Ndalama zambiri ndimazipeza pa bizinezi ya iligo osati kuyimba – watelo Nepman
Anthu m’masamba anchezo akugawana kanema ya oyimba Napier ‘ Nepman’ Longwe yomwe anamasuka ndikuwulura kuti luso lothyakula nyimbo lomwe ali nalo silimubweretsera ndalama zoti angadyetse banja lake kuyelekeza ndi bizinezi ya iligo yomwe akuti amapanga.… ...