![](https://malawi24.com/wp-content/uploads/2024/02/Arsenal-vs-Liverpool-Malawi-276x176.png)
MACRA yalamula mawailesi omwe amanenelera mpira wakunja kuti azikhala ndi chilolezo.
Bungwe la Malawi Communications Regulatory Authority (MACRA) yalamula nyumba zowulutsa mawu zomwe zimanenerera mpira pomwe zikuonera m'makanena akunja kapena a m'dziko muno kuti zikuyenera kupereka umboni oti zili ndi chilolezo chochita izi pasanathe masiku asanu… ...