Musazinyenge, Kwacha ilibe mphamvu olo pang’ono – nduna ya zachuma
Nduna yowona za chuma a Simplex Chithyola Banda yati anthu ku Malawi kuno asamazinyenge kuti Kwacha inali ndi mphamvu isanagwetsedwe posachedwapa popeza ndalamayi ilibe mphamvu olo pang’ono. A Chithyola amayankhula izi lero ku BICC ku… ...