Sitikugulitsa Chilumba cha Likoma – Kamtukule
Nduna yoona zokopa alendo m'dziko muno a Vera Kamtukule yatsimikizira anthu okhala m'boma la Likoma kuti Chilumba cha Likoma sichikugulitsidwa. A Kamtukule anena izi pomwe unduna wawo umakumana ndi akulu akulu a m'boma la Likoma… ...