ku BT kuti akapange zioneselo ku Water Board last minute kuwauza anthu kuti basi akasiye Manyiwo zioneselo zalepheleka

 15. KAPITO ndiye mbalaso ya munthu ndipo ndiwa Satanic ananyamulisa anthu Manyi ku BT kuti akapange zioneselo ku Water Board last minute kuwauza anthu kuti basi akasiye Manyiwo zioneselo zalepheleka

 16. Kapito shouldn’t forget the words he has scattered to maiawians across the country because will be used as a reference nex time

  1. Zikanakhala Choncho Bwenzi Ndale Kulibe Poti Tose Timapemphera Kumaso Timapanga Zandale.Even APM Himself Ali Ndimpingo Wake Womwe Amapempheramo.Munthu Kusiya Ubusa Sikutiwasiya Kupemphera Iyayi Akuluakulu.Ndiye Ngati Zandale Ndiza Anthu Achikunja Ndiye Bwanj Presedent Amapita Kuchalichi.INE WA UDF

 17. Simaudindo oonse amene amasankhidwa dziko lapansi omwe amasankhidwa ndi mulungu, ndipo matsiku otsiliza anthu ambiri azaoneka ngati atumidwa ndi mulungu pomwe ndi afisi olusa, ngakhale satana amazionesa ngati m ngelo wakuunika,

 18. Akapito inu!!!
  Mwamaliza kudya tindalama tija adakupatsa a dpp ndicholinga choti tisachite zionetserozi lero mwayambiranso kulankhula zosamveka shame on u devil.
  U must be the Judas Iscariot urself not munthu amene ukumunenayo.
  Ukayenda siya phazi poti mulomo uzakutsata. Munthu opusa komanso wadyera ngati iwe sindinamuone.
  We demand apology

 19. ngati ndinudi akapito mwanena zimenezi,zangowonetselatu kuti inu ndi Baibulo ndi apongozi.kiyambila kale kunali ma judges,mafumu(David:Solomoni),aneneli…anthu onsewa amasankha ndi mulungu kuti akamugwilire ntchito zake ngati kusamala nkhosa..Dr Lazarus Chakwera ndiwosankhidwa wa mulungu kuti asamele nkhosa zake ndipo akungodikila nthawi yake yoikidwilatu ngati David kudikila Sauli..Chakwera ndiye Davideyo pomwe Arthur ndiye Sauli,,,watchout your toung,ana a Miracle money inu osafuna kugwira ntchito but just waiting for a miracle.

 20. Kapito usandilakwitse tawona chala chomwe ukulozera chakwera zina zinayi zikuloza iweyo kutanthauza kuti zomwenena chakwera ndi president ukuzinena wekha

 21. Kapito is an educated fool. Zoona vuto akuliwona ndikumakanena Chakwera? An educated man being used like a condom like this? God forbid! Should I say his eyes are blind enough that he cannot see clearly? What has become of this fool? Old age or greedy?

 22. Atangolandila galimoto la ntengo wapatali ChAkwela stopped opposing hard and constructively as before. Munthu uyu has shown that he can easily be bought,unlike Tembo who was a strong Opposition Leader. He has betrayed us indeed hence his beeing Iscariot

  1. kuyankhula kwake mmafuna mtaona atavula? nanga ayankhule motani? zanjala amene wayankhula kwambiri nda? who sumon peter to go to pariament? pena pske kumazitsatatu zinthuzi dnt jst comment any how

 23. Kapito Saziwa Kuyamikira Koma Kuipisa,kufuna Ndalama Kt Amuseke Pakamwa,amatero Akaona Kt Ndalama Adapasidwa Wanyambita Zatha Ndi Pomwe Amabwebwetukanso Cholinga Ampase Zina,kumangotipaka Phula Mmaso Basi,iii Kaya!

 24. Iwe Kapito chikusankhire u board chair waku Southren Region Water Board sukumveka mkomwe.Iwe nde Kanyimbi weniweni munthu oipitsitsa kuposa anthu ukuwatchulawo.Chimanga chimakwera chomchija iwe uli kuti? Munthu unawukhwimira udindo wokhala wamkulu wa CAMA,palibe chamzeru chomwe ukuchita koma ma consumer mitima yawo ili ziiii,chifukwa chani?Iwenso ndikofunika anthu akupangire ma demonstrations uchoke.Yudasi weniweni ndiwe munthu okonda ndalama iwe.

 25. Mr Kapito of cama. Mwayankhulaso. Kapito what have you achieved so far as director of cama? We are being sikined alive while you are there watching. Take out the log in your eyes first.The govt and companies have connived to make our lives miserable but you our ‘watch dog’ are sound asleep. Change, kapito, change. And it’s also time to change the the directorship, or are you for life?

 26. Mr Kapito of cama. Mwayankhulaso. Kodi a kapito cikhalileni mu cama ndi ciani cimene munakwanilitsapo. Anthu tavutika zaka zonsezi inu muli pomwepo osacitapo kanthu lero ndiye mukanene amzanu. Cotsani citsotso canu poyamba. Tabeledwa poyela-yela ndi boma komaso makampani, koma inu amene mumati ndinu watch dog muli mtulo tofa nato. Kodi mpando wa cama ndiwosasinthana, wa for life? A Kapito mwalephela.

 27. [READ MY STORY. ON HOW I GOT MY HIV CURED].
  Truthfully, i was tested HIV + positive for the past 8 years. I keep on managing the drugs i usually purchase from the health care agency to keep me healthy and strengthen, i tried all i can to make this disease leave me alone, but unfortunately, it keep on eating up my life. So last Two Months i came in contact with a lively article on the internet on how this Powerful Herb Healer get her well and healed. So as a patient i knew this will took my life one day, and i need to live with other friends and relatives too. So i copied out the Dr Collins the herbal healer’s contact and I contacted him immediately, in a little while he mail me back that i was welcome to his Herbal Home whereby all what i seek for are granted. I was please at that time. And i continue with him, he took some few details from me and told me that he shall get back to me as soon as he is through with my work. I was very happy as heard that from him, as i was just coming from my friends house, Dr Collins called me to go for checkup in the hospital and see his marvelous work that it is now HIV negative, i was very glad to hear that from him, so quickly rush down to the nearest hospital to found out, only to hear from my hospital doctor called Browning Lewis that i am now HIV NEGATIVE. I jump up at him with the a test note, he ask me how does it happen and i reside to him all i went through with Dr Collins. I am now glad, so i am a gentle type of person that need to share this testimonies to everyone who seek for healing, because once you get calm and quiet, so the disease get to finish your life off. So i will advice you contact him today for your healing at the above details: Email ID: [email protected] or you can also add him up on whataspp +2349036950737. CONTACT HIM NOW TO SAVE YOUR LIFE AND DOCTOR ALSO CURE ALL KIND OF DISEASE AND SICKNESS: [email protected] AS HE IS SO POWERFUL AND HELPFUL TO ALL THAT HAVE THIS SICKNESS.

 28. tired of u mr kapito. … mumatero mukasowa bread .. mukapeza bread okwana inu nd abale anu mumatithawa …. nickname urself b4 us consumers. ..

 29. kapito we r tired of uu … umafuna uzitinamiza bread akatha pakhomo pako .. sungapeze njira ina yopemphera bread Kodi. .. ukapeza bread okwana iwe nd abale ako umatithawa ….

  1. Chongofunika yudasiyu apite akamufunse Tembo kuti after election amatani. Akaphunzila zambili tikagonja timavomeleza koma munthu sungalile mpaka 2019

 30. chakela z some hw gd dan u kapito muli nd ntma oyipisa azanu kt inu mkale abwno whle palibe ndchmodz chabwno mwapangapo bt pakamwa kuwola ndkuyipisa mayina aazanu

 31. Akapito mwati Achakwera ndindani kkk YUDASI komadi ndizoona Iscariot weniweni uyu driver wa mcp Yudasi chakwera kkk koma kapito umadzitsata hawu! Yudas Lazaras iscariot chakwera kadzina kabwino achewa sazabvutika kuchonga 2019. Dzina lapelekedwanso nthawi ya easter

  1. uli kuti chakwera ANALI munthu wamulungu osati pano mmutu mumayenda ndale zokhazokha ndingapange chani to be apresident bas baibulo analisiya kalekale mumutu mumayenda zaupandu bas chifukwa ndendale mwamva aunt Jude msanamizidwe

  2. kunyoza munthu wamulungu? iwe #judith ukuona ngati palinso za umulungu apa, kuteroko iwe umamutenga ngati ngelo ameneyi mbava yachabe chabe ngati imeneyi, ameneyi kadzinako kali bhooo kakumukhala ndithu

  3. Mukutukwana Ife tikayamba a police atimange poti wanuyo payenkha ndi game kale. God forgive you. Zoti achewa achewa sibwino ndifedi koma sibwino! Akapito akhala mulungu oweruza anzawo. Nanga zoti wina kapito akuti ndi Pilato tikuti bwa?

  4. Mukutukwana Ife tikayamba a police atimange poti wanuyo payenkha ndi game kale. God forgive you. Zoti achewa achewa sibwino ndifedi koma sibwino! Akapito akhala mulungu oweruza anzawo. Nanga zoti wina kapito akuti ndi Pilato tikuti bwa?

  5. why are you against my tribe ‘chewa’? ndie kt udziwe kut mchewa kudambwe amatani imva izi ,panyapako kukamwa ngati pamnyelo,muuzane alomwe nonse panyapanu musiye kuphatikiza ndale ndi mtundu komaso uphuzire kulemekeza chikhalidwe cha amzako

  6. Ndimadziwa ine ntchito yakudambwe ndiimeneyo mmati yudasi amakhuphunzitsani kutukwanako anthu onyamula zigoba,ziguduli inu Wathu

 32. Nayeso Kapito amatiniza kuti ndiomenyela ufulu, ufulu wake uti omwe akumenyela poti akawatseka chindasi mkamwa amakhala chete galu uyu

  1. Yudas Lazaras escaliot chakwela tamusintha ameneyi ndimbava yamunthu angathawe ubusa kufuna cash. zambale zimachepa tamulandila ameneyi ndipo azabwelelanso kuzimu after 2019

 33. Zomwe Ndikuziwa Ine Ndi Zoti Mdziko Muno Muli, #balaba Ndiye Ndamvaso Za #yudasi Ndiye Kulixo Mkulu Osaimva Wazikwanje Ku Mpotoku Koma Ndi M’busa Akumutcha #simon_petulo Mainawa Akupitililabe

 34. Inuyo akapito tinkaganiza kut ndinu anzelu kale paja koma mmm musatipake matope mumaso , inuyo ndi peter zikusiyana pati. Mukumabisala mutu okha kusiya musana pantunda .

  1. Musatinamize apa kapito anali kukuwa kuwa kale paja ankati zinthu sizikuyenda bwino nanga lelo alikut ? Zinthu m ‘mne zikuwonongekela panopa we expected him 2 rise again koma mmm zomwe ankaukila kale paja sankaziziwa. Kudana ndichilungamo kuwopa kumanidwa mafupa what a shame malawi

 35. Akapito munalikuti mmene mitengo yachimanga inapengamu inu osayankhula kanthu,kodi chifukwa cha u board chair wa southern water board anakusankhani wu?kayankhulani zanzeru.

  1. Achisale be careful ngati simudziwa mau a mulungu u better shut up yr mouth otherwise God wil whip u tear u into peaces.

 36. Mmmm! ths language z too bad for someone to say, if someone like me say like what kapito has said utha kumangidwa ndithu,

Comments are closed.