
Madera ena ku Nkhata-Bay mawayilesi samveka
Anthu okwana pafupifupi 7,200 okhala m'madera ena akumidzi m'boma la Nkhata-Bay alibe mwayi opeza mauthenga osiyanasiyana kudzera pa wailesi popeza mawayilesi samveka kumaderawa kuyambira nthawi ya atsamunda. Madera monga Thotho, Mangw'ina, Musinjiyiwi, Chisangawe, Masasa, Chitundu… ...