
Bambo wadzipha ataba nkhuku
Bambo wa zaka 38 mu mzinda wa Lilongwe wadzipha podzimangilira ku denga la nyumba yake atazindikira kuti abale ake adziwa kuti iye anaba nkhuku ya m’bale wake. Watsimikiza za nkhaniyi ndi wachiwiri kwa ofalitsa nkhani… ...