Samalani uko! A ma truck aopseza kuti anyanyalanso ntchito
Palibe kopumira. Ngati a boma akuti mafuta akusowa chifukwa palibe ndalama za kunja, pompano aonjezekera kusowa chifukwa sipakhala owanyamula. Onse oyendetsa galimoto zikuluzikulu ati kuyambira pa 18 apa ayamba kunyanyala ntchito. Malinga ndi Malipoti, madalayivalawa… ...