Chiwamba ayipidwa ndi malipiro a pa Malawi
Mlakatuli Robert Chiwamba mu ndakatulo yake yomwe watulutsa kumene wadandaula ndi malipiliro omwe olemba ntchito akupatsa anthu a ntchito. Mu ndakatuloyi yomwe mutu wake ndi "Malipiro Pa Malawi Pano", Chiwamba wanena kuti ndalama zimene amalawi… ...