
Akanganya awili omwe akhala akuchita za umbanda ku Mulanje awanjata
Apolisi ku Mulanje anjata njonda ziwiri zomwe zakhala zikuzinganiziridwa kuti zakhala zikuchita za umbanda mbomali. Mneneri wa apolisi ku Mulanje a Innocent Moses watsimikiza za nkhaniyi ndipo iye wati njonda ziwiri mayina awo ndi a… ...