A five year-old girl is missing after a group of 10 other Malawians she was travelling with were attacked by a hippopotamus in Limpopo River as they tried to cross into South Africa using an illegal entry point two weeks ago.
The Herald of Zimbabwe reported on Monday that some of the Malawians sustained minor injuries in the attack.
The paper quoted Limpopo Police Spokesperson, Colonel Ronel Otto, who said the girl and her mother were part of a group of 11 Malawians who wanted to enter South Africa illegally near Beitbridge border post on New Year’s Eve.
“Along the way they were chased by a hippopotamus and some sustained minor injuries. They ran away in all directions and since then the five-year-old girl went missing.
“Despite extended searches nothing has been found yet. Members of the South African Police Search and Rescue Unit as well as the Air Wing intensified search operations during the weekend,” Otto said.
The mother of the girl is said to have reported the matter to police after she tried to look for her without success for a week.
Malawians and other nationalities face a lot of problems when crossing Limpopo River. Some are attacked by hippos and crocodiles while others drown or are attacked by criminals who pretend to help them to enter South Africa illegally but instead rob, rape, or kill them on the way.
Citizens from Zimbabwe, Mozambique, Zambia and Malawi flock to the rainbow nation to look for greener pastures and there are thousands of them staying in South Africa illegally.
Meanwhile, the South African government has stopped deporting illegal immigrants from Malawi but it is still arresting them.
Too bad. R.I.P
kukhalabkumlawitu ndikulimba mtima kufikazaka 15 ndekuti wakalamba tsikuntsiku ndimavuto kumalawi .kulibe chokomera onse ungalozeko kuwerenga news ku back page umva kuti team yathu yathibulidwa ukalowa nkati umva kuti wankhonya wathu waziwona kuzambia,othamanga wathu wakhala bambala 115 palibe chabwinotu kukhala kumalawo ,moti kukhala m’malawi nkulimba.fodya yemweyi timatenga nthawi kumulima kuthilila kunazale nkumchotsakumpititsa m’munda , akamagulatu amangogula ngati ndimango omwe tangotchola patchile kapena gwana okhala ndimphutsi nkati .kumalowa munda wampunga mulimatope zinthu kukuluma m’menemo kukhala kumalawitu nkulimba mtima.musamangotiwona tikusekereka mumtimamu mulinkhawa zambili ,tikamakuwemvani sindekuti zinthu zilibwino .tinangozolowera kumayankha kuti tilibwino koma mavuto atifupikitsa awa.KUKHALA MMALAWI NKULUMA MTIMA.usiku ukagona zomwe umamva ndiwinzulo tikayikeso wina kumanda .zomwe umawona kukacha ndiwanthu alipachigulu kuthamangila kuchipatala ,nkhani zakuchipatalakoso akuti mochale yawonongeka kapena mankhwala kulibe .KUMWALILA NDIZAKA 21 ndekuti wakalamba kkkkkkkkkkkkkkkkkkkk
Chonena ndilibe ndingoti RIP
Its bd. RIP
eeeeish i think this one i from mangochi
Sole moenda ndichoncho
Xory..RIP young-girl
midyomba imakonda zimene ndi atumbukanu mutha
Eish zovuta iz
Achewa azolowela kupita ku estate ndi ana omwe ngati kwawo,sorry for the child
Ena sanganiza amene wapanga zimenezi zofuna phechepheche sadusamo kawiri soka lagwera kwa iye
lol Get rich nd die tryng o
Maxwell Jimmy Jaffale Makumba Allah akudalitseni pauthenga wanu womveka bwino ndi malangizo anu abwino. Amene tamva izi tiuzense anzathuwo chifukwa ena sakuwerenga nkhan ndipo sakudziwa kuti zachitika zachisoniz.
Sorrie, it happens
Kuthawa Ana kuno ulendo Ku Jon ndizimezo ma party weekend abale anu kuno njala
Shame
So sad
Eish dat terrible… RIP Young girl!!!!
Imfa yake inalembedwela pompo ena anapulumuka bwanji?
we people have to think carefully.yes we r in poverty but we have to care about our lyf.coz is important
Mvuu nazo zili pa chilala. Madzi, chakudya zikumasowa. Tikumaziyamba dala kwao.
Kkkkk si government or poverty but as the title says it; search for greener pasture. Kukhala malo otukuka doesnt mean kut utukukanso why osaona njira zina konkuno kumuzi. Akakakuphani kumeneko or deport banja lizafikira pati kuno?
Its zimbabwean couple nt Malawian unopenga we admin
Koma mulimba?
Mmmm plz Malawi!
Eix that was bad,really sad
Azibambo ena ndi mbudzi zamuthu mene pamaophwera pa malo ameneo iwo ndikumaitana nkazi ,mwana opanda passport amaganiza bwanji, lero apasira mwana mikango ya mulipopo,eish foolish mother,and ldiot father,
and naikhalanso this rainy season imene mtsinje umene uja umakhala wadzadza. anthu ena amaganiza mopusa!!!
Very sad.
choyamba ndipereke uthenga wopepesa ku banjali limene lataya mwana wawo. Koma paja akulu amati kupewa kuposa kuchiza komanso uko kwathu ngati nyumba nyumba yathu ikudontha pamene mvula ikugwa,,ikakata muja, timakwera pamwamba nitiponyapo tiudzu pamene pakadotha paja. AMalawi tiyeni tichepetse kuyenda njira ngati zimenezi. Akuti njira zachidule. Musamanamizidwe kuti maulendo a pa bus ndiwodula, ai. Kaya ndiwe wa ku lilongwe, takwerani mabus monga intercape, munorruramah, ingwe, mkango, chilipa ndi mabus ena ovomerezeka. passport ndi k48500, nde ngati ukufuna kuti ituluke mwachangu, mungodizako k10000. Mabus sadula ndi k27 000, kuchokera ku Lilongwe. mufika kuno in 35 hours. ndarama zowonetsa munjira sikuti zingapitirire k20,000 ai. chimafunika ndikuzichepetsa komanso kumazimvetsa chison mukafika malo ofuna ndarama. Ino ndi nthawi yamvula imene mtsinje wa Limpopo umabzala zedi. Ng’ona zimangoti belubelu. Maulendo oterewa transport yake ndiyodula pafupifupi k140,000 kutsika mmunsi. pamene ulendo wapabus zonse zimatha k110,000. amai ndi abambo, anyamata ndi asungwana, ulendo wachidulewu, ndi ulendo wowopsa, ulendo wosafunikira wana. ndi pempho langanso inu madalaivala omwenso ndinu aini amagalimoto amaulendo ngati amenewa kuti sinthani nthawi yamaulendo anu. nthawi yamvula ngati ino, ndi bwino kuimika. chonde chonde chonde aMalawi, kwerani mabus mukamabwera kuno. And osangoti bola ndakwera bus, koma musanakalipire ndarama, fufuzani bwino lomwe basiyo. mabus osachititsa njengunje ndi mabus a Intercape, Munorurramah. Moyo ndi mpamba! Moyo ndi kapitolo! Moyo ndi makiyi! Usamalireni! Utetezeni chifukwa mukafa, simukagula wina
Koma zina ukamva! Tizizimvesa Chisoni mma border mu eti. Amamva Chisoni olo utalira?
thaiming’i man ndi imene imafunika. Usamazionetse ngati uli ndi ndarama. pokwera mubus muja, uzikwera kumapeto. Apolisi amakhala pakhomo aja, amakhala asanja kale..nde olo utawathira ka R10, alandira basi.
Mau ogwira mtimaa MukupezekA kuti mulandile AtondiDo bwanaaa?
kkkkkkkkk eishhhhhhh atondido okha basi?????
Iweso ndi kape bwanji?????? passport kudisha mpaka???? hahahahhaha am nt a savage sindimapanga zimenezo kulemeleretsa makape
iwe ndie ndi mbuzitu,,,bakha iwe. Nde ngati usadishe ukuti ituluka?
Yet yet akufuna aziwanamiza anthu ameneyu ngatinso kujon kuno akukuziwa. And tiuzenso mtundu waMalawi kuti podiza passport.po, osangompatsa munthu ai koma kumawapatsa ovala ma.uniform a blue aja coz enawo nde umaliranso
Sometimes when u rush, u crash and sometimes instead of getting greener pasture, u get browner pasture.
Mgcini Maseko Alex Magawa Langson Magawa Adam-Son Ando Mwakikunga Webster Ng’ambi Mwenibanda
blame it on incompetent governance whose policies are making Malawians slaves
Zachidule,
Pali uchi pali njuchi
Shame sorry to hear that ,and that our govt is killing people because it can’t provide ppl’s needs