DPP Councillor rapes, impregnates a 16 year old girl in Mulanje

Advertisement

…already released on bail

Malawi Police in Mulanje district have arrested a Democratic Progressive Party (DPP) Councillor, Biston Chikadewa for Nambiranje ward in Mulanje west constituency for raping and impregnating a 16 year old girl, Malawi24 has learnt.

According to information reaching this publication, the suspect , Biston Kadewere sexually assaulted the girl some time back at least six months ago but could not be arrested.

ArrestedIt is said that on Tuesday, November 10, 2015 some people in the area protested on the matter as to why police were not arresting the Councillor a development that forced the Mulanje police to nab the suspect on the same day.

Kadewere appeared in court on on Wednesday where he was answering charges of defilement.

In the court the Councillor pleaded not guilty and has now since being granted bail at a bond of K50,000.

The victim was a standard six girl at Ngumera primary school in the district.

She is now five months pregnant.

Advertisement

278 Comments

 1. Kungoti wogwirirayo ndi ntchito yake ndinamudziwa ku xool pa mulomba cdss amapanganso zomwezo. Nde poti ali m’boma ndichifukwa amutulusa pa belo ndiye dpp imeneyo. Akanakhala wachipani china mukanamumva hule kaliyati mmene akanachitira koma poti akakhala pa nkhate sangapheke

 2. 16 years old is matured and so can no longer be call rape. This a planned deal as the girl did not shout. Then if she is pregnant , there is nothing wrong in having children and can still school latter.

 3. Dpp councillor erapwela opanda mapwala wandipwalira mwana.unamufila km amaveka bho,mafutso omwe akumakufusani bwampini yemwe akumakutumaniyo.nkhumba xokhaxokha

 4. Guyz ngati kuli ku gwilila ndiye kuti tsiku lomwelo anapita kupolice komanso tsiku lomwelo anapezeka ndi mimba eti? Musiyeni munthuyo ndichibwenzi chake ichi musatenga ma chance poti ndi khansala akanakhala munthu wamba sizikanamveka izi inunso mukudziwa.

 5. Ndipemphe apolisi amugwirenso mwanayo chifukwa AGALU amenewa anali pachibwenzi. Mukayamba kuwamanga anawo mwina azikana kukhala pachibwenzi ndimunthu wankulu.

 6. Chonde Malawi24 nkhani zanu mzilemba bwino. Nkhani zimangothera mu malele osadziwa kuti yathera pati!! Investigate in full details first before publishing it,chonde.

 7. Zikuwavuta kulamulira dziko nde aganiza zoti azifweba ti banyana banyanja ,funso nkumati kdi ndalama yake nkukhala yotha phavuyi ‘ (fotseki) uzikafweba ana ako ngati uli ndi nkhuli , coz ndi eazy kukulola zofuna zako, masimba akho,”

 8. Vuto la a Malawi ctfuna kugawana coz rapin dis young girl ctnena kut mafeeling anafika 100 % kufuna kukwima kut 2019 alowenso amalawi eeesh.zoona munthu wa normal kukapanga zimenez

 9. Ucixiruo Ndio Umeneo Coz Munthu Oganiza Xangapange Zmenez Adzamuvoteraxo Kma? & Kungot Popeza Al Nd Money / Nd Mp Xo Bail Yacitka Kale Dzkol Lidzafka Pat? Xo Aja Amapanga Nd Ana Ao Zdzngowathera Ngat Palibe Chomwe Chichtike

 10. Malawi 24, ndinu amantha. Nkhaniyi mwilemba mokondera, mwaboza ndi molakwisa mwadala. Dzina la khansala ndi Biston CHIKADEWA osati kadewere, ward ndi NAMBIRANJE osati namilonje, zna la sukulu ndi NGUMERA osati mkumeya iai! Mwachita izi mwadala ndi cholinga chofuna kubisa choona chake ndikuti anthu asamuziwe bwinobwino olakwayo. Ngati olemba nkhani, sindikukhulupira kuti mungakhale mukulakwisa monsemu ai. KALIPO_KALIPO.

 11. Inali dil bobo, nanga kugwilira mpaka kufundisana nchoch kutheka, komaso doloyo ndi wa 19 yrs od nde anaona kut saiz yake nd imeneo

 12. Sichipani koma umunthu, kungoti wapanga zimenezo ndi councillor wa DPP, koma chipani sichimalimbikitsa zimenezi, malamulo agwire ntchito posatengera zimene tikuyankhula pano. Wachipani chilichonse amalakwa, monga anachitira Sithole mwiniwake wa Mpapapi, kutenga ana asukulu awiri nkukagonanawo sabata yathunthu, koma mpaka pano nkhani imeneyi sikuoneka mutu wake kapena kumveka. Zonsenzi nchifukwa chakuti panopa ndi MP.

 13. My Head Stand Up,,,can 16years Girl Accept Rape??,,,ive Seen The Girl Of The Same Age But Having Two Children..Ithink Reality Checked Here..,girls Of Now Adayz Are After Money.

 14. if leaderz r in forefront who r we lets sing…followx3 follow the leader remember at prmry xul

  1. Mbuzi yachabe iyi kungomuphela mwana sogolo fokoff..

 15. Aaaaa Atuluka Akadakhala Kuti Waba Khuku Tikadati Akaswera Koma Waboma Tikudziwa Kumbukani Pa 21 paja panafa athu angati anamangapo ndani boma lake ndilomwelo zochepa mamani cool down ma brooo???

 16. Ali ndi mitima ya anyani olo presdent amene akungonyenga tiwana kwao ku tcholo. Ndingoti NONSE A DPP NDINU ANYANI KU MALAWIKO MUMUUZENSO MKULU WANUYO PETER AKUNUNKHA AKASAMBE Ngati wina za munyansa aimbe pa nambala iyi {+258 846978734 Nampula}

 17. Blame the girls themselves for the insatiable hunger for money. The councillor failed to honour agreement and therefore it became rape case, abduction, defilement and name it. Day time school girls and night time street hookers.

 18. D P P Chipani Chawina Aliyese Mwana,mkulu,gogo & …..

 19. This is what real malawi leader is capable of m’malo mwachitukuko koma busy kulowa m’masiketi nde malawi muti azatukuka??Enaonso zao mzomwz kma kusagwdwa

 20. Kugwilira ndi kugona ndi mkazi wan’gono kapena wamkulu mokakamizidwa (momuumiliza). Udindo wa u Councillor ndi wolemekezeka ndiponso waukulu. Kodi DPP ati ndi boma afuna azitikakamiza zinthu, mavuto tisakufuna??

 21. Hahahahaha! He’s tampered with the forbidden fruit,I doubt if he will get away with it even though he’s reportedly on bail.

 22. Kkkkkkkk…kumalawi kukakhale nkhondo, mudzimenyana ndi mipini? Zida zankhondozo mukatenga kwaani? Ngati zimakanika pa police station kumakhala mfuti ziwiri, koma ogwira ntchitowo Ali mbweeeeee!!!

  1. kkkkk,nawe tiatsikana tamasku ano 14 yrs akumakhala ali nd mwana nde munthu akanene kt wa’16yrs wagwililidwa?zosamveka zmenezo iiisssh

 23. Koma musati chipan cha dpp mutchuleni dzina lake munthuyo chifukwa mukuipitsa mbili ya chipani chathu bkz even dpp singakondele nditchitidwe wa uve ngati uwu pls pipple dont say that to dpp

 24. Zaka 16 aaaaaa ok ndinamvapo Mtogoleri wopuma akuti ngati pantima pali mabele ngati akumavala zoyimisira mabere brah aaaa wakwana ameneyo ndiye ali ndi mimba aaa sikamodzi anali pachibwezi nkhaniyi musatengere zandare poti ndi wa DPP ndoizowona boma silikuyenda bwino koma zogonana ndizina so nina muchangoshayiwa mahala for nothing yena azomusiza mungakhulume manyara anavana kukoma

 25. she is now having five months old pregnant??? koma sukulu ndi yofunikadi kkkkkkkkkk

 26. Hahahahaha i hope akazatulukamo naye azapeze tsiku lozazabweleranso kuzalemba pa khoma kuti DPP COUNCILOR WAS HERE.Hahahahahaha!

 27. Mmmmm 16yrs?!,aaah tieni tiganizirenso masikuaano ameneyo ndiwankulu,anali pachibwenzi awiriwo,ndepoti apatsana mimba azit wagwiridwa?!,nthawiyonseyi akhalapanchikondi,koma makolo,osakangontula bwa?,nanunso atolankhani kumafunsisa ndi kumatiuzazoona,osati m’mene mwayimverera aaaah! Ndizabodza mwangokondera apaaa munamize andaa,anthuanari pachikondiiiii,zankhutu!

 28. No asamumange coz msikanayo amaziwa chmene akuchta akanakhala kt nd mwana bwez sakavomera kt akhale pachbwez nd mp?

 29. Jafali chaande,jafali chande,jafali chande,kutsogoza big bullets pa 29mins atachinya chiukepo msowoya pa 27mins,analandila mpila kuchokela kwa dalitso sailesi,jafali chande sanachitile mwina koma kuupha mpila ndikuugwetsela muukonde.anachita njengunje otsekakumbuyo kwa moyale barracks.BIG BULLETS FC 2,moyale barracks 0.hehe,payaka moto pakamuzu stadium.ikufuna kusintha bullets kutulutsa mussa manyenje kulowetsa mnyamata aimable nikiza,reject ya mzuni.#BIG Bullets,ma favourites!!

  1. atumbuka ndi anthu ngati wina aliyense ena opephera ena ayi ena anzeru ena ayi koma zina ndizixelexa alomwe atani?ena ndi achipani ena ayi what makes u special for what ur not for whom ur?ignorat at its best

 30. ameneyo ndye mbuyache ,paja gwaladi ndi amene amaimba mmisonkhano yake kkkkk mwana mbuu make mbuu chitukuko chopanga ana #DPP

 31. Let chilungamo chioneka potengera ku mtsikanayo anali pa sukulu moti future yake yaonongeka.Ndipemphe a court kti chonde mkulu ameneyu alandire chilango chokwima kti anthu ena amaudindo atengele phunziro.Let me also ask amabungwe oyang’anira za maufulu achibadwidwe kti alowelerepo kmanso ndikanakonda kuti Wolemekezeka a Nduna aGender women n children affairs alowelelerepo poti nkhaniyi yachitika ku dera lawo kti chilungamo chioneke posatengera kti councilloryo ndiwa DPP.

  1. Ayahaya Ndinu Chisilu Mwamva? Yu Say As If Ulibe Mano Mkamwa. What If Mwanayo Akanapeleka Matenda Kwa Mwamunayo Mkanati Chayani? 16yrs Ndi Munthu Wakulu Ameneyo

  2. ZAKA 16 AAAAA NDIYE NKUMANAMA KUTI AGWILIRA? ZA CHAMBA ETI, MASIKU ANO TIMAPEZA TIANA TA ZAKA 11 TILI MMA BHARAMU, NDIYE MUZITI 16,.

  3. ZAKA 16 AAAAA NDIYE NKUMANAMA KUTI AGWILIRA? ZA CHAMBA ETI, MASIKU ANO TIMAPEZA TIANA TA ZAKA 11 TILI MMA BHARAMU, NDIYE MUZITI 16,.

 32. i cant comment since i dont know how the word rape has being used.could it be he raped her directly or they agreed but because she is not yet 18 yrs thats why it is called rape.

  1. Get out man,kumene kuja anthu amakwatila ali mafana nde 16 yea$ iz nt ajoke ,wadya money mwana ameneyo zitchito zake zachitila umboni basi,die had wa dpp nde ine wina afune asafune

  1. I Pray 4 u but “malawi24” cannot write anything abt malawi? there’s only bad news in malawi? i dnt comment badly at all

 33. @Noree, simwana uyu. Ndiwamkulu ameneneyu. Chomtengetsa mimbacho nde ukuluwo.
  Simunamve kuti mzimai wamng’ona kwambiri pa dziko lonse lapansi adabeleka Ali ndi zaka 5? Zinachitikatu izi Ku Peru.

  1. are trying to say ur not part of nation cause ur not chewa ?was the late dictactor kamuzu ngwazi from chewa tribe?what about the corupt,killing,selling of componies,bakili muluzi&thise one the cashgate lady JB is she also a chewa?hahaha okey alright

  1. kumamvetsetsa si alomwe omwe agwilira ntsikana koma amalawi muzayamba liti kuzindikila kuti ziko limakhala ndi anthu amitundu yosiyana kma onse ali adziki limozi God help us all

 34. Nowadays Life So Sad Story,Koma Munthuyu Ali Pali Pabanja Kapena Ayi Osangomuipitsira MBiri Munthu,Koma Anthuwa Anapanga Zangovuta Ndi Zaka Nanga Wakaziyo Adalora Bwanji Musayalutse,Nanga Wamunayo Mukamanga Asamale Mimbayo Ndani? Kkkkkk Very Bad News

  1. Hahahaha! bt azbambo enawa i dnt knw why there r alot of women that they cn use to slip wt bt they r jst destroyng tnegs future ufiti chan eishi ansantukwanise mmxuu!!

  2. Mesa Umawayikila Kumbuyo Se Koma Ine Ndiazibamdo Enawa kkkkkkkk Slip (Kugona)sivuto Akatopa Amayenera Kugona Koma Ka Act Apanga Ap Nkoyipa.

 35. 16 years ndiwodziwa bwino ntchito ameneyo. Pamene watengera mimba ndiye ndikugwilirila kumeneko ndi chibwezi anatu pano akufuna ndalama

 36. No body is above the law, let the truth flow like water

 37. And so he could not be arrested for being a DPP member?

 38. komandiyetu 16 years STD 6? Mpakedi kutenga mimba. Nanu a Councillor instead of encouraging education you are now in fore front impregnating them.

 39. Mukanakhala inu mukanatanl mabere anali atawawona mkuwasirira ku Mlankho wa Lomwe. i hate promotion of kuyendesa amsikana maliseche in the name of culture. why are mabugwe omenyere ufulu wa msikana in this mother Malawi

Comments are closed.