Zativutanso ku Blantyre: Maminibasi sakuyenda, ogwila ntchito akunyanyala
Atadzadzidwa ndinkwiyo kamba kosagwirizana ndimalamulo omwe abweretsa apolisi apansewu, oyendetsa maminibasi mimzinda wa zamalonda wa Blantyre agwirizana kuti lero sagwira ntchito yawo yonyamula anthu mmisewu. Izi zikutsatira kubwera kwa malamulo atsopano omwe apolisi apansewu abweretsa… ...