Mlonda wanjatidwa ataba zida zoyimbira m’tchalitchi chomwe amalondera
A polisi munzinda wa Lilongwe akusunga mchitokosi mlonda wa zaka 44 wa mpingo wa Time of God pomuganizira kuti anathyola kachisicho ndi kuba zida zoyimbira za ndalama zoposa K3.5 miliyoni. Wofalitsa nkhani za polisi ya… ...