
Akuluakulu oyendetsa timu ya Wanderers awachotsa
Zatsimikizika kuti mamembala a bhodi ya timu ya mpira wa miyendo ya Mighty Mukuru Wanderers awachotsa. Wapampando wa timuyi a Thomson Mpinganjira atsimikiza za nkhaniyi. Mu chikalata chomwe wasayina ndi mtsogoleriyu chikufotoka kuti izi zadza… ...