Dan - Lu

Dan Lu watulutsidwa pa belo

Woyimba Dan Lu yemwe anawona ngati ku maloto pomwe anathilidwa dzingwe Lachiwiri munzinda wa Lilongwe, tsopano watulutsidwa pa belo. Posatengera kugundika kwake potulutsa nyimbo zochemelera boma la MCP, apolisi adanjata Dan Lu pomuganizira kuti wavulaza… ...