Bata labwelera apolisi atawombela ndikupha mnyamata wa zaka 25 ku Mangochi
Bata tsopano labwelera pomwe apolisi ku dela la Makanjira m'boma la Mangochi awombela pa mimba ndi kupheratu Peter Davis wa zaka 25 lero kutsatira mkangano omwe unabuka pakati pawo m'bandakucha wa lero pa malo ena… ...