…already released on bail
Malawi Police in Mulanje district have arrested a Democratic Progressive Party (DPP) Councillor, Biston Chikadewa for Nambiranje ward in Mulanje west constituency for raping and impregnating a 16 year old girl, Malawi24 has learnt.
According to information reaching this publication, the suspect , Biston Kadewere sexually assaulted the girl some time back at least six months ago but could not be arrested.
It is said that on Tuesday, November 10, 2015 some people in the area protested on the matter as to why police were not arresting the Councillor a development that forced the Mulanje police to nab the suspect on the same day.
Kadewere appeared in court on on Wednesday where he was answering charges of defilement.
In the court the Councillor pleaded not guilty and has now since being granted bail at a bond of K50,000.
The victim was a standard six girl at Ngumera primary school in the district.
She is now five months pregnant.
Kungoti wogwirirayo ndi ntchito yake ndinamudziwa ku xool pa mulomba cdss amapanganso zomwezo. Nde poti ali m’boma ndichifukwa amutulusa pa belo ndiye dpp imeneyo. Akanakhala wachipani china mukanamumva hule kaliyati mmene akanachitira koma poti akakhala pa nkhate sangapheke
Big bullets vs kaizer chief
Siyanitsani pakati pa rape nd defilement plz.two counts mai kaliati mukuti bwanji apa???
olo munene conco bola nzanu athotha bas ngat nfanayo ankaphwekesa,haa ngini ili boooo
Ali M’phunzitsi ntchito yauma komanso jailed,why a teacher?
16 years old is matured and so can no longer be call rape. This a planned deal as the girl did not shout. Then if she is pregnant , there is nothing wrong in having children and can still school latter.
You need to your behav…..coz usay as if ulibe nzeru….
a dpp ndi khalidwe lawo
guyz ndi chani iwe simwana wako ameneyo.bail nso ya chani?
Dpp woyeeeee!
Its shame!big man
kkkkk…. kma yaah ziliko!
Rapes and impregnates…. Mwadiwa mwana ali ndi mimba kuti she was rapped?
Dpp councillor erapwela opanda mapwala wandipwalira mwana.unamufila km amaveka bho,mafutso omwe akumakufusani bwampini yemwe akumakutumaniyo.nkhumba xokhaxokha
Kulibe mulandu wakulawathe anthuwo anavanakale kukoma
Guyz ngati kuli ku gwilila ndiye kuti tsiku lomwelo anapita kupolice komanso tsiku lomwelo anapezeka ndi mimba eti? Musiyeni munthuyo ndichibwenzi chake ichi musatenga ma chance poti ndi khansala akanakhala munthu wamba sizikanamveka izi inunso mukudziwa.
16yrs? Ndi wamkulu ameneyo. Both m’matauni ndi m’midzi atsikana akutenga mimba as young as 13yrs. The girl consented.
check time! rape and pregnt cnt take place tgether! somethng(trueth) z mcng! use ur heads nt ur thots,pipo!
Chipani chachisembwere DPP mbuli za a lomwe
point of correction, she is a 16 year old woman
point of correction, she is a 16 year old woman
Ndipemphe apolisi amugwirenso mwanayo chifukwa AGALU amenewa anali pachibwenzi. Mukayamba kuwamanga anawo mwina azikana kukhala pachibwenzi ndimunthu wankulu.
chinali chibwezi amagwirizaza zogonanazo anthu nkhani mmayitengera pamgon’go bwanji mesa amakwatana kawirikawiri
DPP konzan malawi problems….
Chipani cha anthu ogwililira dpp
Thats What Our Govt Is Proud of am gonna rape nkhalamba kuzikumbutsa chkale
Chonde Malawi24 nkhani zanu mzilemba bwino. Nkhani zimangothera mu malele osadziwa kuti yathera pati!! Investigate in full details first before publishing it,chonde.
Zikuwavuta kulamulira dziko nde aganiza zoti azifweba ti banyana banyanja ,funso nkumati kdi ndalama yake nkukhala yotha phavuyi ‘ (fotseki) uzikafweba ana ako ngati uli ndi nkhuli , coz ndi eazy kukulola zofuna zako, masimba akho,”
Owo mutionongela ana inu adpp mwatopa ndi mathanyula eti esha! Zichepe !m,paka bail akanakhala wa mcp pano titava kt wakumaula akt poti ndi manyaka okhaokha
Vuto la a Malawi ctfuna kugawana coz rapin dis young girl ctnena kut mafeeling anafika 100 % kufuna kukwima kut 2019 alowenso amalawi eeesh.zoona munthu wa normal kukapanga zimenez
ubwino wa chisembwele
God of mercy forgive him
Anawa dyela
Mwina akutero coz wakwiya bcoz sadalandirebe njinga zamoto zangongole zija!
he granted a police bail? our Hn Minster WC&S Walfare how do you feel?
sendeza ilibe size,why was she screaming?she was feeling it!
Very pathetic. If left unsqueezed, he will rape more children
Dpp woyee
kulibe kulapirana
Mu west mulibe namilonje ward kufuna kumubisa angandiuze kumene kupezeka ward imeneyi
miswahala ikumawachulukra agalu. amenewa ofunika asiye kulandira
kunyanzitsa chipani
kodi ndi two in one chimenechija ndi chindoko
Ucixiruo Ndio Umeneo Coz Munthu Oganiza Xangapange Zmenez Adzamuvoteraxo Kma? & Kungot Popeza Al Nd Money / Nd Mp Xo Bail Yacitka Kale Dzkol Lidzafka Pat? Xo Aja Amapanga Nd Ana Ao Zdzngowathera Ngat Palibe Chomwe Chichtike
Malawi 24, ndinu amantha. Nkhaniyi mwilemba mokondera, mwaboza ndi molakwisa mwadala. Dzina la khansala ndi Biston CHIKADEWA osati kadewere, ward ndi NAMBIRANJE osati namilonje, zna la sukulu ndi NGUMERA osati mkumeya iai! Mwachita izi mwadala ndi cholinga chofuna kubisa choona chake ndikuti anthu asamuziwe bwinobwino olakwayo. Ngati olemba nkhani, sindikukhulupira kuti mungakhale mukulakwisa monsemu ai. KALIPO_KALIPO.
Meander to confuse direction. Life is precious
Kodi Siufiti Umeneu?
chitukuko mtchito ya khasala ayi wayamba boooo dpp 2019 boma
boma iloooo! manyaka a dpp
Mizimu ya malemu Dr Bingu ndiyokwiya kwambiri ndi nkhani yimeneyi. ..
Inali dil bobo, nanga kugwilira mpaka kufundisana nchoch kutheka, komaso doloyo ndi wa 19 yrs od nde anaona kut saiz yake nd imeneo
No money no Love Kkkkkkkk.
Dpp yandiopsa!
Nde Mot Mupage Zitukuko Mukugokwa..Tiana Tanuwake,tinene Kut Mulibe Baja?
boma ilo!
Ndiye Malawi24 Ineneo.
Sichipani koma umunthu, kungoti wapanga zimenezo ndi councillor wa DPP, koma chipani sichimalimbikitsa zimenezi, malamulo agwire ntchito posatengera zimene tikuyankhula pano. Wachipani chilichonse amalakwa, monga anachitira Sithole mwiniwake wa Mpapapi, kutenga ana asukulu awiri nkukagonanawo sabata yathunthu, koma mpaka pano nkhani imeneyi sikuoneka mutu wake kapena kumveka. Zonsenzi nchifukwa chakuti panopa ndi MP.
zipani zinazi abale
My Head Stand Up,,,can 16years Girl Accept Rape??,,,ive Seen The Girl Of The Same Age But Having Two Children..Ithink Reality Checked Here..,girls Of Now Adayz Are After Money.
pic ndi khan czkugwilizanatu Kkkkkk
Tikukonzeni si kadewere koma chikadewa.
Koma mapaziwo ehh. Simungasinthe?
Kkkkk kaliati woyeee akanakhala wa mcp akanapeza ntchito kaliati apa nanga?
if leaderz r in forefront who r we lets sing…followx3 follow the leader remember at prmry xul
Kkk koma anawazilako
nde mwat kupanga secure mpando 2019 ….haaaa
Mbuzi yachabe iyi kungomuphela mwana sogolo fokoff..
nzoyamwira
If It Is Thrue Arrest Him
Tell us development news not that rubbish we want money and development
Nkhumba imeneyo
Bwanj ameo apite ku state house akathandizeko mwina kungabadwe junior kip it up sir ntchito mwagwira
What a shameful story
Aaaaa Atuluka Akadakhala Kuti Waba Khuku Tikadati Akaswera Koma Waboma Tikudziwa Kumbukani Pa 21 paja panafa athu angati anamangapo ndani boma lake ndilomwelo zochepa mamani cool down ma brooo???
it seems raping has high rate of orgasm otherthan an ordnery wife. so, government should ligalise rape & defilement
Kkkkkkk
suknama mwna orgasm cn mek jnr ku state hwc thru rapn mrz przdnt………
Zilibwino ndi boma la bwampini…….
Chagwa mbale ndndwo & everytin’ aftes 12 nd lunch
Ali ndi mitima ya anyani olo presdent amene akungonyenga tiwana kwao ku tcholo. Ndingoti NONSE A DPP NDINU ANYANI KU MALAWIKO MUMUUZENSO MKULU WANUYO PETER AKUNUNKHA AKASAMBE Ngati wina za munyansa aimbe pa nambala iyi {+258 846978734 Nampula}
inu mapazi onsewo mukati ndi mwana anthu osaziwa kunyenga inu kukonda nkhalamba basi
Blame the girls themselves for the insatiable hunger for money. The councillor failed to honour agreement and therefore it became rape case, abduction, defilement and name it. Day time school girls and night time street hookers.
Ntchito za DPP zikumuchitira umbonikkkk
Ntchito Za DPP Zimenezo Nanga si Chimenechi Ndiye Chitukuko Chimene Iwowo Amaziwa Basi!
D P P Chipani Chawina Aliyese Mwana,mkulu,gogo & …..
kkkk kugwilira 16yrs???? atsikana ake alerowa nde 50%yaamuna are doing the same.akumaziyamba dala
charity
This is what real malawi leader is capable of m’malo mwachitukuko koma busy kulowa m’masiketi nde malawi muti azatukuka??Enaonso zao mzomwz kma kusagwdwa
Nyamake ameneyo
Adziwa Chifukwa Ali Ndi Mimba Kumeneko Ckugwilira Choxan Mawu Oti Kugwilira Muzti Khasala Wapeleka Mimba Bac
Sizachilendo ku dpp panja amulli ankanyenga nkadzi wa mulaka lero ena ndiawa sizachilendo izi
Kugwilira ndi kugona ndi mkazi wan’gono kapena wamkulu mokakamizidwa (momuumiliza). Udindo wa u Councillor ndi wolemekezeka ndiponso waukulu. Kodi DPP ati ndi boma afuna azitikakamiza zinthu, mavuto tisakufuna??
kkkkkkkkkkkkkkkkk moti amachindana mwana ndi gogo
Wasala m’bale wako uja inenso ndimutero.
Ndiye inu a Malawi24 mwapangapo chani chowonetsa ukadaulo wanu??
Kod malisechewo amaenda mmanja? Ngat nd gondolox eee chepetxan
On bale. No fine, no collatel that means no case. Shame to u dpp haters
to me diz pic looks fake its nt capture here in malawi and i cant beliv the news unless i hear it on radio
nkhani ndikundende tifuna tione chilungamo chiyende ngat madz ok amangidwe bas watopa ndikubunyula watopela mwana aaaaaa
Dat z not rape Baba…
Hahahahaha! He’s tampered with the forbidden fruit,I doubt if he will get away with it even though he’s reportedly on bail.
zisatikhuze ife zimenezo chifukwa sanayambirane lero
Better, he is not gay.
KKKKKKKKKKKKKKKKK zamanyazi
Kkkkkkkk…kumalawi kukakhale nkhondo, mudzimenyana ndi mipini? Zida zankhondozo mukatenga kwaani? Ngati zimakanika pa police station kumakhala mfuti ziwiri, koma ogwira ntchitowo Ali mbweeeeee!!!
Ndiye mwati amavelera juuuuuuuuuuuuuuuu wamimba kake
nose amene muknyoza dpp mitu yanu.mkaz wa 16yrs angagwililidwe? zachamba zimenezo iyaaaa!
iwenso nde kuti umagwiririra nanga waziwa buanj?????
kkkkk,nawe tiatsikana tamasku ano 14 yrs akumakhala ali nd mwana nde munthu akanene kt wa’16yrs wagwililidwa?zosamveka zmenezo iiisssh
She is not an adult
azigwiriridwa azimayi nanga mwana ngati ameneyu ndi bambo ako eti
Alomwe paja kukonda zigololo basi paja APM Amakonda yakumbuyo mathanyula
kkkk ok guy 4 evry mstake thrz areason am feeling xory4 tht gal
Ndie dpp imeneyo
Is not amatter a party bt its apersonal feelings.sham to zat man
kutengeka atsikana
Ndanva
mtsogoreri wakareyu anati ngati akufuna brah wakwana?
http://WWW.Umunthu.Com
mmmmh zogwirizana zimenezo musatinamizepo apa.
Koma musati chipan cha dpp mutchuleni dzina lake munthuyo chifukwa mukuipitsa mbili ya chipani chathu bkz even dpp singakondele nditchitidwe wa uve ngati uwu pls pipple dont say that to dpp
Democratic pregnanting pupils(DPP)kkk lol
Alomwe!Alomwe!mukumveka kwambiri,keep it up.
Zaka 16 aaaaaa ok ndinamvapo Mtogoleri wopuma akuti ngati pantima pali mabele ngati akumavala zoyimisira mabere brah aaaa wakwana ameneyo ndiye ali ndi mimba aaa sikamodzi anali pachibwezi nkhaniyi musatengere zandare poti ndi wa DPP ndoizowona boma silikuyenda bwino koma zogonana ndizina so nina muchangoshayiwa mahala for nothing yena azomusiza mungakhulume manyara anavana kukoma
i lk dis act tikhoza kutukuka nazo
she is now having five months old pregnant??? koma sukulu ndi yofunikadi kkkkkkkkkk
not raping…chinali chibwezi….angokwatilana basi
16yrs simwana mwaiwala kuti a phungu athu mosogozedwa ndi women mp anapanga pass bill yot nsungwana akhoza kukwatiwa ali ndi zaka 16?
Peter told him to do so
Shame! Mahule osewa angoti bweeee
Kuti malume
Mkhwani uli mvuto.
miendo m’mwamba d.p.p ike chitukuko kumeneko!
Zopusa basi munthu wazaka 16 anga gwililidwe,anagwilizana ameneo
Point of collection, Beston Chikadewa for Nambilonje ward
Mumawadziwa bwino
Anthu akumulanje kukhwima two much
Amugwilira liti? mimba ndiya miyezi ingati? za ntiii! mwaxowa zolemba mix………
Hahahahaha i hope akazatulukamo naye azapeze tsiku lozazabweleranso kuzalemba pa khoma kuti DPP COUNCILOR WAS HERE.Hahahahahaha!
acts of dpp
Kkkkk chipani chanthu ogwilila
Malawi24.com
Mmmmm 16yrs?!,aaah tieni tiganizirenso masikuaano ameneyo ndiwankulu,anali pachibwenzi awiriwo,ndepoti apatsana mimba azit wagwiridwa?!,nthawiyonseyi akhalapanchikondi,koma makolo,osakangontula bwa?,nanunso atolankhani kumafunsisa ndi kumatiuzazoona,osati m’mene mwayimverera aaaah! Ndizabodza mwangokondera apaaa munamize andaa,anthuanari pachikondiiiii,zankhutu!
Kkkkkkkkk koma macomment ali apa eish !!
No asamumange coz msikanayo amaziwa chmene akuchta akanakhala kt nd mwana bwez sakavomera kt akhale pachbwez nd mp?
zamanyaz 16 years sizoona kkkk
Amafuna 2019 adzathe kuvota.
16yrz, raped?
Democratic preginating pupils (dpp)
Kkkkkkkk.thus it
Kkkkkkkkkkkk
kkkkkkkkkk………………..DPP
Kkkkkkkkk
Hahahaha
Ink Yanga Yatha Ndikulephera Ku Commenter Kkkkk
hiiiiiiiii kkkkk
spelling!
hahahahahha
I got you,,,,,kkkkkkgagagagaga
What a name!
Kkkk koma wabaya alibe mau
Apo mpweeee!! Kkkkk
DPP Woyeee !!
Dpp woyee!
Jafali chaande,jafali chande,jafali chande,kutsogoza big bullets pa 29mins atachinya chiukepo msowoya pa 27mins,analandila mpila kuchokela kwa dalitso sailesi,jafali chande sanachitile mwina koma kuupha mpila ndikuugwetsela muukonde.anachita njengunje otsekakumbuyo kwa moyale barracks.BIG BULLETS FC 2,moyale barracks 0.hehe,payaka moto pakamuzu stadium.ikufuna kusintha bullets kutulutsa mussa manyenje kulowetsa mnyamata aimable nikiza,reject ya mzuni.#BIG Bullets,ma favourites!!
ineyo ndimat uku kulibe zogwiririra and timanyozedwa izi zikachitika kwathu ndiye si izi mwaziona nanunso
Alomwe amenewo mpakana 16 yrs
atumbuka ndi anthu ngati wina aliyense ena opephera ena ayi ena anzeru ena ayi koma zina ndizixelexa alomwe atani?ena ndi achipani ena ayi what makes u special for what ur not for whom ur?ignorat at its best
Aaaaaaaah.guys tawonani timapaz ta counciller.
Zogwirizana zangolowa ndale
ameneyo ndye mbuyache ,paja gwaladi ndi amene amaimba mmisonkhano yake kkkkk mwana mbuu make mbuu chitukuko chopanga ana #DPP
Let chilungamo chioneka potengera ku mtsikanayo anali pa sukulu moti future yake yaonongeka.Ndipemphe a court kti chonde mkulu ameneyu alandire chilango chokwima kti anthu ena amaudindo atengele phunziro.Let me also ask amabungwe oyang’anira za maufulu achibadwidwe kti alowelerepo kmanso ndikanakonda kuti Wolemekezeka a Nduna aGender women n children affairs alowelelerepo poti nkhaniyi yachitika ku dera lawo kti chilungamo chioneke posatengera kti councilloryo ndiwa DPP.
Iwe Ukufuna Ukhale Wa Chilungamo Ngat Ndan Dziko Muno Axakadziwa Tsiku Lomwe Amamugwilira Bwanj
Ayahaya Ndinu Chisilu Mwamva? Yu Say As If Ulibe Mano Mkamwa. What If Mwanayo Akanapeleka Matenda Kwa Mwamunayo Mkanati Chayani? 16yrs Ndi Munthu Wakulu Ameneyo
iwe ndi phwala et munthu u dnt wait fo mimba ndikumqti akugwilira foolish!!
Opusa ndiwe, tione kaliyati hule ayankhulanji monga nduna, zisakomere kugunda galu apa!
ZAKA 16 AAAAA NDIYE NKUMANAMA KUTI AGWILIRA? ZA CHAMBA ETI, MASIKU ANO TIMAPEZA TIANA TA ZAKA 11 TILI MMA BHARAMU, NDIYE MUZITI 16,.
ZAKA 16 AAAAA NDIYE NKUMANAMA KUTI AGWILIRA? ZA CHAMBA ETI, MASIKU ANO TIMAPEZA TIANA TA ZAKA 11 TILI MMA BHARAMU, NDIYE MUZITI 16,.
Ali M’phunzitsi yake ya uma,komanso wo kathera kundende,kaya adatani m’phunzitsi?
There’s nid 4 behaviour Change
kkk akathandizile mnyumba ya APM zikuoneka kut ntchito sikugwirika kikikikikokokokukuulol
Sanagwirire koma Mw24 atolankhani ake nda nyapapi bwanji, kungofuna ma comment ambiri basi.
Mahule m’mene atchipiramu wina ndikumagwililira mwana
DPP WOYEEEEEEEEEEEEE
some pipol need Jesus 4 sho
mukutinamiza wawa ndibodza apa kugwiririla paka mimba how come?
And a Police akumalawi mulibe chochita ndikupezerani ntchito
@ Johnson Erimu We Malawians Hv Known Uganda For Civil War Killing Each Other Jst Bcz Of Politics! Shame Shame Shame!
Miyendo m’mwamba changu a DPP ayikepo chitukuko
It can’t be !
Rape and pregnant ?
Or it was something than rape .
They already said, miyendo mwamba tiyike zitukuko. Popipopi. Mcp wooyeeeeeeee!
kodi madikira zodiak ilengeze then mutiuze?
anali akufunaso sikanayo sova aona kuti apanga bwanji.
MENDO 4 BASI TIWANA KUFEWA AKULU KULIMBA POLOWESA
i cant comment since i dont know how the word rape has being used.could it be he raped her directly or they agreed but because she is not yet 18 yrs thats why it is called rape.
walankhula wise, ineso ndimaganiza ngat iwe. osamangoona pamwamba pa nkhan bt ndipansi pomwe
Zoputsa zokhazokha zomwe zikunenedwa kuno iya……Muonekem muti anzeru?
it is rape even if she agreed to it because she is a minor.
rodrick its not about wisdom as you have written but about the reality on the ground
Adpp ndinu agalu tamapangan ztukuko osat kumakwata ana
Hahaha koma amweneee!! Mlomwe wina watukwana mtolankhani wina wagwililira? Haha crazie
is this abwt us alomwe?
nyere zimenez bwanj atsogoleri
Ngati Kuli Kufuna Kukhwima Muzikhwimila Ana Anu Osati Muziononga Future Ya Ena Thats Being Selfish.
pamtumbo panu.16 yrs kumulanje ndimwana? Anagwirizana. Pam’nyero panu apusi inu.
Rape is rape, Maejor even if she was 25,,koma ngati anapanga iye asakufana ndi mlandu
Get out man,kumene kuja anthu amakwatila ali mafana nde 16 yea$ iz nt ajoke ,wadya money mwana ameneyo zitchito zake zachitila umboni basi,die had wa dpp nde ine wina afune asafune
We Ugandans hv known malawi for such events only,thanx to malawi24. shame shame shame.
Such things happen in any country around the world.
But i have never read anything good abt malawi on “malawi24” except football.
the problem is ur focusing only on malawi24,,u hv to read nyasatimes
# Erimu and you like commenting badly, wy not pray 4 us as u r a God fearing man.
I Pray 4 u but “malawi24” cannot write anything abt malawi? there’s only bad news in malawi? i dnt comment badly at all
Ur “malawi24 can even cause war like the case in Rwanda in 2004. let them reduce inciting people.
I agree with u Erimu our national always write bad news apart from footballalso sometimes
#Lumbani thanx, u’he understood my argument.
Thanks you are able to see
On Malawi 24 only bad things makes breaking news.
#Andy thanx 4 getting it right.
These are professional jounalists, they consult before editing its real he raped!
Koma iwe Biston
Ndiye ntchito za Dpp!!!!! azimayi miyendo mwamba timangeko ma bridge kkkkkkkkkkkk
aaaaaah sikugwilira koma chinali chibwenzi…ana amasiku ano anyanya set him free
@Noree, simwana uyu. Ndiwamkulu ameneneyu. Chomtengetsa mimbacho nde ukuluwo.
Simunamve kuti mzimai wamng’ona kwambiri pa dziko lonse lapansi adabeleka Ali ndi zaka 5? Zinachitikatu izi Ku Peru.
What’s wrong with this chaotic chewa people . Most of atrocities are done by Chewa people.What a shame.
are trying to say ur not part of nation cause ur not chewa ?was the late dictactor kamuzu ngwazi from chewa tribe?what about the corupt,killing,selling of componies,bakili muluzi&thise one the cashgate lady JB is she also a chewa?hahaha okey alright
Alomwe’s party now raping in action. Chitukuko chobeleka tsopano.
kumamvetsetsa si alomwe omwe agwilira ntsikana koma amalawi muzayamba liti kuzindikila kuti ziko limakhala ndi anthu amitundu yosiyana kma onse ali adziki limozi God help us all
Ku Mulanje ndikwa atumbuka naweso iwe. Belekanani ngati nkhumba muzingowina mavote
Let him face the music for his vices
Kuonaso mapazi akewo aaa mkuonjeza a 24
Nowadays Life So Sad Story,Koma Munthuyu Ali Pali Pabanja Kapena Ayi Osangomuipitsira MBiri Munthu,Koma Anthuwa Anapanga Zangovuta Ndi Zaka Nanga Wakaziyo Adalora Bwanji Musayalutse,Nanga Wamunayo Mukamanga Asamale Mimbayo Ndani? Kkkkkk Very Bad News
She is having a five months pregnant???..Malawi24, you are murdering the Queen’s Language
and he gave the girl pregnancy.kkkkkk!!!
kkkkk…anthuwa akujaila kwambiri..kkkkk
Hahaha DPP ndi bomadi la Chitukuko eti??
Wel done anawa akuzolowela, keep it up
Puleni yakuluyi ndyamoto basi amaupeze nkhani imeneyi ithe 16 simwana
Puleni yakuluyi ndyamoto basi amaupeze nkhani imeneyi ithe 16 simwana
Sinali rape koma chibwenzi. Mpakana kufika popatsana mimba. Anachita kuchalira?
Ee pompompo kapena yabooka kkk mthawi yomwe amagwililayo sadakuwe immediately bwa kuti athandizidwe koma kudikila mimba nde akukana kkk
Kkk achikulile mwina amafuna kunkhwima
Kugwilira hahahahahahaha mpaka mimba esh anatopad
Nde inali fast game mimba same tme kkk
muzimvesesa. akut de incident happenned 5 months ago. and police where not arresting him
KKKKK,ZAKE ITS NT DPP BUT HIM ALONE
Big up mr mumatha ana azadelela kkkkkkkk mbuz imadya pomwe aymanglira
Big up mr mumatha ana azadelela kkkkkkkk mbuz imadya pomwe aymanglira
Usilu Bax Asize Yanu Atha Kuti Mukapange Impregnate Kamwanako Eish.
Aaaaah amachta kutiyamba asikanawa nde mumafuna titani?
Owo Nanunso Muligululimenero Shame Kufunskukhwima Bax Osakhimila Ana Anu Bwsnji.
Hahahahahahaha akufuna azawine zisankho amenewo
Tiyeni Ukoooo!! Ndinyasi Zakezo Sazawinanso Ameneyo.
Kkkkkkk komatu wapanga chtukuko coz makolo amwanayo savutika adya dorrar heve
Uhule Bax.
Uhule wachan watukula mudz pamenepo
Bola Kungozipha.
Hahahaha! bt azbambo enawa i dnt knw why there r alot of women that they cn use to slip wt bt they r jst destroyng tnegs future ufiti chan eishi ansantukwanise mmxuu!!
Mesa Umawayikila Kumbuyo Se Koma Ine Ndiazibamdo Enawa kkkkkkkk.k
Mesa Umawayikila Kumbuyo Se Koma Ine Ndiazibamdo Enawa kkkkkkkk Slip (Kugona)sivuto Akatopa Amayenera Kugona Koma Ka Act Apanga Ap Nkoyipa.
Aaah i do hate this kind of behaviour kumakhala kuzazika ndi ma demons kwinaku arah?
Aaah i do hate this kind of behaviour kumakhala kuzazika ndi ma demons kwinaku arah!
Okae Bola Ukudziwa .
Yeah
Anthu adpp ndi amisala…….chifukwa chake dziko lili ndimabvuto ambiri,,
kkkkkkkkkkk amagwirizana ameneo .Mwasowa chochita a police inu akuba akukanikani.
Mind this picture has been circulated and posted in different pages,so this story might folse!
Find out how it started ana amasiku ano aonjeza mavalidwe ndi makhalidwe,i can’t take a side here.
Very fast rape then preg
16 years ndiwodziwa bwino ntchito ameneyo. Pamene watengera mimba ndiye ndikugwilirila kumeneko ndi chibwezi anatu pano akufuna ndalama
no 1 is above de law..y realise him so fst lyk dat he need 2 sve de jail acording 2 de constitution
No body is above the law, let the truth flow like water
And so he could not be arrested for being a DPP member?
Munthu salakwira mtengo!
komandiyetu 16 years STD 6? Mpakedi kutenga mimba. Nanu a Councillor instead of encouraging education you are now in fore front impregnating them.
Too bad….. Too politic…… Shame!
Mukanakhala inu mukanatanl mabere anali atawawona mkuwasirira ku Mlankho wa Lomwe. i hate promotion of kuyendesa amsikana maliseche in the name of culture. why are mabugwe omenyere ufulu wa msikana in this mother Malawi