A Malawi ambiri ndioyipa, mavutowo nchifukwa choti mumanyoza azitumiki a Mulungu – wakalipa Salanje
…wati kusolobana kwa zinthu vuto si atsogoleri M’busa wa mpingo wa God's Chapel a Hastings Salanje omwe akuti posachedwapa anabedwa ndi zigandanga zomwe zimafuna K2 biliyoni kuti amasulidwe, wati dziko la Malawi likudutsa m’mavuto adzaoneni… ...