Chili chonse chomwe mwamva chokhudza mkazanga ndibodza – Mlaka Maliro
M’modzi mwa oyimba odziwika bwino mdziko muno yemweso ndi m'busa, Mlaka Maliro, wati nkhani zomwe anthu akufalitsa zokhudza mkazi wake Bernadetta ndizabodza ndipo waopseza kuti athana ndi aliyese olimbana ndi mkazi wakeyo. Nkhaniyi ikubwera kutsatira… ...