Malawians in Chiradzulu district have been asked to desist from conducts that can contribute to the spread of the HIV/AIDS epidemic so that the district should develop.
The call was made on Wednesday during the commemoration of the 2015 World AIDS Day at Tchoda school ground in the area of Sub Traditional Authority Maone in the district.
Speaking at the event, Chiradzulu District council chairman, Councillor Emmanuel Kamwendo, who was also guest of honour, said the epidemic is one of the major constraints to development.
“There is need for people to ensure that they are safe because mostly it is difficult for a person who is not healthier to take part effectively in developmental activities,” he said. Chiradzulu District AIDS Coordinator (DAC), Chris Nawata, told Malawi24 in an interview that his office is not satisfied with the progress of the fight against HIV/AIDS in the district since they have not yet reduced the spread of the epidemic.
Nawata said they are implementing HIV preventive programs such as medical male circumcision and HIV/AIDS testing and counselling aimed at reducing further transmission of the epidemic in the district.
“We are doing our best but somehow we are going down and we really haven’t registered required progress in terms of further spread of the epidemic,” said Nawata.
The day was commemorated under the theme “Getting to Zero: New Infections, New HIV Related Deaths and Stigma and Discrimination towards 90:90:90”.
Statistics indicate that 1.1 million people are on HIV medical treatment in Malawi and 34,000 of them are from Chiradzulu district.
Please don’t believe that!
Circumcision does NOT reduce the risk og getting HIV.
Only condoms can protect you.
yuoths lest join hands on fighting for ths
Zabodza chilungamo nchakuti anthu ena amachoka madera akwawo kumakatengera mankhwala ku CZ
Cause of cutural activities
wanzelu ndiamene amadziwa momwe mthupi mweke mulili,zilibwino kwaomwe akulandila mankhwala.koma sizonyaditsa kukhala ndi HIV AIDS.chiwelengelocho chachuluka
AIDS singachepe ndimalangizo, bola mukadayesa chilamulo pankhani yakugonana.
Kkkkkk anthu openga mwapanga bwanji
Kkkkkk anthu openga mwapanga bwanji
CZ ha 34000 what else, is it more/less compared with other districts?, always mumatisiya ndi mafunso, be professional pliz
CZ ha 34000 what else, is it more/less compared with other districts?, always mumatisiya ndi mafunso, be professional pliz
More People Don’t Fear HIV These Days Coz Of ARVs… I Stl Belive HIV In Malawi Is Way Beyond 11percent As Documented. Youths And Young Adults 16 – 40yo) Bieng The Dominating Victims… Thus My Opinion
pliz pliz muzimvetsetsa chimgerezichi.kuti 1.1m akulandira chithandizo cha HIV ndipo anthu 34000 ndi a mboma ka Chiradzulu.izi zikutanthauza kuti anthu amboma la CZwo ndiozindikira komanso amatengapo mbali pothana ndimatendawa finally zikutanthauzanso kuti maboma ena chifukwa cha mbuli (asena amati ubulutu ) akadwala samapita kukayezesa kapena akapezeka ndikachi animalko umapita kwasing’anga kumati olodzedwa
Tsopano mwati titani mwatiuza figure imeneyi? Kodi mukuona ngati anthu angaleke kugonana? Ena si mpaka mwayamba mathanyula kuleka akazi okongolawa.
Eee Mwamvatv Osadzayesera Dala Kukwata Mukafika Ku Chiladzuru
Konko
Kodi chirazulo imeneyi uchifwamba 1 hiv 1 koma ndiee
Asaaaa akadziwa ndani?
headline ndi nkhani parallel
Ambuye angoyikapo dzanja basi zisintha.
Others are From mozambique ambiri amachokela kumeneko because kufupi ndi ku chiladzulu
Mmmmm Sindikugwilizana nazzo Edzi ili mmaboma omwe muli ma border ndi maboma omwe muli zokopa Alendo. omwe walemba izzzi kafukufuku wakoyo umuyambilenso olight.
Thats Truth Chieff
sad news Our God please assist us
Thats a huge figure, Malawians please take care. The whole Europe less than 1m are on HIV and aids treatment
the eating habbit matters!….they eat for nutritive food value while most of us eat to fill our stomachs…for just energy.
inenso mwandiiwala simunandiwelengele hehehe
kalero amati karonga yili number tsopano mkuti chiradzulo
Inkaopsa kale HIV,pano ingofanana ndi chinfine,enanu musama comente zoti zikome,mwinanso muli nayo,kuchipatala ndiye kuli mayankho,bola iwo akudziwa ndipo alipa treatment
Eish!
Eish!
Out of statistics its more than that
Out of statistics its more than that
65000 of them are from Thyolo
Wakuudza ndani?
65000 of them are from Thyolo
Wakuudza ndani?
Osamati Thyolo! Panopo ndi ku United states
Mukadamakambabe za hiv ?nazimva kalekale nkhani zimenezi go ahead..
Mukadamakambabe za hiv ?nazimva kalekale nkhani zimenezi go ahead..
why chiradzulu district
why chiradzulu district
Eish apa nde zafika pa mpani pani2. Kodi nde kuti fans yakimeneku vuto ndichan? Umbuli or kuchepa olangiza? Amangokwata basi! Kkkkkkkl chiladzulu hoyeee!!!
Eish apa nde zafika pa mpani pani2. Kodi nde kuti fans yakimeneku vuto ndichan? Umbuli or kuchepa olangiza? Amangokwata basi! Kkkkkkkl chiladzulu hoyeee!!!
That’s their own business!
That’s their own business!
#chiradzulu de best dstrict in mw az far az hiv/ aids z concerned
#chiradzulu de best dstrict in mw az far az hiv/ aids z concerned
Anthu Ambiri Ku Chiradzulu Ndi Achawa Ndipo Mbolo Nzodura Nde Zatheka Bwanji Figure Imeneyo?
Mudakakhulupilirabe kuti mbolo yodula sitenga matenda? Bodza ilo lankhunkhuniza
Anthu Ambiri Ku Chiradzulu Ndi Achawa Ndipo Mbolo Nzodura Nde Zatheka Bwanji Figure Imeneyo?
Mudakakhulupilirabe kuti mbolo yodula sitenga matenda? Bodza ilo lankhunkhuniza
mwina ndiye kuli akatswili azimenezi
Kkkkk, koma CZ nde eeeetu
Kkkkk, koma CZ nde eeeetu
yachepa figure, is more than that.
yachepa figure, is more than that.
Kkkkk cz
Kkkkk cz
Apa zikusonyeza kuti aphatikiza ndi omwe anapitira ntchito ku Chiradzuluko eti?
Yes amawerenga wina aliyense yemwe ali m,boma mo,kaya ngwa ku Rumphi akugwirako ntchito awerengera limodzi
Apa zikusonyeza kuti aphatikiza ndi omwe anapitira ntchito ku Chiradzuluko eti?
Yes amawerenga wina aliyense yemwe ali m,boma mo,kaya ngwa ku Rumphi akugwirako ntchito awerengera limodzi
nde ndiochepatu
nde ndiochepatu
Anthu ambiri amadera osiyana siyana amalandirira kuchiradzulu chifukwa ndikomwe anayambirira kupereka ma Arv’s
Yaa Brenda ndikuvomerezana nawe, chitsanzo pa ndunde zaka zambuyomu anthu ankachita kuchoka maboma ena timaona ife ndili volontiya ndiye anthu asakambe mwano azilangizi tilinawo ochulukaso Tadala, Nyaude ndi ena ochuluka osat kuchepa kwa alangizi akunenera enawo.

Men affecting women,men God will punish you severely.
Men affecting women,men God will punish you severely.
ndikudziwa bwino ndikwathu uku
ndikudziwa bwino ndikwathu uku
Ndie?
Ndie?
Ohhh ya we a wining de batle out of 16m……onl 1:1 t@s gud devopment….
Ohhh ya we a wining de batle out of 16m……onl 1:1 t@s gud devopment….
DAC wa chiradzulu uli pa ntchito
DAC wa chiradzulu uli pa ntchito
Amenewotu ndi omwe ali mkaundula, nanga omwe sanayezetse ndipo sakudziwa za status yawo? Mmmm Ambuye atithandize ndithu
Amenewotu ndi omwe ali mkaundula, nanga omwe sanayezetse ndipo sakudziwa za status yawo? Mmmm Ambuye atithandize ndithu
Eish!chiradzulu is verry dangerous
Eish!chiradzulu is verry dangerous
1.1Million in Malawi only?
1.1Million in Malawi only?
what percentage in national colleges????……
what percentage in national colleges????……
Does that mean Chiradzulu has the most people on HIV medical treatment? Which district has the most HIV positive people?
Does that mean Chiradzulu has the most people on HIV medical treatment? Which district has the most HIV positive people?
Mangochi is most high popu.
Mangochi is most high popu.
Mijomba ndiyomwe yaononga chiladzulo,akumabwera kuchokera mangochi ataonongeka kale,at chifukwa anavinidwa ndiye sangagwiritse ntchito chishango.
Mijomba ndiyomwe yaononga chiladzulo,akumabwera kuchokera mangochi ataonongeka kale,at chifukwa anavinidwa ndiye sangagwiritse ntchito chishango.
Kkkkkkkkkk too bad.