
A Chakwera ati Chitani Ulimi musadzimve u Big
Mtsogoleri wa dziko lino, Lazarus Chakwera, walimbikitsa a Malawi onse kuti asangodalira ntchito za mu ofesi koma adzichitanso ulimi komanso kusatsa malonda a zolima ponena kuti dziko la Malawi liri ndi chuma chochuluka mu ulimi.… ...