Chipani cha Kongeresi chagwidwa kuba
Awatsekela mipopi ku likulu la chipani chachikulu chotsutsa mdziko muno cha Kongeresi. Pa chintchito chotseka madzi kwa anthu ndi kampani zonse zakuba chomwe ayamba a bungwe loyang'anila za madzi mu mzinda wa Lilongwe, dzulo apezeka… ...