Mnyamata wa zaka 18 waphedwa ku Balaka
Apolisi ku Balaka akusaka anthu amene anapha mnyamata wa zaka 18, Gift Libuda, yemwe anali mu folomu 3 pa sukulu ya St Charles Lwangwa Secondary. Malingana ndi mneneri wa Police m’bomali a Gladson M'bumpha, mnyamatayu… ...