Ku-Li-mbuli?: Siine mbava, aphwanya poti n’nawaletsa kupha wakuba – walira mwini loji ku Mulanje
…wati katundu wa ndalama zoposa K700 miliyoni wawonongedwa A Edson Nachuma omwe ndi mwini wake wa malo ogona alendo omwe awotchedwa Lolemba a Edga's ku Limbuli m’boma la Mulanje, akanitsitsa mwantu wa galu kuti iwo… ...