Chipani cha Kongeresi chagwidwa kuba

Malawi Congress Party MCP

Awatsekela mipopi ku likulu la chipani chachikulu chotsutsa mdziko muno cha Kongeresi.

Pa chintchito chotseka madzi kwa anthu ndi kampani zonse zakuba chomwe ayamba a bungwe loyang’anila za madzi mu mzinda wa Lilongwe, dzulo apezeka ali ku likulu la chipani cha Kongeresi.

Malawi Congress Party MCP
LWB yadula madzi ku likulu la Kongeresi.

Malinga ndi malipoti, a LWB amene amayang’anila za madzi mu mzinda wa Lilongwe adula madzi ku likulu la Kongeresi ati chifukwa chipanichi chimaba madzi.

Malipoti ati chipani cha Kongeresi chinali ndi ngongole ku bungweli yodutsa K6 miliyoni. A bungweli atapsa mtima ndi kudula madzi ku likulu la chipanili, a Kongeresi m’malo mosaka ndalama ndi kulipila anangoganiza zoyenda madulila. Ati analumikiza madzi mwa chinyengo.

Malinga ndi a LWB, ngongole imene a chipani cha Kongeresi alinayo ku bungweli tsopano ikudutsa K106 miliyoni kamba ka mkhalidwe okubawu.

Advertisement

268 Comments

 1. A malawi24 nanu ndimbuli antchito yanu kodi wakuba simumamuziwa kuti ndi chaponda ndiye mukulimbana ndi munthu woti sanalipile mabilu amadzi ndiye kuchita kuyima pachulu come 2019 vote ndiyomwe idzalankhule kuti kodi wakuba ndindani

 2. Amalawi tisataye nthawi mkumaganizabe za MCP,zipani zinazi zikungokwanilitsa Democracy koma osati kuzalamulilaso Malawi wathu uno ayi nanga tawonani kuba madzi eni eni nanga kulili ma Billion!!!!!!!!!!!!!!????

 3. anthu osaganiza inu mmalomoti muziona kuti likuyenda bwanji mukalimbana ndizamadzi kkkkkk koma amalawi tidatani kumalimbana ndizopanda pake tamanenani za 5000 ija osati zimenezo idzawinatu muwona

 4. NEVER NEVER NEVER! CHAKWERA 2019 NDEKUTI CHANI? TAMBALA WAKUDA NDEKUTI CHANI? a Malawi ozindikira tidadziwa kale ku Chakwera Have no leadership skills with his Jelousy, Rudness, Stigmatisation and Provocation which is in chakwera’s behaviour! why can I lose my vote to him? mr chakwera khalani pansi nanga tawonani zikuchitikazi mapeto ake 2019 muzidzangotakata wosadya muwona!

 5. aaaa!Inu a news 24apa sipomapala anthu mkamwa kut a mcp ndi adpp azikanganiranapo kenako inumukamawelenga ma coments awo muzingomaseka ai apa sipopangira zopusazoyi.Ngat mumachitakutumidwa tsikulina mulungu adzakuyankhulani.Kapena chodzatseketsa tsamba lanuli simudzachidziwa.

 6. a news 24 tiziti ndinu oima panokha kapena thandizolanu mumadalira chipani cholamula?Ngat ndichoncho kunalibwino tsamba lanuli muzilitcha kut dpp news24 osati malawi news 24.

 7. Do you believe there is a herbal doctor that cures HIV, I was positive for 9 years and Using ARVS , until I was cured completely by Dr. TIam, his herbal medicine is so strong and reliable. Call or WhatsApp him on : +2348037284837

 8. Mupite ku capital hill ma office aboma madzi anadula kalekale bwanji osakamba zimenezo? a malawi 24 akutumani? akuba simukuwaziwa monga? tamalembani zomveka.

 9. Zapang’ono Izi Koma Maize Gate Cashgate Mukungozikhalira Muzakhala Axulu Mukaxaulura Xa Maizegate Bwinobwino .Sindza Votatso

 10. Ngati simukudziwa inu atolankhani osadziwa ntchito yanu mudziwe izi ndipo mufufuze nkutipatsira zoonadi.ESCOM ili ndi ngongile ma BILLION amene akulephera kulipira ku WATER BOAD.WATER BOAD ali ndi ngongole ma BILLION amene akulembera kulipira ku ESCOM.Now pakati pa MCP ndi WATER BOAD wakuba ndi ndani???ESCOM ikulephera kupereka magetsi kwa nzika za dziko lino moti dziko likuluza ma BILLION daily chifukwa chakusowa kwamagetsi ndiye pamenepa WAKUBA ndi NDANI.

  MUSAMALOWETSE NDALE POLEMBA NKHANI NGATI MUKUFUNA KUKHALA ATOLANKHANI ABWINO kuti anthu ambiri adzikonda kuwerenga nkhani zanuzi

 11. Ati koma afuna dziko litukuke. Ngati akuba ali out of government azaba bwanji ali mu boma poti sitizawafusa. So pathetic

 12. Malawi 24 and Malawi voice you are both pieces of DPP shit…. your posts show who really you are….. make research before posting such no sense posts….. are idiots guys!!!

 13. Kodi anthu amene abadwa 1990 Ali ndizaka zingati ndiye mungauze zamavuto a MCP ngati akuwadziwa mwakumbutse njala ya 2001 amva chifukwa akuyidziwa inutu MCP ikulandani chifukwa simudziwa ndale yamadzi a company ndikuba ndalama zachimanga zoopsa ndiziti

 14. kuba ndi kulephera kulipira bill ndi zinthu zosiyana ndiye mukamapeleka ma comment yanuwo muziyamba mwaganiz chifukwa paja Charlity Begins At Home. SO BE WISE AND CLEVER. So 2019 is around corner.

 15. Kuba Ndi Kulephela Kupeleka Bill Ndi Zinthu Zosiyana. Ndiye Tikambnyozana Sgtimgadzatukuke. Chanzeru Ndichongoyang’na Kutsogolo Basi. Vote Ya Munthu Iri Numtima And It’s Only Almighty Knows Everything Ngati Amatha Kusintha What More This? Chachikulu Ndichalti Vote Ya Aliese Iri Mmtima Mwake Sitimaponyelana Vote.Inu Mukulalatanu Musatengeleko Mwayi Olalatilapo Ndhkumanyoza Atsogoleli Ayi Dzipatseni Ulemu. Choti Mudziwe Ndi Chakuti ~ chality Beggins At Home. So Be Wise Amd Clever.

 16. MCP ndiyowina-wina olo muiyipitsile mbiri yake mkungotaya nthawi yanu chitsanzo ndi MOCK ija yangochitika kumene (by-election) 6-1.

 17. Asaaa!Mmaso mwa ambuyanu mwagundika kunyoza MCP mwati aba madzi.Madzi ake ati osakanizirana ndi manyiwa? Koma #pamkunya panu mungakhale #mavuzi psyuuu! kufira ena #machende lelele nkumati aba.Nkhope zopindikazo ngati mphepetele mwa nyini tikuonani 2019

 18. Chokani alomwe inu mukhaula this tym ma propaganda muku user wa sakuthandiza olo ndi pangono how can you say stealing bill ya water board? Thats un internal matter between water board and MCP

 19. Iwe unganene kuti congress ayigwila kuba chifukwa cha bill yamadzi.Wakutumayo,apa Sitikuwonapo Chanzelutu Dpp Pamodzi Ndi Iwe Nose Paulendo 2019.Tatopa Nanu

 20. kuseka kapena kudula madzi is that an issue?apanga zomwe amapanga kwina kulikonse ngati mwalephera kulipira osati zokuba zanuzo iyayi,inunso olembanutu muzikhara ngati kumwamba mumakufuna mwamva

 21. Ndichifukwa chani mukulirabe mpaka pano? Mesakambakakuba komweko inu a DPP musamatubwe ndikumanyoza anzanu ice a Malawi ozindikila tonse tinadziwa kale zausilu mukunena apau ndani sakudziwa zoti inu a DPP munatapandalama zankhaninkhani zaboma mwazina siizi mukumapatsa a 24 ndicholinga choyipitsa chipani chathu.Chomwe timadziwa ife a MCP choyamba ndikukhulupilira Mulungu =( Ndipo chikhulupiliro tilinacho 2019 Malawi adzasangala muzonse kuthima kwa magetsi idzakhala 20%, osati 99% ilipanoyi ayi Bank not K2000 idzatha, Makoponi adzatha chifukwa ndinjira imodzi mwazomwe mulinazo zobera ndalama muboma . Mwachidule ndingoti chinthu chikawola chimatulutsa fungo lonunkha inutu mwanunkha ndizochita zanuzi . %

 22. Kuba ndi Bill,ndizosiyana, zina ngati sitidamve bwino ayi ndithu, ndibwino kukhala kaye. Mumaoneka ngati tinzeru tilimo koma a ayi ndakaika.

 23. Kodi kudula madzi chifukwa chosalipira ndikuba auzeni anthu zoona kodi mukuganiza kut or mutauza anthu zoipitsa MCP muona ngat anthu sadzaisankha tatopa ndi kulamulidwa ndi ma foreigner akwa America akungotibweretsera mavuto m’dziko muno apakira 2019 muona

 24. Umbuli omwe tili nawo a Malawi ndi chifukwa chake andalewa amangotibela ngongole ya madzi sizikugwirizana ndi kuba kwa mmboma aliyese amamudulila madza ngati asakulipila musatengelepo mwayi muziti MCP ndi yokuba nokha simungasiyanise kapena mumamwa mmijigo simuziwa kuti a water board amamudulira madzi munthu ngati asakulipils

 25. Ngati mumamva kuti kupusa ndie kumeneku. Kodi simukutha kusiyanitsa paka pa kusalipira ma-bill ndikuba eti. DPP ndiomwe imaba osati MCP mwamva.

 26. Boma likubela anthu pomwe chipani cha Congress chikubela boma. Pamenepa cha nzeru ndi chiti? Mbava zokhazokha kukumana kkkkkk

 27. Its only sewage water nothing to be proud of. Angokumba basi kuyika ma tank kenako kuyika ma solar panel escom out waterboard out basi zatha

  1. Pali njira ziwiri payipi ina ikulowa pa metre kuti inuyo mukamate/kutunga madzi pa metre ija imayenda imakupatsani manumber momwe mukugwiritsira ntchito madzi imaneyo bill ndiye kuba anapita panjira yachiwiri ija ndikukamangirira payipi tap yotungira madzi yotisikudutsa pa metre. Njira imeneyo anayipanga yotumidzira madziwo kwa adzanu amene akufunanso popi wamadzi ndiye iwo anagwiritsa ntchito paipi imene.

 28. Ngati sakuchita manyadzi kuba madzi nde kulili chuma cha boma azachiba bwanji? MCP 2019 palibe kulamilira Malawi akafuna akapange ziko lawo ndi anthu aku Nsanje district

  1. man muziganiz zamages tikuvesa nang za unima de whole malawi 4 thousand okh km ayamb kuteng a 2015 chonsech n 2017 anth omw akhoza bho 4rm 10 to 15 akupitilir 4 thousand kd malot ang’on wak ali kumudz uja atheka muzigani za ndale panj amapanga ndal kutereko zoduliran madz nd ndales open ur eyez

  2. and just coz i left xul i hav no any ideas for things concerning school, for is shirt happen and for electricity is all about time we have nuh electric but we have peace while in time of Bakili we had everything but non peace woman was taken private parts even other men blind people where thrown in river as a food for crocodile. …… wat do u think now gor for ma explanation???

  3. kkkkkkkkkk but mi never gonna stop until my people are free as it was in the beginning, so shall it be In the last days when the youths them a pree

  4. Man even xol.term.1 is nothing ..term 2 s nothng ..but final term is vry omptrt..mungoti pheee.DPP yamaliza udyo..nde xol sitengera za trm 1 or 2..koma final.trm..u.mst no dat bro..anthu akuona zakumamaliziro..osat kumayambiliro..kulibwino kuvetsa kuwawa munthu kuchiyambi..komaliza udzavetse kukoma..kut ufufute khaza zomwe wamupanga..aziiwale malingana ndizokoma zomwe ukupatsa..kodi.mukundiuza kut zomwe zikuchitikazi..ndiza bhoooo..nayosotu MCP..ndalama zake imapangira kumalawiko..nde ngat zu2 zikuvuta umati itani..but is better simaba..koma bill inachuluka..cz inali pa 6 million ..bwanji samadula monse munja..& zot kunali.bill ya 6 million sananene..akunena pano….zilingat kukuuza za mwana kut wabadwa..koma osakuuza ..za m’mimba..ndani angavomeleze kut mwanayo ndi wake pomwe sanauzidwe za m’mimba..khaniyi ndiyabodza.angofuna kupeza njira yogwetsela..MCP..nde tingolowa ndi yawo inja ..
   Ayambakale kunjejemera..
   MCP MORE FIRE

  5. Red Chiwanda akakhala mako si hule sibwedzi atamuonesa 90° bambo ako atatota muja, koma poti nao nyere inawabandula anachindidwaso nkukubereka iweyo and utati udzawafunse si mdala wako ekha anayamba kubodza a sasamba ena ndi ena adyamoso all of this = yo mother is also a bitch

  6. ur comments ar so childish and are not carryin any weight u need to grow up in mind..change dat jnr to snr..maybe u wil come wif gud comment

  7. even though mine childish, bt r elderly, but stupid still in yo mind, mphonongolo zili mmutu mwakomo thoo, bro ndiwe munthu opusa hvy

 29. Lazaro chakwera ndi Mgalatiya kuyamba ndi za uzimu kumalizira ndi za kuthupi ameneyu mulungu adzamukang’antha ankafunse Yona Mulungu kumutuma zina iye kukapanga zina!

 30. Iwe ndi mbuzi ndithu a misguided person sent to tarnish the image of MCP ulembensotu kuti MCP yalipira ma bills aja….ngati iwe amakutsekela madzi kunyumba kwako oti umalandila ndalama kuti ulembe nkhani zoipitsa ena nde kulibwanji chipani??? Ngati Escom imadula madzi kuma department aboma kulibwanji kuma premises achipani chotsutsa boma???

 31. Inu amalawi 24 tiudzeni bwino ndipo tisate chimodzi basi, kodi mwati a Mcp aba kapena kuti atsekeledwa mapaipi amadzi? Tsono kuba ndi kusekeledwa ndi zinthu zosiyana kwambiri kapena mwati atsekeledwa ku ndende chifukwa chokuba. Inetu amalawi 24 ndiinu anthu ophunzira kwambiri koma pofuna kuwaudza anthu mudzitha kulongosola momveka bwinobwino ndithu ndipo siizi mwakamba inu apazi ai. Tero ife timadalira inu kuti tidzitha kumamvako tinkhani tochiticha uko kumalawi komanso kudzungulira maiko anzanthu.

 32. Inensotu ndinaba madzi koma sadandigwire akadzandigwira mudzandilembenso. Mmene amabela a water board ma bill ngati akugawa ma sweet ndiye ungaleke kuwabera anachenjera ndi awa a Escom pobweretsa ma meter a pa pole mukanaona nyekhwe inunso mubweretse ma meter a madzi a pa pole ndiye tidzayimika manja mmwamba

 33. Malawi ino zovotera anthu I think zingotha..Tingogulitsa dzikoli basi kwa ena ake other wise tiIngoberana chonchi.Koma chifukwa cha umphawi ndi umbuli aliyense azavota thinking things will change..kaya ndangodutsamo ine

 34. Kodi ndalama zomwe chipanichi CHIMALANDIRA ku parliament zimagwira ntchito yanji mu nthawi ya a Tembo izi sizidachitikepo

 35. inu a malawi 24 musatinyasep mwav khaniy mwayamb dzana mpaka pano poti nd mcp nde kuilengeza 3 days nanga k57 bilion anaba apm nd nduna 7 bwaj simunalengez kwa masik atat kmaso mutaluz pa zisakho za 17 october munangot dwiii apa agalu inu isiyen mcp mixiii

 36. Htinali ndi udf magetsi sankavuta monyasa chonchi,, kubwera bingu magetsi kumavuta ngati ndi a koloboi,, kubwwra joice babda anali bhobho ngati ice cream kubwera awa mukuti a proffesor awa mmmm ai nabolaso bingu,, koma uyu nde ii ai educated fool weniweni. Dpp diseal petrol palibe, darkness pali ponse

 37. Mpangono apo za chaponda wa dpp zikungopondelezedwa., anakakhala wa opposition bwezi atamumanga no kumsiya,, dpp nde mbava zotheratu,, moti the same is happening even kwaiwowo , wanzelu aone kuti dpp chomwe amatha mkunyoza not kupanga chitukuko.. tatopa nazo stop talking nonsese pangani zanzeru.. tizayamike ndife not inu kumaziyamika zinthu zoti simukupanga., mkani munapanga ziwe la ngona kumsanje chifukwa mumazimva anzeru kwambili kuposa azinzanu but the trueth is munaphunzira but wisdom mulibe izo nde muziwe

 38. AAAA, MCP KUZOWELA KUMWA MADZI WA MZITHABWI NDI NG’OMBE, TIMAVUTIKA NTHAWI YA MCP NDI KOLELA WANTHU YAWA OSATIPATSA MADZI AUKHONDO.

  1. Kolela iwe ife timadwala nthawi ya mcp komati mmawa kukamacha wanthu 10, alikuchipatala ungandiuze chiyani za mcp iwe ine. ndinabadwa zaka 4 chilandilileni ufulu 1964. ndakula mu mcp.

  1. Iwe ndiye omvesa chisoni chifukwa suzindikira.Ndiliti chipani chakocho chinayamba kulephera??.Ukuganiza kuti amalawi angabwelere kulamulidwa ndi Mcp??.Uzaziona dikira

  1. every person has a right to express wishes. But it is MCP that will never more rule this nation. You will see when 2019 DPP bounces back

 39. agalu inu ndikilani 2019 galu wanuyu amp ndidzamugweba. Ndipo muzingopemphera kuti ndisadzakhele woyang’anila kudela kwathu ndizidzangopeleka kwa chakwera kaya chabwino chowonongeka muyindiwa mcp.

  1. olo mutani mutani ndalankhula ndalakhula iweyo lomwe galu wotha ntchito sungandipusitse. Mashamein ngati ndiwufiti inewo sungamake ndine mwala kumene wagenda subwerela, blessings ngakhale itakhala vimbuza party sindingadandawule. Awunyolo mufuna muwoneke wozindikila koma ulindikatulutulu mutumwako undisamale ndiwe chigendele. Uyo wapsantima undipeze inbox sindilimbawma ndiwana osapola pamchombo. Anyani ndipantundu wanu wanu wose

 40. kkkkkkkkk chipani ichi chinayamba kuba kalekale kodi sichinasiyebe eeeerr ndimawona ngati m’mene Ali ndi pastor zithu zisithatu koma wachake ndi wachake basi

 41. …basi ndimafuna nditadzavotera #MCP mu 2019 ndasintha maganizo..M’busayu Ndi mbava ndaona..ngati akuba Ali panja..akalowa ??

 42. mcp zoti izalamulira ingoiwala chifukwa anthu ambiri akuziwa mbiri ya mcp.komanso anthu amene amaikonda anamwalira ndi ukalamba.asala ndi achinyamata ndiye wachinyamata ozisata sangabetse vote yake kuvotera lazaro chakwera.

  1. munthu agogo ako chifukwa cha umbuli anavotera mcp.iweyo waphunzira bobo mpaka ku univesity and ukuzindikira ukufuna ukhalebe mbuli kukavotera mcp.mcp chipani cha nkhalamba ndi anthu osazindikira ufulu wawo

  2. Nzoona ine poti ndimasapota Mbava za Chimanga, ndizavotela DPP basi! Nzoona munthu openga ungavotere MCP? Koma Mbava ndi zolephera kupeleka magetsi ndi madzi. Nkhalamba pa mpando kakaka koma mwana alipo, Eeeeish!!

  3. Wana aise BIGMAN, MCP is the only government after 2019. Keep on being in denial while MCP is going into government kuzakulamliranso iweyooo

  4. part of dicampaining mcp mukunama panyapanu makape,,,,after o water iz lyf,,,,do you mean chakwela madziwo amanyamulila kunyumba kwao?

  5. Solo mungatanimutani MCP inasintha basi ndipo tilipabuyopake basi mulila simunati dzana inali 5-1 osaonabe patsogolo m’bale kkkkkkkk

  6. dpp is the only regine that had shown progress as far as development is concerned.it had also managed food security.chimanga sichikusowa komanso sichikudula.during udf regime chimanga chimachita kusowa anthu kumakagona ku admarc.

  7. Umbuli osadziwa nawo food securitywu bakhala nawoni ku evil dpp yanuyo, real Malawians are going for Chakwera not dull dpp leaders omwe atalemba JC lero sangakhoze, zianthu zakatangale, zokanika kuganiza, nepotistic, regionalistic and poor minded, dpp is a walking devil, okhawo akudya cashgate ndiwomwe mukuwaikira kumbuyo a satana anuwo a dpp

  8. Why why kulimbana ndi anthu osakonda dziko lawo? Alekeni Malawi ndi wa Malawi ndipo eniakewo adagwirizana kuti after 5yrs tizivota,2019 tizavota.Chodziwika ndi chakuti DPP ya laphela,or ayambe mabodza amadzi sangagwilizane ndi njerwa za moto tikuphulazi aaaaaaaa!

  9. Byelection inakutcholani bwani sagwada? MCP yakutsekulitsani mmimba mwakamwazi ndiye liwiro mwayambalo mugwanalo mdothi.

  10. Hahahahaha..uku nde timati kulumidwa ndi chickeni..dog alipo..mwaona kut zakukanikani ku ndale mwat mubwele.ndi imeni..hahahaha..malawi aliyese akudziwa kale kut iyo..ndi sanje..chabe..tingati inuyo a DPP.malipira ma bill aliwose..tionelana 2019..mungot pheee.& tikatenga ..tatengela2 ..4 gud..ana mwaonjezamo mu boma.muona ngat mwa mbuyanu..nyamanu…

  11. Awoso at dzina lawo.a Big man wankulu..alibe kalikose komwe angaloze kut DPP yapangira ..avutika ..or wantambala..nde mkumati..MCP..singalamulire..mwabwela lit inuu.pa,social netwrk..kut mudzitha mau chonchi..only chichewa news ..but english news..ngooooo..no coment zakuphwekerani etttt..pachi demeti..

  12. you can say whatever you like but you can not ignore the fact that dpp will continue to rule up to 2029.becz i cannot see any political party that can lead malawi to canaan than dpp.mcp zawo zinada kale sizingayele

  13. iwe ukuti chan ..umbuz nde umenewo cant u see by your asaaleted eyes tht the world is passing through avilie stage nde dpp ikawine chamba basi..mwinatu phone ukulogerayo ndiyobwereka cz munthu wanzeru zake sangalembe lololouticated shit

  14. malawians we had a long outstanding syndrome whereby we throw every mess at president even if its none of his fault.when escom is not performing we blame it at peter.is peter a prof of engineering? no he is prof of law.when 1billion is frauded at MOH allawance scam you blame it at president. is peter a MOH? no he is a head of state.a malawi tinakhala bwanji

  15. NEVER NEVER NEVER AMADULA MADZI NDEKUTI CHANI? MCP 2019 NDEKUTI CHANI? a Malawi tonse ozindikira tawona kale kuti chakwera Have No Leadership Skills With His Jelousy,Stigmatisation and Provocation which is in chakwera’s behaviour kkkkk?

 43. Osati chagwidwa kuba paja mudakulira ku midzi eti? Imene ikufunika kulipila ndi Bill ya madzi osati zachifine walemba apazi

  1. Iweyo udabadwila kumudzi udakulira kusamba madzi akumtsinje mchifukwa chake nkhani ngati imeneyi sungayivetse ndizofunika amtown izi

  2. Ndiye nkhani ya umbavayo eni ake akatakwetu ali ku Dpp omwe asaukitsa dziko lino hahahahaha mpak pano magetsi ndi awa zikuwakanika kupanga fix ndalama alibe adaba zochuluka

  3. Kaliba ofatsa tamvera kuno, usamuwuze nzako kuti adabadwira kumudzi, kapena kuti nkhani imeneyi sangaimvetse. Iweyo poti waimvetsa, uwawuze a Malawi24 kuti asinthe malembedwe amutu wankhaniyi. Ndiye iweyo, uwawe malembedwe ena kuti alembetso mau (akubawo) asamvekemo. Chifukwa inu, mukudana ndi chilungamo chake chankhaniyi.

  4. @Kaliba a LWB kuzadula madzi chifukwa cha bill then a MCP malo mokalipira bill akuzilumikizira madzi okha ndiye mukuti umenewo si umbava?muwombera mfiti mmanja mpaka liti?kukulira ku mudzi si kupanda nzeru ai.

  5. @Benson Makhunya, iweyo ndiwe kape of the year ineyo ukundidziwa kuti ndine ndani? Ndipo ndimapanga zotani? Ukudziwa komwe ndinabadwila? Apatu ine ndapeleka maganizo anga okha ndiye ndikudabwa kuti enanu mulikufuna kukhala ochenjela pamene ndinu makape ine ndakupemphani kuika comment yanu ngati apa? Uku ndikusaupeza mtima pa zomwe walemba wina

  6. Kumaupeza mtima pa zomwe enafe talemba atleast zikhoza kukuthandizani, osati kukamwa pambanuke ngati mwana wa Timba! iweyo ukutani kulemba zako?

  7. Iweyo wakuuza ndi ndani kuti analumikiza madzi eni ake osadziwa? Iti ndi timaganizo tainu anthu otsatila Dpp osati momwe eni office ya Mcp akudziwila pa za nkhaniyi

 44. zikuwonetseratu kuti anthu awa ndi oyipa,… ndipo ndneneretu iwe chakwera pamoz ndi MCP yakoyo vote yanga simuzayiona 2019!!!!! Go to hell!!!!!!!

  1. Komaso nyapapi wako opanda mano wankhope yonyasa pama president ose dziko lonse lapasi pitala dziko lino lamukanika ndiye bolaso joyce Banda mchifukwa chani akukanika kupanga fix vuto la magetsi? Ndiye oteleyu mkumati professor kkkkkk koma Malawi sadzatukukadi ndithu coz anthu adaonjeza kuchepa nzelu akungowombela mmanja zili zonse

  2. ngakhele utakhala tilipo ife tikavota uzingopemphera kuti patsili ndisadzakhele oyang’anila zisankho ndipo galu wako uja amp adzakhaula ndipo nthawi yowelengaso ndizidzangopatsa chakwera.

  3. Munthu wa mtundu wanji okuba ali kunja kwa Boma?????? Abusa amenewo???? ndye or kugunata kwake kwa mtundu wanji kukavotera bakha ngati amene uja????

  4. Ndiye apa zangowonetseratu, inu ndipamene simumafuna kuvomereza zotsatira zachisankho chifukwa mumagwiritsa ntchito njira zobera mavoti.Tangoganiza m’mene walankuliramu, upezeke kuti wabera komanso ndikuluza mungavomereze kuti anzanu awina? Mankhalidwe amenewo ndi aja, umamva kuti chipani chakuti chapita ku court chifukwa chamankhalidwe ngati akowo.

  5. And a mcp sanabe koma kuli bill yoti apereke,, not zakubazo ai,, iwe monga mwanzeru zako ngatii achule akowo ali achilungamo report ya company ya ku germany ija imafufuza za cashgate inasowera kuti,, nanga isa njaunju anafa ndichani? munthu otetezedwa ngati uja kupezeka ataphedwa mpaka pano okuphao sakupezeka what do yu think.. anapha ndiowow nde sangaziulure okha.. watchout bro,, ichi mchipani choona chilitengera dziko kuumphawi onunkha uja,, kubwera wina uzaona zinthu zizayenda bwino

  6. Peter eeeeeee! Wakwanilitsa maloto ake but kukadapanda kuchepetsedwa nthawi yake akadatitha tonse,Malawi uja wafika poipa koopsa.Chipatala mankhwala kulibe,Magetsi tisanene,kumwetsa anthu madzi akusuweji aaaaaaa! Mchipululu simofela

  7. Dpp my foot ,,, my vote goes to chakwera ,,, or atati tivote kutulo,,sindingaphonye ,,,, Chakwera chakwera chakwera basi,,,,,,

  8. zikuchita kuonekelatu kt mbuzi imeneyi siingatengeso boma kuvutika tavutika kokwana kma kungolowa chakwara imene ndimasapota ineyo boma lidzayenda bwino osati zimene akupanga afinyezi zatikwa.

Comments are closed.